UYU WATHILA FIRE ONSE A MCP PA IMFA YA CHILIMA AKUTI AWASINJA AKAPITA KU NTCHEU

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 5 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 33

  • @ahmedsema1880
    @ahmedsema1880 หลายเดือนก่อน +1

    Nthira 🔥🔥🔥🔥

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama หลายเดือนก่อน +1

    Chilima dzofuna ndamene anapangitsa kuti amalawi tivutike chochi paka kupangitsa kut tivote kawili dpp itawina kale lelo ndizi menedzo wafa yekha Matama dpp 2025 boma basi

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 หลายเดือนก่อน +2

    Good

  • @HestingsLufasi
    @HestingsLufasi หลายเดือนก่อน +1

    Palibe chokuchitsela pa group sunalakwe auze ndi mfiti a MCP

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o หลายเดือนก่อน

    Ngakhale ku Salima azasamale pamayankhulidwe ao pa msonkhano wao. Akamadzanyiza zipani zina ndithu adzachoka ndi minyala.

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika หลายเดือนก่อน

    Zoonadi bro mudziwavere chisoni azanuwa km chingauluke bwanj chizatera

  • @AlexPhiri-in1re
    @AlexPhiri-in1re หลายเดือนก่อน +1

    Zoonadi m'bale ❤

  • @user-rz9rm4cb8x
    @user-rz9rm4cb8x หลายเดือนก่อน

    Ndipo asilikali ena amakhala kunkhalango konkuja kulondela nkhalango

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q หลายเดือนก่อน +1

    Iweyo nde wandilankhulira moona zeni zeni ndithu ife atitseka pakamwa

  • @peterkakhome6976
    @peterkakhome6976 หลายเดือนก่อน

    MCP inapha chilima,

  • @user-bw2cv9sd7x
    @user-bw2cv9sd7x หลายเดือนก่อน

    mcp ikafika ku tcheu isinjidwe

  • @KestonNGUBO
    @KestonNGUBO หลายเดือนก่อน

    Auze iwe uli bho

  • @katalamajames4947
    @katalamajames4947 หลายเดือนก่อน

    ndiposo mumuuze adiminiyo machende ake pamtumbo pamake

  • @EsterKapungwa
    @EsterKapungwa หลายเดือนก่อน

    Kma nde wayakhula bwino bro mcp yakupha

  • @JANETANDAUDE
    @JANETANDAUDE หลายเดือนก่อน

    komatu mukavote chaka chamawa osamangotokota mumavota FB kkkkkk

  • @mrperfectmw
    @mrperfectmw หลายเดือนก่อน +1

    Zoona zimenezo

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b หลายเดือนก่อน

    Zowona Chilima anachita kuphedwa di zinawonekeratu tsiku lomwe lija

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b หลายเดือนก่อน

    Zimakhala zophweka zikakhala kwa munthu wina amene akunena kuti akatorika ndi ndale, aganize kuti kodi zimene anaziwona Chilima zija akanakhala kuti ndi Bambo wawo aphedwa chonchija akanabva bwanji

  • @Yussuf-b1p
    @Yussuf-b1p หลายเดือนก่อน +1

    Mukunena zoona mani

  • @MasterHeadson-ki7ji
    @MasterHeadson-ki7ji หลายเดือนก่อน +1

    📌

  • @chrisgremu740
    @chrisgremu740 หลายเดือนก่อน

    Machende ake uyuuu

    • @MosesNjanje
      @MosesNjanje หลายเดือนก่อน

      Inumso anuwo bgy ka times 10

  • @JordanGoliath-q5x
    @JordanGoliath-q5x หลายเดือนก่อน

    Opusa iwe mot uzikalima kwanu ukusowa zochita palibe chomwe ungapeze uzingotaya nthawi kape

    • @UseniMailosi
      @UseniMailosi หลายเดือนก่อน

      Chikangawa party

    • @MosesNjanje
      @MosesNjanje หลายเดือนก่อน

      Ukanankhara osamala nthaw sukanaika comment koma zuonetsa kut nawemso uli mgulu lotaya nthaw

  • @UsenLashid
    @UsenLashid หลายเดือนก่อน

    Chakwela ndi nduna zake anampha Chilima Wina afune asafune

  • @ChancyJere-pz5sv
    @ChancyJere-pz5sv หลายเดือนก่อน

    Kkk asijidwe amene awa 2025 kukhala kusijina wosati masewelo

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt หลายเดือนก่อน

    Mwalankhula bwino big.

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 หลายเดือนก่อน

    Lipoti loveka bwino chakwela anapha chilima.

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y หลายเดือนก่อน

    Zoona Fadaaaa 😢😢

  • @user-gg9hw4oj2v
    @user-gg9hw4oj2v หลายเดือนก่อน

    🔥🔥💪💪

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no หลายเดือนก่อน

    Mukunena zona mn

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q หลายเดือนก่อน

    😭😭