Uyuyu ndi chitsiru. Pali katangale amene akuchitika ku police; immigration; court; etc. Ndizimene amayenera kulimbana nazo osati ma nurses ndi ma dictors yet iyeyo sanagwirepo ntchito ku chipatala. Kandodo anasamutsa onse a kumwera muzipatala za ku Lilongwe. Imeneyo ndi nepotism. Amayenera kuthana ndi vuto limenelo osati kukalipira dokotala ayi.
Thanks mr vice president
Kuzatiyendera kuchikwawa hospital thanks very march
Mr president u done the best way bt it's part of the government to get the Doner minister of finance must find the way to get money for hospitals
Mmmmm
Mr vice president please yambsnipo nkhani ya ma reform Idea ya Chilima must come out