Achinyamata afika potopa kuti topi ndi MCP. Akuti inu mumachosa utsiku ife utsana.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 26

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz หลายเดือนก่อน +4

    Amalawi akhala ngati Kenya very soon suree

  • @burtonjere-wn3qu
    @burtonjere-wn3qu หลายเดือนก่อน +4

    🔥 🔥 🔥...OSAOPAAAAA , OSATOPAAAA ,OSAFOOKAAA

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q หลายเดือนก่อน

    😂😂 tingogawanapo ma president kumweraakhare niwawo pakati akhareso niwawo anthu akumupotoinu mumasaridwa nanuso mukhare ni president wanu

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk หลายเดือนก่อน +1

    Osawopa osafooka osatopa ndipo sanati tizichosadi choncho

  • @adrianobrigida3402
    @adrianobrigida3402 หลายเดือนก่อน +2

    Mcp must go

  • @SaidDayton
    @SaidDayton หลายเดือนก่อน +2

    You must tell themselves ..we are tired with that MCP😮

  • @user-ev4or2kg4z
    @user-ev4or2kg4z หลายเดือนก่อน +1

    Boma la tonse lidatha pamene a utm atuluka choncho panopa paline boma lolamula

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w หลายเดือนก่อน +1

    Mwachita bwinooooooo!

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi หลายเดือนก่อน +1

    Osaopa fisi ameneyu watikwanah

  • @user-ne7rn4ki3c
    @user-ne7rn4ki3c หลายเดือนก่อน

    Zaka 4 ngati 31 zomwe dictator kamuzu adalamulilira meankhanza tatopa nayo mcp ipite

  • @alexanderlipenga1330
    @alexanderlipenga1330 หลายเดือนก่อน

    Nde mwat achinyamata akuonetsa kutopa kwao pochotsa mbendera. Zopanda pake izi tatiyeni tikamang'ale ku parliament atisinthire presidential age bill itsike nafe tizipikitsana nawo. Osati kukhalira kachoseni mbendera, zipakeni pent, mukhale a molaro, tengani zikwanje mukasokoneze msonkhano wa awo, tiyeni kunseu kutupisa mmatumba activist. No more time to be manipulated by these old guards.

  • @imraanJafal
    @imraanJafal หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Yah kuipasa moto

  • @StellahMsodoka
    @StellahMsodoka หลายเดือนก่อน +2

    Chilakolako Cha kuba

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk หลายเดือนก่อน +2

    Chotsani ndithu, we are tired

  • @THOCCOChimbali
    @THOCCOChimbali หลายเดือนก่อน

    Gule kwawo 😂😂😂

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx หลายเดือนก่อน +1

    Amenewa akufuna mademo anyoooo.
    Akudziona ngati dzikoli ndilawo

    • @NancyNicolas-lj6jn
      @NancyNicolas-lj6jn หลายเดือนก่อน +1

      Kkkķkk. Adziwe kt pano malawi sikugawa mpunga ationelela kwakwana agalu amenewa achina chakwela

    • @alexanderlipenga1330
      @alexanderlipenga1330 หลายเดือนก่อน

      Ma demo anyoo ukuba zinthu ayiii
      Tsiku lina tizangosiya osalandira lisiti pogula katundu for some days. *No tax demos* muzaone😂
      If you see things carefully our so called omenyera ufulu they do pa zinthu zomwe zili funded not that matters to our country. Moti apapa kuchosa mbendera kuli ndi impact yanji as if yasitsa msonkho

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga หลายเดือนก่อน

    🔥🔥🔥🔥❤️

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน +1

    MCP ndi ufiti weniweni. Zochitika za MCP zilingati nyau. Let me explain why. Chinyau chimayitanitsa ndalama koma ndala zija iweyo opereka supindula nazo. Momwemo MCP IKUYITANITSA TOLLGATE KOMA MISEWU YAKE YONYANSA.

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa หลายเดือนก่อน +1

    Osaopa tri nanu

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba หลายเดือนก่อน

    Mwapinduranji umphawi ulipobe

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z หลายเดือนก่อน +2

    NO PAIN NO GAIN BOYS

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂lyedzekeni lmeneyo kkkkkkk

  • @EdwardKachinjika-c8q
    @EdwardKachinjika-c8q หลายเดือนก่อน

    Mwapinduliranji?

  • @HamzaAyame-ch3et
    @HamzaAyame-ch3et หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂