😅😅😅😅😅 amati tambwali sametedwa na apa apa pokha uyu #GILING'ANDE nde wayamba kumetedwa, EPISODE iyi kuyiwonela ndiyimila Kaye pompa apa pomwe AMFUMUKAZI Akuti ukandipeza kunyumbapa sindiyipitiliza kwinako ayi until next week kuti ndizayilumikize bhobho yonse coz na apapa apa GILING'ANDE nde wayamba kuyandama MMADZI muja, #ITS A CHE MALILO'S TIME NOW.😅😅😂😂 Until next week Wednesday again,,basi ine ndili pano phaa waiting room 😅😅😅😂😂😂 more 🔥🔥🇲🇼🇲🇼.
Maliro mabodza iwe iiiih kkkkk
Ineyo Farai nde amandisangalasa ❤❤❤❤
Big up fumukazi wello done more fire.
Next ....Farai on Fireee!!! hahahahaha koma yaaa!!!
Kodi mfumukazi anasiya kukamba milandu 😂😂 tayisowa washout
Kkkkkkk koma abale ntchito ndiyosayamba giring'ande zako zada amene wadesa ndi padera ndi maliro kodi nanu mfumu nkadzi nthawi zonse mumangokhalira woli woli kumachita ndiinu otengeredwa chisanzo ganidzanipo bwino banja silimatha kamodzi ndi kamodzi pepani tikhululukireni .❤❤❤❤
Banja la apadera labebatu🎉🎉🎉
Kuli love to love lero
Uximu ulink admit 😂😂😂😂😂
Kkkkkk tourism, 🤣🤣🤣🤣 kumeneko kulemekeza ntchito ya uhule.😂😂😂😂
Kkkkkk amaliro nvomerezani zakuvutani nafunea safuna mamuna wa ulesi iiiiyah chibwana kkkk😂😂
Ukukoma zedi❤❤❤❤padera nonse koma guys mubeba
Maboza akumowa😂😂😂😂😂
Nthawi ikumachepa,,komaso mukumaitulusa mochedwa,
😂😂😂 ati mwaipeza itathamo
❤❤❤❤ mfumukaz wavuta kuno
Banja la apadela lero lakomatu
Ine kusirila ndithu
Wawa Wawa makonsana kumalawi kwacha kkkkk giling,Ande
PADERA, KATUNDU WAMAPULANI ONYEZIMIRA. CANT WAIT KUONA DC, GILING'ANDE MR SHOPRITE AKUKWATIRANA NDI NAGAMA, LIKHOZA KUKHALA BANJA LACHITSANZO HEVE.
I'm watching from Cape town
Marilo ni zobakwambiri
Giling'ande akut kunjan wena😂😂😂😂😂😂haibo😂😂😂😂😂😂😂uyabheda wena ngempela
Tourism😂😂😂😂ngatibe zofanana ndi uhule😂
Akutitu munawapasa zungulira nkhonde
Kkkkkkkk apadera mwayamba maboza sopano ndi amariro
Mfumukadzi mwalakwitsa 😢shoprite amakukondani komaso mumakhalana😂😂 next
Giling’ande wavala Gucci 😂😂😂
Kkkkkkkkkkk
Koma ambale padela anakoza
😂😂😂wabwera giling'ande mumatisangalasa komaso kutiphunzisa keep this good work am proud of u gyz
Nice work
Maliro waonomga banja lanzako akut tifanane
Maliro upole moto, wasokoneza banja la mfumukazi
Anamoyo mwayakatu kodi bwanji 😂😂😂😂😂apamdera mwayamba nanu mabodza kkkkkkkkk
Koma nafuneya watha mawu
Mmakwana makosana
ndangonvapo wa tourism 😂😂😂 namoyo umulandre Faraih ndi makofi azwe kut m'mudzimo mwa mfumukaz
Khunjani wena🤣🤣🤣🤣
Am Watching Capetown but too nice gyz
Mr ShopRite amatha kma 😂😂
Padera umakwana
Mfumu kazi kususuka awa😂😂😂😂
😂😂😂 Tourism entertainment eti
Tingatibe Za Uhure Comco kkkkkkk Mr. DC
Uzibwelabwela padera
Mr padela banja lakoma koma Eeeeeèe minthulo😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉
Maliro anakonza , kulankhula ngt zowona
Komatu Maliro wamuyambitsira mavuto Giling'ande.
Inuyo Guys pitirizani mukuitha kwambiri kwake.
Apadera ni 🔥😂
Fumukazi upezeni tima
Apadera ndi maliro azibambo amabonyo
Yesu WA Ku Nazareth 😂😂😂
Komatu Giling,ande ukhalike wati Tourism entertainment 😂😂😂
Mwati apadera ndachani kma😂😂😂😂😂 🔥🔥🔥
Koma padela iiiiiiiii
Padela iweyo ndi problem, munthu wosaveseseka and pano ndiwe Mr difficult.😂😂😂😂😂 Umayitha m'bale umayipasa Moto .
Mfumukazi ❤❤😂😂
Fumukazi wakumananazo
Mfukazi kuthesa banja choncho😂😂😂
Maliro akuti uzimu uli admit 😂😂😂😂
Padela amatha😅😅
Malilo ndi padela, ulemu wanu 🔥
Koma padera u made my day 😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 kom mpka ma push ups
Maliro wabhudula mpunga wagulu😂
Km apadela banjali ikanakhala lenileni makhala n madam anu amakumvelani
Apa ex wa fumu khan zake 🤣🤣🤣😂😂
Padera moto moto umatha aise
koma apadela umbombo😂😂😂
Nice Job
😂😂😂😂😂😂
Mavuto sakhala a munthu modzi maliro sukunama kkkk
Maliro wamfikitsa bwino Giring'ande
Yes
Haibo kkkkkkkkkk
Koma anthunu, you are the best in Malawi comedy.
Kkkkkkkkk padela ndikatundu
Guys You're 😂 best ❤❤
Assa amaliroKkk😂😂😂😂
So NYC🎉🎉😂😂😂
Mumakwana ndimakukondani guyz
PADERA ana alikut kod
Kkk Koma padela
Padera😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma padera giling'ande ali kut Top 2 kkkk
Koma inuyo aPadela inuyo!
ntchito yabwino guys
Maliro walipalapasapo banja lija ndithu mothandizana ndi padela
Maliro kupatsa Moto🤣
Maliro wasokoneza banja la eni eish
Me waiting next
😅😅😅😅😅 amati tambwali sametedwa na apa apa pokha uyu #GILING'ANDE nde wayamba kumetedwa,
EPISODE iyi kuyiwonela ndiyimila Kaye pompa apa pomwe AMFUMUKAZI Akuti ukandipeza kunyumbapa sindiyipitiliza kwinako ayi until next week kuti ndizayilumikize bhobho yonse coz na apapa apa GILING'ANDE nde wayamba kuyandama MMADZI muja,
#ITS A CHE MALILO'S TIME NOW.😅😅😂😂
Until next week Wednesday again,,basi ine ndili pano phaa waiting room 😅😅😅😂😂😂 more 🔥🔥🇲🇼🇲🇼.
wathetsa banja maliro😂😂😂😂
Zofanana ndi uhule kapena uhule kumene? Tourism entertainment!
Nice move
Anthu aumu eeee amatha
Tourism intertinement
Thanks mama
I love you guys ❤🎉🎉
❤❤❤❤❤❤
Tourism kodi
Kkkkkk haibooo