Ndaika mavela program ya nkhanga zaona ndikumwa ka castle lite wanga ndikangova dzina LA Richard chimwndo ndimasaza munthu oipa kwambiri PA ntumbo pamako Richard chimwendo banda
IWEYO UKUTI NTANYIWA NDI GALU WA CHIWEWE IWEYO NDIYE GULUKUNYINDA NYANI WENIWENI, NGATI IMAKUBOWA LIMPOPO USAMAMBERE CHIFUKWA RADIO IYI NDU YA ANTHU AMENE AMAFUNIRA DZIKO ZABWINO NOTI IWEYO WA CHIKANGAWA PARTY MFITI YAKUDYA MALILO
Openga ndi ofunika kukumana ndi mizimu ya anthu 9 ndi iweyo amene ukunena za chifunga chomwe ku alibe mukanthidwa posachedwapa mwangoti poti okufa salankhula awatu alankhula mwatisala mu mbatata inu
Teach them Akuoangati anafikapo.mwabisala mmadzi msana waoneka am much stick on those watch men kaa nku Tz diko God shall guide u to Meet the guy. No fear
Iwe ndiwe wabodza lochititsa manyazi tsiku limenelija Chifunga chinachita mpaka chigawo cha pakati komanso dzuwa silinawoneke tsiku lonse anthu onse amakuvera iwe mitu yawo simagwira bwino akufunika chithandizo mwa changu
Man of the moment
May almighty protect you mr comrade
Yomweyo Ntanyiwa, kutchaya kugwesa. Iwe unabwera kuzakhara for sure. Chillungamo chidziwike. Osamangophana ngat ngumbi iyaaa,
Ndaika mavela program ya nkhanga zaona ndikumwa ka castle lite wanga ndikangova dzina LA Richard chimwndo ndimasaza munthu oipa kwambiri PA ntumbo pamako Richard chimwendo banda
Mtanyiwa iweyo unabwera kudzakhazikika🎉🎉🎉🎉🎉
a Ntanyiwa good bless you chifukwa cha chulungamo chimene matuuza amalawi wonderful ntanyiwa
More fire comrade time will tell God be with us.
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa
Dr ntanyiwa mzimva kukoma kwambiri kumenemuloko timakunyadilani ambuya apitilize kupasani zisisi zochuluka kut amalawi tipeze ntendele
Nafeso Timakunyadilan biggy
Indee akachama chumewo angwekumene MULUNGU amakonda aliyetse yesu sachokera khomo lamawo
WELL Come Mr ntanyiwa
God bless mr Ntanyiwa 🙏🙏🙏
Actor of the year...umakwana bro,,,,,ukanawauzas achna suleman aja aptes ku majetek ky
Kunali a Watson Deleza, mayi Chilongozi, John Tembo lero ali kuti, think about this, mutha posachedwa, ndi ana omwe adzakulavulirani
❤❤❤❤ Mr Mtanyiwa
more fireeeeeeeee ndi Comrade Ntanyiwa
More faya my comrade mtanyiwa may lord give you long life n health life muomboli wa malawi
IWEYO UKUTI NTANYIWA NDI GALU WA CHIWEWE IWEYO NDIYE GULUKUNYINDA NYANI WENIWENI, NGATI IMAKUBOWA LIMPOPO USAMAMBERE CHIFUKWA RADIO IYI NDU YA ANTHU AMENE AMAFUNIRA DZIKO ZABWINO NOTI IWEYO WA CHIKANGAWA PARTY MFITI YAKUDYA MALILO
Alibe chisoni anthu amenewa
Mwadzuka bwanjii antanyiwaaa timakunyadilanii
Ifeso timakunyadilan mbali yakuno
Mary Chilima ngakhale atapeza mwamuna wina olemera kwambiri koma mwamuna wache Saulosi Chilima sazamuiwala
Yense akunyonza ntanyiwa anapha nao chilima afiti opephera
Iwe wabwera
Mr mtanyiwa ulemu wanu bwana tankufani mamawa unno
Aziphana okha okha basi akuti menyela nkhondo tilichete.
ine chete payadi ndikunjoya LIMPOPO CD Ntanyiwa moto kuti buuuuuuuuu
Mumaitha mt a nyiwa
MUKAMPULUTSE NDIPO IYEYO AKUULULIRENI ZONSE ZIMENE CHAKWERA ANACHITA AMEN CHAKWERA NDI MCP.ZIGWE PERMANENTLY
Comrade tsikulina maganizo anga tsikulina muyendele a banja anafedwa chikangawa.
Mo fire comrade umatiyimilira, ndicifukwa timakukonda ku zambia kukafikidwe manyaka congress party adziwe kuti ndi makape. Inenso munthu wina anandiuza kuti kunalidi chifunga ca sizinaoneke & cinali cokozadi cifukwa akuti tsiku limeneli kunali dzuwa osati dzachifungazo ai. Mbuzi zimenezi dziyaluka caka cino dzimadutsa mbali.
Kodi a commision of inquiry anapita kukafufuza anthu ku chikangawa?
Openga ndi ofunika kukumana ndi mizimu ya anthu 9 ndi iweyo amene ukunena za chifunga chomwe ku alibe mukanthidwa posachedwapa mwangoti poti okufa salankhula awatu alankhula mwatisala mu mbatata inu
Mbambande,.... Ntanyiwa
Tinakusowani big man takulandilani
🔥🔥🔥🔥🔥
God bless you MTanyiwa
Chakwela mbuzi
Koma chakwela mene akutizuzilamo kumafuna kubela azingotizuzabe
Ntanyiwa iweyo umatiimirila
Ulemu wanu big
EYADI AMENEWA AKUPHA ANZAWO NAWONSO APHEDWE MDZINA LA AMBUYE YESU MNKHRISTU.AMEN.@ KKKK NANGA ZOMBA POLICE MASTERS MESS OFFICE YOMWE IMAPANGILA MAPOLICE ONSE MA UNIFORM.AMUDZIKO MUNO ATANI OSAMASOKERA MA UNIFORM.WO NGATI KALE LIJA.? POLICE ZOMBA QIARTER MASTERS YATANI ? A CHAKWERA AIPHA?
Nchifukwa wa MDF uja analendezeratu kuti kuli chifunga sinanga anadziwiratu kuti chipangidwa now it makes sense
Unabwela kudzakhal ntanyuwa Moto kuti mphaaaa
A POLICE AWACHITA BWINO NDIPAMENE AZIWEKUTI MCP SIZINTHU CHIFUKWA A POLICE ANASANKHA KIGWIRA NTCHITO NDI MCP AKHAULE KUMENE
Teach them Akuoangati anafikapo.mwabisala mmadzi msana waoneka am much stick on those watch men kaa nku Tz diko God shall guide u to
Meet the guy. No fear
Iwe ndiwe wabodza lochititsa manyazi tsiku limenelija Chifunga chinachita mpaka chigawo cha pakati komanso dzuwa silinawoneke tsiku lonse anthu onse amakuvera iwe mitu yawo simagwira bwino akufunika chithandizo mwa changu
Ang'aluleni
Chakwela kungochosa agalu awiliwa nyengo zake zitha kusitha
Ineso ndakhala ndikuvela zoyankhula za MA act onse akumalawi Kom chakwera ndatopa nawe mwina anthuwa amangiyankhula ine ndekha ndithananawe mwapadela
Pitirizani kuti pasirezani nkhani tikukunyadirani
Moto wa mapesi uyu watha Basi kkkkkkkkkk
Utagwe ndiweyo mudzina lamulungu chisankho usap
Ndiwe galu wachiweŵe
Kkkk ulemu wanu mcp yatikwana
Mwati atagweyo ndani?
ai zikomo
Ife timakunyadilan
Zag z bug decision so far ever mtanyiwa go on wc investigations
uziva kukoma
Knowledge of your mom was like that the
Uyuu amanama kwambiri ndinasiya kumukhulupilila
Ndiwe kape wamva ,ntanyiwa ndi machine
Osatulukamo bwaaa,,, ukufunamo chaaa,, kupepera
@Thanthwe2020 Muuzeni
Stop taking drugs
Zomvela amisala izi
Alipo anakutumani kuti umvele, tsipa lako
Nawe ndye kut ndiopenga zed kamba wapezeka bwanji mugawo la anthu amisala osamazitenga udolo muzatha kuvakuwawa nthawi zina ndithu
Mpatumbo PA agogo ako fiti yodya maliro iwe
Ndikazaziwa kumene umakhala ndizakudya wamoyo wamva
live
Zilibwino apolicewo azizigulira uniform yo coz a police akumalawi ndi Andale ambali ya mcp
Ntanyiwa eeee ndinumaso amalawi pitilizani ntchito mukugwirayo