ZOCHITIKA KU MALAWI LERO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 มิ.ย. 2024

ความคิดเห็น • 81

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 วันที่ผ่านมา +6

    Muzigula magalimoto a ana anu kms muzigawana pa mtundu panu...mulemere musadzafe mpaka muyayA

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 2 วันที่ผ่านมา +3

    Kkkkkk chithyola bwanji kwacha ikungogwesedwa bwanji idyani mukhute

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 วันที่ผ่านมา +4

    Mtukula MCP ndi mbava zake

  • @HaneephrhBitton
    @HaneephrhBitton 2 วันที่ผ่านมา +2

    Kumavela nkhan ngat izi kulingat kuyika nyimbo ya English usakunva chilichose 😂😂

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mtukula pakhomo kwayani mukungotibela nkumatukulana nokha nokha za ziii!.Mega farm gulani ma tractor zochitika zioneke pa ground mukukanika,project ya madzi pezani akufuna kwabwino athandize project imalizike mukukanika,Pezani akufuna kwabwino migodi iyambike anthu Apeze ntchito mukukanika kungodziwa kuyankhula,upandu kumanga anthu ndi kupha basi.

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mmmm mm anthu oipa inu ndalam zanu zimenez idyan thaw yanu mukapuma kumwamba ngt kuli Malo anu 😢😢😢

  • @patrickkadzeya3020
    @patrickkadzeya3020 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mulungu adalitse dziko la Malawi, court ya Chita bwino kwambiri, ndiye kuti dziko la Malawi li Chita acknowledge Bukhu la Bible.

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mtukula Chithyola😂😂

  • @GiftPhiri-tt7nn
    @GiftPhiri-tt7nn 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndalama mukupatsa a mcp okhaokha ife kumaitanitsa ma ID koma ndalama osalowa , Mulungu atichotsa ku Egypt

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 วันที่ผ่านมา

    ❤There must be strategic plans to liberate Malawians from a quagmire of facultative parasitism:(depending on donors since colonial era)Don't we have pundits to blaze a trail prosperity?

  • @FionaKhoma
    @FionaKhoma 2 วันที่ผ่านมา

    All the best ref jins

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 2 วันที่ผ่านมา

    Kungoyayankhula motipusisa mwagawana kalekale ma billion amenewo,olo mutipase mutukula pakhomo koma 2025 Chakwera ndi MCP akuchoka,kuyitanisa Ndalama yonseyo cholinga mugule ma vote athu,

  • @StevenThanila
    @StevenThanila วันที่ผ่านมา

    Jod well done SC Lali

  • @user-ug8rj6ut9y
    @user-ug8rj6ut9y 2 วันที่ผ่านมา +1

    Agulila anaawu magalimoto abwapiniwi

  • @swadikimbwana7680
    @swadikimbwana7680 2 วันที่ผ่านมา

    Drs ask money from the patients so as to be attended. Quickly. This is happening al most all Hospitals in Malawi especially Mangochi

  • @hassanmuhudiin722
    @hassanmuhudiin722 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiye Mene munayambira sewu wake UTI mwamanga ndinu mbava nditu

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo วันที่ผ่านมา

    Ku Germany mwaitana anthu kudzafufuza za ngozi ya denge, kenako mukusainilana ndalama kweni kweni timva ziti, a chithyola gulani ma Benz tsopano dziko mwaliononga kale ili🤭

  • @Fridayasani
    @Fridayasani 2 วันที่ผ่านมา

    Azapatsa chiyembekenzo makolo ako m,mbava inu mulungu akulangani asatana inu

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q 2 วันที่ผ่านมา

    Sindimafuna ndiziva izizi zimandinyatsa kwambili kazibani popeza kuthekela mulinako

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 2 วันที่ผ่านมา +1

    Nanunso apolisi mukumangopusisidwa ndi andale

  • @user-ei5fc4bl1d
    @user-ei5fc4bl1d วันที่ผ่านมา

    Mudyenso anthu osakhuta inu, koma dziwani mudzazisiya zikadakoma.

  • @jezalakaphuka7325
    @jezalakaphuka7325 2 วันที่ผ่านมา

    Odzafufuza za ngozi ya ndege abwera ndi thandizo

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h วันที่ผ่านมา

    Ndalama imeneyoyo abakale yatha imeneyoyo anthuwa mbuzi galu kwabasi

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 วันที่ผ่านมา

    Mtukula pakhomo wachian za ziii , kadzikwezan mitengo yazinthu poti ndiye kudya kwanu, zinthu kudula , mulungu akuonen mwabweretsa umphawi oopsa , malo motsitsa mukungokweza ayi zikomo ,

  • @omegasheibamussa3900
    @omegasheibamussa3900 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kkkkkkkk phatumbophanu nonse

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 วันที่ผ่านมา

    Mugulenso magalimoto ena!! Ayi zikomo

  • @VishonVishon-sj4cx
    @VishonVishon-sj4cx วันที่ผ่านมา

    Okubaiwe tikupelekela ngongoleyo ukamugulile nkaziwakoagalimoto

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 วันที่ผ่านมา

    Zachamba eti kumakongola ndalama kumati mukufuna muthandize athu zopusa eti

  • @user-hu4gu7op7n
    @user-hu4gu7op7n 2 วันที่ผ่านมา

    Ndinu agalu nonse kuyambila liti zimenezo muno mumalawi zikuchitika,

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y 2 วันที่ผ่านมา

    Mtukula chithyola😂😂😂

  • @Wisdomfred-mq3ic
    @Wisdomfred-mq3ic วันที่ผ่านมา

    mbuzi Za anthu nyamako

  • @samalanimacdonald9373
    @samalanimacdonald9373 วันที่ผ่านมา

    Pamenepo ndalama yonse chithyola watengelatu mbali yake

  • @OffenLebinala-k9b
    @OffenLebinala-k9b วันที่ผ่านมา

    Kuthandiza MCP osati amalawi mene tikuvutikilamu?

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 วันที่ผ่านมา

    Mutu ngati gututu

  • @D.RJALLI-qo6yd
    @D.RJALLI-qo6yd 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe namatongo chithyola tasingoba ndalamayo iwe galu iwe wachabechabe

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 2 วันที่ผ่านมา +1

    Idea iweyo ndi Ana ako

  • @user-vv6rv4it4j
    @user-vv6rv4it4j วันที่ผ่านมา

    Awa agula magalimoto enA galu ameneneyi

  • @D.RJALLI-qo6yd
    @D.RJALLI-qo6yd 2 วันที่ผ่านมา

    Anthu akufunika kumwalila mwadzanga kuti malawi iyende bwino ndiye inuyo achithyola akumkuyu

  • @BerthaNgwenya
    @BerthaNgwenya 2 วันที่ผ่านมา

    Mukungogawana pachibale

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 2 วันที่ผ่านมา

    Ndizo mukuyiba ndalama izo masimba yinu

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 วันที่ผ่านมา

    Pathako Pako iweyo duna yazachuma wava eti

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 2 วันที่ผ่านมา

    Ukuchita kusekeleratu kkkkkk

  • @EvansNaphazi
    @EvansNaphazi 2 วันที่ผ่านมา

    Munthu wakuba uyi

  • @GidionLufani
    @GidionLufani 2 วันที่ผ่านมา

    Ndalamazo udye ndi Iwe ndi chakwela osati athu osawuka ayi gale iwe

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y 2 วันที่ผ่านมา

    Muziwagulila ana anu magalimoto 20

  • @PatrickChalimba
    @PatrickChalimba วันที่ผ่านมา

    Aziphedwa

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y วันที่ผ่านมา

    Aaaaa zodya anthu aku Lilongwe basi

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 2 วันที่ผ่านมา

    Mukagawe ku kasiya ma 600 pin kachikena

  • @ThomasChiwaya-qx9mf
    @ThomasChiwaya-qx9mf 2 วันที่ผ่านมา +1

    Zachison abare

  • @user-hw4yw7ex4j
    @user-hw4yw7ex4j 2 วันที่ผ่านมา

    Ma vote.

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 วันที่ผ่านมา

    Kuchepesa umphawi wa a MCP,

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w วันที่ผ่านมา

    Zausatanic basi zisilu zimenezo

  • @user-fx8vj9vf3h
    @user-fx8vj9vf3h 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaaa kaya bola mutikumbuke

  • @user-ci5ik8kx6s
    @user-ci5ik8kx6s 2 วันที่ผ่านมา

    change the name of mtukula pakhomo and find another name

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk 2 วันที่ผ่านมา +1

    🎉🎉🎉🎉

  • @AufiThera
    @AufiThera วันที่ผ่านมา

    Bola musagawane kubomako

  • @BensonAbdul-li1bc
    @BensonAbdul-li1bc 2 วันที่ผ่านมา

    Eeee zachisoni

  • @JackAmoss-zg2zw
    @JackAmoss-zg2zw 2 วันที่ผ่านมา

    Koma amalawi munawatola ndithu eish

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaaaaah! Kaya,

  • @user-en5rb5zh1t
    @user-en5rb5zh1t 2 วันที่ผ่านมา

    Aganidza mochidwa zisilu zimenezo

  • @PeterThomas-lw3io
    @PeterThomas-lw3io 2 วันที่ผ่านมา

    Mitumbo yanu
    Nonsense mcp

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d 2 วันที่ผ่านมา

    Chokani agaru inu

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 วันที่ผ่านมา

    Chakudya cha abale a achakwera

  • @user-xv9en6se4i
    @user-xv9en6se4i 2 วันที่ผ่านมา

    Mbava

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 2 วันที่ผ่านมา

    Akagule magalimoto aana 60

  • @YusuffuDaud-cs7yu
    @YusuffuDaud-cs7yu 2 วันที่ผ่านมา

    Okuba inu

  • @nmbongeni27955
    @nmbongeni27955 2 วันที่ผ่านมา

    Chisilu

  • @user-qv8vr5dq2x
    @user-qv8vr5dq2x วันที่ผ่านมา

    Chithyola mimba yako

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 วันที่ผ่านมา

    Kunyasa ngati manyi uzigula magalimoto ana ako pwala lako galu

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 2 วันที่ผ่านมา

    Mtukula Chithyola😂😂

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 วันที่ผ่านมา

    Pathako Pako iweyo duna yazachuma wava eti

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 วันที่ผ่านมา

    Pathako Pako iweyo duna yazachuma wava eti

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 วันที่ผ่านมา

    Pathako Pako iweyo duna yazachuma wava eti

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 วันที่ผ่านมา

    Pathako Pako iweyo duna yazachuma wava eti