ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Team Gaga let's gather here 😢😢
Zinveka my man,,Koma kumbari ndi kuno kupatula kuti iyiyi ndi acting Zinveka ndi tambwali weniweni aaaa kkkkkkk
Ziveka ndi cruck
Amuna angati zakhwima alimo muno ambili
Gaga wayikana mission mix thumba mulibe kalikose 🤩🤩
Kkkkkkk anyway Gaga ndikatundu
Kom gaga akut madilagu amukwana 😂😂😂
kkkkkkkkkk zimveka Ayi guys you are the big man 😁🤗🤗🤣
Zagwima wazelezeka eure😂😂
Zimveka nditambwali heavy 😂😂😂
Zimveka mmene anakwiyila mkaz muja mpakana kumseketsa😂😂😂
Zimveka uja osazamphweketsa amwene eeee amatha kunama😂
Zimveka ndi khuluku even in real life si acting yokhayokha iyi aaaaa
Ziveka ndiwokhoswe oluma ndkupelelra iiiii amaliza azimayi uyuuu
Kupatula anambewe ndi my phili azimayi nonse amutonde wadula zinveka wawafusira😂😂😂😂😂😂
Koma ziveka eti 😂😂😂 ndakutaila kamtengo
Kutsekula unyolo ndi makiyi kkkkk
Kkkkk kkkkk km gaga😂😂
Pakufunika chifunilo abwele ngati mzimu
Kkkkkkkkkk mayi phili akumana ndi gaga😂😂😂😂😂 mpaka kusowa chokamaba mayi phili gaga ndi one llove you guys ❤❤
Ziveka ndi dolo🔥🔥🇲🇼💯
I'm still waiting,Tonde ndachoka naye kutali sindingamusiye zibwanabwana
Ziveka ndi khuluka kwabasi😂😂😂
Zimveka ndi tambwali heve😂
Koma Gaga 😅😂😂😂😂😂 koma ine abale uyu azandi komola 😂😂😂😂😂
Gaga usakane unasungisa nkhukuu kapereke ndramayo bs panjatu umanena Kuti urindindarama zonyasa 😂😂😂😂😂😂😂
Gaga nd dolo😮
😂😂😂😂😂 koma falawo akhale nchalite yomweyo bwanji
😂😂😂 koma adaa
Zimveka mmmm 😂😂😂😂😅😅
Koma ine ndikufuna chifuniro a abwere among eke khati zinmu
Zakhwima wayaka moto kkkkk mude wavuta
Mayi Phiri miseche ndiku court komwe ayi zikomo
Zakhwima the great
😂😂😂😂😂
Dzakhwima ati akakwatile kwathu kwa a Navitcha 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Kkkkkkkkk koma gaga iiiiiiiiii iyotu mwabaya yaulinjino ukumuziwa kale mole panjati anakusekera kunyumba yosatha akusinja uona
Gaga azbambo 😂😂
Kkkkk zankhwina woyeee
Love is a beautiful thing in the world 🌍
Gaga wasamba mmanjatu ya nkhuku 30 akut sakuidziwa 😅😅😅naye ziveka akut mkazi uja ndi Link chabe zilikotuziliko😂😂😂
#1 drama series 👏👏👏
Zankwima mkazi wamukonda uyu 😂😂😂😂
Zimveka nd shashiton
😂😂 kom zankwima wapengadi ndi love
Koma Gaga eeeeee
More fire 🔥🔥🔥🔥 guys keep it up 🎉🎉🎉🎉
Ineyo ndikufuna Make Dora is long time ago 🎉🎉
Ankhalango anatiyankha kale kuti iwo aja anachoka for good basi,sazaonekanso mu tondemu anatero basi muzikaonera ku mitekete ndachina black Nina kumeneko
Koma Gaga😂🙌
Gaga yomweyo😂😂😂
Koma zakhwima ndi mbuzi, ukwatira bwanji nkazi oti sunamufunsire?
Gaga suzatheka paka ma drug akwana Devia😂😂
Anambewe mwafunira mwana mkz
Azimveka kkk ndi hule kkkk
Gaga 😄😄😁😁😆
zimveka sanachenjele bwino
Greatng all guys
Very good
Ndipo tikuyembekezera kupitiriza kukutumizani nkhani zabwino
😂😂😂 koma gaga
𝐙𝐚𝐧𝐤𝐰𝐢𝐦𝐚 𝐦𝐨𝐫𝐞 🔥🔥
Komazakhwima iweyo umaitha palibeso 😂😂😂😂😂umakwana aise
Koma gaga😂😂😂😂😂
Zimveka iwe ndikatundu
Gaga sadzathekaso
❤
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Kodi ndekuti Chifunilo uja anamwaliradi?😢
Ayi anangochoka mu sewero for good koma a chibiriti anatisiyadi for real
Ziveka nyimbo? Iwe garu kwabasi
Koma mr zimveka eeeee muli ukhuluku😂😂😂
Zakhwima mwakula mukwatile
Naye zankhwima wazelezeka
Koma Gaga 😂😂😂😂😂🎉Nazombe wasuta MA drag
Nice
Enjoy the episode
🎉🎉🎉 koma ziveka
Azimveka mabodzatu cholinga nkaz apepere machine
Ziveka umakwana 😂😂
Zakwima akufuna mude basi palibeso wina akufuna kuposa mude
Gaga ndi best
,😂😂😂😂 koma gaga
Koma azimveka mmmmm inu ndi chakwera weniweni ndithu
Wawina Gaga kkkkk
Km ziveka kaje masenela😂😂
Zimveka muli lyrics 😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
Komatu mukutimvesa kukoma saname
Zakwima amatha😂😂😂😂😂
Gaga😂😂😂😂😂😂😂
Makwana guys zikukoma
Man zimveka 😂😂😂😂😂
Gaga ❤
Km zamkhwima😂😂
Zimveka ukunamiza Mwana chani kkkk
28:59 ❤ Zakwima
Zakwima 😅
Zimveka ndi nkhani zina
Zimveka great man
Gaga akamuna😂
❤️❤️❤️❤️
Koma zankhwima ayi zikomo😂😂😂😂😂
Gaga more fire😂😂😂😂😂😂
Z² ndi madolo sure
I love Zimveka
Koma Gaga iweyo ndi 1 ndithu
Team Gaga let's gather here 😢😢
Zinveka my man,,
Koma kumbari ndi kuno kupatula kuti iyiyi ndi acting Zinveka ndi tambwali weniweni aaaa kkkkkkk
Ziveka ndi cruck
Amuna angati zakhwima alimo muno ambili
Gaga wayikana mission mix thumba mulibe kalikose 🤩🤩
Kkkkkkk anyway Gaga ndikatundu
Kom gaga akut madilagu amukwana 😂😂😂
kkkkkkkkkk zimveka Ayi guys
you are the big man 😁🤗🤗🤣