Gyz tikamanena kuti mavuto ali dziko munowa sawona mtundu kapena chipani koma ndi a tonse a malawi tikamanena billy amaona ngati ife amisala lero sizi? Gyz vuto si billy koma mcp chifukwa imalemba anthu ganyu azinena zabwino zaiwo pamene pa ground palibe chikuchitika nde anyamatawa ayitutumuka awona kuti akungotaya nthawi chifukwa dzikoli palibe chikuenda.Uwuwu ndi umboni oti mcp yagwa chifukwa zomwe walankhulazi ndi zina zimene mcp yalephela kuchita tsoka ndilo nthawi yawo yatha alibe nthawi yoti angakoze zinthu panopa adzingopakila atilephela a malawi uyu amadzitcha kuti mcp boy nde walankhula zolephela kulephela kwa makolo ake, kumvomeleza kuti makolo ake alephela ife sititekeseka voti ndi a dad 💙💙💙💙💙💙❤❤❤❤❤ boma la a malawi
Mesa inu a billy mumati muli mu boma momwemo mwaionera patali kuti azanu akatenga boma muzazuzika komano nthawi yatha mwachedwa bwana billy muzakhala oyamba kumangidwa tina kuikani kare kugulu la anthu oyamba kumangidwa tikasintha boma chonde musa tuluke Mcp bwelelani komweko abwana
Iwe namachende iwee don't take us for granted, tinakutuluka kalekale limodzi ndi satana mzako ben longwe, munlo etc , ana anjoka asatana okudya manyi inuu, otimenyela nkhondo ife kuno kumalawi ndi ntanyiwa, bakili muluzi tv, bon kalindo, masautso banda, etc
Namachende iwe malata ndi iwe benlongwe mapulani anu tawadziwa mukufuna adpp kuti mwakole chonde born kalindo ndi onse omenyela maufulu pls musamale ndi Ben logwe ndi biley malata Pali chimene akufuna anamachende amenewa
Adad chonde galu uyu okugwa khunyu uyu musamulandile ndi mbale wake ben Longwe agaluwa adikire kukalowa ndi chikangawa asathawe lero akhale komweko ndipo afere komweko chonde adad tikakukondani ife ana anu
Chilipo akufuna iwo awa
Ben ndi billy
Alipo akufuna amusake iwo.
Usatuluke ukhale komweko
Kkkkk wamuza boh
Ma original activisists nonse mwawaona ma fishermen akuwedzani mukawagonekera khosi atumidwatu awa.
Billy Billy bwanji unkhale I we president mwina ziyenda chifukwa muli ndi nzerutu a malata
Kodi Billy Malata munalikuti? Nthawi yonseyi mumasapota Chakwera ndi MCP yake, ndipo mwalankhula bwino kwambiri. Si unatenge mbali.100%.
TAKE CARE DPP NDI BILE MALATA
Too rate 😂😂😂 bon kalindo more fire simunthu wamba ameneuja🔥🔥🔥🔥
Achina boma ndlomweli mutipeza ku DPP simunati
BIlE MALATA AFUNA KUSENDERA PAFUPI NDI ANTHU A DPP
Mr Namzimkambe is talking but he is talking nonsense and rubbish this guy is real monster devil himself
Anthuwa apangana akufuna akole ntanyiwa
Zoona aBilly Malata mwabwera pamodzi ndi ife aMalawi osauka?zikomo kwambiri ❤❤❤
I've ndi galu kwabasi, kagwere uko
Takumvani che malata koma chonde zimenezo muka walangizeko apa banja pako zikomo
KALINDO .NTANYIWA.BAKILI TV .NDI ENA NONSE MUSACHIKHULUPILIRE CHIGALU ICHI ANA AMA HULE AMATELO
Athu awa osawakhulupilanso chifukwa ndamene amatoza amthu iyeyu malatayu,Beni logwe,munlow anthu amenewa ndagalu mchende awoso
MUSAPUSE AI BILE MALATA SANATULUKE MCP MUSACHITE MASEWERA AI NDICHIDA CHA MCP
Ineso nkuonaso choncho ngakhaleso Ben Longwe akukaikitsa zedii
Adziona kuti aphedwa limodzi koma ayituluke
DDP yikuwina ndichifukwa wayinyowa kuti afela limodzi kufa kwa MCP ndikumeneko
Billy malata pantumbo pako ukunamidza ndani panya pako galu iweee do u think we ar stupid as u think
ABilly Malata mwalnkhula bwinotu lero nthawi yonseyi munali kuti?
We can never trust you Malata. Ukalamkhule lero? Never!
Mwayamba liti kuzindikila zimenezo kkkkk MCP anthu mwayamba kuzindika sopano mubwelako nonse by June MCP kuzasala Chimwendo ndi chikangawa Vinyo watha😂😂😂😂
Mmmmmm amalawi tilibenanu zochita mr
Wabodza uyu watumidwa musamale naye ziripo zomwe akufuna achite. Lero zoona zimenezi koma bambo ameneyu umunthu alibe umunthu. Sindingakhulupirire munthu wachipongwe.
Mbambande bwana billy malata....apa mwabwela ndi more 🔥🔥🔥
khuluku iwe ukumiza ndani
Kuteroku mwakonza imeneyo cholinga wina akole koma mtanyiwa kapena bakili muluzi TV simunga wapusise walembam,madzi
Kod mkutulo kapena malodza munatchukatu inu lero zakuwawan ai zikomo khalan komko anzanu amenyera ufulu atopa inu munalikt?
APM Mulungu wamumenyera nkhondo yekha
Achina ntanyiwa ndi anzanu samalira ndi Billy Malata ndi pusi pusi ameneyu njoka muwudzu
Chenjera nawoni anthu ngati awa ndidzopangana izi ngati kuli kumenyera ufulu asiyeni okha osawayandikira chonde chonde😳
Bon kalindo ananena Kuti 2025 tiona zinthu
Kkkkkk malata pantumbopako oipa iwe
Gyz tikamanena kuti mavuto ali dziko munowa sawona mtundu kapena chipani koma ndi a tonse a malawi tikamanena billy amaona ngati ife amisala lero sizi? Gyz vuto si billy koma mcp chifukwa imalemba anthu ganyu azinena zabwino zaiwo pamene pa ground palibe chikuchitika nde anyamatawa ayitutumuka awona kuti akungotaya nthawi chifukwa dzikoli palibe chikuenda.Uwuwu ndi umboni oti mcp yagwa chifukwa zomwe walankhulazi ndi zina zimene mcp yalephela kuchita tsoka ndilo nthawi yawo yatha alibe nthawi yoti angakoze zinthu panopa adzingopakila atilephela a malawi uyu amadzitcha kuti mcp boy nde walankhula zolephela kulephela kwa makolo ake, kumvomeleza kuti makolo ake alephela ife sititekeseka voti ndi a dad 💙💙💙💙💙💙❤❤❤❤❤ boma la a malawi
Kodi bro ,munali kutiko thawi yosei mmene timavutikilamu ,mesa mumadyetsedwa mabazi ndiabwana anuwo
Ndiwaboza uyu osamum'vela
Pamtumbo pako Billy malata
A billy abilly abilly abilly pano mcp yaipa ayi khalani komweko ku mcp mwatidoda doda kenako nkumati mwathawamo kkkkkkkkkkk
Omwe akutukwanawa ndi aboma ndilomeli usadere khawa pitiliza
Person with no integrity, mulungu akungomenya nkhondo aliphe
😂😂😂😂 matchela awa ukodwa wekha msampha umenewo ufuna umukole Ntanyiwa ndi bakili muluzi tv wanya tikuponda tikakupeza wamva iwe billy 😂😂😂😂
Galu ameneyu kobasi akufuna amukole wina mosavuta aziti tili limozi kkkkkkk
Muli ngat njoka muudxu
Bodxa nkhumba imeneyi ikufuna kulimbana ndazake
Eni ake a Channel ichi ndi mbuli kwambiri, why are you lying kuti Malta watuluka Mcp? U may have more viewers but no subscribers
Mesa inu a billy mumati muli mu boma momwemo mwaionera patali kuti azanu akatenga boma muzazuzika komano nthawi yatha mwachedwa bwana billy muzakhala oyamba kumangidwa tina kuikani kare kugulu la anthu oyamba kumangidwa tikasintha boma chonde musa tuluke Mcp bwelelani komweko abwana
Zaziiiiiiii nde ufuna kipudisa ndani
Kkkkk koma malata mwadya zaku mcp zatha apa mwaya kuukila ayi ambuye akuyendeleni
ayi chilipo apangana aw musamvele
Ben longwe ndimuzako Bill malata ndimwe agalu or dogs 🐕🦺🦮
Paja iwe pamutu pako sipamayenda bwino pakumumabe ngati pamwana ndi chifukwa chake sumaganiza bwino
Amalawi musqmumvere billy malata ndi wamisala komaso amutuma a mcp chikangawa
Udziwa kuti iweyo Ndiyimba kukalowa
Malata chilipo akufuna atsusa kuti awone mavuto otsusa otsakhulipilila uyu ndigalu kwabasi
Che billy malata mwatani sopano Kodi dziko likukhulupilireni bwanji?? Mesa inu ndi anyamata ojiya a chakwera?????
Iwe Malata ngati ukufuna chikhululuko ukandilimire mmunda
Nyambo iyi mesa pompano amati ntanyiwa tuluka aaaaa osamuvela
Akutuma " WAMKULU BVUMBWE OTANTHA PA TSEKERA" khalani komweko muthandizane kumwa Magazi ndi mikodzo yo Mukamaliza muzanena. Momwe umatumbwira iwe muja ndani angakukhukupirire Mphyodza Magazi ndi mikodzo iwe, Munthu wokupha.
Kadyeni Dzilope kuchikangawa KO. Akutumaonso ndi Mbuzi ngati iweyo . Ndiwe m'bututu wa MCP omwe amawugwiritsa Ntchito kutayiramo madzi Onunkha Dzuwa likalowa,ukachokako MCP idzikatayira Kuti Madzi Onunkha Dzuwa likalowa? Khalani komweko muzigwiritsidwa Ntchito ngati ma Tissue a Ku Chimbuzi.
Tisachedwe mapwalako malati
Mwala oyendayenda supeza ndele I trust kalindo ntanyiwa ndi bakili ndi ena osasunthika Koma enanu shupt
Akunamatu ameneyi, amutumatu uyu
Kape iwe
Mwayamba kuthawako ku chikangawako
Galu iwe wayamba liti iyeyo akufuna kupusisa anthu mutuwake
Ndalama zatha mukatelo koma Amalawi😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Vinyo watha 😂😂😂😂😂
Mutu otupawo
Agalu Inu
iwe ndi mbuzi ya munthu ukuganiza kuti mbwelela zakozi azikuvela ndani ma activis anakwana iwe get out
Kanyele uko iwee palibe amene angakumvele mbwekela zakozo, zimenezo uzikawauza akwanu and akwanu akenso opusa okhaokha ngat iwe coz ochenjera ngat ine pano sangamvele zopusa zakozo
Tamia Ja akuyitanako usapiteko MCP Ndichakwela akufuna kukupha
Malamgngizo abwino Mr Malata , though too late too ,nyengo yamala
Bodzatu lili, ndipo enanu ndithu tsiku lina mudzafera nazo ku tulo izi.
Manyazi mulibe?.
Tilipamoto.
😆😆🤦🏽♂️❤️.
Attention to all freedom fighters! please don't listen to or not even to dare to do your things openly with this dog
Iwe namachende iwee don't take us for granted, tinakutuluka kalekale limodzi ndi satana mzako ben longwe, munlo etc , ana anjoka asatana okudya manyi inuu, otimenyela nkhondo ife kuno kumalawi ndi ntanyiwa, bakili muluzi tv, bon kalindo, masautso banda, etc
Njira imene wadutsayi MALATA uchedwa nayo peza ina chifukwa ife amalawi ndife ooopsaaa kwambriii takuwelenga kale zofuna zako pati.Ndiwe kape sungakwanitse kuyandikilana KALINDO, NTANYIWA or BMTV.
Abilly malata inu mukufuna chani chiwa no da iwe tiye uko
Apm mwapepetura anthu awa
Malata ukunena chilungamo 😂😂😂😂😂😂 ana onse otaika bweran ndthu😂
Iwetu usatipusitse billy malata mzeru zako tikuzidziwa ukufuna udzikamba zodzudzula boma akutuma ndi a MCP, cholinga chakuti ufukirane ndi mtanyiwa,wa bakili muluzi TV ndi enaose amene amadzudzula boma, nomse odzudzula boma musachimvele chitsiru chimenechi, kodi billy malata tanena zoona ukufuna kufotoza chiyani mau ako akupepuka sakulemelela, alibe weti, tsopano ine ndikuuze izi ndukutuma kuti upite kwa amene anakutumawo ukawauze kuti mzeru zathu zija azidziwa kuti ukufuna uyandikirane ndi amene amadzudzula boma amalawi adziwa akuti ndikagwele uko kutali mwana wa satana.
akunama akufuna wina wake amupeze mosavuta
Nane ndikuganiza chomcho akuona ngati gulu la mtanyiwa ndikalindo limuyandikila
Wachepa ameneyu
Iwe malata usapusitse amalawi
Inu suja munkasapota MCP ndi Chakwera ? lero ndiye mwatani komano mwachita bwino popeza mwazindikira
Awona kut boma sikuwapasa ndalama😂😂😂
Achitsilu inu mukuona ngati ungatipusise mwapangana yofoyila 😂😂😂 😮ngoooooo
Yesani ulimi kaye, sizikumveka mfundo mulibe mbwelela zokhazokha
😂😂😂 7 branches of government?????
Kodi kwatani Ku MCP kwanuko Ben longwe naye akutukwana mufuna mutauze Kuti Chan ifetu wathu ndi bon kalindo ndi ntanyiwa
Anamumana ndarama amene ndiye waying,arura
Billy malata pamtumbo pako uzipusitsa zitsiru zimzako za mcp ndiwe munthu oipa kwambiri umuuzeso chakwera kuti pamtumbo pake
A Billy Malata mwalankhulatu bwino lero.Abale munalikuti Abale nthawi yonseyi
Namachende iwe malata ndi iwe benlongwe mapulani anu tawadziwa mukufuna adpp kuti mwakole chonde born kalindo ndi onse omenyela maufulu pls musamale ndi Ben logwe ndi biley malata Pali chimene akufuna anamachende amenewa
Iweyo umakhala ntwi yosaka ntanyika atakupma amcp iweyo ukuzembera ndani ife wathu nd kalindo bakiri muluz tv bwana ntanyiwa ntwi yonsei unali. KT galu umayenda nd chikangawa party
Kkkkkkkk amwene ka koma uyu siomukhulupilila for now ndi zake Ben longwe alipo akumuzembelela atalephela njila zao zose 😂😂😂😂😂
Iwe ulibe mzeru oyenda ndi lupanga adzafa ndi Lupanga iweyo wasala pang'ono or Mfundo zako is useless and mfundo less
Tilibe nawe ntchito iwe
Lero limenero mukuyakhula zimenezo inu ausilu abilly zopusa
Adad chonde galu uyu okugwa khunyu uyu musamulandile ndi mbale wake ben Longwe agaluwa adikire kukalowa ndi chikangawa asathawe lero akhale komweko ndipo afere komweko chonde adad tikakukondani ife ana anu
Akunama ameneyu akufuna kupala maboza muzipani mwina azikhala ngati sali ku mcp koma alikomwekobe
Bwana malata apapa nde mwafika tilipambuyo panu
Ma passport a fake ..... chikangawa govt
Billy mapazi ako
Mwezi onweuno mumanyoza ntanyiwa ndi wa bmz kut iwowo ndi opoila pano mwabwelaso mukunyoza mcp ife tiziti chani?
Awa atumidwa awa musankhulupilire
Wa chifufu uyu osamutengela😂😂😂😂😂😂😊