YAPHULIKANSO NKHANI ZAMAPASIPORT YAFIKA APATU | ZOMWE ALENGEZA LERO ZAMAPASSPORT |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 30 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 36

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 3 หลายเดือนก่อน +3

    First time kukhala opanda ma passport ku Malawi mcp mavuto kwabasi mwalephera vomelezani

  • @modestamhango611
    @modestamhango611 3 หลายเดือนก่อน

    Yakula ndi nsanje omwe anayamba kalewo amayenera kupitiliza kupanga ku Blantyre ndi Mzuzu komwe. Enawo angofuna adyepo kuzolowera katangale.

  • @MayamikoMukhwapa
    @MayamikoMukhwapa 3 หลายเดือนก่อน

    Mukuyamikila ma passport amenewatu akubwezedwa anthu akamapita kunja inu zimenezo simukuziwa? Kapena mwadya chibamzi

  • @BenjaminKamanga-p8w
    @BenjaminKamanga-p8w 3 หลายเดือนก่อน

    Mbuzi za anthu palibe zimene munatsitsa anthu akulephera kupeza passport ena akayipeza amalipira ndalama zopyolera K300 000, agalu inu

  • @MayamikoMukhwapa
    @MayamikoMukhwapa 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi chizunguchitu Malawi ena samanva osayankhula chichewa bwanji mukuauza anthu akunja kapenatu

  • @MustafaRashid-qb1lb
    @MustafaRashid-qb1lb 3 หลายเดือนก่อน

    How can u see 50thousands when has we get passport with big amount 230thousands are u for sure

  • @charlesbanda3498
    @charlesbanda3498 3 หลายเดือนก่อน +1

    Zikumveka ngati padyedwa ndalama tu!.

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 3 หลายเดือนก่อน

    Izi nde zakumachendeno passport yake it ya 50 sauzande yo usilu eti

  • @sheila5812
    @sheila5812 3 หลายเดือนก่อน +1

    Pena ngati utuluke, koma utuluka bwanji opanda passport?😢

  • @VictorKamanga-v5e
    @VictorKamanga-v5e 3 หลายเดือนก่อน

    Uyu watumidwa ndi company yomwe ikuo1nga ma passport pano

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya 3 หลายเดือนก่อน

    Simukuwerenga bwinotu. You are in a hurry to finish

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 3 หลายเดือนก่อน

    Pena ngati nditukwane pena ngati ndingokhala chete

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 หลายเดือนก่อน +3

    Aaaa mwalephela kupanga passport tangomvumelezani chilungamo kuti passport tikupangitsa kunja nthawi onamidzidwa inatha amalawi anapenya 1993 mugoganidza nokha ma passport akale aja ndini anabwedzenda luka kuti passport sili bwino AAAAA KOMA MCP NDIYONONHADI MWAVA KUPANGA PASSPORT YAKATON KKKKK NDIKUMATI MUFUNATSO 2025 MUDZILAMULILABE MUFUNA MUTITANI AMALAWI AYI AYI

  • @MisheckNtanbalika
    @MisheckNtanbalika 3 หลายเดือนก่อน

    Km malakhulidwewo tinva 😅

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 3 หลายเดือนก่อน

    Malawi poison party

  • @WisePhiri-cr6wh
    @WisePhiri-cr6wh 3 หลายเดือนก่อน

    Banana government

  • @robenallie6985
    @robenallie6985 3 หลายเดือนก่อน +3

    Muziyakhula chichewa ndife a malawi

  • @Kimu-lp3ge
    @Kimu-lp3ge 3 หลายเดือนก่อน +1

    Malawi sidzitheke

  • @CardoJustin
    @CardoJustin 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi passport yamalawi azungunso amalipiranawo? Ngati ndi amalawi bwanji amazikakamiza chizungu?

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 3 หลายเดือนก่อน

    Osamankhulaso chizungu mwamva ifeyo ndife osaphunzira

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 3 หลายเดือนก่อน

    Eeeich koma guys this government 5yrs bt nothing done on the ground mavuto

  • @MarvinChilombo.flourish
    @MarvinChilombo.flourish 3 หลายเดือนก่อน

    kutereku there is a possibility that you are interested parties. Malawi wafika poti sungakhulupilire aliyense, maka inu a majekete. Akuti MABLEM

  • @Amanmaluwa
    @Amanmaluwa 3 หลายเดือนก่อน

    Nanga osamanga omwe akulepheresawo bwanji ziphuphu zikukhazikika pa Malawi mchifukwa anthu akuvutika

  • @UCHIZTembo
    @UCHIZTembo 3 หลายเดือนก่อน

    I can't trust what you are telling people now how is that possible

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 3 หลายเดือนก่อน

    Boma la chakwela 😂😂😂😂😂😂😂 mukulephela zooona kupanga ma pass port Mbudzi za wanthu 😂😂😂

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 3 หลายเดือนก่อน

    Uchitsiru inatsika ntengo kwambuyako pano tikulipira 600,000 kwach

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa 3 หลายเดือนก่อน

    Akunama si k50000 tikutenga ma passport pa mutengo wa k 3,50000😢

  • @AdoptedNaijaBoy
    @AdoptedNaijaBoy 3 หลายเดือนก่อน

    Azitchila kut akupangayi mwana wa biggy😂

  • @AgnesMatola
    @AgnesMatola 3 หลายเดือนก่อน

    Bwezani Boma komwe mudalanda AGalu inu😢

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 3 หลายเดือนก่อน

    Iwe monse muja 😂😂😂😂 ndinu zisilu 😂😂😂😂

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 3 หลายเดือนก่อน

    Koma kumalawi kuno kuli nkhanza iiiiii

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet 3 หลายเดือนก่อน

    Inu thulani pasi udindo please

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 3 หลายเดือนก่อน

    Galu iwe mbuzi za wanthu

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa 3 หลายเดือนก่อน

    Bodza kulimbikira

  • @AndrewSosola-h9f
    @AndrewSosola-h9f 3 หลายเดือนก่อน

    Utitayisa nthawi