ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Kkkkk koma zovuta ndithu😂😂😂. Boma ndilomweli😂😂😂
Nanga wachigayo azinyamula chigayo kupita nacho ku filling station
Akunama nkhani njakuti kulibe mafuta zaka zonsezi mmesa timagula mafuta dzigubu momwemo? Alimi apanga bwa? Zigayo zienda bwa? Zisilu zina zikuti boma ndilomweli la manu? Gyz mmalawi muno mulibe presdent ndipa cikangawa panyoo pako ndithu
Angonena zoti zativuta kodi nanga akumdzi awapeza bwanji
Ulamulilo wavuta kuchikuli kulibe filing station ndiye azitani Kuti apezeke mafuta kumeneko chakwela Kodi unkayesa u present ndi atumiki mumpingo mmmm
Ndie nanga wa generator adzibweletsanso generator
Anthu atenge phunziro amati dpp ikulakwisa lero ndiye zimene amalawi ndiziko lawonongeka ndi mcp
Mr Mangochi number one ❤❤
Go ahead mr Mangochi
Malamulo okomela athu olemela omwe, amathila full thank.
Apapa ndye zavutad
Ndipo kusintha kwake kwakukurutu
Tangobweletsan mafuta mmalawi muno, sizomwe mukupangazo za ziii zenzen, chitseko chakupanani,
Angovomeleza kuti zawavuta basi osati anamizile kutseka ma filling station mkumati akugulitsa mnzigubu
Mjomba yosopeyi jamanjamwe na chilima mwatujigalile mavuto aga
Zovesa chisoni zikuchitika mulamulilo uyu Malawi wavunda uyu
Number 1
Iiiiiiiiiii seriously imeneyo ayii apa zafika panyasi yeeeeeeeetu
Nanga truck tingayikakhe ? Chakwera ukufuna titani ife?
Kkkkkkkk apule osavinidwa apa mukumva bwaaaa kkkkkk kuyendetsa dziko sikuli ngati family
Izi ndiye nkhazatu eeee malawi akupita kuti tsopano osangonena kuti zativuta mafuta kulibe bwanji
Chakwera delivery boma ndilomweri 😂😂 akutero uku 😂😂😂
Powerful speech from our own beloved freedom fighter Lyton Mangochi, proud of you comrade ❤❤❤❤
😂😂😂😂😂ziko ndilomwelo la machande
Koma ndezomvesa chison Malawi wanga Chimwendo wanenepa ngat Nguluwe ? Hahahqhqhq
Zauchitsiru amdzigubuwo akupatsidwa ulere mafutawo apa ndiye game topazi anthuwa zawavuta amaoneka ngati madoro koma sadziwa kalikose sadziwa kagwilitsidwe kantchito sadziwa ndalama koma kunyengera(dzigwede) anthu otembeleredwa mukakhuta mmakwanumo ndi ana anu muli amalawi tikuwalanga ai mukudzilanga nokha ndithu muona zomwe zititike chaka chanawa
Kkkk 😂ndikuseka ngat zabwino eee km mcp kkk aaah bas mwatimalidxa ndithu
Apa ndiye ulimi wothilira uja uliponso kupusatu uku munthu unyamuke chigayo chadiziro uzipita nacho ku filling station
We have no president in malawi😮😮😮😮
Kutseka ma filling station ⛽ is not a solution, bwelesani mafuta okwanila kutseka sindiye kuti fuel adzipezeka
Kod dzingayo koma chilango kwa anthu akumudzi
💪💪💪 salute mr Mangochi
Penapake tumaganiza zongogulitsa malawi fukwa mene amuonongeramu mzovuta kt zzakomzedweso
Galimoto ikathera mafuta kutali tizitani
Kayatu 😢
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏 Lyton mangochi
Mmmmh guys dziko lija likupita kuti mmmh 😂
Koma mukupanika ku Malawiko nanga mafuta akuthera kutali ndi filling station
Apa chakwera basi nzeru zamuthera nzeru wasala nazo pano ndizobera mavoti ndicholinga azafinyeso malawi mulungu atimenyere nkhondo
Ubusa wa anthu akumidima asatana nanga ubusa odzodzedwa ndi mulungu aaaaa ndakayika mwina yesu yemwe amamupembedza wakukasiya Tu osati wakumwamba
Koma dziko la umphawi aliyense amasanduka kape, ndipo mistake yimene tidapanga posankha fisi uyu chakwera, mmmmmmm. Kaya.
Kkkkkkk Malawi wanga uyo🙌🙌🙌
Manyi Alibe nzeru agulukunyenda amenewa
BOMA NDILOMWELI MY FOOT
Anyamata angopangana akaphwasule zimenezo azikangothira ulele.
Zosayenda ambuye alowelele
A Mera ndi anthu opanda nzeru, akulephera ntchito akulandira ndalama zaulere
Bwaji dzuro a Mec amathira ma Dramu petrol pa maula filling station all most 8 Dramu anali pa 3 tonner
Kn ku Dz tabwerani zikuchitikanso kn aaaa MERA changu bwerani mudzaone kn
Pajonz pano anthu timagura zigubu iye akut ai mmmmm chakwera zakuvuta bs 😂😂😂😂
Aaaaa kodi athuwa anthu akumudzi akuwayika pati???? Zawusatana basi
Zayamba liti izi
Nanga wa chigayo adzinyamula chigayo kupitanacho pa filing
Mmm wachigayo choyendela mafuta azichinyamula kukathila mafuta zooona?.
Mmmmmh apatu sizinayende bwino amayenera kuganizila athu ena
Ngati watseka ndie kt alibe ndlama
😂😂😂😂😂more fire mangochi❤❤❤❤❤❤
Mavuto azaonenitu awa eish!!!!
Aaaa koma chakwela athipha amalawi UYU CHAKWELA NDI MCP YAKOYO AAAAA MINYAMA YOYIYAMBA DALA MALEMU CHILIMA WATIDZUDZITSA AMALAWI
Just Make Fuel Available.... osati izizi mukupangazi😡😡
Awande manyi enaso awa 😢
Silamulo muzigubu komanilamulo josaki zigubu nilamulo
ndipo wangobwerad kuzaononga malawi
Tsopano otsilila mbeu muwatani?
Ndiye galimoto ungakakhe kuchokera kwanu
Koma abare dziko lokomera andalama ili mmmmmmm ambuye nkatheni wakutsogoloyo
Boma nilomweri
anthu awa nde zawavuta kwambili ndipo wakan chakwera😂😂😂😂😂
Sopano ochita ntchito za ulimi,?
Izo zinthu izoo imwee kunyera pogona
Kunkuyu komanso Dan Luu akut boma likuyenda bwino akupanga chitukuko chapasipasi Dan luu ngat ukufuna ndalama panyapako ndithu ndi kunkuyu.
😅😅😅😅guys ndi politics mafuta amatha kugulitsidwa mzigubu Loma pali ndi zigubu make,awauze athu zigubu make akufuna botanical zangiwavuta awa.
Koma boma ili palibe walipininga kapena waliloza abale nanga chilichonse chingowavuta bwanji ? Nanga mpakaka kuseka malo ogulisila mafuta nanga anajenletafe tipanga bwanji ? iiiiiii mulungu wanga koma muziziwona zinsezi ?
Ulemu wanu Bwana Lyton Mangochi
Akuti boma ndilomweli
Nanga bolt pa nyanja lipanga bwanji
Chodabwisa a opositipn mwangoti. Duu mukofuna a. Malawi titani?
Guys ingosekani border ya songwe ndi mwanza basi mademo akwanila
Atseke ma filling station onse
Za manyazi
Zachibwana zonsenzi kaamba ko votera mbuzi za anthu ngati izi kachaje ndi owuma mutu ngati gwafa
Gyz a citetezo ali mmalawi muno sakuteteza malawi koma mcp ife akutiteteza ndi mulungu mmalawi muno mulibe presdent
This government is malabastand, Boma lichoke ili malawi wayaka uyuuu!!!!!
Zazii tangobweletsani mafuta ambiri anthu sangagula KU black market akagula straight KU filling station.Galimoto ngati yafela panjira apanga bwanji Zachamba boma la MCP
Boma NDI lomweri 😂😂😂nyini dzamanu
Kkkkk koma ichi pena😂
Machendeawo awa kulephela uku zawavuta
Iwe chakwera machende ako ukufuna tizinyamula water pump ku farm pa thako pako posasetapo ndipo sindikuopa mwana wasatana
Fuel akamapezeka paliponse palibenso chifukwa chogulira mchigubu zakuvuta chakwera
Boma ndi lomweli==Chimbama
Boma la mcp ndilofoila komanso uchitsilu , Nkhani ndiyoti mafuta aziitanitsa ambili basi , ukuku ndikupepela kwa boma
Chakwera machende ako
Achakwera abuse akufuna kutipha basi tavomereza pot mwa tipha kare
Nanga kugulitsa mafuta muvigubu pali vuto, Malawi mwatani kodi
Nde kutseka ma filing station kuthandza chani mmalo mongopeza means yot mafutawo azipezeka okwanira China nde uchimva boma ndlomweri kupusa bas
Chakwera is not a pastor but a wolf in sheep's clothing
Boza ili 🤣🤣🤣🤣
Chakwela kumenya kugwetsa 😂😂😂
Koma ndipo 😂😂 apa nde wagwetsa a Malawi 🇲🇼 😅😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 boma la chakwela 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Afikenso mbali zakuno
Amalawi apa zavuta kukaniza mafuta ngati akukapepha
Kulemphera kwa boma uku
Kkkkk koma zovuta ndithu😂😂😂. Boma ndilomweli😂😂😂
Nanga wachigayo azinyamula chigayo kupita nacho ku filling station
Akunama nkhani njakuti kulibe mafuta zaka zonsezi mmesa timagula mafuta dzigubu momwemo? Alimi apanga bwa? Zigayo zienda bwa? Zisilu zina zikuti boma ndilomweli la manu? Gyz mmalawi muno mulibe presdent ndipa cikangawa panyoo pako ndithu
Angonena zoti zativuta kodi nanga akumdzi awapeza bwanji
Ulamulilo wavuta kuchikuli kulibe filing station ndiye azitani Kuti apezeke mafuta kumeneko chakwela Kodi unkayesa u present ndi atumiki mumpingo mmmm
Ndie nanga wa generator adzibweletsanso generator
Anthu atenge phunziro amati dpp ikulakwisa lero ndiye zimene amalawi ndiziko lawonongeka ndi mcp
Mr Mangochi number one ❤❤
Go ahead mr Mangochi
Malamulo okomela athu olemela omwe, amathila full thank.
Apapa ndye zavutad
Ndipo kusintha kwake kwakukurutu
Tangobweletsan mafuta mmalawi muno, sizomwe mukupangazo za ziii zenzen, chitseko chakupanani,
Angovomeleza kuti zawavuta basi osati anamizile kutseka ma filling station mkumati akugulitsa mnzigubu
Mjomba yosopeyi jamanjamwe na chilima mwatujigalile mavuto aga
Zovesa chisoni zikuchitika mulamulilo uyu Malawi wavunda uyu
Number 1
Iiiiiiiiiii seriously imeneyo ayii apa zafika panyasi yeeeeeeeetu
Nanga truck tingayikakhe ? Chakwera ukufuna titani ife?
Kkkkkkkk apule osavinidwa apa mukumva bwaaaa kkkkkk kuyendetsa dziko sikuli ngati family
Izi ndiye nkhazatu eeee malawi akupita kuti tsopano osangonena kuti zativuta mafuta kulibe bwanji
Chakwera delivery boma ndilomweri 😂😂 akutero uku 😂😂😂
Powerful speech from our own beloved freedom fighter Lyton Mangochi, proud of you comrade ❤❤❤❤
😂😂😂😂😂ziko ndilomwelo la machande
Koma ndezomvesa chison Malawi wanga Chimwendo wanenepa ngat Nguluwe ? Hahahqhqhq
Zauchitsiru amdzigubuwo akupatsidwa ulere mafutawo apa ndiye game topazi anthuwa zawavuta amaoneka ngati madoro koma sadziwa kalikose sadziwa kagwilitsidwe kantchito sadziwa ndalama koma kunyengera(dzigwede) anthu otembeleredwa mukakhuta mmakwanumo ndi ana anu muli amalawi tikuwalanga ai mukudzilanga nokha ndithu muona zomwe zititike chaka chanawa
Kkkk 😂ndikuseka ngat zabwino eee km mcp kkk aaah bas mwatimalidxa ndithu
Apa ndiye ulimi wothilira uja uliponso kupusatu uku munthu unyamuke chigayo chadiziro uzipita nacho ku filling station
We have no president in malawi😮😮😮😮
Kutseka ma filling station ⛽ is not a solution, bwelesani mafuta okwanila kutseka sindiye kuti fuel adzipezeka
Kod dzingayo koma chilango kwa anthu akumudzi
💪💪💪 salute mr Mangochi
Penapake tumaganiza zongogulitsa malawi fukwa mene amuonongeramu mzovuta kt zzakomzedweso
Galimoto ikathera mafuta kutali tizitani
Kayatu 😢
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏 Lyton mangochi
Mmmmh guys dziko lija likupita kuti mmmh 😂
Koma mukupanika ku Malawiko nanga mafuta akuthera kutali ndi filling station
Apa chakwera basi nzeru zamuthera nzeru wasala nazo pano ndizobera mavoti ndicholinga azafinyeso malawi mulungu atimenyere nkhondo
Ubusa wa anthu akumidima asatana nanga ubusa odzodzedwa ndi mulungu aaaaa ndakayika mwina yesu yemwe amamupembedza wakukasiya Tu osati wakumwamba
Koma dziko la umphawi aliyense amasanduka kape, ndipo mistake yimene tidapanga posankha fisi uyu chakwera, mmmmmmm. Kaya.
Kkkkkkk Malawi wanga uyo🙌🙌🙌
Manyi
Alibe nzeru agulukunyenda amenewa
BOMA NDILOMWELI MY FOOT
Anyamata angopangana akaphwasule zimenezo azikangothira ulele.
Zosayenda ambuye alowelele
A Mera ndi anthu opanda nzeru, akulephera ntchito akulandira ndalama zaulere
Bwaji dzuro a Mec amathira ma Dramu petrol pa maula filling station all most 8 Dramu anali pa 3 tonner
Kn ku Dz tabwerani zikuchitikanso kn aaaa MERA changu bwerani mudzaone kn
Pajonz pano anthu timagura zigubu iye akut ai mmmmm chakwera zakuvuta bs 😂😂😂😂
Aaaaa kodi athuwa anthu akumudzi akuwayika pati???? Zawusatana basi
Zayamba liti izi
Nanga wa chigayo adzinyamula chigayo kupitanacho pa filing
Mmm wachigayo choyendela mafuta azichinyamula kukathila mafuta zooona?.
Mmmmmh apatu sizinayende bwino amayenera kuganizila athu ena
Ngati watseka ndie kt alibe ndlama
😂😂😂😂😂more fire mangochi❤❤❤❤❤❤
Mavuto azaonenitu awa eish!!!!
Aaaa koma chakwela athipha amalawi UYU CHAKWELA NDI MCP YAKOYO AAAAA MINYAMA YOYIYAMBA DALA MALEMU CHILIMA WATIDZUDZITSA AMALAWI
Just Make Fuel Available.... osati izizi mukupangazi😡😡
Awande manyi enaso awa 😢
Silamulo muzigubu komanilamulo josaki zigubu nilamulo
ndipo wangobwerad kuzaononga malawi
Tsopano otsilila mbeu muwatani?
Ndiye galimoto ungakakhe kuchokera kwanu
Koma abare dziko lokomera andalama ili mmmmmmm ambuye nkatheni wakutsogoloyo
Boma nilomweri
anthu awa nde zawavuta kwambili ndipo wakan chakwera😂😂😂😂😂
Sopano ochita ntchito za ulimi,?
Izo zinthu izoo imwee kunyera pogona
Kunkuyu komanso Dan Luu akut boma likuyenda bwino akupanga chitukuko chapasipasi Dan luu ngat ukufuna ndalama panyapako ndithu ndi kunkuyu.
😅😅😅😅guys ndi politics mafuta amatha kugulitsidwa mzigubu Loma pali ndi zigubu make,awauze athu zigubu make akufuna botanical zangiwavuta awa.
Koma boma ili palibe walipininga kapena waliloza abale nanga chilichonse chingowavuta bwanji ? Nanga mpakaka kuseka malo ogulisila mafuta nanga anajenletafe tipanga bwanji ? iiiiiii mulungu wanga koma muziziwona zinsezi ?
Ulemu wanu Bwana Lyton Mangochi
Akuti boma ndilomweli
Nanga bolt pa nyanja lipanga bwanji
Chodabwisa a opositipn mwangoti. Duu mukofuna a. Malawi titani?
Guys ingosekani border ya songwe ndi mwanza basi mademo akwanila
Atseke ma filling station onse
Za manyazi
Zachibwana zonsenzi kaamba ko votera mbuzi za anthu ngati izi kachaje ndi owuma mutu ngati gwafa
Gyz a citetezo ali mmalawi muno sakuteteza malawi koma mcp ife akutiteteza ndi mulungu mmalawi muno mulibe presdent
This government is malabastand, Boma lichoke ili malawi wayaka uyuuu!!!!!
Zazii tangobweletsani mafuta ambiri anthu sangagula KU black market akagula straight KU filling station.
Galimoto ngati yafela panjira apanga bwanji
Zachamba boma la MCP
Boma NDI lomweri 😂😂😂nyini dzamanu
Kkkkk koma ichi pena😂
Machendeawo awa kulephela uku zawavuta
Iwe chakwera machende ako ukufuna tizinyamula water pump ku farm pa thako pako posasetapo ndipo sindikuopa mwana wasatana
Fuel akamapezeka paliponse palibenso chifukwa chogulira mchigubu zakuvuta chakwera
Boma ndi lomweli==Chimbama
Boma la mcp ndilofoila komanso uchitsilu ,
Nkhani ndiyoti mafuta aziitanitsa ambili basi , ukuku ndikupepela kwa boma
Chakwera machende ako
Achakwera abuse akufuna kutipha basi tavomereza pot mwa tipha kare
Nanga kugulitsa mafuta muvigubu pali vuto, Malawi mwatani kodi
Nde kutseka ma filing station kuthandza chani mmalo mongopeza means yot mafutawo azipezeka okwanira
China nde uchimva boma ndlomweri kupusa bas