Vuto laku Malawi ndi NJALA mtenda NSANJE. Lero mwayiwala amene anawononga dzikoli. Mwayiwala kale inu a Saduki,olo Peter Muthalika atawina masankho adzatisangalatsa,adzakhonza dzikoli? A Malawi anzanga Kodi mwatani inu. Mupemphere ndipo akukhulukirani,kuMalawi,sikukufinika a dad, Kabambe,Chihana lero, answer ya Malawi ndi munvere nyimbo za za Bob Marley,Peter Tosh. Burning and Looting. How many rivers do we have to cross before we can talk to the boss?????? 🤔☹️🙁
It's not about who love between chakwera or peter wa mtalika, it's aall about Malawi,ngati Peter mumakonda it's your choice,koma ine ndi kuti ndi munthu modzi amene wa bweretsa mavuto ku Malawi kuno. Apemphere ndipo akhululukidwe. Zabwino zimene anapanga ndi zochepa kwambiri IFE TILIMBE MBALI,ndipo sidan ndi Malawi Aliyense. Koma timalondala chilungamo.
Peter Muthalika ukaledzera Konyagi usamayankhule za manyi galu iwe, this country ngati tili pa umphawi iweyo Muthalika unapanga contribute, mwakhala Boma Kwa zaka 13, why this country silinatukuke? Panopa mubwelesa Chiani chachilendo? You deserve to be at page house. Mbava number 1 ndiwe ndi Chisale
😅😅😅😅😅😅😅 ku Malawi 🇲🇼 😍 kuli zi ndalama
God bless Apm 💙💙💙💙
Zose zakwela ndi chakwela kkkkk more fire ADadi😅
chakwela mmutu mwake sumuyenda bwino by the way akudwala
The way I love pita muntharika I don't know how I can explain ❤❤
Wonderful Mkuche ndiwe cadet pumulani mfiti ndipo nonsense ndinu macadet
Nawe Nankhumwa usatitaise nthawi iwe idzakuwinisa chimimba chakocho dzikol lafikapo
koma a Chakwera nchani kwenikweni,nduna mpaka 31 😢😢😢😢😢,dzikoli mukuliganizira zotani
DPP WOYEEEEEE🎉
Koma mkuluyu ali nzeru kumene akuziwa ndi kuona mmene a Malawi akuvutikira
Manyaka apule
mmalo mochepetsa nambala ya nduna,awa akuonjezeranso aaaaaa,awa nde alephera basi
Chakwela mbuzi ya tsogoreli, onse osapota chakwela ndi zitsilu mbuzi zokha-zokha zamano kusi, akaporo
Chakwera aaaaaaaaa nde manyi apulesideti
Am watching from zambia lundazi the truth is that this your president chakwera he's a faire
iwe ukunyoza adadi uli ndivuto adada ndi umunthu wabwino
@@YusufuUsumani tell dem
Abale ndle ndale pena mudzizimvesa Peter wanyoza patipo iiiiii ai Mulungu titalikiseni ndi zoipa kutali ndi satana abale
Chakwela ndi olephela pa chilichonse gaulu ameneyu
Vuto laku Malawi ndi NJALA mtenda NSANJE. Lero mwayiwala amene anawononga dzikoli.
Mwayiwala kale inu a Saduki,olo Peter Muthalika atawina masankho adzatisangalatsa,adzakhonza dzikoli? A Malawi anzanga Kodi mwatani inu. Mupemphere ndipo akukhulukirani,kuMalawi,sikukufinika a dad, Kabambe,Chihana lero, answer ya Malawi ndi munvere nyimbo za za Bob Marley,Peter Tosh.
Burning and Looting. How many rivers do we have to cross before we can talk to the boss?????? 🤔☹️🙁
Kugawana ndalama za misonkho ya a Malawi
Dpp boma
Lazarus malephera kuyendetsa dziko kuvomeleza ndibwino
First view
Mthalika chisilu unanalephera kale madala inu
Iwenso chitsilu ! muthalika ndi Chakwera Sangafane boma lachikangawa lì
Chakwera ndi ndi munthu olephera
Kunkuyu peleka black box
😢😢😢😢😮
Kumkuyu black box ili Kut
Boma linawakanika kale awa nawoso angosowa zochita,,,MCP and DPP cannot be our #1 priority in the upcoming 2025 elections😢😢😢we better try Mbakuwaku
Kavotere wekha mbaku waku wakoyo😂😂😂😂
@@ShamimuBisani ife monga a Malawi tagwilizana za DPP iwe ngt ufuna mbaku waku ndekut ndiwe waku Mozambique 😂😂
@@salmankhanofficiel.5018 iwe ukundiyankha chonchi ndayankhula za mbakuwaku ndineyo ayi sndimatha kunyoza munthu pliz mudziwerenga bwino ma comment then mkuyankha Mulungu adzitidalisa tonse moyo uno ndiomwe ulimkudzawo Mulungu atipase zosowa zathu koma zikhale zabwino Mulungu odziwa kudalisan akudalisen koposa zikomo
@@salmankhanofficiel.5018 palib chfukwa chondinyozera sndinayankhul za Mbakuwaku wayankhulayo ukuopa wandiona kupusa ndneyo ai ndathokoza zikom kwambri pomdinyoza Mulungu akudaliseni zikom kwambri zikom
@@salmankhanofficiel.5018 walemba za Mbakuwaku ndi munthu wina ukubwera kundinyoza ineyo amatero kuonana kupusa kodi iii ndathokoza zikomo kwmbri Ambuye adzikudalisani koposa koposa
Chakwera mu ma speech Ake samakunyoza iwe Peter, manyazi ulibe ? Nkhalamba iwe galu ndi okutsatila omwe afisi killers of Albinos
Kodi ama bandle aja ndinu uchitsilu ndiotani momwe chakwela wawonongela zithu wina angamanyoze Peter iwe ndi chitsilu kobasi
Muzingodya ndalama zo koma Peter akuwina timadyatu ifee tili nda adadi
Sitikunyoza a dad koma analephera undindo wawo,kwaine a dad ndi premature ejaculation,he is not a reberator,or a solution to Malawi 🇲🇼
It's not about who love between chakwera or peter wa mtalika, it's aall about Malawi,ngati Peter mumakonda it's your choice,koma ine ndi kuti ndi munthu modzi amene wa bweretsa mavuto ku Malawi kuno. Apemphere ndipo akhululukidwe.
Zabwino zimene anapanga ndi zochepa kwambiri
IFE TILIMBE MBALI,ndipo sidan ndi Malawi Aliyense.
Koma timalondala chilungamo.
Peter Muthalika ukaledzera Konyagi usamayankhule za manyi galu iwe, this country ngati tili pa umphawi iweyo Muthalika unapanga contribute, mwakhala Boma Kwa zaka 13, why this country silinatukuke? Panopa mubwelesa Chiani chachilendo? You deserve to be at page house. Mbava number 1 ndiwe ndi Chisale
@@TamUs-u2h MCP, never again imfa ya Chilima ku Chikangawa ikutiwawa heavy
Iwe takuwona ulimugulu la anthu okupha usatinyase chakwera wakoyo wapanga chan pazaka 4? Kupha kuba ufiti wamasanasana ndizomwe apangatu anthu oyipa inu afiti anthu opanda chisoni ngat mkudya naye idyani ndalamazo koma muzabweza agalu inu afisi MCP kwake kwatha tione anthu ena
Mesa garu wakoyo Chakwera anati asintha zinthu ndye ukuti chni nweso paujeni pakomopomso paujeni ndati paujeni...............nonsense