Ipemerere pamenepo asekula nayo mmimba Bakili muluzi tv kkkkkk Nkhumba imeneyi yafufuma zoonadi am feeling so happy when am watching and listening BMTv
Ur welcome big bro tv Bakali Muluzi ❤❤❤ awuze chilungamo cho agalu amenewo, thanx bakali muluzi mumakwana kwambiri poyimilira A malawi ife God bless you ❤❤
Weldone, The wise and Intelligent man. Ngodala amene abareka ndi kulera inuyo Brother from BAKILI MULUZI TV. Stay safe ✊ ✊ Stay blessed 🙏🙏 Be protected in God's Name. MCP mwathedwa mzeru ndipo zamanyazi Chakwera anyamata akowo akupeperesa. Bravoooo Malawi Defence Force osalorera zopusa . God bless you all.
Zamanyazi agalu amenewa atitopesa kwabasi God bless bakili channel 📺 ❤❤❤ameen
Pokhapo poti history is the best teacher don't ever forget coz pamandiwaza ❤❤
Ipemerere pamenepo asekula nayo mmimba Bakili muluzi tv kkkkkk
Nkhumba imeneyi yafufuma zoonadi am feeling so happy when am watching and listening BMTv
Mcp muyaluka simunati
Ulemu wanu brother ifeyotu timakunyadilani ndipo mumatiimilira .we are tired of this stupid Government
Bakili muluzi TV nde Yomvera m'malawi ozindikira yemwe Ali mu 89% ya kulira ndi ulamuliro wa Mr Chikangawa ❤❤❤❤
Inuyo bwana mulandire ulemu wanu wapadela dera komaso kwama fanz onse timavela bakili muluzi tv❤
The best TV,,,,,Bravo MALAWI ARMY
History is the best teacher
Ur welcome big bro tv Bakali Muluzi ❤❤❤ awuze chilungamo cho agalu amenewo, thanx bakali muluzi mumakwana kwambiri poyimilira A malawi ife God bless you ❤❤
The bestb❤❤ we love you brother pitilizan ntchto mpake tisinthe chipam cholamula ndpo tikazasintha MCP izathe mmalawi muno
Bakili muluzi tv number one every day I'm following your
Agalu awa ali very desperate.... Maula prison ikuwadikira....
Thank you BMTV....
History is the best teacher mumakwana inuyo
Agalu achabechabe awa
Bakili muluzi go on this is my favorite Chanel 😍
History is the best teacher ❤
Ndipo zomwe apanga asilikalizo mulungu awadalitse 🙏🙏🙏
Weldone, The wise and Intelligent man. Ngodala amene abareka ndi kulera inuyo Brother from BAKILI MULUZI TV.
Stay safe ✊ ✊
Stay blessed 🙏🙏
Be protected in God's Name.
MCP mwathedwa mzeru ndipo zamanyazi Chakwera anyamata akowo akupeperesa.
Bravoooo Malawi Defence Force osalorera zopusa .
God bless you all.
Ndipo Amry yachita bwno kuwakanira Ana opusa amemewo keep it up.the good work
History is the best Teacher
Richard Chimwendo Banda Akukoza Zokupha Norman Chisale.
Izi Anayamba Kupanga Pakanthawi Koma akusowa Support
I support Bakili Muluzi TV inspiring the nations
Ndamuona maso ndi maso bale wangayu kuno ku Jos keep pushing my brother and favorite history is best teacher 😂
B M t v i s my best t v so inu Aame ulemu wanu mwapadela chimwendo nd satana weniweni l m watching form cupe town
Bakili muluzi TV number one 🇲🇼🇲🇼💯
Mcp mwakhala madzi amodzi lazalasi nazakowo ilitu ndidziko. Bakili Muluzi Tv we love you Sir 😍
Vuto ndi umphawi ndichifukwa a police akugwirisidwa ntchito ngati anthu opanda zeru 😢😢😢😢
Following from mpumalanga south africa big up comrade
Sitinati chakachino ntinva zinthu chaka chake ndichino kalikonse kobisika tikaona ndiponso tikanva watching from Mozambique 🇲🇿 ulemu wanu brother potiwululira zisisi
Ife sitizasiya kumvera mpaka imfa bakili muluzi tv ❤❤❤❤
Ndikuona Nkhondo Yoopsa Ikuchitika Pakati Pa Apolice ndi a Army.
Chakwela Anapha Chilima Ngati Bodza 😢😢😢😢
Bakili Muluzi TV Ulemu wanu Comrade akanyimbi amenewa atitora kwambiri. Kukhalira kuseweletsa misokho yathu. Tikudalira inu kuchotsa nyasi zamtsogoleri ameneyu. Belezebuluwa.
Our lovely brother Bakili Muluzi TV kuwabweresa poyera onse amene sakupuma nayo bwino DPP koma kuyalukatu osawasiya pitilizani ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Congratulations our own army...osapanga nawo zopusa..ku police konko
Pano ndikumangilatu ndende ya chimwendo kunkuyu kamajekete Jezebel chikangawayo ndiyeee samazatuluka
Zapawa brother anena kare kut athu akuvela bakili muluzi tv 😂😂😂😂 l love this channel wina alila😅😅😅
Umakwanaa boss ❤❤❤❤
Hmmm tiyeni naoni agalu amenewa lero mwalawilira palibeso kudikira usiku ❤love the best TV
😂😂😂atchera kumwezi nkhanga zaona BMTV🔥🔥🔥❤❤
Comrade osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka atuluke crocodile mboma ndi team yake yonse chipani chakupha ngati ichi chisazaloweso mu boma basi
We love you comrade more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chikañgawa ayaluka ndi nduna zake zonse ,
Jezebel nkhope yako imaopsadi kosonyeza ndiwedi satana 😊
Exactly 💯
All the best Bakili Muluzi TV 🎉🎉
This coming year wina amva m'madz alaka laka akanapanda kubadwir ku Mw... Long live #BKM TV
Zilombo, thanks Malawi army🙏🙏🙏pitilizan kuteteza aMalawi.thanks my God protect you all
Zikom kwambiri
Bakili TV number ❤
God bless you, history is the best teacher long live.
History is the best teacher umakwana bigy akwezaso malata
Ngakhale Chimwendo Banda akudziwa kuti a Malawi ambiri including iyeyo amakonda kumvera Bakili Muluzi TV
Adanena kale broo mix kunkuyu kamajekete samamvela nawo chifukwa saiziwa nt kkkk
Ndipo inetu ndimafuna amutchule yemwe anamuuza kuti ndege yazaza timuziwe zoonadi chilima angapite ngati nkhuku zoonadi lelo kumavina mumseu ayiwala ndithudi 😢😢
Thanks for the lunch mr bmtv
We never give up just go deeper the best ever TV in country wide
Mantha awo ndi DPP...long live Bakili Muluzi Tv
Home is best ,we are here as home always
Bakili Maluzi TV imabhebha ukakhala wa opposition side😊
😂😂ati nkhumba kkkkk ky milomo ngati mbali mwa phuno za ngo'mbe
Army congrats koma ndipemphe taonesani mphamvu kuti muonese anthu amenewa nyekhwe😊
Maso amakhala palemba kudikilila bakili muluzi TV
Bakili muluzi tv umakwana ❤❤❤❤
Ife amalawi sife mbuli tidzaonana 2025 a mcp mwachenjela pogona tidzaonana podzuka
watching all the way from kapinjonjo area
Khumba imeneyi 😂😂 point taken 😅😅
We are here for you my step father
True big boss
Best tv ever in Malawi timakunyqdirani Mr yankho ndi 2025
Thanks big ulemu wanu
Ulema kuhame ❤❤❤
Ndichfukwa chake ndimakonda bm tv more fire big man
Best tv
Iwe mulungu adzikuonjela masiku aumoyo wako ndithu.❤
Our pangolin
Ulemu wanu boss ❤❤❤
Mcp eeee yanditopetsa umakwana bakili muluzi tv ❤
Thanks bro God bless you osafooka ❤❤❤
May God continue guide you during this special job
Mbava nkhumba yachita kufufuma
Best TV ever
Anthu atutuwanji osafunila amalawi zabwino, munakhala bwanji anthu a MCP inu, mukutivetsa kuwawa ziko lokhala lathu zoona izi, kumalawi kuli njala, mafuta agalimoto kulibe , nawo mafuta ophikira akudula, nawoso augar chimozimozi zithu zake zonvuta kuzivetsetsa????????😢😢😢
Respect to my king ❤❤❤❤❤❤❤
Sitingafoke kumavesera beat teacher ❤
Inuyo ndi one man ❤❤❤❤
Love you ❤
We are with you brother God bless you
All the best BM TV
Salute ❤
God bless you brother man...
Sindingasiye kumvela bm tv, more fire big man
Koma bakili muluzi TV sazatheka akubwera bho❤❤❤
❤❤❤❤❤❤❤❤ ulemu wanu boss
Yes arm is our hope not police
Bakili muluz TV ❤❤❤❤
Komatu yah , tiyamike Mulungu basi
Anthuwa akufunika kt m c p iruze bas kt azarawe chirango ndithu achakwera akungoseweresa ndarama pomwe anthu akurira kt katundu wadura eeee
Big boss 💪❤🎉
Ameneyud chimwendo bandayi adzamangidwedi
I was waiting for you big
Mulungu akufuna kupulumutsa a Malawi thus why chilichose chili pa mbalambanda
Mulungu azilange mbuzi zimenezii🙏🙏
Osatopa osafooka agalu amenewa ayaluka chili chonse chikukhala pambalambanda palibe chinsnsi chikangawa wazele zeka ndi mwazi wa chilima