BON KALINDO LERO WANG'ALULASO__19 October 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 34

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Yes opposition wake up pls 🙏 we don't need this government again be strong 💪 guys 🇲🇼 opposition pls wake up now 🙏 💙 😢 we begging you guys 🙏

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    ❤❤❤ mr DC. Opposition please wakeup ndinakuwuzani kuti mec inene anthu wose omwe ali ndi ma ID district by district.
    Ife tili kumbuyo kwanu osusa koma musagone tikufuna kukoza.

  • @emmanuelmuyilaa
    @emmanuelmuyilaa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Awuzen Dc...Boma lolephera ili

  • @RajhMatola
    @RajhMatola 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chipatala chasalima chikukozedwa pan akalindo kazikamban haq osat zokuuzan anthu akunamizan

  • @jamesmsonkho4830
    @jamesmsonkho4830 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ma audio nde aaaa anenedwa koma amalawi iiii alitulobe ndithu zovesa chisono ngati action sikhalapo mcp iiii live izatengaso boma

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ulemu wanu bwana DC timakunyadilani

  • @SerahPhiri-l4i
    @SerahPhiri-l4i 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kod aboni kalindo angopanga zachakwera vuto chani kwenikweni moti azipangako zazeru akuchedwa nazo ine chizonda matapila ndatero

    • @DennisTobias-b4r
      @DennisTobias-b4r 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Akulimbana chifukwa ndi driver wa Malawi right now, bus ngati sikuyendesedwa bwino anthu samaloza ma passangers ai a maloza driver, wabwadwa liri let me remind you, ma presidents onse ngakhale chakwera amazuzula a dpp kuti sakuyendesa bwino

  • @PatricePhiri
    @PatricePhiri 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Auzeni awa anthu osanva

  • @elijahkasawala9122
    @elijahkasawala9122 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zomvela anthu aulesi izi

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mukungolimbana ndi a chakwera koma chakwerayo sakuyankhani nkomwe, ndie vuto lanu nchiyani? Mbuyomu mwakhala mukuti muvula n muyenda munseyu muli chivulireni chifukwa chot ma alubino akungofa koma lero muli kumbuyo kuikiraso omwewo amene ankapha alubinowooo ndie nkumati amalawi azikutsatani inuyo?? Shame on u akalindo. Chanzerutu ndikuyang'ana kwa Yehova basi not munthu obadwa kwamunthu ai coz ulamurilo wolamulidwa ndi anthu ndiolephera basi

    • @Kabwilachikangawa
      @Kabwilachikangawa 46 นาทีที่ผ่านมา

      Nanga si magazi amuchulukira mmanja ayankha bwanji

  • @elijahkasawala9122
    @elijahkasawala9122 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Musapake central region njala yakoyo. Yakukulila ndi nsanje. DPP sikuwina next year

    • @Kabwilachikangawa
      @Kabwilachikangawa 50 นาทีที่ผ่านมา

      DPP WOYEEEEEEEEEEEEEEEEE💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

    • @Kabwilachikangawa
      @Kabwilachikangawa 48 นาทีที่ผ่านมา

      Elijah kasawala vote is for Dpp 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC mwana woyipa kwambiri

  • @ibrahimjackson-cg6tc
    @ibrahimjackson-cg6tc 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma lake lachikangawa haaa paka ndikuopa2 kukwela ndege

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A opposition akumakhumudwitsa kwambiri, nowoso chemuthalika must come out and start to be more active in these issues

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The dc

  • @SerahPhiri-l4i
    @SerahPhiri-l4i 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ife tikanavota mcp

  • @CharieChristo
    @CharieChristo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DCCCCCCCC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Paja mulibe zochita inu zilubwani km musamalote kt mcp idzachoka m'boma mukunamizana mukhalila zomwezo or mutamaphatikiza mkulila km boma linapita ili vomelezani

    • @trickermussa472
      @trickermussa472 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mcp isachoke boma kuti ikupanga chani

    • @Halima-i4x
      @Halima-i4x 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kom pangan manyazi inu mcp mene akusuzila anthu aaaaaaaa ukuzinamoza ndiwe ndiboma lakho lakupha anthu lo zaziiii 😏😏😏😏😏😏😏

    • @ibrahimjackson-cg6tc
      @ibrahimjackson-cg6tc 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Amene akuimila Boma ili kumbuyo mitu yawo sigwira

    • @GiftManyowa-i2t
      @GiftManyowa-i2t 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Zanzii iwe ukakhl ukuona ngat ziko likuynda bwino ndeno Boma lake liti asazachokeyo

    • @Kabwilachikangawa
      @Kabwilachikangawa 47 นาทีที่ผ่านมา

      CADET OPUSA ULI MBUUUUUUUU KULI IWEKO

  • @LucyThambo
    @LucyThambo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo mukuyakhula kma apposition sakumva

  • @ashlackndema3232
    @ashlackndema3232 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DC 😅

  • @SerahPhiri-l4i
    @SerahPhiri-l4i 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kod aboni kalindo angopanga zachakwera vuto chani kwenikweni moti azipangako zazeru akuchedwa nazo ine chizonda matapila ndatero