ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Chilanga chabwino kwambiri.La 40 lawakwanila,hule,mbuzi,chitsilu cha munthu banja sichibale.Akolo Ake anamuvutikila iwe nkukapha.
Aaaaa ndikachikwama kkkk akavare waiti ameneyo
Umenewo ndi okamwalira osati kukaseva ndende ay
Pamenepo Ana awo akhala amasiye, zotsakhala bwino ayi
Hmmm ambuye atithandize tonse
Nanga chakwera adapha chilima,,,kunkuyu adapha witika,,,milandu yawo izaweluzidwa liti?
Azimayi mudzikonda munthu osati ndarama ayi ndiye mwaona izo mupite bwino 53 sipano mukawasatila amna anu
Mai mtima ulipheee, chuma akadyera kundende, akwera yakuphwa
😭😭pakana zaka 53
Zachita bwino kkkkk mwina akazi azitenga phunziro
Akalowe bas
Nanga chakwerayo akakhala zanga zingati Pomupha chilima ndi anthu 8? Zachamba tamumasure unyoloo mkamange chakwerayo ndinu achamba apolice akumalawi
Apanga bwino
Muthuyu chigamulo chachepa wamphatsogolo la ana athu lomwe pa retirement ya prophaser anakakhara akulemba mabuku osiyanasiyana uyuyu anakamuza Life in prison ment
Atengereko phunzilo azimayiwa
Malawi inathapo ndi mcp
Koma kokanjoyatu paka bagi manja kundende
Opha nzake naye aphedwe
All the days of your life sheeee
zinakhala bwanji kuti aphe mamuna wake
Chilanga chabwino kwambiri.La 40 lawakwanila,hule,mbuzi,chitsilu cha munthu banja sichibale.Akolo Ake anamuvutikila iwe nkukapha.
Aaaaa ndikachikwama kkkk akavare waiti ameneyo
Umenewo ndi okamwalira osati kukaseva ndende ay
Pamenepo Ana awo akhala amasiye, zotsakhala bwino ayi
Hmmm ambuye atithandize tonse
Nanga chakwera adapha chilima,,,kunkuyu adapha witika,,,milandu yawo izaweluzidwa liti?
Azimayi mudzikonda munthu osati ndarama ayi ndiye mwaona izo mupite bwino 53 sipano mukawasatila amna anu
Mai mtima ulipheee, chuma akadyera kundende, akwera yakuphwa
😭😭pakana zaka 53
Zachita bwino kkkkk mwina akazi azitenga phunziro
Akalowe bas
Nanga chakwerayo akakhala zanga zingati
Pomupha chilima ndi anthu 8?
Zachamba tamumasure unyoloo mkamange chakwerayo ndinu achamba apolice akumalawi