Dziko likuyenda bwino .yekhayo wamaganizo oipa achiwembu ndiyemwe akufuna kuti zofuna zake zikwanitsidwa but with God back to sender.oipa athawa yekha ndipo aoneka pa mbalamanda.
Akufuna kubweretsa di nkhondo a Mcp koma adziwe kuti kunja kuno kuli mulungu amene anawolotsa ana a Israel pa nyanja yofira ifenso amalawi atiwolotsa kwa akadzidziwa
Inuso Ambuye azikudalisani comrade salo❤
Mumakwana BG man kp it up 💪💯💯
😂😂😂 koma brother Sallo! I salute u😂😂😂
Anamiwa sanadye ndalama,
Amaona ngati kukakhala zachilungamo Koma awona kuti kuli zachinyengo
Munthu olandira ndalama sakanachokako
Brother Salo akunena zoonadi amalawi ife ndife anthu wogona kwambiri
Kuli bwino nkhondo ingoyambika bas,
Bro Sallo Malata akukufunini mukapelekere umboni uku
Koma namiwa ndakondwera kuti wachokamo.mademo sangapange chifukwa adikire kaye results of enquiry.namiwa olo ine ndinadandaula pomulowetsa mmenemo chifukwa akanamuyenda pansi anthu nkutaya chikhulupiliro
Brother Salo mumaganiza bwino ofunika kumawamenya
Mau koma amenewo Brother Salo
Sho brazer awuuzen
Dziko likuyenda bwino .yekhayo wamaganizo oipa achiwembu ndiyemwe akufuna kuti zofuna zake zikwanitsidwa but with God back to sender.oipa athawa yekha ndipo aoneka pa mbalamanda.
🤪🤪🤪👹🐊
Iwe ukuti nkhondo ingoyamba ndiwe chitsiru kwambiri umayidziwa nkhondo mxiiii
Akufuna kubweretsa di nkhondo a Mcp koma adziwe kuti kunja kuno kuli mulungu amene anawolotsa ana a Israel pa nyanja yofira ifenso amalawi atiwolotsa kwa akadzidziwa
Cry for my beloved country
Iwe Salo machende ako. Pita kusiukulu
Sono ine ndili ndifuso nkhani ya NRB azipani zosutsa angoziyangang'anila nzikuchitika izi?
Akufuna kuyambisa khond kodi akhondowo akufuna akhale IDiami wodya matako anthu ache
Palibe chomwe mukupindulirira amalawi kungofuna kuti anthu azichemerera zabodza tatopa naxo izi
Awa a mcp awononga nde dzochoka pali nkhondo madeemo basi kupanda apa aaaa amalawi 2025 tikufa ndi mcp
Palibe chotukwana ndi zowona brother salo
Tipephe kuti amangidwe onse ose akuluakulu aNRB ngati sakungidwa amenewa mkwiyo woopys kwambiri pazonse akupanga
Iweyo ndiweso wamatha kwambili uyambe iweyo
Bodza ilo brother sallo tiyeni tiyende limodzi namiwa sanadye bazi
Ndipo sanadye olo pang'ono
Koma bon kalindo umakwa mune zikukwalila kujoz pano a police akugwira moipa komaso Anthu akumvayako kujozi kusakhutisidwa zimene akupanga namthu chakwera mbuzi yamunthu ayiso bulambuzi imadibwa koma ikhare galu chakwera iwe tiye nazo wakhura watha poti wazimvera zulo kumene kunali atolankhan ose
Ukunena zoona
Salo nawe uliso chisilu wamva? Ukuti ulibe chipani koma izi ukulakhula apa Mesa zikuonekeratu kuti side yina? Uli wa Dpp takuziwa
Braz ifeyo tifetife Kom achike bc
Big up brother
Inuso Ambuye azikudalisani comrade salo❤
Inuso Ambuye azikudalisani comrade salo❤
Inuso Ambuye azikudalisani comrade salo❤
Inuso Ambuye azikudalisani comrade salo❤