Problem ndi munthu ovotayo, kuvotela Dzitsilu, Pastor angakhale mtsogoleli wa Dziko? Education yake ndi yotani, ma Subjects ake anaphunzira zotani. Dzitsilu dzikupanga run Government.
A president a Chakwera ali ndi kufooka pocheuka ngati zinthu sizikuyenda ,komanso from day one,anaonetselatu kulephela utsogoleli posankha nduna potengela kuti zidawathandiza kupanga sponsor campaign. Apule alibe chikondi ndi dziko ,he is more than a typical political when the expectation were that he is a man of God. Bodza komanso kukamba kopanda action zaononga mbiri yawo . Akuyenera akhale pansi ndikumvesela uphungu ochokela wa anthu omwe alibe cholinga pa ndale koma kutikula dziko ndipo sikupusa kupempha mzeru even from the opposition chifuka is about taking the country forward.
Solution is not borrowing that is creating burden to the future generation.. Solution is citizenry start producing including you Brian, Jona and Wonder create programmes that can encourage production. Social capital/ network ought to be there for building of human capital. We messed up selling companies, we messed up stopping mega farms Kamuzu built with Malawi Young pioneer that was the basis of production and exportation. We only looked at the bad side if at all it was really bad
Analowa m'boma mwangozi amenewa i doubt ngati 2025 apitilize body language can speak. Nafeso kuvotera munthu woti economics zero sazawa za economy akungozizimuka pochita zinthu
Apa zafikapa nafeso tibwera ndi ma kk 47 athu tikamabwera siati Ali ready or nkhondo chifukwa choti sakufuna kutuluka muboma afuna kukhalira makanimo kuno mfuti sivuto ikhala yachisawawa kumeneko zili chaka chamawa Kaya apa ndikufufuza Malo kumoshiko ndigure ndingomanga nyumbako chifukwa malawitu basi watheratu
Shame on them indeed I strongly agree with you great leaders on Times They were talking too much,we thought they will deliver But mmmm very bad Lord help Malawi You created us to be Malawians Father God in Jesus name,rescue us,wake these leaders of this nation from their carelessness and selfishness; Thinking of themselves while Malawians are suffering. In Jesus name we pray Amen.
Mvuto si boma km ife timafuna kusintha paja Banda yo analiso modzi mwa anthu amene amayipasa moto lero zatani coz anamuchosa ku nyumba ya chifumu basi tizione mpaka tizigwire
You guy's you are the best regards for us Malawian 🔥🔥🔥🔥
Problem ndi munthu ovotayo, kuvotela Dzitsilu, Pastor angakhale mtsogoleli wa Dziko? Education yake ndi yotani, ma Subjects ake anaphunzira zotani. Dzitsilu dzikupanga run Government.
Koma zinthu adanena kale kti MUDZAONA NYEKHWE MUKASANKHA MOPUSA,NAYI NYEKHWEYO.
Bomali lizipita lalephela atulepasi udindo a mcp mwalephela kuyendetsa boma
Ali busy Kufuna kubela ma vote shame on them mavuto ake amenewa?
Nde wina aziti boma ndilomweli🙌
ANTHUWATU AKUDZIWA KUTI AKUTI USER IFEYO AMALAWI NDIPO AKUDZIWA KUTI AKACHOKA SAZABWERERANSO MBOMA. NDIPO KUKUFUNIKA IFEYO AMALAWI TIKHETSE MAGAZI KUTI ANYANI AMENEWA CHOKE. CHIFUKWA ATI IWOWA SANGACHOKE MBOMA. NDIYE IFEYO TIKUYENELA KULIMBA MTIMA KUTI MPAKA TIPHEDWE BASI MPAKANSO ZITSILU ZIMENEZI ZICHOKE MBOMA. GRACE TCHINGA ANALOTSELA KALE ZA CHIPANI CHA MAGAZI. LERO CHIPANI CHIJA MCHIMENECHI .
Respect Dr Joyce band former president
I love u guys for gd message
Kkkk boma ndilomweli lopoila ndithu zaukape zenizeni😅😅😅
Moses kunkuyu mbava yen yen Kaya umwana wake anali otan munthu wabodza ameneyu😂😂😂
And I quote 'Network sabwerekana' I second our former Her Excellence.
Chakwera knows that his time is over that's why he doesn't care anymore
Kkkkkk dziko lathu mwachuluka mbava zikulu zikulu koma zimaziva kuti zozindikila koma zili eputy muubongo wao
Mulungu anawachotsera mzeru awa kkkkk
Come on you gyz
Ku UNGA anabwelako chabe ,kukathelako ma dollars
A president a Chakwera ali ndi kufooka pocheuka ngati zinthu sizikuyenda ,komanso from day one,anaonetselatu kulephela utsogoleli posankha nduna potengela kuti zidawathandiza kupanga sponsor campaign. Apule alibe chikondi ndi dziko ,he is more than a typical political when the expectation were that he is a man of God. Bodza komanso kukamba kopanda action zaononga mbiri yawo .
Akuyenera akhale pansi ndikumvesela uphungu ochokela wa anthu omwe alibe cholinga pa ndale koma kutikula dziko ndipo sikupusa kupempha mzeru even from the opposition chifuka is about taking the country forward.
❤❤❤ Mwalangula anyamatha
Solution is not borrowing that is creating burden to the future generation.. Solution is citizenry start producing including you Brian, Jona and Wonder create programmes that can encourage production. Social capital/ network ought to be there for building of human capital. We messed up selling companies, we messed up stopping mega farms Kamuzu built with Malawi Young pioneer that was the basis of production and exportation. We only looked at the bad side if at all it was really bad
Shaaaaa mafuta ngambwi ngbwi mu train mudali atanyamulamo nthoch😢😢😢😢😢
Apule ananena okha ndipo zilipo tinasunga, anati nsiziwa zambiri that means connection alibeso ngakhale nduna ya financi ulibeso connection, vote yanga amayoooo
❤❤
Joice anali ndi nzeru kwabasi ngati si nkazi koma Chakwera ukutanimo mu Boma ili
Anthuwa alibe chikondi ndi anthu awo samadandaula mavuto awanthu Bola Iwo zilibwino koma akudwala kuti tsiku limakwana adzawafuna amalawi😊
The level of Malawi has reached its better just to sell the country... maybe they can manage wiser than chikangawa.
Kumkuyu was humble for the 1st time
Angovomeleza kuti kuba anyanyiza muulamuliro wao ndiye achepeze kuzitamandira avomeleze kuti telem yaoyi zavuta
Boma ndilomwelidi la Malawi zoona .chikufunika ndikusitha chipani ndi Sogoleri
Kkkkkkkkk anthu oyakhulutsa pambali km chakwela iweyo 😱😱😱😱😱
Akungoba ndalama ku Mera achipani cha mcp
Anakakamira Boma nzeru zochita alibe bola alemera basi nanga ankaoneka choncho dzana
Ku Malawi tilibeko president tili ndi nduna zonkha ndizomwe zikuyendetsa Boma basi tizankhara ndi president 2025
Ngati amamva apule achitapo kanthu thanks
Kkkk mr confirm
Cabinet members yose ya chakwera
Ndiyoputsa akulepela kukotsa sinthu akweni zuro analakhula kale kumiteeng ya zipani sosutsa
Times serious anthu inu simu tenga mbali keep it up brother's his country we don't have readership 😢😢
exactly
Analowa m'boma mwangozi amenewa i doubt ngati 2025 apitilize body language can speak. Nafeso kuvotera munthu woti economics zero sazawa za economy akungozizimuka pochita zinthu
Munavota nokha ndye ndzmenezi ,limeneli ndphuzilo,tiganize bwino 2025.
Ineyo ngat zika yadziko andale akhale oyimba pawokha boma palokha Malawi ayamba kuyenda bwino
Akom magaeziwa akula mmatama ayiwala
Shaaa komaaa nkhani zake nzosautsa,,mafuts ngambwingambwi analephereka??eish 🙆💔
Zonsezi zikuchitika chifukwa cholephela kuyendatsa bwino dziko. Siubusatu uyu 😅
Zopesa chisoni my home kom tupele anakuusani osafa 2025 boma tupere pamosi nd dpp oyeserekusangaso m chakwera pamenepo kuposa
😂😂😂😂😂😂 boma ndi lomweli
Ipase moto Alusandrio 😂😂
Dziko la Malawi ndilomvetsa chisoni atsogoleri olakwitsa awa asatilankhulitse kuipa awa
Eshiii zowawa
Apa zafikapa nafeso tibwera ndi ma kk 47 athu tikamabwera siati Ali ready or nkhondo chifukwa choti sakufuna kutuluka muboma afuna kukhalira makanimo kuno mfuti sivuto ikhala yachisawawa kumeneko zili chaka chamawa Kaya apa ndikufufuza Malo kumoshiko ndigure ndingomanga nyumbako chifukwa malawitu basi watheratu
Palibe zo bwelekana ma nextwo6
🔥🔥🔥🔥🔥🔥 kuti bhuuuuui
Ku Malawi nkokoma
What I really don't understand is that chakwela and his team is moving around with his convoy of huge team where did he get fuel😂😂
Kodi anabwera pa sitima from Mozambique aja tamwa kale tamaliza?
No more mcp get out🔥🔥🔥
Ndiyankhure Pano mosabisa mau.tikuvutika kusowa fuel Pano chifukwa ma dollar 💵 atha kuba
Andevu zamwayi a kukhuyu mungochedwa nawo chifukwa awa ndamene amatotera ndalama kupitisa ku mcp
Na apa pamafutapa ataya mavoti
We have a sleeping President i HV never seen bf in Malawi
Vomelezani, kulamula dziko kwakukanikakani
Rest in peace Mcp
1:15:54 1:15:59
Chakwara warephera kukoza zithi
Akukanika kupeza mafuta koma kukacha mmawa nkumati akupita kuntchito eeee shem on u.
Maulemu madolo ,timenyeleni khondo😂
Tisamangoonera ayi. pazinthu zmwe zikulakwekwa ayi.kd Asilikali mulikutiko.
Apa ndamva aBig kachaje akt tizithira pangono pangono kma truck ikupita Mozambique yanyamula fodya nde muipatse 30Lts Kodi akafika kapena akupita Bt yomwe ndi 200 Lts Kodi akafika apa angotiuza kt no fuel 4 trucks bc
Achakwera patumbo pake ndi nduna zake zonse mbuzi za anthu
NDUNA YONAMA
Chakwela felled for everything he must step down
We don't need chakwera anymore
Chakwela ndi galu kwabasi
Guys a malawi mafuta tikugula sitikungongola ndiye ndalama zikupita kut!!!??
Mumatha madolo asambwazeni ndi afiti awa azingoona soka sanati,,, dziko ili kuli mlengi wagwa nayo kungoononga dziko.
Kapumen bwino guys
Dziko lathu mpaka pamenepa ai apule mwationjeza
Siku lina awa azandiitane pa program imeneyi 😢
Akt mavuto ndomwewa tidzivutikabe mpaka 2030😂😂😂
A Chakwera anyannya kuzizira.Msewu wa Tsamgano..Neno watenga zaka 12 kamanga 7kilometres
If you don't think this is crisis then what is it??😂😂😂😂 Bravo brovo guyz🔥🔥🔥🔥🔥
Bolaninso kuchigayo
Komatu nde mavuto osatha
Sakonda dzikol. Chakwera is weak. The lack of Accountability will cost him.
Boma ilili ndi lachamba
Ndipo live
Koma nduna yazachuma akamutenge Mlimi wafodya kkkkkk guys Pena pake tizikhara serious
Akutimenyera campaign abomawa asiyeni
Zoona athu awa sakupanga bwino
😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅ndinanenatu eee ndiye mwaona nyekhwe eeeee
Shame on them indeed
I strongly agree with you great leaders on Times
They were talking too much,we thought they will deliver
But mmmm very bad
Lord help Malawi
You created us to be Malawians
Father God in Jesus name,rescue us,wake these leaders of this nation from their carelessness and selfishness;
Thinking of themselves while
Malawians are suffering.
In Jesus name we pray
Amen.
Mvuto si boma km ife timafuna kusintha paja Banda yo analiso modzi mwa anthu amene amayipasa moto lero zatani coz anamuchosa ku nyumba ya chifumu basi tizione mpaka tizigwire
We support you guys serious
Why is checking like that be approve
Boma lolepheta ili
Kod akut mafuta amagulisa pamakwacha makwachawo alipo kapena ayi
Forex inakathera ku Unga
Eeeee guys zithu nde zafikapo km izz mpaka lit
Brayan banda asamaname
Kd mesa iwowa anali nalimlangizi waboma chinachitha ndi chiyani
Awa km kupha not ma plan oendetsera dzik
Kumkuyu uziyamkha ngati wamzelu chifukwa ukutiwuza ife sife Ana wangokula mutu iwe
Ku Canani tikafika tatopa
😂😂😂😂 Moto ukusowa simukunama ma guys
Shap
Kodi ojambula video yi alibe stand? Zithunzi zikungoyenda yenda.
Ndalama ahongera anthu kuti awinenso nde moyo wake umenewu, ayi sikomo
😂😂😂😂😂i can confirm kunalibe guys