ZAKHALA BWANJI KUT UTM ITULUKE MU MGWILIZANO??? TAMVANI IZI ABALE!!

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 17

  • @chelseajackson3200
    @chelseajackson3200 3 หลายเดือนก่อน

    Excellent critical analysis with less biaseness. In addition, any agreements should be constitutionally & legally binding.

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 3 หลายเดือนก่อน +5

    Program yapamwamba kwambiri pa Zodiac, ndipo ma analyses odziwantchito yawo, osati ngati a ku MBC amangosapota MCP ndi chakwera ayi.

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 3 หลายเดือนก่อน +2

    Usi
    Uvice wake mma book sadzawelengedwa kuti anali vice president wa dziko
    Ngati ndichoncho Chimulirenji aloweso mma boku

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki 3 หลายเดือนก่อน +2

    Mwini wa wamgwilizano wapita palibe kudikila watha watha

  • @LewisJumbe
    @LewisJumbe 3 หลายเดือนก่อน

    Apapa pali bwino,ayembekeze chani? Mufuna aphenso ena?

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 3 หลายเดือนก่อน +2

    Apha chilima

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy 3 หลายเดือนก่อน

    These gyz amandsangalatsa

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 หลายเดือนก่อน +1

    MCP you mast go

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 3 หลายเดือนก่อน

    Koma school ya ubusa ,achakwera amkaphunzila mabodza
    Bwanjii anatinamiza like that
    Kuma ka signer mgwilizano
    Ndiye anzathu inu ophunzila dzima dokotala dzanudzo mumaphunzila mabodza etii
    Dzima dr mbwee alimaboza okhaokha.
    Ife anthu akumudzi mumatinamiza chifukwa chiyaniii
    Fertilizer otchipa mtengo
    Mmmm chichakwera mchabodza ichii
    Misewu akulima ku town amakhalako
    Kuno kumudzi ai
    Mumatifuna nthwawi yamavoti
    Chichakwera chisabwele kuno
    Chifukwa mabodza ake tatopa nawo

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug 3 หลายเดือนก่อน

    Did u not see that sanapangepo kathu

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 3 หลายเดือนก่อน +1

    Mumatitsegula m'maso anyamata inu.

  • @kunjemangandale1118
    @kunjemangandale1118 2 หลายเดือนก่อน

    Utm yaganiza bwino kwambili acoding to the death of skc ndipo manganya ndi fisi

  • @FranciscoJendala
    @FranciscoJendala 3 หลายเดือนก่อน

    anthu ambiri amafuna mgwilizano utatha tipange zosangalatsa anthu ambiri osati zaochepawo akufunakukhutitsa mimbazawo

  • @Stewartchikoja
    @Stewartchikoja 3 หลายเดือนก่อน

    Zatha zatha

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug 3 หลายเดือนก่อน +1

    Bodzatu ili palibenso kudikira Mr Kaiyatsa mukuyankhula ngati simumakhala ku Malawi bwanji

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki 3 หลายเดือนก่อน

    Kd inu mgwilizwno siunali wa chipani ndi chipani unali wa chilima ndi chakwela ankaka anakana pa tv kt siinapeze lalata yamgwilizano

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 3 หลายเดือนก่อน

    You. are wrong completely utsi is not party