ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
❤❤❤❤❤❤❤ Love you so much Mr Comdrade Ntanyiwa ndiweyo amene ukuteteza mdziko lanthu Ambuye akutetezele
Monica chakwera ndiwe Mai oipa padziko lose lapasi 😢😢mulungu akupase nthenda yakusi
Good work big am listening right from north of Mozambique in Nampula.
You're number one Comdrade Ntanyiwa
Limpopo FM you deserve your respect
Ulemu Wanu Limpopo FM, watching from England. SKC Rip 😢😢😢
God is not asleep still sitting on the throne and is watching. 😢😢😢
😢😢😢 Ameeni eunice ameen osafooka ku pemphera iweeso mulungu akudalise
Allah akutetezen
Live from Port tiutseni soona shonde this is the best way take care always about Malawi people what's all Malawian is going to be frrend sheep about shilima 😭😭😭😭
Ppp
Asapiteko kumaliloko bolani alilile kunyumba mmmmmmmmm tili ndi matha ife. Atiphelaso APM wathu.
Heart broken
Kumvumbulutsa nkhani kopotsa MBC 😂😂😂
Koma chakwera😢😢😢😢😢😢😢 ndi anzako tapangani dzinthu dzomanga dziko musaiwale nanuso mudzafa
The best Radio station in Malawi
Limpopo fm ulemu wanu❤
Zovuta izi ngankhale Satana wankhuzidwa kwambili chifukwa cha chakwera
Y Malawi
Palibe mulandu munthu kusapita kumaliro so it's better for APM not go to the funeral service, thanks Mr. Mtanyiwa
Khoswe wa PA mpani saopa kuola
Timva zinthu
ambuye akudaliseni pitilizani osafoka zimatelo akufuna kubwelesa nkhondo ziko ngakhale thelele timadya bola tili ndi mtendele osati khondo
chilima wafeladi manja mwa ng'ono sure chikumbu mtima ndichachabe
bola asatire malangizo
Ukuwopa chani tangobwela kuno ku Malawi ngat ndiwe woziwa zinthu
Guys zinazi osamangokhulupilira mwamva... A Malawi koma eeiisshhh
Limpopo fm woye 😂🎉😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Koma inetso sindimafuna kumva za MCP makolo anthu anavitika kale ndimava chisoni mpaka lero anthu kumakavotera MCP
Ndi wasatanic uyu galu ameneyu
Tilitchelu tiuzeni zambiri
Very good tikufuna anthu ngati inuyo kuti Malawi ankodzedwe
akutetezeni allah pachina chilichose allah'ma ameen
Khoswe wa mpani saopa moto.
Mulungu akukuteteze Comrade
Ndipo inu alimpopo pulumusani aMalawi sakuziwa Kuti akupita Kuti ndipo ndizithu zonvesa chisoni zikuchitika ziko lamalawi Kodi ana akubadwawa azatani 😭😭😭😭😭😭
Bola asapiteko APM yo
We love you too much Mr without you were nothing, keep on giving us all information thanks
Woipa athawa yekha
Mr Ntanyiwa kawawa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Cifukwa cakuuma mtima mu 2020 a Malawi munasankha Satana kuyendetsa boma. Kaini anapha Abele . Anacita izi polephera pamaso pa Mulungu. Pamene Chakwera wagwetsa Dziko, waona ca nzeru kupha anthu.
Braz ndinu mpulumutsidi wa dziko la Malawi tapitilizani abraz zomwe mukupangazo
Ntanyiwa
Anthu tipulumuka chifukwa chainuuuuu
Misozi yosatha usiku usana
Kd kupanga zonsezi cholinga kufuna kukhalaso boma ayiii kah muthu umawina chifukwa chachitukuko 😊
kkkkkk uncle chakwela uli mmadzi
Timadabwatu
Malawi okomera tonse uja mmmmhhhh
Ndipo please call APM asapiteko akafela zaweni
Mumakwana big
Mnthanyiwa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndipo amene ali number ya APM please muimbileni asapite kumaliro please please azakonze nthawi yodziwa yekha akapepese kubanja la VP please chonde ndikanakhala kumalawiko nkadzseyesa njila yonse paka ndiwaziwise please
Akufuna atsalemo okha mudziko muno aaaa😂😂😂😂
Ngiyabona mthanyiwa khuruma wena thetha kakhuru
Chokanso iwee namachende okupha iwee ukuona ngat sindikuziwa maphwaxy ako
So sad indeed 😢
Eeeee koma zimagalimoto zafikazi mwadziona eeeeeee akuti kuopseza anthu
mufuna mutiwuze kut imfayo yikukhuza gulu lanthu ambiri et? nde mpaka ena azipereka nsembe okha kufa nawo??? koma zinthuzi zikupweteketsa mutu bwanji?????
Ukubwera bwino
Eish xilikotu ziliko😢
Inu a Limpopo ndinu akathyali munkat phoni ya chilima yasowa koma akubanja akut zonse alinazo kunyumba kwao zitsiru inu ndipo ngat mukumpangira kampeni peter mugwa nazo
Ndani yemwe anakapereka kubanjako nawe mmm
Ngati akapereka, aopa kuyaluka coz ma investigators alamula kuti airtel and tnm ipange trace ma phone. Tamaganizani anthu pliz, osati kakaka MCP ikupanga zopusa
Ndipo ngati akapereka, akudziwa ma investigators akangolamula kuti tnm and airtel to trace network, ayaluka. Think 😅, osangokonda chipani, kondani munthu wamzeru
Inunso ndinu ofoila. Tizaona nthawi yopangatu ma investigation
😭🇲🇼
Zisisi ndi zamwini mulungu
No bus can drive there liers
Chonde chonde chonde chonde a DPP Mvetselani ndipo tsatilani malangizowa please
Khoswe wa PA mpani saopa moto
Inu musatinyase apa tamangopitani uko tsiku lina chizachitike kwanu udzawone mmene moyo umawawira
Ndipo ameneyu nduoipa
Wakhuta Bonya ameneyooo mutayeni
Iwe nde bwanji osamupitila konko?? Usiye zopanga comment ma TH-cam video ndipo umupitile konko ngt uli dolo. Ndiwe wamanyi kwabasi
@@LeendaDeborah2005 inunso openga kwambr mpaka kuletsa azanu to comment kd ukukhulupilira kt galu ameneyo angakuthandize iweyo