CHAKWERA ndi APM TINGAWASIYANITSE BWANJI?...KANDIMVERERE 14/05/24...CHAKA CHAMAWA kuli gule.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 พ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 527

  • @nkhangani.t
    @nkhangani.t 10 วันที่ผ่านมา +2

    nkhani yokhudza age singapange affect utsogoleri zosatheka because tikayang'ana dziko lonse lapassi azitsogoleri azipembedzo komanso ena andale ndiachikulire so ife amalawi tisafoyire ndi bill ya agemet leadership isnot age but wise.

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v 17 วันที่ผ่านมา +19

    Account number one ili ndi ife? Why blame the people, Chawezi you are exposing your stupidy ndipo uwononga Mibawa TV imene sinali political.

    • @petersomanje5632
      @petersomanje5632 16 วันที่ผ่านมา

      Aaaa chawez ndwe mbuzi ya munthu ndwe wa mcp galu iww

    • @JohnManuel-vm5mw
      @JohnManuel-vm5mw 12 วันที่ผ่านมา +1

      Chawezi mbuli ndiwe ndi makolo Ako ndi mcp nonse

    • @user-oq7hi3hd4p
      @user-oq7hi3hd4p 12 วันที่ผ่านมา

      You are so pompous. You can't say over 20 million Malawians are savages. Thus stupidity.

  • @hawabanda-xs5fx
    @hawabanda-xs5fx 16 วันที่ผ่านมา +7

    Bola ndi Peter sitimagona ndi njala timwamwaso tea

    • @isaacchirwa9518
      @isaacchirwa9518 16 วันที่ผ่านมา

      Nde dziko limenero m'bale wanga, or nthawi ya Peter ija enanso tea sankamuwona because 900 kwacha ankati wakwera mtengo kwambiri, panonso chimozimozi

    • @riversofgrace8350
      @riversofgrace8350 15 วันที่ผ่านมา

      Inu mumadya ena samadya that time mwene .. moyo sukoma mbari zonse or nthawi zonse

    • @JohnManuel-vm5mw
      @JohnManuel-vm5mw 12 วันที่ผ่านมา

      Peter yemweyi Ali khenge

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 15 วันที่ผ่านมา +2

    Iwe dpp ndi matchini wena lilongwe mene anayisithila

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 16 วันที่ผ่านมา +4

    Akulu mukuti Chaweziwa ndi mbuli yamunthu ndithu mmutu mwawo mwadzadza mamina. Zoona munthu amene ali nzika yamalawi sangamatsutse kuti zinthu zakwera ndipo zikusiyana kwambiri ndi nthawi ya a Mutharika.
    Amibawa chonde mudziyamba mwayeza ubongo wamunthu musanamibweretse apa. Ndimati ndikuuzeni kuti akuluwa akubwera awa a chaweziwa asadzabwereso pano ndipo muwauze apite adzikapanga campaign ndi a Chakwera coz uyu ndi wa MCP

    • @chimwemwechathapo6405
      @chimwemwechathapo6405 16 วันที่ผ่านมา

      iweyo kulesa kuti ziko siliri pabwino?.. omwe mukunjoya ndi boma ili ndiwomwe mumabakira bomali... koma ziwani kuti akamakupasani dolazo sakupaza ndi azibale anu omwe. abale anu akuzunzika ngati ife ndipo akugona ndinjala inu mukudya bwino ndi chakwera

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e 16 วันที่ผ่านมา +2

    Chawezi which side u re?tell us now,

  • @TarPoor-ye9jx
    @TarPoor-ye9jx 16 วันที่ผ่านมา +7

    Vuto ndilot ukakhala pasana pa mjovu usamati kulibe mame ngat Inu muli oziwa mavuto amalawi osamangopanga blame dpp only u should blame also government as well. When dpp was ruling thing wasn't same ndpanopo things is worse Inu zot amalaw akumfa ndingala of course mvura inavta koma ena sanakolole kamba ka fertilizer anadura and wa sabuside sanalandile pitan ma shop akumudzi mukayang'ane soap,salt,soda, body lotion and chigao chadura umeneo ndi umoyo wamunthu wakumudzi that everyday life ndemusamabwele pano kumanena za dpp that nonsense inuyo mwalandila ndalama kuboma ndipo muchta kuoneka kut ndnu a mcp please amibawa musatipangise kusakupangan follow pazawande ngat ameneyo ndibwino mundu aziima pachilungamo but don't blame dpp just blame all politics if their doing wrong. Mcp is very corrupting government don't think the Malawian their don't see it ... let's wait and see 2025

    • @Mike-du7zt
      @Mike-du7zt 13 วันที่ผ่านมา +1

      Kkkkkkk amufuse hope chisanu

  • @peterjoshua2595
    @peterjoshua2595 16 วันที่ผ่านมา +4

    Uyu mukumuti Chawezi agwesa mibawa, I follow Mibawa chifukwa cha Bima

  • @MayankhoKalenga
    @MayankhoKalenga 8 วันที่ผ่านมา +1

    Chawaz amakonda amalawi alind zeru l would like to meet dat dude

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 17 วันที่ผ่านมา +5

    Mr Sandra ma feel anu mkulu akuyakhula mfundo zompand mzeru chawezi wanuyu,alanine kuti Malawi wakwera kwambiri muthWi yachakwera,koma akuganiza ameneyu.

    • @user-hg6qp4hs2m
      @user-hg6qp4hs2m 16 วันที่ผ่านมา

      Chawezi...by the way you are very very very useless. Don't think you are too wise.
      Sandram plz tell your friend
      Zasataniki zunena nzakoyo akagwereuku Kaya

    • @user-df3wo4us7h
      @user-df3wo4us7h 16 วันที่ผ่านมา

      Ndi kape

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 17 วันที่ผ่านมา +5

    Mmm chewis ukuchita kuonekerat kt iwe ndi wa mcp bas ,anali ose ku amaleca

  • @SameKaposa
    @SameKaposa 16 วันที่ผ่านมา +1

    Koma chawezi ndiye wathilidwa mphepo eish watukwanidwa ase

  • @georgenambazo6031
    @georgenambazo6031 14 วันที่ผ่านมา

    Cholinga Cha program Yi kd ndichani!? Ena azinyozeka kd?

  • @robertnambazo9936
    @robertnambazo9936 17 วันที่ผ่านมา +8

    Chawezi sukuziwa how Malawian are crying out there uzipita kumudzi and see how much people are suffering kulephela kudya phalala ayise

    • @KingsonSmart
      @KingsonSmart 12 วันที่ผ่านมา

      Mzofunika Civic education izi kuti tidzizindikira osamangolozana Chala kuti iwe walephera ayi

    • @johnbullyohanittokasikizim7127
      @johnbullyohanittokasikizim7127 3 วันที่ผ่านมา

      Tiyeni tizingoganiza ngati nyerere osati zaanthu andalezi.

  • @aloysiusdidymus7869
    @aloysiusdidymus7869 16 วันที่ผ่านมา

    Common sugar nayo anakhuzidwa? The same sugar ku Zimbabwe is cheaper than kuno

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v 17 วันที่ผ่านมา +15

    Chawezi ukuonekela kwambiri kuti ndiwe wa MCP

    • @benjulius6070
      @benjulius6070 16 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂ndikape uyuu

    • @JohnMakokola
      @JohnMakokola 16 วันที่ผ่านมา

      Iyeyo zoti mafuta magalimoto sugar ndi zina zotero zinasika saziwa wa mcp uyu

    • @user-df3wo4us7h
      @user-df3wo4us7h 16 วันที่ผ่านมา

      Ndi kape

    • @user-rk3gq7gd8f
      @user-rk3gq7gd8f 16 วันที่ผ่านมา

      Wa mcp uyu usasokoneze amalawi iwe ena ambili amapita kusukulu kukathesa umbuli koma iwe unakangowonjezera

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 16 วันที่ผ่านมา

      Kodi kape ameneyu ku MBC Kuja anachokeranji uyu ndiwa matama kwambiri.. Osokoneza anthu..

  • @user-zq3uf5bc8v
    @user-zq3uf5bc8v 16 วันที่ผ่านมา

    Hie hie guys where is chawezi banda is it work at mibawa TV

  • @masalinodovu1705
    @masalinodovu1705 16 วันที่ผ่านมา +4

    Chawezi wagwa anyone iwe. Ukawauuze adakutumawo Kuti ovota ndifeyo komanso mcp 2025 ikupakira basically ationongera dziko. Mcp ikachoka ndipo siidzabweleranso mboma

  • @NedsonKachoka
    @NedsonKachoka 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiwo chitsilu kwabasi pa m'nyelo pako machende othimbilirawo

  • @lovenessmtambalika-ky5vj
    @lovenessmtambalika-ky5vj 13 วันที่ผ่านมา

    Zoti anthu akudya phala lothira jollyjus achawezi mukuziziwa? Panotu amalawi akuzindikira chikaipa kuchosa kusakha , inu bola mukumapita kuja mukulandira ma allowances tiganizireni ife tikati tapeza ndalama talima ma ganyu

  • @JosephChitseko-ro9fv
    @JosephChitseko-ro9fv วันที่ผ่านมา

    Chawezi pathakopako garuwe

  • @NumbDee
    @NumbDee 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi ndi wa MCP

  • @OdreckNdemanje
    @OdreckNdemanje 16 วันที่ผ่านมา +4

    Yes,Mutharika did it in 2014,he tuned around the economy after Joyce Banda and cashgate.
    I think Chawezi is out of his mind.

  • @allandaviemawingo4719
    @allandaviemawingo4719 16 วันที่ผ่านมา

    Pamene chawezi akulakwitsa ndipati? I have watched this program twice hoping that I will find where he went off track, I can't see...tandiunikireni able polakwikapo.

    • @chimwemwechathapo6405
      @chimwemwechathapo6405 16 วันที่ผ่านมา +3

      aise.. galu amagwedezera nchira munthu yemwe amamupasira chakudya.. ndye chawez akuonekeratu kuti ali ndi ma benefit from mcp coz analyst saona mbali. iyeyu mwachidule watumidwa coz mfundo akunenazo akanafunsa kaye chakwera kuti iye anati 6 months azakonza ziko koma wakanaika. ndye akalese munthu wanea za 2 years?.. akudya nawo za mcp uyu ndipo ngati nawe ukuliona bwino boma ili sungakambe zoipa za chakwera coz ukudya nawo zabwino kuseri

    • @allandaviemawingo4719
      @allandaviemawingo4719 16 วันที่ผ่านมา

      @@chimwemwechathapo6405 kkkkkk ai aise, ine sindimakhala kumudziko...komanso i have never benefited from any government whatsover, koma i was just analysing zomwe akunenazo...kwaineyo there is sense in whatever he is saying...sure aise..koma ulibwino aise?

    • @Yamikie-yamikie
      @Yamikie-yamikie 16 วันที่ผ่านมา +1

      He is taking like mmbomamu simukuchitika zoipa
      Always kusambwaza dpp.. Nde poti akuti ndiyolipilidwa.. Nde we don't know who is paying for it

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi ndi wa mcp

  • @danielmakina5770
    @danielmakina5770 13 วันที่ผ่านมา

    Chawezi wazionongela mbili ndithu koma ndiye ndimakukonda bwanji ok

  • @MayankhoKalenga
    @MayankhoKalenga 8 วันที่ผ่านมา

    Chawez ❤

  • @PeterMakaika
    @PeterMakaika 14 วันที่ผ่านมา

    Ameneyi ndi kape Chawezi...

  • @user-qz1rp5mh9e
    @user-qz1rp5mh9e 12 วันที่ผ่านมา

    Chawezi muwononga Tv yathu Mibawa Ipay for you lets go for zambia

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 16 วันที่ผ่านมา +1

    Chawezi ndiwe mbuzi program yopepera,,, dolo ndi Brian Banda sawonetsera kuti ali mbari itiyo

  • @user-ux9ik4zr5x
    @user-ux9ik4zr5x 16 วันที่ผ่านมา

    I agree with you Chawez Banda

  • @NicholasKwajama
    @NicholasKwajama 10 วันที่ผ่านมา

    Anyamata onsewo akufuna ku parliament

  • @user-pd2uw9rn5s
    @user-pd2uw9rn5s 14 วันที่ผ่านมา

    Mapazi ako chawezi

  • @SamSaiti-bl6bk
    @SamSaiti-bl6bk 14 วันที่ผ่านมา

    A Chawezi!!!!

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 15 วันที่ผ่านมา +1

    Joyce banda anawononga dzikoli apm anakudza apatso akudziwakuti ama sokonedza ni chilima ku dpp ndiameneso akuba ku mcp dpp moto

  • @JosephChitseko-ro9fv
    @JosephChitseko-ro9fv วันที่ผ่านมา

    Chitsiluwe ndale basi garu

  • @EdsonNjaidi-ts4mj
    @EdsonNjaidi-ts4mj 16 วันที่ผ่านมา

    Awa kkkk

  • @SherrifJussa
    @SherrifJussa 15 วันที่ผ่านมา +1

    Objectivity apa palibe , kuchita kuonetsera mbali a Chawezi😂😂😂😂

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 11 วันที่ผ่านมา

    Chawezi mmmmm

  • @davienomale1722
    @davienomale1722 16 วันที่ผ่านมา +2

    I don't want to insult chawezi but please don't let him come again find someone neutral not msabwe ya mcp iyi.

  • @LeonardChimbaza
    @LeonardChimbaza 13 วันที่ผ่านมา

    Mibawa ,Chawezi asapezekenso pa Mibawa tisiyabkionera.

  • @berthabanda4483
    @berthabanda4483 13 วันที่ผ่านมา

    Chawez tayamba wakumana nd mtola mkhan wa bakili muluz tv

  • @KellyHart-pi4hd
    @KellyHart-pi4hd 8 วันที่ผ่านมา

    Koma mkulu uyu mukuti Chaweziyu ndi mbuli yophunzira srs ndipo wandinyasa

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga 13 วันที่ผ่านมา

    ku MIBAWA...ngati kuli programme ya manyi.nde ndiyimene mwabweletsamo CHAWEZI BANDA

  • @RivinessiRivinessierick
    @RivinessiRivinessierick 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kma iwe iwe panyapako usatichimwitsendithu uzinamiza amakowamva

  • @badanidube8315
    @badanidube8315 14 วันที่ผ่านมา

    Ameneyo mpangileni tsiku Tilankhurane ndi ine pa online

  • @Milanzi-nb5fv
    @Milanzi-nb5fv 15 วันที่ผ่านมา +1

    Zonsezi nzopanda nzeru, chanzeru ndichakuti MCP singawinenso koma😂😂😂 or mukambe za ku America athu akumuzi chomwe amafuna kudya. You don't know how people are suffering mmizimu, ukayankhule mmizimu uone ngati ubwele wamoyo😅 I understand ndiwe wa MCP koma simukuwinanso😅

  • @user-qz1rp5mh9e
    @user-qz1rp5mh9e 12 วันที่ผ่านมา

    Ku Zambia fuel ndi wotchipa mzeru zakuvutan Mozambique pompa

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 17 วันที่ผ่านมา +7

    Chewezi ukamuvotera wekha chakwera wakoyo, shuga ali 4500 kuzibabwe akuchipa koman ndi ochokera ku malawi, chifukwa chan? Adaaa sungatipusise ataaa

  • @user-qe2lz7mx7u
    @user-qe2lz7mx7u 10 วันที่ผ่านมา

    Bwanji anthu sanafunse a chakwera ndi chilima fisi iwe

  • @binahdouglasselengu
    @binahdouglasselengu 16 วันที่ผ่านมา +1

    Komaso a deus misamamutenge chawezi tisiya kuonerq channel chanu. Zoona anlyst azikabakila chakwera nkona kalindo akut kulibe anlyst genuine ku Malawi..

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l 16 วันที่ผ่านมา +1

    Chawezi keep on reminding Malawian kuti Peter muthalika palibe chomwe azapange kukoza dzikoli

  • @user-gr9bt9xt1p
    @user-gr9bt9xt1p 15 วันที่ผ่านมา

    Kodi popangira vn ndipati?

  • @PeterMaster-yi9ep
    @PeterMaster-yi9ep 13 วันที่ผ่านมา

    The guy is right

  • @uchizJoelMumba
    @uchizJoelMumba 10 วันที่ผ่านมา

    Akulu Akulu chilungamo chawawa ndipo chilungamo anakoza kotero wina apapa akwiya bcoz kachilungamo kamabaya

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z 14 วันที่ผ่านมา

    Mcp yapanga chani,tiyeni tiwelenge ndiye tiwelengeso zomwe inapanga dpp,muona kuti pali Big difference, dpp inathesa njala,chuma chimayenda bwino,zithu zimagulika athu akumudzi amatha kupeza fertiliser.

  • @Dalitsajamu
    @Dalitsajamu 16 วันที่ผ่านมา

    Iwe galu kwabasi chawezi chakwera wakupatsa ndalama eti

  • @HedgensChisale
    @HedgensChisale 16 วันที่ผ่านมา +2

    Chawezi kodi ukufuna ndikutukwane???? Kapena ayi

  • @JohnPetro-vv3er
    @JohnPetro-vv3er 16 วันที่ผ่านมา

    You are also one of them munthu osazindikila chawezi

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 10 วันที่ผ่านมา

    Chawez wabowesa

  • @Kapoloma-qv9gm
    @Kapoloma-qv9gm 16 วันที่ผ่านมา

    Empty tin make noise alot

  • @SurprisedPug-dd4og
    @SurprisedPug-dd4og 14 วันที่ผ่านมา

    Akupatsa ndalama zingat?

  • @user-fh4rj9gh7f
    @user-fh4rj9gh7f 13 วันที่ผ่านมา

    Mulungu akuwone

  • @user-yh3dw6qu7z
    @user-yh3dw6qu7z 16 วันที่ผ่านมา

    Iwe chawezi ndiopenga.monga monga sukuona kuti malawi waonongeka.opusa

  • @user-ez8uk7py8n
    @user-ez8uk7py8n 16 วันที่ผ่านมา

    Uyu ndi wachikape osalimbana naye wadya Bazi chawezi

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi masende ako please Siya tchito sukuziwakanthu iwe

  • @ChikondiChagoma
    @ChikondiChagoma 14 วันที่ผ่านมา

    Km utolakhani kumibawa walephereka, objective palibe mmmmm mkwa
    bwino ndsiye kusata mibawa radio. In truth ma president ose Ali ND maweekness and strength km zopanga point Muthu mmmmmmm Chawezi sindngamulembe ntchito

  • @user-th1rr6nf7j
    @user-th1rr6nf7j 12 วันที่ผ่านมา

    Mbuzi

  • @user-fx4pp2xt7g
    @user-fx4pp2xt7g 16 วันที่ผ่านมา

    Iweyo ndi chakwera wakoya nosenu ndangaru

  • @user-em1qi8kj9h
    @user-em1qi8kj9h 15 วันที่ผ่านมา

    Aisee ndiwe wa sukuludi ndi nzeru zkozo udzavutera wekha chakwera yo

  • @NtchindiChirwa
    @NtchindiChirwa 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi vuto ndi umbuli more 🔥 fire

  • @kapiniali4216
    @kapiniali4216 14 วันที่ผ่านมา

    Chawezi wamizala kwambili garu

  • @IsaacBaluwa
    @IsaacBaluwa 15 วันที่ผ่านมา

    Akuluwa mulungu aziwakhulukila akanaziwa mmene anthu akuvutikila mmakomomu sakanamba izi 😢😢😢😢😢

  • @FelisterBenedicto
    @FelisterBenedicto 13 วันที่ผ่านมา

    Amampasa ndalama ameneyo iyaaaa

  • @RodneyWandani
    @RodneyWandani 14 วันที่ผ่านมา

    Mibawa tv please asichiru awa ndisazaoneso

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 14 วันที่ผ่านมา

    Ngati iyeyu ndiwa mibawa ndiye kuti mibawa ndiyautsiru ndipo itha

  • @ZecoKubwala
    @ZecoKubwala 16 วันที่ผ่านมา

    Sadakambe za two years apa za ndale saziziwa ndani ,

  • @user-qz5gj3tf2t
    @user-qz5gj3tf2t 13 วันที่ผ่านมา

    Chawezi economic yako unaiphunzila molakwika yongotengela pepala pa window. Suziwa kanthu iwe.

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi iwe ndigalu pamozi ndizakoyo ukudana ndi chilungamo

  • @lovenesskampira
    @lovenesskampira 15 วันที่ผ่านมา

    Kodi bwande amamutengeranji ameneyo chawez ozindikirayo

  • @ChilangoNdalama
    @ChilangoNdalama 15 วันที่ผ่านมา

    Iwe chawez panyopako pamoz ndi banja lako kuphatikiza ndi amene wakutumayo nyonyonyo

  • @user-ot6lt8iy8f
    @user-ot6lt8iy8f 14 วันที่ผ่านมา

    Chawez ndiwe mbuli ya ikulu koma ukufuna azizitenga ngat dolo coz chakwela wakudyes chi banz ,ndiwe mbuz ya munthu

  • @user-eq8hr8li8h
    @user-eq8hr8li8h 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi machende ako galu

  • @FelisterBenedicto
    @FelisterBenedicto 13 วันที่ผ่านมา

    Amadana nd Dpp ameneyo mxiew

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 16 วันที่ผ่านมา

    Man chawezi takuonani ndinu a mcp mwandibowa kwambilitu chakwera wakudyetsani chibanzi

  • @JosephLahaji
    @JosephLahaji 10 วันที่ผ่านมา

    Umbuli ku Malawi ndi o chuluka,akunena zoona chawezi.

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi ukunama ndipo musayankhule mozitukumula amalawi akuvutika

  • @user-yd8xf4nq5e
    @user-yd8xf4nq5e 15 วันที่ผ่านมา

    Chawedzi ukuononga mibawa

  • @D.RJALLI-qo6yd
    @D.RJALLI-qo6yd 7 วันที่ผ่านมา

    Eeee ndachakwele ndi amene wapangisa 10 tirion yabwela bwanji galu iwe peter anasiya 3 tirion ngongole ndiye mukubwebweta pamenepo mwakuudza Ana akupasa chani achakwela anuwo chimuthu ngati chakwela wanuyo galu iwe

  • @user-kx4og4mv5y
    @user-kx4og4mv5y 11 วันที่ผ่านมา

    Agalu Inu ndinu andale A MCP why you just blame DPP kumanena kuti MCP Ikuyendesa bwino ziko

  • @MayankhoKalenga
    @MayankhoKalenga 8 วันที่ผ่านมา

    Chawez amanena ma wises

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 15 วันที่ผ่านมา

    Mesa doko anapanga abingu munakalakhula mabodza ku Mozambique 🇲🇿 agalu inu

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w 11 วันที่ผ่านมา

    You saying the truth but just minimize zoti ndife mbuli

  • @MasterJailos-kv5sd
    @MasterJailos-kv5sd 13 วันที่ผ่านมา

    Kuzambiya chuma chikukwera bwanji wadya zingati namachende inu

  • @esthergweje4038
    @esthergweje4038 12 วันที่ผ่านมา

    Chawezi umatinyasa kwambiri ndi nkhani Zako tisaname ukamati Malawi wasintha ndiye Kuti chani mmene tikuvutikira ife panooo uziyankhula zopepera zakozo

  • @mathewszimba5046
    @mathewszimba5046 16 วันที่ผ่านมา

    Wabwera kudzawononga program chawezi

  • @LawrenceDickens-jk3zx
    @LawrenceDickens-jk3zx 16 วันที่ผ่านมา

    Buli ndiweyo chawezi asaaaah

  • @AhamadiAlifu
    @AhamadiAlifu 16 วันที่ผ่านมา

    Akuti chawezi kaya akuti kawiza ameneyo wawukape zedi komanso ndi mcp mmaso mthinamo mumuwuze

  • @Cosmassaiwa
    @Cosmassaiwa 16 วันที่ผ่านมา

    Chawezi wanyula ndipo ndapeza ndiwe ulibe information

  • @user-hr2cg3ku1l
    @user-hr2cg3ku1l 17 วันที่ผ่านมา

    Mmmmm umadziwa chiyani