So APM was right after all, though I am not affiliated to any political party, koma his words were true, Malawians should be careful otherwise evil will rule this country once again, lero ndi izi......😡
In the name of the Father, the Son and the Holy Spirit ✝️ Amen. Heavenly Father, stand with your children as Malawi is wailing in search of your mercy 🎚️
Anamiwa tangoyiyambani nkhondo basi ifetu tili ndi futi zomwe tidathawa nazo nthawi ya oparetion bwezani ija tidaku young peania koma ndilibe chipani koma simandinyaza zomwe akuchita a chakwera futi ndiye kuthapa kutaya chakwera chakwera undilakwiza😢😢😢😢😢
Koma wa police ndi munthu opanda dzelu ndithu akupanga ngati iye amakhala ku ameleka koma adzibale ake akumvutika ngakhaleso iyeyemwe ndi phawiso apolice khope ngati agalu basi zisilu zaanthu
anthu osowa zochita kumapita ku mademo zaziiii mungofelapo chabe chosecho olo nyumba yomwe mulibe even galimotoso mulibe mafuta mukathilila machende eti eni ndalama ali duuuu
Za mademo izi zikuchedwetsani ,kapangeni maganyu mupeze zosowa pamoyo wanu, I remember in 2019 people were demonstrating pofuna kuti zinthu zisinthe but look now ,anthu anatenga maudindo they don't care about the lives of people who were fighting for their freedom .Panopa akungodya kumakhutitsa mimba zawo
komatu ma demo ndi dziko lililetse alipo ngakhale anthu ena mukamakhuta ma nyumba mwanumo kumanena chipongwe mesa chakwerayoso akapanga ma demo ndelele asiyilenji anthu aaaa iyayi
Zimandiwawa kulingalira mumtima anthu tinali kufuna kuti zithu zisithe koma kusitha kwa zithu tayikaso Moyo pachiswe
Ineso kpmaso ngakaremoyo wanga zindikufa bwino ndisomwe akupanga chakwera munziko latu
Ufulu tinkaufuna uja ena akuuononganso zimandiwawa ineyo
So APM was right after all, though I am not affiliated to any political party, koma his words were true, Malawians should be careful otherwise evil will rule this country once again, lero ndi izi......😡
Kwamunthu osowa zochiteyotu nthawi ino sinthawi yodalira a boma.muone pamenepo okhaokha akuba. Ali ndi zolinga zakuba osati mademo mbava izoo
APM ankanena zoona, plus makolo athu I remember my father told me, how evil MCP was. And he was fully doubt of it's change.
Chakwera anali number one kupangisa ma Demo lero akutchinga amzake...there is God in heaven.
Zifukwa zosaveka zomwe mukukamba chifukwa loko. Utakha iwe sungakwanitsem
In the name of the Father, the Son and the Holy Spirit ✝️ Amen. Heavenly Father, stand with your children as Malawi is wailing in search of your mercy 🎚️
Amen
Amen
Tingogawapo dziko lamalawi akumwera akhale ndi president wawo Chigawo cha pakati akhale naye chakwera wawoyo
Ife akuntcheu chakwera ai
Chikangawa waononga dziko lokoma lija
Akupanga a police zi ndizija zimayambitsa kuphwanya ma shop zina çoz chotiphera ufulu wathu
Apolice nanu ngatitu simukuvutika ngati Ife pano,kapena mukurandira ma 1meter salary,chonsecho tikuvutikira limodzi
Chikangawa dziko akulitengera m'manja mwake,
We r tired of this government
Chakwera uja SADZIWA democracy
this guy really doesn't what to do its unfortunate the guy who people trusted in voting is no more , so sad
Democracy yot azikawononga zitukuko mtown
Amalawi tikutoledwa ndi garu chakwera
Mumuuze mtambo ndiazake ndiamene munabwelesa chipani chankhazachi pampando inu nomwe choseso zimenezi mukutipwetekesa
Ine ndikuona kutii iyiyi ndinkhondo tikufunikaa tivomereze kutii chakwere akufuna nkhondo ndiye ifenso tikuyenera kumatenganso zikwanjee popita kumademo
Ananena kaletu kut kukhetsedwa mwazi. Si izi?
Zoona akufuna nkhondo munthu oipayu👹
Chakwera tsiku lina uzamva kuwawa ndipo uzalira ndikukuta mano kwangosala ka nthawi
Koma Zomwe akupanga anyamata a MCP ndi azitsogolere awo izi, akubweretsa nkhondo mudziko muno (Mulungu alowelerepo ndinthu 😢)
Meaning there is no need for police to protect our country let's anyamata azikwanje control malawi
Police will regret soon. Apapa ndekuti palibeso kwapatsa ulemu .... Awawa ndadani adziko.... Tiona akuswedwa apoliceno
Mchifukwa chake amafa ngat agalu awa
Muyerekeze kuzapaga kuno ku Soweto ghetto ndix ...tizamphana ... heavy
Ndithokoze anthu onse amene apita ku ma demonstrations.... Anafunika akhale a dziko londe osati ku lilongwe kokha
Lets fight for our democracy
pakufunika kwa genda ndi malengeni anyamata azikwanjewo
Action ikufunika Udf Dpp Utm Pp Pdp mukutani tikubweleratu kumudzi party serious ndiyeno mukugogona basi koma malawi 🇲🇼 wanga ineeeeeeee
Anamiwa tiloleni tigwileko a police awiri okha ,tichite nawo, timagwira awiri okha asiya kutilowa kuntoso .
Kkkkkkkk
Apolice sopano kuphwanyano ma ufulu a amalawi
Don't give up guys
Anamiwa tangoyiyambani nkhondo basi ifetu tili ndi futi zomwe tidathawa nazo nthawi ya oparetion bwezani ija tidaku young peania koma ndilibe chipani koma simandinyaza zomwe akuchita a chakwera futi ndiye kuthapa kutaya chakwera chakwera undilakwiza😢😢😢😢😢
Afiti akupha anthu asalakwa akumusiya chakwera kumadzudza anthu
Zovetsa chisoni Kuti akuluzabe mavoti a anthu ambili tsiku ndi tsiku tsoka achakwela inawalowa kalekale kwambili kuchikangawa kunja
Ku malawi kuno mungololeza mfutii tiziphatokha
Koma wa police ndi munthu opanda dzelu ndithu akupanga ngati iye amakhala ku ameleka koma adzibale ake akumvutika ngakhaleso iyeyemwe ndi phawiso apolice khope ngati agalu basi zisilu zaanthu
APM ankanena koma kusamva lero ndi izi, fisi ndi fisi
Kusamvadi mmmmmm
Pajatu adad anati muzaona nyekhwe
We don't have a leader in malawi
Don't call them mayouth or mabouncer onyamula zikwanje koma MCP thugs
Tayambani kupha apolisiwo Ngati Ku Mozambique Ndi gulu la zikwanjewo
Aaaaaaàaa Koma abale ,where's democracy in our country?
Malawians you were warned. Swallow that!!
Mayo Malawi mayooo
Later fight each other guys 🤔 😒 🇲🇼🇲🇼🤛🤛
Democracy kulibe ku Malawi ,azitsogoleri timasa kuno ngozikonda
anthu osowa zochita kumapita ku mademo zaziiii mungofelapo chabe chosecho olo nyumba yomwe mulibe even galimotoso mulibe mafuta mukathilila machende eti eni ndalama ali duuuu
APM ananena, aMalawi musavotere MCP, if you do, evil will rule this country, ife timvekere opanda mano achoke, Mulungu akhululukire mtundu wa aMalawi
Mai Malawi 😢
Za mademo izi zikuchedwetsani ,kapangeni maganyu mupeze zosowa pamoyo wanu, I remember in 2019 people were demonstrating pofuna kuti zinthu zisinthe but look now ,anthu anatenga maudindo they don't care about the lives of people who were fighting for their freedom .Panopa akungodya kumakhutitsa mimba zawo
The days are going next year out from Power
Zikuoneka kt chakwela
Alibe umthu kd mesa iye amapanga madem lelo kupanga ena zikuvuta akuopa chan 😅😅😅😅😅😅
Atupele, Peter,kabambe ndi chihana muli kuti? Nde mukatelo muziti next year waboma? ATAKUVOTELENI ndani pomwe amalawiwo akumfa ndi chanjala😢😢😢
Vuto kuyakhula nkosavuta koma kuchita mademoko ndiko kovuta nde ngt mukulephela pano after zisakho zizatheka mmalo mot ziyambile pano kuliziiiiiii
Mademo muzipangitsa zigawo zonse tsiku limodzi sangakwanitse kuwapanga block.
Chikangawa akufuna nkhondo ndiye iyambe alamule achewa akewo amupha posachedwapa
One party state is back zomwe timkafuna zimenezi
never mind we will show demonstrations on ballot papers next yr
Yea I support this idea than going to the streets
Ambuye bwelani muzaliweluze dzikoli
Mukabwera ku Ndirande tipezana
Ine nili ku zambia but kwathu ni kumalawi ayi democracy kulibe or kamuzu angadabwe
Malawi wanga ukupita kut uzindisewelesa 😢😢😢
We know what we want
Osawagwila azikwanje bwanji amatumidwa amenewo
Ufulu omwe tikaufuna unja ena akuonongaso zimandiwawa mumtima........zimandiwawa ... inetyo
Apolice aku malawi dzitsilu ndithu
Kwabasi
Ndipo nyinizamsyiawo zamakwinya makwinya uwundiumve akupangau ndichiyambicha nkhondo
Tionana ku vote,achewanu
komatu ma demo ndi dziko lililetse alipo ngakhale anthu ena mukamakhuta ma nyumba mwanumo kumanena chipongwe mesa chakwerayoso akapanga ma demo ndelele asiyilenji anthu aaaa iyayi
Kodiak mwanji Anthony amapanga mandatory akamapanga mademo
Tiyeni tasiye kaye akulu akuluwa akhale pansi akakambirane nkanyumba komata, ngati ilindewo akakuthumulane nkanyumba kameneko,khaya yazikwanje khaya yamanja khaya yamitu akakutumulane osamangwatuma ana aweni ayi,komanso osayiwala ana anu muzatenge kuti azizakuleletsani pandewo ikachitikeyo.
Anthu MCP ANATENGA DZIKO NDI MADEMO LELO ADZAWO AKUWALETSA NO DEMOCRACY AGALU KWABASI
(Kumwamba kuziwike kuti kuli mulungu ) mcp mukuputayi ndi jahena Ambuye mulowelelepo
Emusipi Emusipi Emusipi mjamanyi
Awatu ndithu abweretsa khondo komaso maufulu awathu anaphwanya ndifukwa sakufuna mado
Timothy Ntambo uli kut tuluka unali patsogolo nd mademo anyoo kupangira Congress ndpo Muthalika sanamwe madzi chifukwa cha iwe Ntambo lero zikukuvuta bwanji uchotsa anthu akowa??iwenso ukunva kuwawa??ai ukutinamiza zakhala bwino kut ukuwonq nd maso pamene pafika Malawi mu upandu umene unatsogolerq iweyo .Misonz ya a Malawi ikhale pamutu pako😭😭
Koma ndye kuzidzuzatu
Osathawa anthu osowa zochita inu, awulesi amanja lende, mukutisokonezera business anthu mu LL MUNO
Dziko ra malawi lobvesa chisoni apolice akufuna chani apa😢😢😢
A police ovetsa chisoni mavalidwe ,mayendedwe ,mfuti zao mmm dziko vutika mosausa
Zidayenda izi anamiwa osadikila Chaka chamawa bwanji masiku atsalatu ochepa
Malawi wanga
Kodi apolisi ophilisa usi okhesa misozi akumapeka koma oteteza anthu ayi
Mademo oyambira chigawo chakumwera or pakati sangaphule kanthu koma kumpoto chifukwa kuli anthu azindikila
Vuto mumangotigwirisa ntchito nkumadyerers nokha tdaoners mtambo ife. Mot iweyo sikumvera
Awa sima demo
😮
Kwachema😢
Add of hitting anapangaso ngati zimenezi boma likamagwa zimakhara ngati izi
Sono apolice akupangapo chani za anthu azikwanje zaziii zokha zokha apilice akulilongwe ndiupepela
Back to one party system 😢
Za police ndimanyi apamimba za anthu izizi
Ndiulamulilo wa MCP ai boma likuchitisa manyazi osati masewera ndipo mzovesa chisoni,chomwe mungaziwe ndichoti anthu omwewa ndiomwe mutawafune pazisankho kt akuvotereni
Abusawa ndiye andikwana bwanji
Don't give up gys
Mademo akufunika kukachita ku dc komweko kwa dcko kukaotchapo ofesiyo sakuziwa tchito
Inu mukubweretsa chisokonezo
Boma lapita ili mupanga zithu zonse mukufunazo koma mugonja.God is controlling muzonse.mwaonatu bvuto lopanga zithu mwakwiyo umapanga zithu molakwika mumati zithu zisithe lero ndi iziiiiiiii
Musàpiteso kwa munthu kukapempha chifukwa chilungamo sakuchifuna ingokonzani tsiku loziwa nokha mukangotulukila ku ma office onwe mukufunawo nchibwana aluchitachi aboma
Ndipodi zikutikhudza kwambiri anthu kumafa chifukwa chakudya chitedze Ndi zinthu zonga chinangwa eeeeeee boma lomzuza Ili mmmmmmh
Apolice ndi anthu omvetsa chisoni kulolera kuphwanya ufulu wa Malawi chifukwa cha ndale
Malawi police and their actions,,kuipisa mbiri ya bomanso komanso kuonjezela udani pakati pa amakawiiii
Izizi sizifunika kupempheraso ayi apa ndi man to man 😢😢😮😮😮
Comrade namiwa atiuza kut mademo alipo, muletselanji,mkuopa chani,mwayambakale kunjenjemela koma sitinavot
Kodi akamathila utsiwu zimatanthauza chani ine zimandidabwitsa
Police yathu ikupanga zibwanah akuyesa ife dzitsiru
Kumeneku ndiko kupepera kwa amalawi zoona kawilikawili mademo kulephereka kuoopa anthu azikwanje zikwanje anapangila anthu a mcp okha kapena bwanji zikuoneka kuti mumalamulo athu mulibemo malamulo ovomeleza mademo ndiye zisiyeni zimenezo muzaphetsa nazo anthu osalakwa zamademo zithelethu mumalawi zikuoneka mulindimantha kwambili amalawi mumatha kuyankhula chabe zisilu za anthu
Amalawi tikuvutikatu
Anthu tinali kufuna kuti zinthu zisinthe lero kusantha kwa zinthu taikanso moyo pachiswe