Basi kufuna kwapala anthu nkamwa basi Chakukudzani ndichani?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 1 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 333

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 วันที่ผ่านมา +8

    Uyunso ndi msogoleli wagulu la zigawenga la kulilongwe lija likumatenga zikwanje lija , olo muzimuona akamayankhula .

  • @MercyChipeta-h4d
    @MercyChipeta-h4d 2 วันที่ผ่านมา +4

    Mzanu akutanthauza sazayendayenda it's what he was meaning. Not buying expensive cars while Malawians are suffering.

  • @Russell-sq9rm
    @Russell-sq9rm 2 วันที่ผ่านมา +4

    Akuwoneka kuti umphawi wamupweteka 😁😁😁

  • @Malawian-q5f
    @Malawian-q5f 2 วันที่ผ่านมา +5

    Awa ndiwomvetsa chisoni, ine sindingasapote president wolimbikitsa kupempha. I Have two choices to make , it's either Utm or Dpp. I rest my case. A mcp pachiphwisi panu

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂 Kodi waledzera uyu? Asiyeni akabambe mukuyankhula ngt ndani? Paja muli pa mgwirizano ndi Mcp wapanga po chani razalo wakoyo kabambe samatanthawuza kuti adzidzayenda pansi, mudzikhala ngt munthu wamkulu nanunso m'mene akuzunzikira adzimbuyanu mmamidzimu mungamasapotere razalo? Kabambe woyeeeeeeeee❤❤❤

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 2 วันที่ผ่านมา

    President oyankhula akugonayu nde uti😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 2 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂 timupatse mpaka zaka 30 mmm iwe ndi galu basi 😂

  • @BashilMuhamad-zx3mc
    @BashilMuhamad-zx3mc 2 วันที่ผ่านมา +1

    Malawi 😂😂😂 More fire. Ee kadye kuda😂😂😂

  • @SleepyCrow-ow6tc
    @SleepyCrow-ow6tc 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ma program akuluakulu ake at, program imamkhara yomangopemphapempha aaa iwenso utipwetekesa et chifukwa choti inuyo zanu zikuyenda ndiye bas tikhazikike tikhazikike aaa usamaretu iwe

  • @HalordLuban-c3z
    @HalordLuban-c3z 2 วันที่ผ่านมา +1

    President awumodzi ndi achitsiru ndipo alibe mzeru ngati akufuna kupempha kwambuli ozawoyo anakangopempha osati zopusa akunenazo ndiposo atiyankhulitsa pambali ife amalawi

  • @Mariam-f8j5y
    @Mariam-f8j5y 2 วันที่ผ่านมา +1

    Galu wamunthu iwe usatilakwise bakadya chibanzi Chomwe akupatsacho ndibanja lako usatisusule Mabala

  • @ChaimaChikunkhu
    @ChaimaChikunkhu 2 วันที่ผ่านมา +1

    Muti uyu ndi president wa dziko liti😂😂

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 2 วันที่ผ่านมา

    IZINSO NDE ZITI.😂😂😂😂😂😂😂CHIPHA MASO CHENICHENI HAHAHAHAHAHAHHAHAA PRESIDENT MY FOOT😂😂😂😂😂

  • @Moffat-oi4yx
    @Moffat-oi4yx 2 วันที่ผ่านมา +1

    Machende Ako okuba iwe wapangapo chiyani zikoli lakukanikani

  • @mozykavalo7352
    @mozykavalo7352 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma ummmmm kkkkkkk iiiii ai kunali kwabwino kusayankhula koma poti akuoneka kuti watopa ndi umphawi ai amupasa udindo otsogolela oimba ng'oma

  • @edwinnyasulu2088
    @edwinnyasulu2088 วันที่ผ่านมา

    Munthuyu wasokonekera sakudziwa direction 😂😂😂😂😂

  • @JohnMughogho
    @JohnMughogho 2 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂 maluzi akuphweteka chabe .mpaka zaka 31

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mbuzi

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 2 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂 kodiso ndi president ameneyu bwanji Ngati Aku sizina 😂😂😂😊

  • @kingSoko-wf4pe
    @kingSoko-wf4pe 2 วันที่ผ่านมา

    Ambuye mtengeni wamupweteka uyu simukumuona masowo anatopa ndi kabanga angayankhule Cha nzeru

  • @IbrahimJackson-i8h
    @IbrahimJackson-i8h วันที่ผ่านมา

    Kkkk😂😂😂😂 koma uyu ai palibe vuto poti akadali ntulo mwina akadzukamo atiuza kuti amalota maloto

  • @ErnestAllex-f1n
    @ErnestAllex-f1n 2 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂 or nkhope yokhayo ikufotokoza zambiri kuposa zopusa walankhulazi mutu ngat mbolo mxeew😢

  • @innocentlipita3630
    @innocentlipita3630 2 วันที่ผ่านมา

    Nkhope imeneyi siyofunika u president inuyo usinga'anga wakukhalani

  • @InnocentMlelemba-dr6eg
    @InnocentMlelemba-dr6eg 2 วันที่ผ่านมา +1

    Chitsiru wagudwa etiiii?? Mbuzi

  • @AmissKumakanga
    @AmissKumakanga 2 วันที่ผ่านมา

    Namachendeyu andikwiyitsa mwina ndindekha enanu mukuti bwanji?

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 2 วันที่ผ่านมา

      Ndipo akundinyasilamo nkhope yoopsyaaaa

  • @marychipofya4945
    @marychipofya4945 2 วันที่ผ่านมา

    Komatu ndalama zisamafike potipeperesa chonchi....aziwauza aku banja kwake zimenezi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 วันที่ผ่านมา +3

    Achitsilu awa tachionan distance ya mphuno ndi kamwa 1 km aaa

  • @RichardThanks-y9n
    @RichardThanks-y9n 2 วันที่ผ่านมา +1

    Umphawi wamukudzula

  • @idilissmuyer2914
    @idilissmuyer2914 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kkkkk koma akuyang,ana amenewa chitsilu cha munthu ameneyo

    • @FrankChanza-l3g
      @FrankChanza-l3g 2 วันที่ผ่านมา

      Kkkkk km ndiye ichi mbava zokuba misonkho

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kape uyu wa chabe chabe, angakhale President uyu, nheeeee, bwampini uyu wa ziiiiiii. Akufuna ka udindo ku MCP, fisi uyu😂😂😂😂😂

  • @mickiaskumbasa136
    @mickiaskumbasa136 2 วันที่ผ่านมา

    Savage 31 yrs ukawapase amayi ako amayi mburi yeniyeni ukufuna fover kwasatanayo bulutu

  • @EnifarSeleman
    @EnifarSeleman 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiwe garu kobasi,chipani chake chiti?

  • @MathewsChitambe-m6o
    @MathewsChitambe-m6o 2 วันที่ผ่านมา

    Nkhope ngat chotsekera pa chimbuzi, savage ngt iwe ungafanana ndi Dr of economics iwe ?

  • @PiusChawinga
    @PiusChawinga 2 วันที่ผ่านมา

    Ng'ombe iyi, timpatse another 31 years? Sugar tidzagule zingati panepo ?Chichoka chinthu chakochi

  • @HelbertKalumbi
    @HelbertKalumbi 2 วันที่ผ่านมา

    Mboli yakenso ameneyo , akungobisalira ku umodzi party, actually he's one of the Mbuzi zomwe zikukhapa anthu makwalalamu

    • @Mariam-f8j5y
      @Mariam-f8j5y วันที่ผ่านมา

      Kobasi mbuzi yamunthu zofuna kutilakwitsa basi

  • @geofreykandabongomani4715
    @geofreykandabongomani4715 2 วันที่ผ่านมา +2

    Akuyang'ana ngati chule kkkkkkk

    • @HandEllah
      @HandEllah 2 วันที่ผ่านมา

      Nachee ameneyu wamanyi kwabas mpaka zaka 31?😂

    • @McdonaldSairo
      @McdonaldSairo 2 วันที่ผ่านมา

      Kkkkkk

  • @manzyjk8453
    @manzyjk8453 วันที่ผ่านมา

    Kkkk mwati ndi president amanei kapena kapolo chane

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 วันที่ผ่านมา

    Awa ndi achitsilu kwambili bambo iwe wady zingati mulungu akulangeni nose ndi asatanic akowo galu iwe kwabasi Lazaro ndiye kanyama kanji

  • @princekaponda
    @princekaponda 2 วันที่ผ่านมา

    Uyuuu sisogoleli ..chake sichipani koma NGO... Yogwila ntchito ndi bomaaaa... Nde akuti tipanse 31 years koma

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 2 วันที่ผ่านมา

    Chipani cha my wife and kids 😂😂😂😂😂

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kodi imbwaaa iyi nde iiiii????? Usatinyase wamva iwe ingopita kwa chakwera wakoyo Kaya ukungofuna akugayire ndalama zqbowokazo fotsek... 💔💔

    • @PiusChawinga
      @PiusChawinga 2 วันที่ผ่านมา

      Imbwa mwee

    • @FrankChanza-l3g
      @FrankChanza-l3g 2 วันที่ผ่านมา

      Mbole yako ndi Lazaro wakoyo

  • @AdamRobert-u9v
    @AdamRobert-u9v 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe nde mbuzi yeni yeni sukuziwanso zomwe ukuyankhula, utichimwisapo apa

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi uyuyu ndindani? Ifetu zotiyamba dala sitikufuna, ndipo uyuyu pa........ Pake

  • @HalordLuban-c3z
    @HalordLuban-c3z 2 วันที่ผ่านมา +2

    Mbuzi yeniyeni

  • @ThomasBlack-hw3jr
    @ThomasBlack-hw3jr 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe ndiye wadya zambilitu mpaka ku yankhula utaseka Maso ngati ukufunsira mkazi wachibwenzi ntumbuka wopanda Nzeru ngati iwe tachionereni pita uko

  • @DanielNabeni
    @DanielNabeni 2 วันที่ผ่านมา +1

    achisilu awa Chakwera athandiza anbuyako,galu iwe

  • @DorothyKaimfa-ns8su
    @DorothyKaimfa-ns8su 2 วันที่ผ่านมา

    I think thupi langali ndi 1 bodies 😅😅😅😅😅😅😅 Chizungulire mapapo onse

  • @geofreykandabongomani4715
    @geofreykandabongomani4715 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ameneyu ndi galu kobasi chule kobasi ameneyu tamuinzeni Kaye akasukusule mwina sakueona bwino

    • @HandEllah
      @HandEllah 2 วันที่ผ่านมา

      😂 Ofunika kumugenda😂

  • @ChrissyBhima
    @ChrissyBhima 2 วันที่ผ่านมา

    Tamuwoneni kuchikamwa kwakeko?

  • @EnelesKanyerere
    @EnelesKanyerere 2 วันที่ผ่านมา

    Olo nkhepe ikuchita kuoneka kt ndiyazikwanje yokha yokha

  • @JohnstonNyirenda-zw6jd
    @JohnstonNyirenda-zw6jd วันที่ผ่านมา

    Muli nzeru umu komaa😂😂😂😂😂😂😂

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman 2 วันที่ผ่านมา

    Zi anthu zopepera ngat Inu sitikukufunana ngat athandiza Inu B's kumangodya bs

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward 2 วันที่ผ่านมา

    Panja ndiwe udapangitsa kuti soya pieces ayikeko mafuta eti chako chipani waluzakale ufuna ugwire ganyu eeti

  • @ChimwemweJuwao
    @ChimwemweJuwao 2 วันที่ผ่านมา

    Mmmm koma a m c p nkhope ngati ngo'na kungooneka Mano onkhawo koma abare

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 2 วันที่ผ่านมา

    Muuzeni akaotche makala kudoloba komaso Ayambe kuzola betasol atumbukuka nanuso mumatipangitsa manyazi,ol ol mavitamin c akusowa mthupimwawo

  • @JaneMoyo-b7i
    @JaneMoyo-b7i 2 วันที่ผ่านมา

    Naonso ndi maganizo awo ku chipaniko ku UTM.
    Nanu yankhulani maganizo Anu za kuchipani kwanuko. Ife tizitengamo fundo basi osati kumapangana criticize

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 วันที่ผ่านมา

    Chitsilu Ichi chitha kukulakwisa akachita kuyera ngat.....

  • @happyluhanga3387
    @happyluhanga3387 2 วันที่ผ่านมา

    Akuyankhula zomveka chabe kuti 31 years ndipomwe a pala

  • @bashiramani8964
    @bashiramani8964 2 วันที่ผ่านมา

    Uyu asatitukwanitse. Ndipo ameneyu mmene akuwonekeramu si uja anatenga chikwanje ndi azinzake aja? Galu ameneyu . Mbuzi yopanda mzeru

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite วันที่ผ่านมา

    Khope ngati konyerela ndi chakwela wakoyo

  • @MikeGomani-o3f
    @MikeGomani-o3f 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiwe chitsilu pamodzi.ndi amako pamodzi ndi present wakoyo

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 วันที่ผ่านมา

    Panya pako what is umodzi ngati uli president iweyo wapangapo chani

  • @SiliAmanu
    @SiliAmanu 2 วันที่ผ่านมา

    Amwene mukafuna kupemba Ku MCP usingoyenda streti .kukapemba .umodxi party which means uliwekha

  • @ReginaMulipa
    @ReginaMulipa 2 วันที่ผ่านมา

    Machende okudawo ngati kanyimbi khope ngati saona ndege 😂😂😂

  • @AmanaHambalie
    @AmanaHambalie 2 วันที่ผ่านมา

    Choonde izi muzitilakwisa anthu ngati awa ngotukwanitsa mafupa akumanda awa
    Ndizosadabwisa kuti kachipani kaoko situkadziwa

  • @isaacthawani5442
    @isaacthawani5442 2 วันที่ผ่านมา

    Uphawi wakupweteka Sasamba iwe ndie ku panda zerukoo dziko

  • @VeroMaster-lo1mu
    @VeroMaster-lo1mu 2 วันที่ผ่านมา

    Ngati wakhuta kangone osawauze anthu zochita aliyense akuva yekha kuwawa shupit

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m 2 วันที่ผ่านมา

    Zomwe akuyankhulazo ndi face yawo zikungofanana. Maphazi ake

  • @MayamikoMlenga
    @MayamikoMlenga วันที่ผ่านมา

    Akabambe akunena zoona ndithu nawo aumodzi asatinyase apereke mfundo zawo tizimve osati zimenezo musiyeni kabambe wathu amenye nkhondo

  • @KonzekaniMwamwituMwaungulu-q1h
    @KonzekaniMwamwituMwaungulu-q1h 2 วันที่ผ่านมา

    Tangopemphani ndalama Baba akuthandizeni

  • @GomiwaGommzy-lv7pl
    @GomiwaGommzy-lv7pl 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi akuluwa samaona kunene atasinzinatu kkkk

  • @EmmanuelChavulla
    @EmmanuelChavulla 2 วันที่ผ่านมา +1

    Chitsilu iwe pantumbo Pako akugula eti, galu mbuzi ndi Chikangawa wakoyo.

  • @JoannaNAMA
    @JoannaNAMA 2 วันที่ผ่านมา

    Mbuzi yamunthu imeneyi, zoona mmene mavuto alili mdziko muno zoona timupasenso Chakwela 31 years mpaka kwacha ifika pa 25,000 pa dollar imodzi ya America

  • @tiongenyondo-j3o
    @tiongenyondo-j3o 2 วันที่ผ่านมา

    Hahahahah!!!.....nenani waka icho mukhumba akulu, don't go through corners.🤷🤷🚮😅😅😅

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 2 วันที่ผ่านมา

    Uyu umphawi wamupana muone mphunozo akuyangana ngati Ali nkhichini

  • @MuhamadMpate
    @MuhamadMpate 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe nthawi ya kabambe ndalama simatekeseka ngati zausilu zakozo iweyo ukhazikike pa chakwera wakoyo

  • @CentTiger
    @CentTiger 2 วันที่ผ่านมา

    Mazila ako ndi kingnkongwakiyooo!!

  • @shukurajaaffarie-cr2nm
    @shukurajaaffarie-cr2nm 2 วันที่ผ่านมา

    Lero lokha nditukwaneko UYU EKHA NDIE MAPWALA AKE ndi2di

  • @HandEllah
    @HandEllah 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ichi ofunika kuchigenda😂😂😂

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 2 วันที่ผ่านมา

    Chimunthu choipa mtima ichi ngati chakwera kumtumbo sete zilithoooo

  • @SoldieNdovie
    @SoldieNdovie 2 วันที่ผ่านมา

    Usabwelenso kuyakhula zopusa ngati izii

  • @MphatsoChilangiza
    @MphatsoChilangiza 2 วันที่ผ่านมา

    Kuchi kamwako ngati chule weni weni kodi ndimapasa ndi chimwendo chambuzi

  • @FosterZulu-b3j
    @FosterZulu-b3j 2 วันที่ผ่านมา

    Awa ndi achitsilu kwabasi,amakhala kt? Galu iwe zedi,mukagwela nose kudzenjeko Imani nawoni achakwelawo

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje 2 วันที่ผ่านมา

    Awa asanditaise thawi ndikuwavere, tonani uwo ndi mutu

  • @FaithSteve-t6h
    @FaithSteve-t6h 2 วันที่ผ่านมา

    Pa zaka 30 mukufuna tonse tithe ndikufa kapena mukufuna chan tsopano asilen ena avinekoso sinu oyamba kutuluka m,boma ayi

  • @idenmkumba-q8j
    @idenmkumba-q8j 2 วันที่ผ่านมา

    Chitsiru iwe mesa kabambeyo amagwila ntchito ngati civil servants ndie umafuna azithandiza ngati president? ndiwe galu kwabasi

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 2 วันที่ผ่านมา

    Takayambani kaye kugona chifukwa ndkuwona kuti tulu mudakalinalobe

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 2 วันที่ผ่านมา

    Wati zaka 31 kwa chakwela kkkkk abale anga munthui tisamubuleme ai tingowona nkhopeyo itiuza mayeso iweyo ukufunikila madilama ukhoza kumawina kwambili osati ndale ai ima naye chakwelayo mwina ulindi chifukwa ndi kabambe kufufuza za chuma chake iweyo chako chilikuti wapangapo chani padziko pano nkhope ngat izi anthu ake amakonda zogwilila ana

  • @ernestmponda156
    @ernestmponda156 2 วันที่ผ่านมา

    Machende akonso pati?

  • @AuswardNkhata
    @AuswardNkhata 2 วันที่ผ่านมา

    Umodzi paty ndi cha iye ndi ana ake ajoine sitikudanda

  • @Vincent-k4y
    @Vincent-k4y 2 วันที่ผ่านมา

    mapadzi ako iwe ndi chakwela wakoyo wanva 😱

  • @ChrisPhiri-s2p
    @ChrisPhiri-s2p 2 วันที่ผ่านมา

    Mphuno ngati akupwanya ndi njerwa galu iwee

  • @OmexMainala
    @OmexMainala 2 วันที่ผ่านมา

    😭😭😭😭😭 ndaomongaso bundle yanga eshiiii et kumakanvela chitsiluchi eshiii

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 2 วันที่ผ่านมา

    PALIBE AKUGONA MUNO TILIBE ASITIKALI KUNAKAKHALA KUTI ASITIKALI ALIPO BWEZA ATATULUKA NTHAWI YAMADEMO IJA KUTHAMANGITSA ANTHU AJA ANATUMIDWA NDI CHAKWERA NDIYE OSADANDAWULA AI AMENE SATHA KUGWILA FUTI TIDZAMUPHUZITSA TIDZAFUNA ANTHU ACHIGAWO CHAPAKATI CHIGAWO CHAKUMWERA NDI CHIGAWO CHAKUMPOTO ANTHU 60 NDIWAMBILI ZEDI

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha9790 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe mbuzi siungakhala president ukuchita kuwonekera mbava yeneyeni,,
    Dr kabambe ndimunthu oziwa zinthu, usayakhule za Dr kabambe ndiyo president wathu chakachamawa 2025

  • @MustafaAli-p6s
    @MustafaAli-p6s 2 วันที่ผ่านมา

    Iwe amene anakubala simuthu ayi kom unabadwa kuchoka kwa khumba ziwona mavuto amene akukumana nawo athu kumalawiko uziyakhula zaku nyero apa ukachita chimpuno kukula ngat chimimba Cha chinwendo banda

  • @WilfredGunya1
    @WilfredGunya1 วันที่ผ่านมา

    Iweyo ugawuze zochita chikwera mene uririmo Galu kwabas

  • @ChimwemwePhisoh
    @ChimwemwePhisoh 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma akuona ankuluwa

  • @HarrentBanda-f7o
    @HarrentBanda-f7o 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiye timuthandize chani kodi madala inu mutiyankhulisa pambalitu koma

  • @sanudiphimba8619
    @sanudiphimba8619 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk mwati president wa umodzi party ndi ameneyu? Eeeeee koma akufanana ndichija chimalowa m'matope chijatu.

    • @PatriciaAlomwe-oz8wc
      @PatriciaAlomwe-oz8wc 2 วันที่ผ่านมา

      Wandisekesa wamva chiti chimenecho?

    • @DalitsoMatope
      @DalitsoMatope 2 วันที่ผ่านมา

      ​@@PatriciaAlomwe-oz8wcndindani ameneyi

    • @MarthaMtengera
      @MarthaMtengera 2 วันที่ผ่านมา

      DK my vote ❤