ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ndipo ndizoona kep up guys
Kkkkkkk guys ❤❤❤
Only facts guys
Zosatheka ukamuvotera wekha
Chakwela ndi galu ndithu
President uyu ndi phala ropola ndipo malawi ilibe mtsogoleri ndithu ndipo chakwela ndi galu
Sound so swt guys
Kkkk koma selina
Amalawi munasankha chitsilu bwanji
Mr ndi mrs ndakunyadilani poyankha funso langa ndimati ndiziwe kuti manganya akamayenda saononga ndalama ndiye lero ndamva kuti amaononga ndalama zambiri yomwe ndi misonkho ya dziko kukagula kavweche pa vigwagwa mzuzu
Chosadziwa anaimbira mfiti manja
Ma 30pun esh
Chakwela namapwala uyu
In mumatenga mbali ndasiya kumvera za umve
Unya galu iwe
Kondwa Banda mukuyankhula zenizeni
Amazatisanzika Kuti akukajambulitsa ndi msogoleri wa ku U. A. E.
Gwede gwede ya opposition mulibe khalidwe
Chilungamo ndi mwano
Uzimvera timvetsetse,yazitsiru ija, Gwede gwede tisiyire tokha wamva?
Dressing ya ntundu wanji, ma cadet
Panopa wina aliyense ndi cadet, kuphatikizapo ndi nyau zomwe, iweyo watsala wekha ku Bagamoyo ko
Iweyonso ndi cadet
Kumeta kwa ntundu wanji?Nyau
Bola ukuona nyawu
Vuto inuyo zoti munapita ku school palibepo, mbuli. Inuyo a Mibawa zoti economy yavuta dziko lonse lapansi monga simudziwa? Mmalawi muno tatchulani president amene wakumana ndi mavuto azanyengo ndi ndani. Chakwera kungolowa anakumana ndi covid, kenako cholera, kenako ma cyclone owophya, chilala mvula yosagwa bwino. Koma muzonsezo Chakwera wayesesa kuchita zinthu zotamandika Nsanje to Chitipa. Njanje wakonza sitima zikuyenda koma afiti inu simunganene. Pafupipafupi district iliyonse chitukuko chachiti, koma poti ndinu asatana simungayamike ngakhale mukuona. Olo mutelo CHAKWERA ndi mcp mpaka 2030 wooooooooo
Ukamuvotera wekha, zosatheka kuwina chakwera wakoyo