ZOMWE WALANKHULA VP MICHAEL USI LERO KU CHILOMONI POSALABADILA ZOCHOTSEDWA MCHIPANI CHA UTM

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 2 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 103

  • @aaronziyeretsa6420
    @aaronziyeretsa6420 3 วันที่ผ่านมา +4

    Thumbs up to Dr Michael usi our lovely vice president
    You are true servant of God
    Kuyenda awiri simanthadi you are doing a great job assisting our president Chakwera.
    May our God be with you all you and the president
    I just remember muli ku Adra ntchito zanu zidali zomwezi

    • @symoldicky
      @symoldicky 2 วันที่ผ่านมา +1

      😂kkkkkkkk koma anthu manyaz alibe

    • @user-hh8eu8dr4u
      @user-hh8eu8dr4u 2 วันที่ผ่านมา

      You are sick in your head

    • @StoneckJali-s3n
      @StoneckJali-s3n วันที่ผ่านมา

      Uku ndiye Kutumikiira anthu

    • @kaphika
      @kaphika วันที่ผ่านมา

      Bravo Dr. Usi.

  • @monicagondwe228
    @monicagondwe228 3 วันที่ผ่านมา +2

    Kukhala ndikumeku za ndale pambali. God bless you

  • @RuqaiyaAroni
    @RuqaiyaAroni 3 วันที่ผ่านมา +2

    Mr Usi woyeee!!!( Osati ajawa amangolubwalubwa mmalo momanga chipan ndikumaphwatsuso)

  • @samuelchipula2545
    @samuelchipula2545 3 วันที่ผ่านมา +4

    BOMA ndilomweli a usi kuti Moto buuuu❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @PATSON-q6t
    @PATSON-q6t 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaaaaa zachimanga zomwezi mapakana ID amber mmm koma zikoli ambuye muli ongole ndithu amen

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 3 วันที่ผ่านมา +3

    My vote so far ndi running mate ya Chilima basi Usi....

  • @LukeyOwen-p1r
    @LukeyOwen-p1r 2 วันที่ผ่านมา +1

    Please stop using cameras when doing governments work

  • @ChikondiSabe
    @ChikondiSabe 3 วันที่ผ่านมา +2

    Tangomvomerezani kuti akuchosani inu mukukakamila bwanji?? Alipo saziwa kt inu munali wa mcp ku utm mumangobisalirako? Mumvomeredze kt kabambe ndi sogolere wa utm basi inu muzingopita ku chikangawako basi

  • @henryhenry6632
    @henryhenry6632 3 วันที่ผ่านมา +3

    Dr Usi, VP wa Malawi , ka utm ndiye mkachiyan

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaaa alibe ndindani peter Muthalika ndamene alibe fundo amati akazawina azamanga nyumba ya getrude ku mzuzu

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 2 วันที่ผ่านมา +1

    KODI MUMUNYENGERERANJI CHITSILU MANGANYAYI NSIMUKUDZIWA KUTI ZIMENE AKUCHITAZI AKUTUMIDWA NDI CHAKWERA ANTHU AWA NDIWO ANAPHA CHILIMA 100%

  • @retirementtoafrica
    @retirementtoafrica 3 วันที่ผ่านมา +1

    Alabadire chani, izi zikugwirizana ndizaku utm? At least he can now work freely. I hope he can move on. Ndzulo wanena kuti zakukhoti alibe nazo ntchito, I hope he keeps his word.

  • @MikeGomani-tb9np
    @MikeGomani-tb9np 3 วันที่ผ่านมา +5

    Akuluwa alibe mfundo.

    • @henryhenry6632
      @henryhenry6632 3 วันที่ผ่านมา +1

      @@MikeGomani-tb9np kape iwe, ndifundo zanji zomwe ulinazo iweyo

  • @BenardChilemba-k8w
    @BenardChilemba-k8w 2 วันที่ผ่านมา +1

    Chimangachi sichanthumba mwamunthu...awa akugwira ntchito ya boma..za utm zikhale pambali

  • @ChrByson
    @ChrByson 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kd somungapereke chimanga kwa anthu popanda kuwanjambula

  • @JamesBrown-gx8my
    @JamesBrown-gx8my 2 วันที่ผ่านมา +1

    Chimanga chaulelechi mwayamba kupangira kampeni😢

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 3 วันที่ผ่านมา +1

    Vice president wogiya, ndiye anthu akupatse mavuti chifukwa cha kuseza matumba. Ali ndi wabwino paja anthu a kumalawi kupepera zaka zonsezi samkapanga zimenezi bwanji a Malawi mudzifunse. Ntchito ya amabungwe iyi

  • @EmmanuelNtago
    @EmmanuelNtago 3 วันที่ผ่านมา +6

    Anapanga create njala mwadala lero akubwera ngat okhuzika kugawa chimanga anthu kuombera Mmanja,,kaya ndi fertilizer

    • @sangwasa
      @sangwasa 3 วันที่ผ่านมา +1

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 moti anabweretsa covid ndi hurricane Fred ndiyemweyu?

    • @JoliumChakhala
      @JoliumChakhala 3 วันที่ผ่านมา +1

      @@EmmanuelNtago muziwopa Mulungu mukafuna kulankhula

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 3 วันที่ผ่านมา +1

      @@sangwasa 🤣🤣🤣🤣paja pothawira pamakhara pa covid ndi cyclone mpaka 5 years,,,achina devaluation onse aja ndi kamba ka Covid?🤣🤣covid sanabweretu Ku Malawi konkha osamaiwala kkk

    • @StanleyChamasowa
      @StanleyChamasowa 3 วันที่ผ่านมา

      Chosaziwa anaimbila nfiti mmanja

    • @symoldicky
      @symoldicky 2 วันที่ผ่านมา

      ​@@sangwasawhatever koma chilungamo nchomwe kut njala ikuzuza amalawi lelo ndi man made. Anzeru akudziwa taking it from the back like it or laeve it

  • @ChrispineKalakanyani
    @ChrispineKalakanyani 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ntchito ya bwino Dr Usi mulungu akudalitseni

  • @ChifuniloNsanama
    @ChifuniloNsanama 3 วันที่ผ่านมา +1

    Kodi ngat anthu Ali ku utm ma udindo awo ndi osavomeleleka iweyo manganya kukhala ku mcp anakuvomeleza ndi ndani.
    Kunokhala ndi moyo wawuchisiru basi ozinva
    Mumawona ngati chipani cha utm chingasowe ochisogoler opanda iweyo usi
    Chisiru chowumira

  • @mbelengamavuto2517
    @mbelengamavuto2517 3 วันที่ผ่านมา +2

    Ndale zopepela za usi

  • @ManuelTembo-w5d
    @ManuelTembo-w5d 3 วันที่ผ่านมา +2

    Kani manganya ndioipa chonchi no wonder unapha nawo chilima ndondocha ya chabwino

  • @SEEJSHJEFFREY
    @SEEJSHJEFFREY 3 วันที่ผ่านมา +3

    Koma Kodi mntchito ya Dotma yogawa zakudya ndiya VP? Malawi wake up please this is stupidity at the highest extent

  • @StanleyChamasowa
    @StanleyChamasowa 3 วันที่ผ่านมา +1

    Chigawenga ichi ntchito kulankhula mopepela chimanga cha Joice banda icho

  • @prophetjacksonmakonda63
    @prophetjacksonmakonda63 2 วันที่ผ่านมา

    Tsono kujambulitsa ndi anthu atanyamula matumbaku si kuzimonda kumenekunso.?
    Manganya kodi ukuwaseweretsa anthu osauka chifukwa cha ndalama zawo zomwe zamisonkho?
    Ukuseweretsa moyoyo, sukalowaditu kumwamba iweyo seriously

  • @erickkhoko
    @erickkhoko 3 วันที่ผ่านมา

    Thumbs up!!

  • @LydiaMushala
    @LydiaMushala 3 วันที่ผ่านมา +1

    Kkkkkk faka iweee tiwadyere ma tiyeni zanthu zomwe izii ma candidate size anthu wambaaa chidziwq nchipande poomora😂

  • @ubs7030
    @ubs7030 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mwana usi more fire.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 วันที่ผ่านมา

    A DPP akagwilitsa ma camera omwewo palibe kusiya

  • @JohnTchirati
    @JohnTchirati 2 วันที่ผ่านมา

    Wagulidwa ndi MCP chifukwa cha udindo

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 2 วันที่ผ่านมา

    Chimanga choti anthandize amalawi chaulele phaka kumajamburana zoona ndale zakumalawi zombuta kwambili

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 วันที่ผ่านมา

    Ngati kulube ojambula tsiku limenelo osalandira chimanga

  • @KABAGHESTEVEN
    @KABAGHESTEVEN 3 วันที่ผ่านมา +2

    Ndale zopepera

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    usi,sakulonjeza,akuchita,ndiolonjeza,,musankha,ndami,

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 3 วันที่ผ่านมา

    Mufune musafune mwini wa UTM ndi amene anapasidwa ndi mwini Ali moyo akambala, akaliati, anjawala onse analipo Chilima Ali moyo koma wanawawona mumutima mwawo kuti ndibava can't be leaders mayo 26 votemayo 27 vote Kodi munalakwa chani a😊 kambala kaliati 😢😢😢😂😂hule izi zawononga chipani anjawala ndi mbuzi kwambiri one don't forget mu bible anapanga ndi Joseph abale ake.. muzamufuna yomweyo tsiku lina

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe 3 วันที่ผ่านมา

      Iwe usatuchimwise ndi yudas wakoyo

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    usi,simungamukwanitse,,usi,ndi,wachisoni,

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 วันที่ผ่านมา

    Pena kamutu kamakhala Ngati kakugwila Koma ayi

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 วันที่ผ่านมา

    Mwakhawula mesa mumati boma silikugawa chimanga apa layamba kugawa zokamba mbweee anyani inu

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 วันที่ผ่านมา

    Komaso zitokota koma Usi ndi one zanuzo kulibe kulowaso boma

  • @PATSON-q6t
    @PATSON-q6t 2 วันที่ผ่านมา

    Ausi muli be fundo mumakhara ngat zinthuzi zamumathumba mwanu bwanji aaaa

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    nose,mwalandila,chimanga,akabambe,ndi,ausi,wabwino,nindani,ongo,lankhula,ndiochita,musankha,ndani,

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 2 วันที่ผ่านมา

    Aaah boma ndilomweli la manu? Inu dzisilu kwambiri ku admark kulibe chimanga, feteleza olo mmodzi zili kwani? Mumangowombela mmanja zilizonse kodi ndikulodzedwa kapena kupepetulidwa? Mudzachangamuka zisilu inu? Feteleza;chimanga ku admark kulibe a mcp anadzisunga mmakomo mwawo dzinachitika kuti pa dziko lapansi? Muli ndi maso koma simuona, muli ndi makutu koma simumva zisilu inu.

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    nindani,anhanene,kt,usi,akulakwa,kuhawila,anthu,chimanga,,ausi,my,voti

  • @MarvinChilombo.flourish
    @MarvinChilombo.flourish 2 วันที่ผ่านมา

    Mokuti anthu onsewo akuganiza kuti Usi akugawa chimanga cha Dodma chifukwa iye ndi munthu osamala za anthu osauka? Political gimmick ngati imeneyi

  • @GerlisonMuwete
    @GerlisonMuwete 2 วันที่ผ่านมา

    Anthu pano mwasandutsa ngat agalu

  • @Godwin-xy9rg
    @Godwin-xy9rg 2 วันที่ผ่านมา

    Ichichi nchosokoneza ichi chilibe mfundo ncha mcp

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 3 วันที่ผ่านมา

    Politicizing the core responsibility of government to it's citizens...
    This was supposed to be done by dodma officials themselves not a political figure like VP ..
    This man has diluted the dignity of the office of the vice president...
    Malawi is a politically silly and sleep nation ..
    You can't see this nonsense in other countries....I regret being a Malawian

  • @LazarousBwanali
    @LazarousBwanali 2 วันที่ผ่านมา

    Reach all corners of de country with dis maize especially machingas pipe are suffering

  • @FredSamuell-p2w
    @FredSamuell-p2w 2 วันที่ผ่านมา

    Akapusa adyeleni chizaziwe ndichipande

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 2 วันที่ผ่านมา

    PAKUFUNIKA KUMAWONETSA ZIMENE AKUNA ATIDZIMULIDWE MANGANYA

  • @khwimamtonga954
    @khwimamtonga954 3 วันที่ผ่านมา +2

    Boma boma

    • @LoyceChipwaila
      @LoyceChipwaila 2 วันที่ผ่านมา

      Boma boma manganya yo ?? 😂😂

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    akanambe,ndi,usi,wabwino,nindani,

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    ife,tikuvutika,mubwele,nacho,kuno,chimangacho,,ausi,mukhale,mtsogoleli,wabwino,

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 3 วันที่ผ่านมา

    A Dodima Ali kuti Kodi Kodi ntchito Za VP ndi zimenezo kapena chimangachi ndalama zake zikuchokera mu thumba la manganya

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 3 วันที่ผ่านมา

    Mukuona uphawi wanu ukutha chifukwa chachimanga mukulandilachi kodi kuti akusisileni fetereza kuzakolola chani ndikulandila bola chani mamvuto kumalawi sangathe komatso sikuti ndiose angalandile iziii chachikulu usi chonde tipaseni fetereza osika tengo

  • @VioletFly-kf5do
    @VioletFly-kf5do 3 วันที่ผ่านมา

    Olandila landilani, okudya ndalama idyani vote ili muntima

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    anjawala,,,mupusa,naye,usi,inuyo,mukungo,lankhula,nzanuyo,akugawa,chimanga,wabwino,nindani

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt 3 วันที่ผ่านมา

    Chilima anazitengeratu kkk

  • @GroupFortyfour
    @GroupFortyfour 2 วันที่ผ่านมา

    Kungoti iyeyi wasowa chochita azingoyendera u vice president wakewo basi..asanamize dziko manganyayo 😢😢😢

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo 3 วันที่ผ่านมา

    Ok

  • @AbdulKapinga
    @AbdulKapinga 3 วันที่ผ่านมา

    Anali chilima iwe usi ndindaniso kape iwe

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    anjawala,moyo,wasanje,,tausiyani,kd,,inuyo,mikwanitsa,zomwe,akuchita,usi,misiyeni,adyetsr ntundu,wake,

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera 2 วันที่ผ่านมา

    Manganya

  • @leganzuze3004
    @leganzuze3004 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mcp kumpatsa VP ntchito yogawa zinthu Iwo akutakata ma file ndi misonkho
    Akumusewera bwinotu
    Azindikira September..😂

    • @Mastonlebiam
      @Mastonlebiam 2 วันที่ผ่านมา

      Chakwela achikuchita zinthu Kodi ma mp 2000000 akuchita nayo chiyani maka asulemani musatipusitse ndinu azibwana mukudya uku mukutukwana zazi

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    akabambe,agawe,chawo

  • @LissaNezala
    @LissaNezala 3 วันที่ผ่านมา +1

    Iiiiii munthu tu uyu anabadwila ku Zimbabwe so anthu ambiri aku Zimbabwe amakhala afiti

    • @AnnahKachidza-e8y
      @AnnahKachidza-e8y 3 วันที่ผ่านมา +1

      @@LissaNezala kuzimbabwe kulibe afiti amfiti ndinuyo mukunyoza munthu amene akuthandiza wanthu anjala usi mpaka 2030 woooo

    • @BerthiaMwantani
      @BerthiaMwantani 3 วันที่ผ่านมา

      Kodi ntchito xofawa chimangayi ndi ya a VP?
      Amasunga Dala kuti atagawe pamene tikuyandikira zisankho..Chimanga tilandira koma vote simuiona mwapha kale anthu ambiri ndi njala ...Ili mukuchitali ndi bodza

  • @ChanceJeregn
    @ChanceJeregn 3 วันที่ผ่านมา

    Kagwere

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 3 วันที่ผ่านมา +1

    Politicians mukutanipo??? Thius misonkho yathu or katundu wa ma donors...what is the VP doing??? Cheap politics

    • @retirementtoafrica
      @retirementtoafrica 3 วันที่ผ่านมา

      Unfortunately ma donor anasiira ntchito mapolititian ngati boma

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 วันที่ผ่านมา

    amusi,usi,apulumutse,anthu

  • @AustinChikaoneka-ow2rv
    @AustinChikaoneka-ow2rv 3 วันที่ผ่านมา

    Munthu othandiza anthu umajambulitsa kumeneko ndiye kuziyenereza

  • @ROSEKATHYOLA
    @ROSEKATHYOLA 3 วันที่ผ่านมา +3

    Abambo inu ndi osokoneza kwambiri

    • @retirementtoafrica
      @retirementtoafrica 3 วันที่ผ่านมา

      Kodi mesa wachoka chipani dzulo. Akusokoneza bwanjinso?

  • @MarthaGama-q1o
    @MarthaGama-q1o 3 วันที่ผ่านมา +1

    A VP alowelela ntchito yawenitu apa, ntchito imeneyi woyenela kugawa sinuyo please Bola chinakakhala cholima nokha 😂😂😂😂

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu 2 วันที่ผ่านมา

    This party is urs usi kabambe ndi njawala munaba chipani

  • @JackMvura
    @JackMvura 3 วันที่ผ่านมา

    UTM ndi usi not kabambe mwini chilima RIP anamupatsa chipani

    • @chrischigoma5854
      @chrischigoma5854 3 วันที่ผ่านมา

      Anakuwudzani choncho SKC yo?

    • @JackMvura
      @JackMvura 3 วันที่ผ่านมา

      @@chrischigoma5854 muli kumalawi kapena kwana chilima asadachoke ku UTM otsatira wake simukudziwa