Afunika kukamba president ngat ayenda aut or akabwela afunika kukamba, comwe comwe amacita nako Keanu kumawi mwacita over mudziko murivisisi but muri umphawi
Palibe chomwe akulakwisa.... Opusa ndi asirikaliwo....they supposed to protect us all not to be cheaply manupulated by stupid dumb leaders... Ngati leader akupanga zopusa...atsilikali ndamen amamuthamangisa not just following nonsese
Bodza bodza asilikali achitezo cha african union kuli south africa Tanzania Malawi kenya moti asikali awiri a ku South Africa aphedwa week yomoino bodza bodza
Kamunthu kodzungulira mutu ka chakwera bwanji otsapeleka ana ako mkadziwako nda bare ako ndi wamisala inu uyoyo komaso zikhare chinkhope kunyasako ndi mtima momwe
Koma izi ndiza boza kuno ku South Africa timonela news😊 ku SABC amanena kuti asilikali A South Africa mothandizana Malawi Tanzania Kenya akumenya as peace keeping force moti Asilikali awiri a South Africa A mwalira
Am following you from Pretoria 🎉❤❤
Poti asilikali a Malawi ndiopusa ndikale alolelanso zopusazo .
But MCP never repeat on 2025
I love bakili muluzi tv news 📰 they tell the truth we are following you from Zambia
Thanks ulemu wanu big God bless you because you make us happy
Thank you boss,,,we always appreciate you
Brothers n sisters tiyeni tigwilane manja Kuti ziko lathulino😢😢😢😢
Anthu amat akumangani ifeee kudandaula
Following mwachidwiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii, you're genius keep it up
Make History ya abraham Lincoln
Good work .... amalawi chakwela akutisewelesa kwambili watikwana
Always your talking the truth story God bless you big man ❤
We are proud of you bg man, only you our hope
Keep it up our jenius
Amalawi chakwera wationongela dziko uyu,,,,, ndipo inu amene mukutaya nthawi pomuwombera manja ndinu opusa,,, anzakeawenga zokha zokh
Zikhale ng'oma anakufikapotu😂😂😂😂
Thanks for the update we have been waiting for this
Confirm that
❤❤ chakwela basi dziko wayigulisa palibe za Malawi apa 😢😢
Always respect
"a Malawi akufuna kumwa Tea" 🔥🔥😂
Kkkkkkkk inde inde tufuna tea ife
Big up💪✊
Am following you, please may you Also teach us about Hutu and the Tutsi of Rwanda as Paul kagame is president of Rwanda
Best tv in africa
Respect brother❤
Respect to u brother
Yaaa Chakwela ndi dolo,
Thank br for letting us know 😂
Kuyendetsa dziko mumawona ngati limayendetsa ndi dziko limodzi, amathandizana chinchilla ndithu
Salute big man
Best TV
God bless you boss please musamasowe chonchi
Thank you big wathu true story 🙏🏼🙏🏼☀️☀️☀️
Aaaa ine adzakambe za masambuka death paja peter muthalika akukhudzidwa
@@user-ko1lk3br4rBaai waikamba iweyo mesa ukudziwapo kanthu
I support good deal....
Deal ili bwino kwabasi
We are together big man!!
Thank you blather ❤❤❤❤❤
Good documentary
Popanda bakili muluzi TV bwezi a malawi 🇲🇼 tili mu mdima
Our own legendary
Chakwela you mast go Galu
Mumakwa
I am Fom Moz 🇲🇿
Kukatenga anthu ku D R C kudzaphera mu malawi,ndekuti ku malawi nde koimitira magadzi aanthu nde wafikapo mbusa ,
Respect Bossa yama Bossa
Ulemu wanu bwana ❤
Afunika kukamba president ngat ayenda aut or akabwela afunika kukamba, comwe comwe amacita nako Keanu kumawi mwacita over mudziko murivisisi but muri umphawi
Ndie ayaluka kwambiri
Pastor ameneyo eeeeee
God protect our country malawi 😢😢😢😢
uyu si president ayi kodi kuno ku malawi kulibe asilikali tipange order captain ibrahim traore azatenge boma lathu
Koma mposoo Kuno asilikali tinakwilila ndithu
I am on your point
Best tv
Tonsefe tinaripo pomwe APM ndi DPP amalamura dziko la malawi ndipo tikudziwa momwe iwowa ankayendetsers dziko, ndiye tikudabwa kuti TV imeneyi imangowona zorakwa za boma lapanori, kapena tiziti ndinu murendo ku malawi kuno?
Palibe chomwe akulakwisa....
Opusa ndi asirikaliwo....they supposed to protect us all not to be cheaply manupulated by stupid dumb leaders...
Ngati leader akupanga zopusa...atsilikali ndamen amamuthamangisa not just following nonsese
I was miss you
Bodza bodza asilikali achitezo cha african union kuli south africa Tanzania Malawi kenya moti asikali awiri a ku South Africa aphedwa week yomoino bodza bodza
❤❤❤❤❤❤❤❤❤you brother
Chakwela ndi buzi yamuthu Yona uyu atipha
Ulemu wanu brother
Komaso ngozi iyi ndiopsa kwambili bwanji akanaika pamozi china chavetsa chison china chomaliza galimoto tomwe ikunyamula malilo a chilima vp president zoona ikhale iyi kuboma kulibe galimoto zapamwamba chakwela akuonjeza inu
What then shall we do . ?
Ayaruka garu ameneyi mbuzi kapuku
akulu ndinu apaderadera, god bless you,
This guy mmm atipha
Kkkķkkkkkkk umphawiwu mpaka tipatseni mafuta ife tikupatsani asilikali
Chakwera mbuzi yeniyeni
Zikharr Mbuzi yeniyeni
Asilikari nawonso angoona zinthu zikuonongeka. Bwanji osangopha Chakwerayo basi tione zina
Uremuwako❤❤
Maboza toooo
Chipani chimenechi chatitopesa chzipita,chatidzunza nkhanza zachuluka.
Ku mulanje machine amodzi koma kulibe ma form😅😅😅😅
Muthire fire🔥
Kamunthu kodzungulira mutu ka chakwera bwanji otsapeleka ana ako mkadziwako nda bare ako ndi wamisala inu uyoyo komaso zikhare chinkhope kunyasako ndi mtima momwe
Tikuynela kukhala anthu ochenjela stidzalola tizavotanso kawili
❤ Live
Kupusa Kwa asilikali a malawi
Best 1
Ndiwamisara chakwera
Anthu amat akumangani bg
Tiphwetekanaa
Kumapha mtundu wa a Malawi pofuna kulowetsa ndalama thumba mwawo ,Koma akulu awawa ndi Mulungu yekha awapange sorted ,Mulungu anachokera nzeru anawachotseranso
Tinasankha njoka
Ndimasangalala ndimomwe mumalankhulira mwawukali, galu chakwera ameneyu ndimunthu osanva
Ulemu wanu big ❤❤❤❤❤❤
This country mmmmmm 🙌💔 silidzatukuka . Lili mmanja mwa afalao
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Kuchikamwa kwa chuleko
Atiganizireko zokha za ku imigration boma litengepo ngawo plz plz tikumva ululu kwambiri kokha ku ma passport
Koma izi ndiza boza kuno ku South Africa timonela news😊 ku SABC amanena kuti asilikali A South Africa mothandizana Malawi Tanzania Kenya akumenya as peace keeping force moti Asilikali awiri a South Africa A mwalira
Chakwela amalawi sopepela uoona ngati ungawine
Chakwela ndi president wamisala Komaso
Ziwanda zakumidima zikumuvuta kwambili ndipo Ngati amalawi tingalole kulamulidwa ndi chakwela 💯% zilala milili ikhala yambili kwabasi
Zomvesa chisoni kwambili
🙏🙏🙏🙏
Umakwana bg😂😂😂😂😂😂
Ndipo pa za machine eeee ai akuonjedza tizavotatu koma
Mbuzi ya presidente iyi
Uremu wanu🙏🙏
Uthu oipa chakwera😅
Malawian people amene angazavotele MCP in 2025 ndiwotembeledwa basi Muthu ameneyo mpaka moyo wake onse
Adatisithanitsa km ku Israel tikulandila 4 million mpabwino bwanji
ife dzobeladzo tinadziwakale kut akufuna kuba ma vote mungila yama passport amati sistm ama nama
Osowa cholankhila iwe,ndie mwaluzatu kale ikhale nkhani imeneo zopusa 3:01
❤
Nice
Ife amalawi sitikufuna chakwera tisavotera Peter mutalika
Bambo wa dpp wabodza.Otsati chakwera say your president
KAGAME tu ndi chilombo, amalawi samalani ndithu.tufunsani ife aku DRC tikuuzeni khani zo badwitsa za KAGAME.
Vomerani kuti mulibe anthu oti akuvotereni. Mwakhala mukuononga dziko lino amalawi adatopa Nanu.
Mbava zachabechabe