Ndiposo akazalowa ndende ndikuwalandanso katundu yense chifukwa ndi misonkho yathu anthu akuba awa no ball out ndende to count not house arrest on ndagwilisana nawe Mr salute
Chakwera ndi boma lake la Mcp akuziwa mavuto onse a Malawi akukumana nao kamba Ka ulamuliro olephera koma asankha kukhala chete chifukwa akuziwa kuti zawavuta
ndale zili ndi mwini wake ndiye satanayo zophana chifukwa cha ndale maboma ose a m'mbuyomu apangaso zomwezo kusonyeza kut olamulila chinthuchi ndi mdyelekezi bas
Khani zina pena sungazivetse mulungu yekha basi 😢😢 atithandize mulungu dziko la Malawi lafika povetsa chisoni kwambili mmm
Ndiposo akazalowa ndende ndikuwalandanso katundu yense chifukwa ndi misonkho yathu anthu akuba awa no ball out ndende to count not house arrest on ndagwilisana nawe Mr salute
osaopa osatopa brother mcp tiyidonyole mutu chakwera anapha chilima
Mbuzi zina nkumati boma ndi lomweri kapolo wamunthu, zitsilu asatana anthu opanda chikondi zikutizuza muzambili kunamiza anthu akuvutika kwambiri kumidziku mbuzi zawanthu agalu Inu boma lakupha.....zikamayendela akuwona ngati zawo zikuyenda akuwona ngati aliyese zikumuyendela galu amenewa MCP 😢😢
Osadandaura comrade wathu Mulungu wathu awasiya poyera awa anagoputa kwiyo , kwa Yehova awa.analakwa, kwambiri a chakwera awa
Chakwera
Kunkuyu
Namajekete
Chimwendo
Nkaka
Manganya ndi ena ku maura life sentence
Zoonadi 💯
Zosamyenda
commission of inquiry they eat money without doing nothing😢😢
Uremu wanu comrade osaopa osatopa osafooka
Walasa 😂😂😂😂 indeed devil's zitsilu za atsogoreli....❤
Your right my brother..
Thats good idear keep it up with that story
Welcome to fighting zone keep it up God will bring this MCP down very soon,,
Mumakwana big man
Chakwera ndi boma lake la Mcp akuziwa mavuto onse a Malawi akukumana nao kamba Ka ulamuliro olephera koma asankha kukhala chete chifukwa akuziwa kuti zawavuta
Chakwela ndi manyi apamimba onukha kumatako Kwa president sichimunthu ai ichi chichoke basi
Achimwene ndizomwe tikunenazo ndipo akamanena alibe manyazi pa zomwe dpp inachita mmalawi muno sitingayelekeze ndi mcp kutali kwenikweni olo pa kota sakufika.Achimwene dziko muno mulibe tsogoleri izi ndimanena nthawi zonse, mmutu mwa chikangawa mulibe chilichonse mbuzi ya munthy. Zimene mukunenazi ndizomwe tikufuna ife a malawi atiuze ifeo tili pambuyo pa msusa black box ibwele apa zopusisa ai dzosakayikisa dpp ikubwerela manyakawa chaka chino wakukasiya.
Chilungamo wachilankhula ambuye akuonjezele nzeru ndi madalitso more faya ambuye atiolotse munjila iliyoseyo koma tioloke basi
Zowona akamupitikisa Moses nkukuyu anaripo wowaganizira koma ngozi yowopya ngati iyiyi Sana ganizirepo ariyese kumwamba kukuwona
Auzeni athakati amenewa
❤❤❤ following u
More 🔥🔥🔥🔥
Aise umatha kkkkkkk
Thanks 🔥🔥
Umakwana bale tonse tagwilizana kuti adad boma osamanenanso kuti mr ai kumangoti chikangawa alibe ntchito ndi mbuzi ya munthu.
Mwana wamamuna walankhulatu nice
Chaka chake ndichino sasipekiti apedzeka
Apezekadi sasipekiti 🎉
Anthu otsusa bishop msusa aja anadya ndalama ndi oyikira umboni wabodza,,
Wayamba bwino mnyamata chaka chino palibe kuopa akatimanga APM adzatitulutsa pakangodutsa miyezi yochepa, Chakwera tapha basi
Ndipo true
Auzeni asatanawo
Tisadandaule ayi kumwamba kuli Yehova amenyera nkhondo Amalawi,Analolera ana Israeli kunzuzidwa ndi falawo kufikira nthawi yoikika anawatulusa ndi katundu wawo yense
Chitukuko chimodzi chomwe mcp yapanga cholozeka ndi kuika airport mukhalango ya chikangawa bas
Mcp ndi yakupha
😂😂😂 ndiwe katundu ase osaopa ayi
Malawian good guy
🔥🔥🔥🔥🔥
Umatha aise❤
Ndimakumvesela ambwana kkkkkkkkk ndiwe katundu
ndipo zoona zokhazokha, zomvetsa chisoni kwambiri
Kuyankhula konzeka ma suspect tu alipo koma amaopa kuphedwa
....apite agulu kunyinda awa! Mulungu osatha nyengo, tikufunani😢
Chakwera ndi nyani inu hule
Apakile awa akasome
ndale zili ndi mwini wake ndiye satanayo zophana chifukwa cha ndale maboma ose a m'mbuyomu apangaso zomwezo kusonyeza kut olamulila chinthuchi ndi mdyelekezi bas
Zoona ndale zimatsogozedwa ndi satani koma chakwera phomupha chilima analakwitsa kwambili ndupo mcp chipani ichi chithe sitikuchifunaso
Ndipo zopsyetsa mtimatu zimandinyasa kwambiri 😢
Mawu awa enawa akuopa
Iweyo ulindi mfundo zabwino kwambili
Bruh umatha iweyo kuganiza kwabwino
Thanks
Auze aziweso
Yemweyo galu iwe, akuti ndakuona ndakuona, ndiwanyawu basi 😂😂😂😂
Kkkkkkk guys this is good man
Thanks
This is not true. You have said bad about MCP, but Malawians know the reason you think can accept lies.
Are you true malawian ?? Maybe you are part of them