Tikuonera mfumukazi chfkwa Cha Cosoma nde za ma gulezi tisazidabwe angochepetsako wez bas or else anthu angayambe kuituluka mfumukazi osamaonera Much love Actors and actresses❤
Mwachurusa zovina please next tm zichepeko .... mfumu kazi kudikira agiling'ande sanje yabwanj iyi pa guru la anthu asiye amayi asangalele milandu kunyumba kwanu 😅😅😅😅😅😅😅
musaiwale kuti seweroli litheke zimafunikanso ndalama, timalikonda inde koma sitipereka kali konse kuthandizira kuti alipange seweroli, let us understand, they need to delivery the requirements of the funders ...
Dear Frola: Mfumukazi series is the best drama standing as of now, however it is loosing its touch. We want to see milandu and people being called kubwalo la mfumukazi as planned. Izi Zovina komanso kuphatikiza za mdyangu zikulowetsa pansi fame ya Mfumukazi
Ai guyz kuvina is too much aaah next week izizi zithe guys ai this is not afair aaaah😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
Zasiya kukomatu iyaaaa
Ukadana ndi magule ndekuti u don't follow the theme
Eti inuuu sizikubeba aaaaa
Ndipos. Inu
Zatikwanadi iya
Greetings from North London UK, this is the best comforting version and you deserve an Oscar 😅
Welcome back Jameson ndi Gututu tinakusowani zedi.
Kkkkkkk aaàa mfumu kadzi mumakwana kuiwonesa i love you❤❤❤❤❤❤
Mwayamba zama Indian kuvina 50 minute izi sizabho mukatopa kupanga bolamungosiya 😢😢😢
Ma dance too much guys
kmt namoyo ukhalike chimene chinja amuna anzako 😂😂😂😂😂😂 you made my day dear
Tikuonera mfumukazi chfkwa Cha Cosoma nde za ma gulezi tisazidabwe angochepetsako wez bas or else anthu angayambe kuituluka mfumukazi osamaonera
Much love Actors and actresses❤
Ma dance achuluka,
Koma zilibooo for bring back jemason and gututu
Kumbali yanga cholakwika palibe chifukwa maguleonso ndi akumalawi mkomko kulimbikisana kusasankha mtundu wa munthu timakufilani from Zambia ❤❤❤❤
Ngati muzipanga zovina zanuzo kulibwino musamaponye pa You Tube Pano
Zoti ndi Sewero ayi ndithu ,koma inu nyasi zanuzo😢😢😢😢😢😢😅😅😅😅
My favorite comedy ❤
Koma muchemwali wa kalaka ayi zikomo 😂😂😂😂
Welcome back jamison and gututu🤣🤣
😄😄😄😄🔥🔥 welcome back gututu & jemason
Mmmmm madance abhowa aaaa it's too much,,
Inde tikudziwa kuti a cosoma akupatsani fund koma mmmmm kuika zovinazi kwaonjeza guys please if possible just create another crew for dancing 🎉🎉
Zoonad nyimbo zakenso zitalizitali
Mwachurusa zovina please next tm zichepeko .... mfumu kazi kudikira agiling'ande sanje yabwanj iyi pa guru la anthu asiye amayi asangalele milandu kunyumba kwanu 😅😅😅😅😅😅😅
Kkkk koma anthu mwakwiya nazo zovina analiku nyanja abale kosangalala
Mwa joyatu mpaka kunyanja😮
Magulewo azichuruka kumene chikhalidwe ndiye chimenecho 😂😂😂
Amene anabweresa maganizo azovina ndindaniso aaaa wandibowa kwambiri
Nzeru Mulibe Serious ,Ana ngati amenewo kumapanga zimenezo m'malo mopita ku Sukulu😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😢😢😢😢😢
Gule Ali ndi ukulu nawe
paja mangochi sukulu yinatikanika kale timadalira zomwezi za music 😅😅😅
Ndi chi Khalidwe chimecho inu Kwanu kulibe chikhalidwe??
Kupanda nzeru kwayamba polemba zopanda nzeruziso 😂😂😂
Pitani ku mdyangu asasoka mubesa nkazi uja kkkkk
Kodi ndimagule kapena sewero zatikwana izi mwachotsa chikoka cha film
Jemason & Gututu mumakwana😂😂
Ifenso ndi mashingozi😂😂😂😂 welcome back Sasoka
Koma zovinazi aaaa😮😮 zawonjeza
Asasoka mwanenepatu😂😂😂😂😂
entertainers of the year inuyo mesa 🤪🤪🤪🤪🤪
Guys dance is 2much ❤❤❤ but l you guys
Kukhwepana mmmm koma yaeh😂😂😂
Ndiye itinso imeneyo kuvina mpaka film yonse aaaaa sizikukoma
Zovinazi zutidyela nthawi. Zithe this week aaaa!
Muwauze Abale anu amalidze kuonera ine 2 minutes yakwana😢😢😢😢😢😢😢😢😢😮
Ndasangalala achina sasoka mwabwela I hope kt kwa dyangu mupezekaso
Mercy ukhalike 😅😅😅...km zomavinazo zakwan yooo
Mmmmm ma dance adusa moyezo nde paribe uthengatuu apa chepetsan Kon
Chimene chija ndi chi chani akuti?😂😂😂
my favorite comedy 🤣
Munasowa ma latest 😂😂😂😂
Mudzionela nokha tsopano mwayamba zausiru kumangovinamo basi madata mmene akuduliliramo tizithera zimenezo musiyiletu mokulamulani not kukupemphani
Ine ngati Malawi zikundiwaza kwambiri, komanso tidziwe kuti kuonetsa sewero PA kanema ndizodula choncho zimafunika ma sponsor choncho zinazo ndikufuna kwa othandizawo
Tivine basi 💃🕺
Aaaa zovinazi zikuchulukamo sewero layamba kubhowa tisiya kuonera izi
musaiwale kuti seweroli litheke zimafunikanso ndalama, timalikonda inde koma sitipereka kali konse kuthandizira kuti alipange seweroli, let us understand, they need to delivery the requirements of the funders ...
Ulendo uno ndiye taononga ma bundle ndizovina zokhazokha, mukapitiliza zovinazi tikutulujani iya
Malawi to India dance😂😂
This is our own product, congrats guys
Koma zachikhalidwezi ndiye mwaonjeza kwambiri zikutidyelaso nthawi yaitali
Zovina zachuluka iya nex week zithe zimenezo t❤🎉
Koma nagama u looking very nice yooh osayiwara zama gure mm chepesanid
Khangati influence ya Indian movies ikuonekatu, Mose mwayambira kuvina kuti zimveke bwanji kwenikweni? 😄
Welcome back Jamison and Gututu
Please kuvina please please
Kma anthu mwadandaula kwambiri...kapena ndinu ma director
Timaonera ndiife mesa
Zovinazi ndy nthawi yachuluka ,, padera😂😂😂ukatero ufunapo dollar😅😅😅😅
Watching from jozi Germiston
Koma giling'ande 😂
Mwaxulutsa kuvina, sinabebe
Titani😂😂😂
Anyamata ometa mbali atulukira munasowatu asasoka , akazanu akanafa nd maganizo 😂😂😂😂😂😂😂
Kuvina uku mmm kosabebatu😂😂konyasisa
Kom mfumu kazi😂😂😂😂
Nagama😅😅😅
Mmmmm mwaonjeza zovinazi abale chepetsani
Tiziti zovinavinazi panasowekera zoika bwanji???? Eish zikuononga sewelori tisaname guys. Kuvina mapetu to mapetu!!! Yoooh
Mfumukazi, inakwatiwa ndichidzete kwabasi chofunika kumukupa khofi.
😂😂😂🙌
zinthuzi osamaoneka bwino ngat mukujambulira fone
Jamason ndi ngututu takulandirani koma apa ndiye sizikukomaso ataaaah mwachulutsa kuvina 😢
Ndiye zobhowa kumangovina bas eeesh mayo bundle yanga ine
WhatsApp GB too much Alds nde izi😂😂😂😂😂😂 ndizitulukatu ohooo
Gb akuthekanso?
Koma nanyoni musewelo iliri mulibemo size yake eeee😂😂😂😂😂
Zayamba kuipatu zinthu zinalibwino mwayamba zovinazi ai ndithu sizikusangalasa ai.
These dances depict our culture
Guys akuchulusa kuvina nowadays mmmmm mpka sizikukoma2,,pliz achepese dance
Mwayamba kuchulutsa ma dance
😂😂😂😂😂 koma mfumukazi ayi taa kkkkkkk
Apa ndiye mwayamba zinatu tsopano mwasiya kukometsa tidzingoona kuvinako
The dancing scene is too long.
Zovina thumalichi pilizi!!!! Next episode zisakhalemo plz
Zovina ngati ma filimu a Bollywood buanji? Izi zichepetsedwe or zitheretu
Past 2 weeks sizinakome ataa! Gule watikwana ...Kodi mkulu wachibwibwi uja alipoo amatiwaza kobasi
Kkkkk ngillingande I
Ma dance wo sakulakwika kom akumatenga nthaw yayitali nde mungochepesa nthaw yovinayo bas
please improvement ndiyofunika ma camera gwirisilaniko ma HD camera for high quality.
Please madance chepetsani, sizukoma Kuma dancewo
😂😂😂😂😂 ²⁰²⁵ Mfumukaxi sikundivekera bwno too much madance eish !!!! Plz bola musiponya kumapeto
Padera wadya ndalama yaulele bac ati ndimavana naye aaaaa zalowa zokha😅
Kkkkk koma gayezi ayi mwatopa ndithu
Koma nde zasiyaso kubhebhatu osangosiya ma sewelowa kuyamba ma dance wo
Komanotu apa nde zalowa chibwana kuvina konseku mix iyiyokha sikuchoma
giling'ande anayionela patali eeeeh mfumukazi amadikura 😂😂
Kumbali Yanga ma letesit anasowadi ndi omwe amakomesa komedy yimeneyo kwasala kwa nyamgu comedy akufunika
, ati ife ndima latest 🤣🤣🤣
Mwaonjeza ma gule plz
Dear Frola:
Mfumukazi series is the best drama standing as of now, however it is loosing its touch. We want to see milandu and people being called kubwalo la mfumukazi as planned. Izi Zovina komanso kuphatikiza za mdyangu zikulowetsa pansi fame ya Mfumukazi
Naye padera sanachenjere bwino 😂😂
Gays mwayambano chibwana zanuzi zasiya kusangaratsa aaaa bs tidzingowonera kuvinako mulibuthenga wanji munkuvinako
Pls zovina muchepeseko mmmm it's too much komaso zovina mulibe choti tingaphuzilepo mmm
Mwakoma guys❤❤
Amfumukazi mwatani Kodi aaaaaa nyimbo sizikometsa firm