A Aisha Mambo Alandila 150 Million Kuti Asokoneze UDF - Evance Khaiya

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ก.ย. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Evance Khaiya claims that Honourable Aisha Mambo, chairperson of the UDF convention committee, has allegedly pocketed MWK 150 million from the MCP to sabotage the UDF's political ambitions.
    Pa Nyasa Voicebox, Evance Khaiya wati wapampando wa komiti ya chipani cha UDF a Olemekezeka Aisha Mambo ati apereka ndalama zokwana MWK 150 million kuchokera ku MCP pofuna kusokoneza zolinga za chipani cha UDF.
    #malawi

ความคิดเห็น • 58

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Kodi opposition ikhala bwanji ubale ndi MCP?

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +8

    Komanso UDF monga Chipani cha Opposition chikhalira limodzi ndi cholamula bwanji ? Pangani mgwirizano wo Koma MCP Will never rule again. God will save His people Mphamvu Zanu zingachuluke bwanji inu a MCP Koma simungagonjetse Namalenga. Lets wait and see.

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Osaculusa kuyankhula muzingotipasa uthengawo

    • @lucianogeoffrey4275
      @lucianogeoffrey4275 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Yes, please mukumamalizatu nokhaso nkhani yonse amatero?

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Vuto lake
    Umphawi sizinthu muyaluka nazo
    Inoyo ndi 2024 osati make zana 1965 kunalibe ma phone 🤳 Facebook

  • @adamujosaya-q8e
    @adamujosaya-q8e 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Aisha mambo pamodzi ndi agaru omwe mwawayitanawo mudzagendedwa nawo limodzi komaso kwabwino kumango njamuka kusayana mkuwononga chipan sha UDF please Aisha mambo pamodzi ndi agaru omwe mukut abwere wo Koma a MCP ndat mukufuna mufike 2025 please don't come there this is oning??

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona 20 นาทีที่ผ่านมา

    A Bakili Muluzi analipo ndi Tembo pa mgwirizano koma DPP idawagwetsa pano zichitikansi akalimbila mgwirizano uwu.ndipo tsopano udf iferatu

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 4 นาทีที่ผ่านมา

    Achotsedwe di adzipita Kung, ona ko okha, tengerani chitsanzo cha dpp anachotsa anthu wonse osokoneza

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 7 นาทีที่ผ่านมา

    Inde ayisha mambo achoke ku UDF ndi mayi oipa kwabas aaaa hijabu yabodza bas

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndimaiopa MCP kwambri kupha Chilima ngongole tho fertilizer otchipa chimanga chotchipa eeee MCP mbambande

  • @AnnieNyirenda-d5t
    @AnnieNyirenda-d5t 17 นาทีที่ผ่านมา

    A phweka chikangawa aliyese akufuna mahule onse akupita nkonko ku mcp

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aisha Mambo ndiwadyela😢...amapanga zinthu Ngati sanatuluke kumatako Kwa anthu bwanji 😢😢😢

  • @LeonardChinomba-r5e
    @LeonardChinomba-r5e 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Man ulemu wanu ine ndili kuno ku south Africa koma ndakusatani mu VN yanuyi u spoke well Aish mambo is eival wangovala buyi buyi koma ndi mfiti sakumva chisoni ndi anthu mene akuvutikila son beich

  • @PatrickChirwa-cv5cd
    @PatrickChirwa-cv5cd 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inuyo akupatsani ndalama zingati a DPP? UDF anaipha ndi a DPP osati MCP kuti ikhale ndi ndi aphungu 7 okha out of 36 ku Eastern Region. UDF isaitane DPP ndi njoka.

  • @TwalibiArafred
    @TwalibiArafred 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Hule ameneyo ngt walandiladi ndalama ku mcp aziwe kut malawi sii yambuye akhe..ife tikuvutika mziko muno UDF ndichipani chathu.iyeyo ndi uhule wakheyo akachitile kunja kwa UDF

  • @ChrisEnos-to5uv
    @ChrisEnos-to5uv 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Muthu sungapange dzokozekera ndi m'dani wako kalipokalipo aishawo asatinamize

  • @Fanzo-h2l
    @Fanzo-h2l 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A UDF akuyenera kusamala naye nzimaiyu musaiwala kuti ku dpp analiponso anthi amena amasokoneza dpp Anankhimwa atalandira ndalama ku mcp kuti awononge chipani cha dpp a mcp mukhalike komanso Aisha angotuluka achisiye chipanicho iye apite ki mcp ko 150 million ndi chiyani kuti agulitse anthi a UDF ku mcp

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    AISHA MAMBO NDI GULU LAKO MUKATHERA KU CHIKANGAWA.BASOP!!!

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkazi ameneyi walandira ndlama zamagazi basi wasatanic imeneyi achoke basi sakufunika ku udf

  • @SammyChakwana
    @SammyChakwana 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achindidwa kangati kuti agulise udf ku mcp pantumbo pako nzimayi iwe

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komatu ngati UDF yathu ikutha chotchi ndichifukwa cha DPP not MCP

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zalowa personal tsopano.Mwina anakukani chibwenzi

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma Dani lu watukwanika pang'ono koma mayiwa mpaka awakumbusa komwe anatulukira ayi zikomo

  • @TwalibiArafred
    @TwalibiArafred 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    amene akunenayo kut inu ndi a DPP ndichisilu komso galu pamozi ndi amakhe

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    MULUNGU walinyanyala dziko la malawi chifukwa cha mcp

  • @PaisonUmali
    @PaisonUmali 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    aisha ndalamazo kadyereni ku mcp komweko tulukan mwaulemu

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    2019 mesa anaphatikizana lero mukut bwa aaaa muzipaganawo

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😮 mayi uyu ndi galu kwambasi pa nyini pakenso apite Ku mcp galu ameneyu

  • @AchiwaNikisya
    @AchiwaNikisya 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndi zoona a kunena akhayiyazi ine zinandiwawa pitilizani comrade

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 41 นาทีที่ผ่านมา

    Ase umawelenga bwino kwambiri

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaaaa ndiwe wabodza amadziwadi iweyo ndamenesudziwa Kodi mesa

  • @Bashir-g1t
    @Bashir-g1t 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achoke zachibwa sitikufuna 😡

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aisha mambo inuyo panyini panu pamodzi ndi amuna anuo mapwala awo

  • @chesterkumwenda
    @chesterkumwenda 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    mcp yisapite kumene tikayigendako

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukunama Kodi audf mesa adpp anathawa.kuudf

  • @jamesbanda8602
    @jamesbanda8602 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ufulu wakupanyo ulinawo iwe galu wamapolo panja

  • @AlexBanda-d5v
    @AlexBanda-d5v 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ee koma achakwera atha Azeru tsopano

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe mayi ndiwe chidebe cheni cheni chobooka

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sanalakwe ai koma kuzolowera kutukwana

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zikudabwitsa ndizakuti anthu onse akukuwa kuwa apapa si a UDF onsewa ndi ADPP. Nonsense nonsenu sindinamve mukusapota UDF amene timamudziwa kuti ndi sapota wa UDF ndi ABDUL basi .Leave UDF alone. Mdani wa UDF ndi DPP si MCP AYI. For your I.nformation mbuli iwe a Tcheya anapangapo mgwirizano ndi John Tembo chifukwa Bingu anaipanga chipongwe UDF. Ndiye DPP ndi mdani number one wa UDF. Usachimvera Chikadeti cha Dpp chimenechi.

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Is better DPP than MCP
      Anthu zimene akufuna kuti azidya katatu osati zonsezo
      Mukakamba za Bingu ndiye muyaluka
      Bingu anachita kugula chipani chija chifukwa vice president analipo ndiye palibetso kuyankhula za Bingu
      Acheyawo dyera kwambiri

  • @ShaibuSmart
    @ShaibuSmart 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aishah Mambo Mai mulibe chison

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mayi ameneyo ndi wa MCP ndi galu

  • @UmariBashiri
    @UmariBashiri 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ayi MCP sitikuwamfuna

  • @AidantBwanali
    @AidantBwanali 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bambo ake analind udindo ku MCP

  • @LoyidKarebe
    @LoyidKarebe ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komaanthu atopa tsopano

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mcp ndiye kuti mukuiwopatu

  • @ChisomoBanda-jo4ix
    @ChisomoBanda-jo4ix 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyini yake amenei Aisha ndi m c p yake

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tadziwa kut ndinu adpp zako

  • @StanelyPhiri-kg1ix
    @StanelyPhiri-kg1ix 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Comrade you are not Worthy Freedom fighter

  • @bwenzilanga
    @bwenzilanga 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uchitsilu mayi inuyo

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma 2009,Bakiri muluzi anapanga alliance ndi mcp.

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndye zinatha bwanji taswera limodzi tinachangamuka pano ovota ndi anthu osati azavota yekha uyo wankhope ngt mamunayo

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ku constituency komwe amaimila Aisha ndikomwe kumachokera Abdul Lapken anaphedwa ndi MCP uja,zoona amai amenewa angamalimbe mtima kumaitana MCP kuzochitika za UDF zoona,anthu akudera lake azimuona ndidiso lotan maka maka akwachapola kwe Abdul Lapken amachokerako

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Shame umunthu alibe ufiti koma eesh ndlama🙌🙌