Nde MCP imeneyo, olo nthawi ya tsankho ku South Africa, MCP inali mbali ya azungu okupha anthu okuda ngati Israel. M’busa wachikhristu kutenga mbali ya ayuda odana ndi yesu chifukwa chofuna ndrama. MCP out!!
Ena ayimbaso nyimbo yoyamikila DPP tidziti agudwa?nyimbo zisiyeni ziyimbidwe opindula ndi nyimbozo ziwapindulira ,amene akuyimbawo basi Koma ifeyo tidziti chani zoti nosenu ndi akubah mungakane?
Kutopa naye chakwera osatu bon wapenga kod mukukhuta chakwera akukugailqni ndalamq zokubazo eti kod chokisangalasani ndichan kusapota chakwera akubelatu 2025 chake kulibe
Basi ma action azikhala apa social media amalawi akudya chitedze m'midzimu,,,koma malawi yovetsa chisoni kobasi.akutitu kuli omenyela ufulu,,,,ena akuti ndi président a anthu osawuka apa social media basi daily marecoder pa social media olamulawo akulamulabe anthu akuvutika,,,,katundu daily akukwela mitengo,, Kwacha ndiye ikukugwela m'manja😂😂😂😂pomakafuka ku nsika kukapezaso kwacha yagwa,,,, amalawi tikungotukwana pa social media basi,,,,,very shem malawi,,,,,
Mr president bon kalindo tell them this people's is nonsense 🙄 😒 😑 more fire 🔥
Km mr bon kalindo inuyoh ndi one,Tell them the most go ,don't take mlw like nnyumba mamawo ayih
Ndipo a police kwa lingala alemera heavy mmmm uyu Bon kalindoyi ndi chimachine chimaona kutali
😅😅😅😅 nyimboyi ofunika remix
Kkkkkk koma iweyo eti
Nde MCP imeneyo, olo nthawi ya tsankho ku South Africa, MCP inali mbali ya azungu okupha anthu okuda ngati Israel. M’busa wachikhristu kutenga mbali ya ayuda odana ndi yesu chifukwa chofuna ndrama. MCP out!!
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mupeke nyimbo zambiri kikikiikiki plus Hahaha 😢😢😢😢 Mr Kalindo kuusaka Unyolo kikikiikiki
😂😂😂😂😂😂 kusakasakadi unyolo uku owo.
😂😂😂😂😂😂😂Koma bon
Oyimba akugulidwa ndima 50 million ngati dan lu.ko iyi yokha Ya mr Dc yigulidwa 150 million 😂
😂😂😂 zooona tingoyamba zoimbaz ndimbali yathu
Kkk kma iwe bon kalindo 🏃📀😂😂😂
Kkkkk ati kusakasaka unyolo ayi mumatimilira amalawi
Ena ayimbaso nyimbo yoyamikila DPP tidziti agudwa?nyimbo zisiyeni ziyimbidwe opindula ndi nyimbozo ziwapindulira ,amene akuyimbawo basi Koma ifeyo tidziti chani zoti nosenu ndi akubah mungakane?
Kkkkkkkkk ndaikonda nyimbo yakoyo Kalindo pangani collab ndi Kansime.😂😂😂
Ndipo inuu ft kansiime kkkkkk
😂😂😂😂😂😂 ati kusakasaka unyolo ayi zikomo
Mmm, Awa!! Bax munthu nkulu kulu dairy kumapanga zimenezi,, kuyamba kwa misala bax,, ndye poti niwamasewero
Mukudanana nazo bwanji a Malawi tiziziwa chilungamo basi
😂😂😂😂beans mulipazingati😂😂😂😂😂
Kma Bon 😂😂😂😂
Kutopa naye chakwera osatu bon wapenga kod mukukhuta chakwera akukugailqni ndalamq zokubazo eti kod chokisangalasani ndichan kusapota chakwera akubelatu 2025 chake kulibe
Kkkkkk kuyankhula ndi mipando yokha.
Ipase moto Mr DC azazolowera anyani amenewo
Kkkkkkkkkkk kma ichichi anakonzaaaaaa
Uyu ndikatundu Ana wumbidwa
Wayesera kuyambisa ziwawa koma walephera aise
Basi ma action azikhala apa social media amalawi akudya chitedze m'midzimu,,,koma malawi yovetsa chisoni kobasi.akutitu kuli omenyela ufulu,,,,ena akuti ndi président a anthu osawuka apa social media basi daily marecoder pa social media olamulawo akulamulabe anthu akuvutika,,,,katundu daily akukwela mitengo,, Kwacha ndiye ikukugwela m'manja😂😂😂😂pomakafuka ku nsika kukapezaso kwacha yagwa,,,, amalawi tikungotukwana pa social media basi,,,,,very shem malawi,,,,,
The DC mwana woyipa
The DC on fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Malo molimbikitsa Mtendere, komanso kuti tiziwapemphelera maiko omwe kuli nkhondo kuti Ambuye alowerepo nkhondo ithe, zoona a pule nkumati nkhondo izipitilira, ai zikomo
Koma Bon Kalindi😂😂😂🙌🙌
Kkkkk umantha kuyimba kalindo
Koma amalawi mlibe zochita kapena chani sikulirilose chakwela this chakwela that mumapezako mchere azathu mwina tiku joineni pezani zochita andale palibe amene azasintha life yanu mkungochedwa nazo izii achinyamata plz 😭😭
Auze big
Ndipo inu mene akufela anthu akugaza koma munthu obwadwa ndiumunthu mkumakasainile kut nkhondo ipitilile mmmmmm
Kkkkk koma bone kalindo umakwanatu
Kabwira akudziwa koma za ma delivers 😅😅😅😅
🤣🤣🤣🤣🤣 adah awawa
Koma Bon kalindo😂😂😂😂
Nonsense chikangawa 😂😂😂
Busa inu sakharaso fumu iyaaaa
Zakuwawa iwe sindie oyambitsa nkhondo
😂😂😂😂😂😂koma kalindo
I’ve never seen the worsest president in Malawi like this crook
Ndie osawauza a DPP kuti agile oimbao
Agule oimba azitani nawo dpp ndi katundu
Fireeeee born
Kma yili bho 500000000 kwacha muyipta
Eeee km born kalindo ndatsekha mmmmm
😂😂😂😂 koma ABon inu nd one😂😂😂
Nthabwala za Kalindo tsopano
Zamanyazi boma lake la MCP ndi chakwera
The DC katundu machine
😂😂😂😂😂 koma kalindo
Uyuyu angoyambadi kuimba
Kkkk koma Boni
The DC bon kalindo
Nyimboyo ikufunika collabo🤣🤣🤣
😂😂😂👏
Kayendereni M1
Aaaaaah this guy..
Koma mkulu uyu daily
Katundu the DC
😭😭😭
Zankhondozo ndizako zimenezo
kkklkkk kom ka;indo gys
Kkkkk, kusaka unyolo ?Wakhalitsa
Bwana ameneyu saopa kumangidws
Bwana ameneyu saopa kumangidws
Akufunika ku mental awa
Kalindo akusowa nkhani wabalalika
Nkhani sizinamusowa inu kungoti muli guluso lodananaye
Kapolo wa chabe iwe ukudana ndi bon kalindo
Koma momwe dziko lilimu anthu nkumamuikira kumbuyo Chakwera mukudyatu zochuluka zisiru inu
❤❤❤❤😂😂
Kape iwe mboli yako
Iwe chitsilu ungatukwane bwana kalindo walandila ndalama za magazi
😂😂😂😂😂😂😂uyiponde
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
Kkkk koma
Aaa nonsense
Usamavere
😅😅😅😅😅So 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅Is 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅Is in my own 😅😅in this country I have no 😅and my 8😅😅is the 😅and I 8😅to 😅😅😅
😅😅
😂😂😂😂
Achibale a Bon kalindo mulikut kod apengatu uyu
Ikatero yaluma
Utapenge ndi iwe ndi chikangawa
Bon kalindo is wise and Oona, vuto ndinu amene mukupenga posazindikira kuti mukupenga
Ati kulimba ndi boma, za umbuli ndipo sudati kalindo ulira mpaka 2030, iwe sungagwetse boma olo zitavuta motani
Mark my words n save this date mulamutira only 2 yr n muno mukakhala ma demo oopsya ndipo mcp sizalamulanso from that tym
Dyera it ndinuyo a chikangawa 2030 yake iti??? Dzikoli nde lidzakhala tu masanza mmene muku bera u.
Chosecho ndewe mphawi ukuyikila kumbuyo boma
Iwe MACHENDE a mako Wanva ikudya nawo za MCP