I like your honesty madam, koma his excellency the president once said iwo pomwe adali ku college ankaumba miphika kuti apeze fees and here you are saying ana a school ankalandila allowance.Amuna anu saopa Mulungu madam ndinakhumudwa nawo.
Inetu so inspired as a girl........ therefore girls let's know who we are and our position to stand for our future......osamatengeka with all these things which seems to be so good now✊✊✊✊✊
Very grateful and humble woman your respect I was not expecting to hear this from you Mai malawi❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
After watching this, I have immediately started respecting the first lady. I never knew this lady is such a genius.
Very inspiring and touching. Malawi is blessed, to God be Glory always.
Regards
Woo Hallelujah. Very inspiring. Thanks for sharing Mama
I like your honesty madam, koma his excellency the president once said iwo pomwe adali ku college ankaumba miphika kuti apeze fees and here you are saying ana a school ankalandila allowance.Amuna anu saopa Mulungu madam ndinakhumudwa nawo.
Mai wa fuko has said it all, so wise and humble. Much love from this side ❤❤❤
Mama I am inspired with u,Thanks you remind me in my days when I was in Malawi very peaceful anthu achikondi ,proud ofMalawi
Inetu so inspired as a girl........ therefore girls let's know who we are and our position to stand for our future......osamatengeka with all these things which seems to be so good now✊✊✊✊✊
Very encouraging narrative of her life! Am inspired and Mama you are a blessing 🙌!
Eish Mama mulungu amadalisa olimbikila komanso ndaphunzilapo zambili tiyeti tizilemekeza aliyense komanso kumathandiza ana osauka ❤❤❤
Am very much inspired ❤❤❤.very much respect madam first Lady
My headgirl was Gertrude Mutharika at St. MARYS SEC SCHOOL ZOMBA
Mwatilimbikitsa madam ooh my God continue bless u mamie ❤
Great documentary. Inspirational. Ma booklet wo amwazeni m'midzimo
The first lady ever in Malawi so humble
Very inspiring. She is not an ordinary person
Very inspiring story from the First Lady
Shout out to you cousin Chrispin Chiunguzeni for the great works and the rest of the team
So inspiring our first lady
Enjoyed watching this. Thank you
A great woman with an inspiration story
So inspiring and touching
Very inspiring indeed
Helper wa Chakwela kuwononga Malawi
So inspiring 🎉
She very humble and respected lady
So inspiring
Mulungu samaxhedwa pamoyo wamunthu , onyozekayo mulungu mkuzamukuza Amen
Brilliant lady
We love you mumie❤❤
A genius!
Wow i believe one day will tell a story too😊
I tap the grace ❤
Kuyamba kuvako voice ya monicca
Munali amphawi okay ndalama mwaziona kuwukulu ndi chifukwa muli mbava
Mwadya kwanu inu?
@@milcahkwenda chaka fiti iwe
Nyc
Amene adakulandilaniwo pano alipo ngati alipo eeeee amene ammve nawo ku koma
zaziii
Ndichaniso idzi anthu akuba ngati awa
Ndiponi inu akuchita kulakhula muphuno zithu zake za ziii ngati izi
@@SliviaJosephy😂😂😂😂😂😂😂iiih koma ndaseka
God's time is carzy
Ngati nkotheka mayi ifeso tithandizeni school fees ndili ku college koma mmm moyo ukulimba tithandizeni chonde
UMUWUZE CHAKWERA MBOLO YAKE
Enanso ma first lady anenepo mbiri yawo paja ena analepera form 4
Munthuyu anakula movtika nd chifukwa kubanja kwawo konse ali mbava kuyambila ana makoloso nd anthu oipa moyo kwambili
Bolani president adakakhala masten wa
You're blessed
Anthu akuba inu!!
Ulemu wanu mama koma muziwona ngozi mumalawi pano zikunyanyila so mulipa bwino koma simukusamala anthu adziko lanu
Iwe uzimupasako chikangawa nzelu osati zopusa mupangzi
Maso ngati buluzi galu
😂😂😂😂,,,
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mulungu Apitilize kukudalitsani kwambiri khani yokondweretsa ndipo yopatsa chilimbikitso
👽
Komati muli diso,ndi malooks kapena
Koma moyo mwadutsa inuyo bwenzi mukumva chisoni ndi amphawi koma ayi ndithu kudzikundikila chuma Cha dziko lapansi
Chimayi choipa kukhamwa ndi khanso muli biiiii ngati utaka mfumbi
Mukulongotsola zithu za ziiii,,,inu mayi simunaphuzile bcz mumagulitsa kuchipiku,,chifukwa chake pano mukungotuwa olo mutaba ndalama sizikuwoneka😅
Don't be jealous
@FalesichiutsiFalesi jealous Yotani nanu,,azimayi ophuzila tikuwadziwa awa anagulitsa mbiya kuti adye
Osati kudwala koma kusanza mu basi ija timati yanu yanu
Munthu ukakhala ovutika ukachita bwino umazinza anthu kaya bwanji
Muyenera kuthandizanso atsikana omwe akusowa fees
Fumu itumbikike
Koma ufiti umamukhala mayiyu
Kumakhala ndi ulema. Kumaopanso Mulungu. Osaziitanira themberero pazinthu zopanda umboni. Akulakwira chiyani mayiwa?
Ulemu wanu Mayi wathu
Mai oipa Mtima kumposa Satan.
Ndipo zowona zake satana uyu