the ploblem is us malawians we are qyt mmalo mochithamangitsa pa mpando chichakwelacho mayiko anzathu akanakhala atamuchotsapo kale lija nkale wayambila kutizunza muja imagine munthu wakumudzi angagule sugar 3.2???amalawife tikugona dziko likuonongeka ilii
Even Nkhope ya Chithyola sikuti angakhale nduna ya za chuma inu uyu zili ndi eni ake izi oti awa ndipo even mmutu mwaomo mukuchita kuwonekera2 kuti mulibe kali konse za chuma samazidziwa awa
Koma kod ngt zamvuta isapanga resign bwanji Ife sitili kumalawi koma Pena mpaka kumangogwesa misozi ndithu my lovely country where is going with chakwela 😢😢😢
I don't care if MCP wins infact I want them to win. Ndipa mene amalawi tizagwire ntchito kukonza nyasi zosezi believe me si ziza tengela kuti ndiwe wakuti. Example mwaona mavenda mmene zina yendera
Nthawi ya Bingu mafuta atasowa kunali ma demo omwe ena analuza miyoyo chofera chake sowe. Pano tikuona mavuto enieni osati sewero koma kuli zeeeeee ma CSOs onse akupindura ndi Boma anthu uku akunya ndi mavuto anyoooo
kodi akulu amenewa akufuna chani, kuzidwa athu ayesesa koma eeee, it is a terrifing thing to fall into the hands of the living god' chifukwa kuluyi zinthu zimuvuta mizimu yakwiya kasa anayimba kale.
Kungot amarawi nzeruso muribe inu munkawona ngat kundareko azikapangaso zaubusa rerotu ndi zimenezo man of god kkkkkkkk muwona kt mupanga bwanji ife pheee pa cap town km chisoni chokha tirinacho pot kumeneko ndikwathu
Kodi zingakhale zomveka ndalama yikugwa mphamvu basi chimanga chitsike mtengo inu a Malawi dziko mkupita nalo kuti? Koma kumbukilani mtaya makoko ,Ayii mwanyanya ,Is this Desensitization system of Gvt?
Try and error. Ine Ndinayamba kukhulupirira nkhani zanu Bwana kuchokera tsiku Limene Nkhondo ya Russia ndi Ukraine ina coz mnali mutanena before Nkhondo kuyambika so now ndimakhulupirira kalikonse komwe ndimakaona kwa channel yanu
Mwaonatu Odana ndi Bakili muluzi TV ,tikamanena Kut uyu ndi galu amangoziwa kuyankhura anangochenjera pakamwa Koma kulongosola zinthu go!sugar kusowa,Kuba ndalama,kugwa kwandalama zisanzo zabwino Kut APA tinaponda mwala
Jane Ansah uja, Ambuye azimudalitsa ankalifunira dzikoli zabwino.
Ndipo kwambiri tu mmm
Manyi anu andale nose
"Sindingavotere Chakwera" Jane Ansa (2019).
@@jonathansamalani perekani maganizo anu osati kutukwana
Ndipo koopsa ankatimenyera nkhondo anadziwa kuipa kwa MCP ndipo anali katundu owopsa
the ploblem is us malawians we are qyt mmalo mochithamangitsa pa mpando chichakwelacho mayiko anzathu akanakhala atamuchotsapo kale lija nkale wayambila kutizunza muja imagine munthu wakumudzi angagule sugar 3.2???amalawife tikugona dziko likuonongeka ilii
Timaopa kwambiri ku Malawi kuno
Ulemu wanu bwana wanga ndipo sindiyelekeza kupanga miss history yanu
We warned you, Malawians not to vote for MCP. Thanks very much bakili muluzi tv. May God bless
Coz they didn't know what these people they are.. 🙌🙌
Ndipo kwambiri
Osangopanga resign bwanj garu ameneu😩
pano akati kwachaaaaa kumayankha kuti yaaaagwaa
Thanks you brother God bless you
Paja munanenaso kuti azagwetsa kwacha lero siizi
U always speak the truth boss awa zawavuta basi palibe chomwe akuziwa chokhuza boma
Even Nkhope ya Chithyola sikuti angakhale nduna ya za chuma inu uyu zili ndi eni ake izi oti awa ndipo even mmutu mwaomo mukuchita kuwonekera2 kuti mulibe kali konse za chuma samazidziwa awa
Chakwera azamwalira osadadwala chifukwa akudzuza anthu osalakwa ai
Uyu athipa ndithu
Lake Malawi inaperekedwa kale deposit😂😂😂
😂😂 kodi vice president akutipo bwanji alipo??
😂😂😂😂😂😂😂Nyanja inaikidwa pa lay-by???😂😂😂
@@RiteRoderick
Deposit tinalandira kale man kkkkkkk
Thanks big man,l really appreciate for your big job.Keep it up
Awa dziko amkangolifunirq njilu basi frankly speaking
Chakwela ndionyasa moyo ngat manyi ambava
Kwambiri
Sitikhala ni ndalama yathu Malawi ikhala Zimbabwe 2
Dziko lino president anamwalila kalekale tili tokha
Kukhala ngt analipo sibwezi dziko lathu likumva Ululu choncho zowona izi nde zinthuso tikweraso mtengo kuteloko Malawi Ali pa Moto osati zibwana
Ife nga nga nga pambuyo pa NGWAZI wamuyaya his excellency president Chakwera forever handsome president of MCP boma iloo.
Uyu nde atipha 😂😂
Uyu atipha .koma chakwera nochisoni ayi
Chakwera yi tichoseleni mulungu please kodi amalawi alakwa chani.. anthu akufa dziko mziko muno chitani kuthekera kwanu atate mulangeni ndinu😢😢
Try and error government my foot....
APM my vote
Ndipo kwambiri
chakwera ndi chitsiru cha munthu
Yeah koma kulintchito ku malawi ,ndiamene munafuna tiyeni nazo mukhaula simunati
Mumakwana boss proud of always
Eeee koma makolo Ali pavuto Chewa uyu ndioyopa
Ulemu wanu big man amene mukuimilira Bakili Muluzi TV
Abusa😂😂 zaakanika, ngati amalephera kulalikila ku chalichi chake ndeee what about Kulamulira ziko??😂
Mpaka kugulitsa lake malawi 😂 respect to u big man pitilizani kubweletsa nkhani
Useless president ever 😢
Good work
Malawi yafika pa Zimbabwe
Brother you can't compare Zim ndi MW ndekuti sumayenda koma iwe ase.
Tiposa Zimbabwe ndi Mozambique 😢
Ndipo kwambiri
Ine ndimayenda pano ndiri ku Israel aise, development structure yogola Zimbabwe koma economically Malawi better
Eshii apa malawi uja bas nanga izi ndichani angogwesa kwacha mene angafunire iye kd tiziti ziko la malawi mulibe malamuro angoyang'anira zimenezi uku ndikupha ziko ofunika ona zamalamuro achitepo kathu chonde
Ngati Fiti ziko osaphako chakwerayo bwanji watizuza ndipo dziko lamawi likuvetsa chisoni
Ndiye palichisilu china chivekele mcp woyee zazii
Big up, bakili muluzi channel!!
Koma kod ngt zamvuta isapanga resign bwanji Ife sitili kumalawi koma Pena mpaka kumangogwesa misozi ndithu my lovely country where is going with chakwela 😢😢😢
Amwene malawiwafikapo sitikudziwakuti titani😢
Chakwela ndi mbutuma sakuziwa chomwe akufuna
chakwera is evil president ndipo aMalawi taziwona lero dziko lathu lasanduka ngati Zimbabwe
A Malawi ndife opusa kwambiri. Kumangodandaula osachita kanthu. Tikanakhala maiko ena boma Ili tikanachotsa kalekale
Mbuziiiii Yachabe chabe Gule Wankulu masanziiiiiiiiii Enieni Bwantasaaaa,,,,,Opanda Nzelu Ena mudzimva zikuyamikila kuti Chakwela wabwino chonsecho akukhaula
Koma chakwera 😢😢😢😢😢
Kkkk mumakwana bro
Lazaro alibe maso mphenya oyendetsera dziko analowa m'boma kuti alemere.
Chakwera ndi chitsiru mbuzi yachabechabe😂😂😂😂😂😂😂😂
kodi ku Malawi kuno asilikali alipo 😂😂😂😂zikudabwitsa angozazana ana bas
Asilikali aku malawi alanda makala munsewu basi 😢
Iam also surprised, our soldiers are MCP members.
Chithyola what u think ur if u say people from malawi is happy
Malawi akufunika mapemphero apadera
Koma inuyo big man mumanena zowona zokhazokha munanenanso kuti kutsogoloku adzagwetsanso lero sizii😢
Amalawi tione dzina uja ndameneyo 😂😂😂😂😅zofuna izii ndithu
Kodi bwanji chakwelayo osamuchotsa bwanji Komatu Malawi alipamoto
Asilikali ali ziii ngati sakuona
Chakwera makhulupete apresident muthu oipa tima ngati kuseli kwaphika
I don't care if MCP wins infact I want them to win. Ndipa mene amalawi tizagwire ntchito kukonza nyasi zosezi believe me si ziza tengela kuti ndiwe wakuti. Example mwaona mavenda mmene zina yendera
🙏🙏🙏 brother zowawa bwanji
Awa ndi mavuto zed
Dzitsiru dzachabechabe kod Malawi tangokhara chete ? Chithamangitseni chichakweracho ndi chichitchoracho
Wagwetselanji kwacha chakwela nanga ndalama umapeleka kwanu zija umatibela misonkho yathu. Iwetu mulungu akuone ukutizunza. Dziko waliononga anzako samkapanga izi
Eshh ationesa zilango uyu
Zawavuta awo achotsen zonama zatopetsa awonongazinthu
Kodi kumkuyu mmene anapha Allan witika khani ili patipo bwanji sakumangidwa munthu okupha akungoyenda ati nduna imeneyo haaa malawi
Chichoseni inu ichi inu 😢
Mmmm koma Malawi mavuto alipo ndithu
Kwacha yomwe akuyigwetsayo yimugwetsatu pompano kkkkk
Tikamapanga zinthu chifukwa chakupsa mtima malawi sazatheka ...asogoleri athuwa timawasakha titapsa mtima tiyeni tivote mwanzeru osati tipsenso mtima plz
Koma pa Malawi mavuto satichoka
Chathyola plus chakwera agulitsa malawi wathu ndithu
Nthawi ya Bingu mafuta atasowa kunali ma demo omwe ena analuza miyoyo chofera chake sowe. Pano tikuona mavuto enieni osati sewero koma kuli zeeeeee ma CSOs onse akupindura ndi Boma anthu uku akunya ndi mavuto anyoooo
Keep pushing bro...
Chilungamo chake ndichakuti chakwera ndi MCP yakeyo akuchoka 2025 basi adya zomwezi. Ndipo akutichedwetsa.
kodi akulu amenewa akufuna chani, kuzidwa athu ayesesa koma eeee, it is a terrifing thing to fall into the hands of the living god' chifukwa kuluyi zinthu zimuvuta mizimu yakwiya kasa anayimba kale.
Ndingofunsako anzathu akumangochi za nsewu wa mangochi makanjira zija zilipati????
Kungot amarawi nzeruso muribe inu munkawona ngat kundareko azikapangaso zaubusa rerotu ndi zimenezo man of god kkkkkkkk muwona kt mupanga bwanji ife pheee pa cap town km chisoni chokha tirinacho pot kumeneko ndikwathu
Ngakhareso kuno ku south Africa alipose pose llovo suga galu uwu ndithakat ndithu
I think ndibwino dziko lathu lidzayendetsedweko ndi muthu osaphuzira koma odziwa economy aaaaa malawi akutikhauritsa
Kodi zingakhale zomveka ndalama yikugwa mphamvu basi chimanga chitsike mtengo inu a Malawi dziko mkupita nalo kuti? Koma kumbukilani mtaya makoko ,Ayii mwanyanya ,Is this Desensitization system of Gvt?
Koma zikhale ngoma usiwa unagwira kuposa munthu wakumudzi mcp yakusuka ndikona umaabera marefgs katundu kt udzioneka ngati ndiwe munthu utsogoleri opanda nzeru president ndi nduna onse asatanic anthu osava chisoni ndi mmene amalawi akuvutikira tamuoneni zikhale majekete acewo kuno kuthyolo thekerani
😢😢😢😢😢amalawi tili mavuto osasimbika 😢😢
Kulila ckuzatithela qmalaw tinadzala mbeu yachitedze😢
Chisilu cha munthu kulibe m'busa wopha anthu chochi munthu osaganiza ngati uyu,poti iye akukhutha mimba pira pira amalawi afkufa ndi njala satana achite naye😂
Sindinawonepo president wozunza anthu ngati uyu.
Chakwera ndi galu tsakudziwa chimwe akuchita ndipo avemeledze kutula pasi udido
Useless government 😢😮
Nyani ndi nyani bas 😢😢😢
Km man inuyo ambuye azikusogoleran mumatimvesa kukoma mulungu akuze malire amoyo wanu
Koma malawi nde basi Anathadi😊😂
iwowo kumpandoko zikuyenda coZ akudya misonkho ya amalawi koma think of poor malawianz imagine mwana kuba chimanga coz of njala stupit leadership
Try and error. Ine Ndinayamba kukhulupirira nkhani zanu Bwana kuchokera tsiku Limene Nkhondo ya Russia ndi Ukraine ina coz mnali mutanena before Nkhondo kuyambika so now ndimakhulupirira kalikonse komwe ndimakaona kwa channel yanu
Pajatu akumati akukoza malawi kuti zithu ziziyenda bwino ndiye eeee kaya
Where we can go? This is our home
Koma Inu akamatero akutanthauza chaniii???
We love you boss
Uyu ndi president wamamiana mutu paribe Chimene akusiwa abusa zamaganiza Kuti angakaponde kunja
Ndipo live
Mwana wanjoka chakwera akuona ngati ife ana nthawi yake yasara pangono sure chifukwa midzimu yaathu ambiri ikumudandaura
Palibe chachilendo apa mmesa tinafika ku bagamoyo zambiri zowawa sizinati
Boma samayendetsa ngt tchalitchi