Tili ndi a malawi womwe akuvutika chifukwa cha umphawi ku Malawi ena akugona ndi njala ena akufa ndi njala wina ndikumatenga 90 million akuti kukumbikira galu wachabechabe kamuzu chigawenga chomwe chidapha ndi kuzunza makolo athu.
Inshort , Tonse alliance has come to finish MALAWl, Corruption is now on every where , Corruption now is like culture & behavior of MCP. If MCP will continue to rules am sorry my fellow malawians , my brother's and sisters
We need people like you in our country. The people guided by love, care, humanity, ❤❤❤❤❤. May Allah bless you sir, and the people who are with you.
Wow!! I like you guys first kumva amalawi akuyakhula chonchi public tatopadi amalawi tikusekedwa kwambiri tikamakhala mayiko eni wakewa good job guys
Zikomo Inu abungwe la CDED mulungu akuyendereni abwezedi. Anthu akufa ndi njala.awa utsogoleriu angogwelamo let's do it more fire
Yeah! Apa ndiye anyera mapiko a Chakwera, saulukanso. Abweze ndalama za boma basi, asah!
😂😂😂😂
Kkk I like the topic Malawians nowadays they are clever than before keep it up guys job well done
This is type of people we need in our country
Much respect @ cded!
Dese people works in iniquity, it's why dem nuh care about citizens
Rastafari bless, Selassie I de first🤝
Thank u Mr Namiwa with ur true speaking
Zilikotu kkkkkk
Amabungwe tithandizen chisankho chichitike ....may ..Abale osati september
Chakwera ndiwamisala ngati Habakuku sinyangwe😂 , analonjeza kuti atakanika utsogoleri mu zaka ziwili he will resign pano chikukakamila
That's great message
Ndiye kuchepa nzelu kumeneko, tsiku lokumbukira kamuzu nkuikapo mau onyoza Mutharika, palibepo nzelu apa.
Koma ndie anamukuwizadi mpakana kunali kuimba kuti achoke Chakwera achoke❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ iye alipompotu😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
@@Pangolinimw 😃😃😃😃😃😃😃😃Kunakomeramo mmmmmm ndipo akhaula zedi sanati campaign ikangotsegulidwa kukhala kumugenda koopsa ndiminyala sure 😃😃
Kkkķkk good message ❤
The DC must be a member of CDEDI also once is there,is going to be a fire🔥🔥🔥🔥🔥
Abwezedi ameneo chakwera ndi wawusilu ka amangopanga zinthu za uchisilu ngat kuti kamuzuyo pali cimene Malawi 🇲🇼 muno anapangapo
Uthenga wabwino ndithu ....koma angabwenze or kuyankhapo ???? Chifukwa kudzudzula Anthunu mukudzudzula but nothing changes
Power the massage ❤
Powerful massage Namiwa!
Message the power❤❤
Tidziwa bwanj kut ndalama zabwenzedwa??? Nanga ngat sizibwemzedwa or kuyankhapo kanthu whats the next to benefit us
Tili ndi a malawi womwe akuvutika chifukwa cha umphawi ku Malawi ena akugona ndi njala ena akufa ndi njala wina ndikumatenga 90 million akuti kukumbikira galu wachabechabe kamuzu chigawenga chomwe chidapha ndi kuzunza makolo athu.
Chilungamo abweze sizikutikhudza
More 🔥🔥🔥 we need people like you anthu akuvutika ndi njara ku mwalira kumene pomwe ndarama zikungowonongeka
Umakwana Mr Namiwa
Inshort , Tonse alliance has come to finish MALAWl,
Corruption is now on every where ,
Corruption now is like culture & behavior of MCP.
If MCP will continue to rules am sorry my fellow malawians , my brother's and sisters
Tikuyamikeni inu abungwe ndipo mupitilize
True message ❤❤❤❤
Kuyakhula kwabwino kwambiri ❤
Chakwerayi akulakwisa kwambiri sakuganizira zika zake chifukwa chani?
Asiye kupisila kumene mwayitha makotsana 🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Good message
Abweze bas
Good message Thanks
Inu mumayimiladi amalawi go ahead
Komanso inuyo bola musalandle chibanzi abale
Ndipo sindinaone muthu okuba ngati chakwera
Tidziwa bwanji kuti ndramayo yabwezedwa
Mau amphamvu ndi dangalira brother Namiwa Zikomo kwambiri polimba mtima ndikudzipeleka kwaulere potiimilira ife amalawi. Pali Bon Kalindo, Namiwa ndi journalist wa Bakili Muluzi TV ndi anthu ofunika kwambiri mdziko muno Mulungu adalitse anthu amenewa. Ndipo amalawi ambiri tikanakhala ngati anthu atatu amenewa malawi wathu atachoka mmisinga ya umphawi.
Awo nde mau zoona zake,justice system ikukumeladi anthu andalama,mau mau
Panyapawo tilibe mtsogoleri
Uyu ndi galu Lazarus Panyapako
Abungwe musafoke , abweze ndalama .
Ndakufila cded please mupitilise kuti yankhulali
Chakwera NDI fiti yopanda chisoni, Ambuye akukatheni ndithu iwe chilima zeze
Mmmmh kunja kuno kuli Mulungu ,tiyakhulireni abale tikupsa ife ndi moto
Abweze chakwera ndalama zoonad big
Mabungwe ndi ofuniklad enawa monga CIDEDI.Chekis and balansi nzofunikadi
Good jobs guys
Awatu abwezadi ofunika kuwakakamira akanganya amenewa koma zomwe anangulitsa sung zo tiziwone atiwonjeza kwabili
power the message 💪
That's true, they must give it back, all the way from Johannesburg.
Thanks CED keep it
Pongofunika Ku muchotsa ndi mademo chakwerayo osamangoyanganila ndalama zikubedwa chonchi waoononga dziko olo osamulipila malipiro Ake Kuti aone kuti
90 million yachepatu check
Well done acdedi kuyishosha tiyeni tizuke tonse
Amangidwe ka aaaa chitsilu chamunthu
Boma Lili ndi chipha mtima ili iiiihhhh aliyese mtima uli ziiii no action taken koma tikuziwa ndithu kuti chuma sichikuyenda bwino.
Banja lawo likusqngalala chifukwa chandalama imeneyo wakuba
Eya mbuzi imeneyo ibweze mamuna osatha kugula nsalu kuchuluka nzelu mbuzi ya kukasiya
More fire guy's 👍
Auzeni amvetse bola musalandire mabanzi poti alipotu mabanziwo
Chilungamo kaa . Abweze ameneyo
Ambweze zimbanvazi
Osamusekelela abweze kwakwera
Ndakunyadirani kobasi abungwe, mupitilize ku imilira a malawi ambuye akupasani nzeru zochuluka
Achakwera nndichabosadi ndipo ndarama abwese
Aamenewa ndalama abweze kumeneku ndikupha Amalawi
Much appreciate
Koma malawi wabvunda . Tsiku lina tidzamenyana tokha tokha ayamba kumenyana ndi Andale okha okha
Fire 🔥 mabomba !!!!!!!💪🔥
Mwasowa chonena
Abweze iyah...
Koma ladzalo iii mbusa uyu ndi oononga osakadza okupha akapume ameneyu mmutu mwake mulibe nzeru mbiri yadziko lamalawi mulibe mtsogoleri opanda nzeru ngati ladzaro cakwera
No doubt Abalalika.
Tiyeni nayoni Nyauyi popha nyani sayang'ana nkhope ndie kulili nyau, tiyeni nayoni yatidzudza koopsa tatopa nayo ifee
Chakwera atiyakhe bas ndanena ndanena bas sindikubweza maganizo
Abweze basi .Mbava chakwera ndichilima
Msonkhano umeneuja kunayenela kupita aliyense ngakhale osusa boma
Abweze ndandama zamalawi tikagulile manthwala
Abwezedi ndalamaso mawa mukacha chakwera akusolowela
NRB silibwino anthu akumalembetsa 200 patsiku sakutithandza akachali
Zuzuluni pofunika kudzudzula chilungamo chiyende ngati madzi tiphudzile
Mmmmm azathuwa awonjeza
Abweze ndigalu kwambili nyani😢😢😢
Malawi will never be the same . Politicians wake up . Don't take us for granted .
Mumutenge bon kalindo muzithandizana naye there for it will be fire
Anthuwotu abweze amalawife tikuvutika Koma bambochakwera simunthuothandiza komawokupha
Amafuna apikisane ndi APM njamba rally
Abweze basi sitifuna kutinamiza ife
Tikukuvani bwino Kuno ku mosco amenewa bweze
Abweze chisiru cha president
Utsogoleli wausilu uwu wamamina mmutu
Akudya ndalama zathu chifukwa chakuti sakuopa aliyense
😂 good move and don't show them mercy
😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂Popha nyani sayang'ana nkhope ndie what more Nyau😂😂😂
bring it on lads!
Udzagotha bwanji mwambou
Mau kma awa🙏🙏🙏🙏
Koma munalikuti poturuka lero? 👏👏 napokhapa mwakambila leromu ndititsegula mmaso a malawi mmmmmh ambuye akudalitseni ndikanakonda mma radio athu atamamverako izi juti mwina amalawi angasinthe maganizo posadzachivotelanso chilazalochi ndipo ndatopa nkumuona ine m'busa, mbava ameneyu
NO PAIN NO GAIN ABWEZE BAS
President chakwera akuwonga kwambiri zinthu mumalawi.
Ndichisiru kwambiri