Pana lero sikutha kuvesa zoti a SKC Ali manda,,,,, kaganizira kwambiri simene misozi ikuturukira 😭😭😭 anthu opanda kuganizira za mavuto BOMA la zigawenga,,, ndipo a Malawi dziko iliri tikapanda kutengapo mbari mozipereka ngati cheteee takhala apapayi tipwetekeka,,,, OSAWOPA, OSAFOKA, OSATOPA ✊✊✊ we need to stand up for our malw
Chirima was so responsible for his death,how could he make an alliance with the hard cole criminals who killed Muwalo who was Ntcheu ,Chirima was not a kid that time.😂😂😂
NYC song 🎤🎺🎸🎻🎹🎼💯 koma mwaiwalq jumani. Kamudzu
Good music
The song is just so beautiful and very innocent questions.
Nyimbo yabwino kwambiri akudalitseni mwaimba nyimbo iyi ndikudziwa kuti ndinu olimba mtima
Good voice
Pana lero sikutha kuvesa zoti a SKC Ali manda,,,,, kaganizira kwambiri simene misozi ikuturukira 😭😭😭 anthu opanda kuganizira za mavuto BOMA la zigawenga,,, ndipo a Malawi dziko iliri tikapanda kutengapo mbari mozipereka ngati cheteee takhala apapayi tipwetekeka,,,, OSAWOPA, OSAFOKA, OSATOPA ✊✊✊ we need to stand up for our malw
What a beautiful tribute song 💔🇲🇼😭😭😭
Nice message😢😢😢😢😢😢 Rest in peace SKC and 8 others
Mtima wanji osakhululuka 😭😭😭 Ambuye onetsani ukali wanu pa m'busa wakuphayu💔💔💔💔😭😭😭
Ndani wayimba nyimboyi dzina please
Nyimbo eish. Chakwera he will never have a peace in his life until forever
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥iyinde nyimbodi iyi 😅😅😅😅😅😅😅😅 MCP itionesa zoipakobas
😭😭😭😭😭 zoonadiitu aise bomali ndi lamanyi chinyimbo madala
😭😭😭😭😭😭😭😭 we have missed you SKC🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Nice tune. God bless
Powerful message 🙌
Nice song keep it up please ❤
Komatu zomwe apangazi
Mmm ai sizoona ai pofunikati
Choonadi chioneke we a tiered
Azibale athu kungophedwa Ngati
Agalu kapena anali okuba kapena
Ai pakufunika zioneke bwino,bcz anthuwa achuluka , anthuwo afela chilima ,ndiyeno afotokoze bwino
Kuti anthuwo analakwa chani bcz
Tonse ndi Anthu chigamulo sichoona nkhope ai naye aone zokhoma
Ndipo inu Ambuye vumbulutsani Koma posachedwa paaa Mizimu yawo ikapume mumtendere eeeee abale inu nanga ngati tikumva kuwawa ife anthu apambali kuli bwanji akubanja eishiiiiiiii koma abale inu ine 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Rlp Skc my president 😢😢 chakwera izi unangowona utapanga. Koma mizimu ya anthu 9 awa ikusowesa tendele wa mu tima paka uzalowa manda
Nice song brother
It takes courage to sing this song...may we find closure to our loved ones..tinaluza
Yomweyo chikangawa !!!!!!
More 🔥🔥 Chikangawa Party isowe mtendere nyimbo ndiye zikutulukatu more 🔥🔥 kumeneko
Nice song ❤
Nice message 🙏😭😭😭😭
Wow .... Nice message
More fire
💔💔Malawi 😭😭
Chirima was so responsible for his death,how could he make an alliance with the hard cole criminals who killed Muwalo who was Ntcheu ,Chirima was not a kid that time.😂😂😂
Mutumizire Chakwerayo nyimbo imeneyo amvere
Ngozi yochitikira kwina anthu kumawalozera kwina,ayi zikomo
Chilima ,kasambala ,eish mcp chipani chamagazi 😢
Powerful message
Kasambala zimandiwawa kumupha lowyer OSALAKWA.
Ndipo inuyo
😭😭😭😭😭
Mulungu wathu wakumwamba mutimenyere nkhondo mu mphamvu yanu ndipo inu ndinu mtsogoleri wathu pokululuka miximu yonse yomwe inachitidwa chipongwe chopedwa munjira zoipa chonchi ndipo tithandixeni kuti boma lakupha lilipoli libwerere komwe linachokera
Nice song
More 🔥🔥🔥
Osaopa SKC
MCP must not false things. If was Chakwera, I would have not have gone for a convention. Let others complete.
Kuyimba kwabwino❤
❤
Gud one ❤❤❤
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Boma la chakwera likanakhala lachilungamo, sakanatenga nthawi yonseyija kusaka ndege komaso ndege kusowa mmawa 10 kukayamba kusaka around 5
Ayi zikomo.ndpo ambuye onesani ukulu wanu pa athuwa.ndpo muwabwezere ifa yowawa kuposa apo zowawa kwambiri
Ai zikomo
❤❤❤❤
Mcp ndi banja la kain
Chakwela chikangawa akuziwa zonse.koma atha basi
😂
👌 👏 wowh
More fire chakwera chigawenga😢😢😢😢
Nyimbo yabhoo pakambeni ibwele imeneyoooo woyeeeeeee
Very perfect song
Nyimbo iyi koma😅😅
🔥🔥🔥
🔥 🔥 🔥
Tose tikulira nanu pamozi
💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔😭😭😭😭😭🙌🙌😭😭😭😭😭rest well Mr president SKC and 8 others
Nice nyimbo 😢😢😢
Rest in peace chilima
💔💔💔💔🔥🔥🔥
Chakwera ndichigawenga basi.
😭😭😭😭😭😭
💔💔💔💔
Anthu oyipa awa sazapeza mtendere the rest of there lives
😧😧😧😧
Pa reapt bas 💔💔💔💔💔💔💔💔
Only God knows
Nice song 😢
😭😭😭😭😭😭😭😭
Titled ndi Chani nyimboyi please
CHIKANGAWA
💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💔💜💔💔💔💔💔💔
Koma😭😭😭😭😭
Haaaaaas😂😂😂
Nice song
❤❤❤❤❤❤❤❤❤