I respect you Mr Bon K The DC bcoz you speak nothing but the plain truth..and you don't fear anyone but you fear God only....May the good Lord protect you at all cost
Bravo the D.C.. .. you have represented the Malawi people by warning the Germanys who dubiously want to buy our island from these unfaithful leaders of today, Chakwera
you guys dont know anything about lease... coz the same agreement that happened between Golden peacock and Malawi Government, but youre being fooled. politicians are just the same
Koma bakili muluzi wake ndi yemwe uja amanena kuti MCP ndi ya magazi manja uja kapena ndi wina siuja amatiuza kuti MCP ndi chipani cha kupha lero chasanduka chabwino amulakwisa mwana
Dzuka MALAWI dzuka! !!!.....Likoma island will fully belong to Germany company. Likoma island will become an iconic international tourism center where a marvelous CASINO will be established. But the agreement is not clear on how Malawi will benefit from the CASINO. And also it's unknown how much this island have costed.
Here in south africa there's a place where they have their own president and currency so it will bethe same with malawi 1day Germany coming back buying our island?? Ooh no malawi ukupita kuti??
Kkkkkk kodi Bon lilindo yo ndi openga mutu wake ukuyenda bwino bwino koma kodi iyeyo Mesa ngwa DPP brother's party kodi ngomenyala ufulu kapena kumphwanya ndikuwophyeza ufulu wa Malawi kodi aku wona ngati a Malawi ndi ana ake or what
Ndipo sizingatheke UDF ndi MCP kupanga Alliance.this it's my real party .. Shanil Zimbiri anaphedwa ndi Chipan cha MCP chomwechi .and Atcheya aja Ali ndinkwiyo kwambiri pa imfa ya Shanil Zimbiri Muluzi .. koma kuitanidwa Kwa akuru akuru ena a MCP ku UDF convention sizikuthanthaudza kuti we are together with MCP ..sikuti ndimadana ndi The DC ayi this guy it's my poor president
Amene akufuna old man brothers party be they in a side of opposition you have a light, UDF, afford or MCP you have a light to decide but not kuwapusisa Malawi that is nonsense. Kanundu umamenya iwe umamngula kuti?
UDF kuitana Mcp ndiye kuti mwana wakumbukira kholo lake,ngati UDF kulibe lero nchifukwa cha kusayamika kwa Dpp so if I was Atupele I could have form alliance with Mcp
Pita nayo uko nkhalamba yakoyo zomwe ya Chita udf ndi maganizo abwino ndiye democracy ukufuna kuti paralytic president Peter to rule never never. Ndipo English yako Kalindo shame on you.
Atupere muluzi sadziwa chimene amafuna, and he's so weak in politics, he will never rule Malawi as long as he keeps combining he's party with other parties!!!
Misozi ya Kalindo simdikuiona wina akut Kalimdo akulira 😂 chilungam chowawadi et Kalindo alibe zonyasa ndye aulura bwanji zonyasa zake km.kusadziwa mkufa mkomwe Bon Kalindo timzamkumbukira siku lina zmwe akunenazi just wait and see
I respect you Mr Bon K The DC bcoz you speak nothing but the plain truth..and you don't fear anyone but you fear God only....May the good Lord protect you at all cost
Onse odana ndchilungamo kugahena . My vote DC go ahead
ndipo bakili mMULUZI was agood leader
Zinakanika kale Mcp ndi udf inamulephera Bingu kumuchotsa
You're only one you know how to fight for poor people in 🇲🇼 we proud of you always ❤keep it up
don't believe in these politicians, if you believe them you are the one to be fooled.
Wanya nayo invitation ya MCP Ku UDF. Ukunamizira a Malawi kuti akutuma mabodza basi. Peter wakoyo Anya nonse. UDF MCP boma❤❤❤❤❤❤
Zowona,vekhawula va DPP!!!
Zisiru agaru! Musamamvere winiko machendeanu tiphana chaka chino ndipo muziwanso agaru oipa asatana nyini za amanu.
Mcp ndi chipani Cha mphavu ndipo chizawina 2025 chikuptiliza kulamulira 🎉🎉🎉🎉
Machende anu bro
@@Dysonkhofimbole yako nawe, panyapako galu iwe ndatitu mapwala ako
Zimenezo zoganiza zako Kalindo, iwe siwandale ayi. Udzakhumudwa, MCP itawinanso. Leave Atupele Muluzi alone.
Pantumbo pako iwe ukuti chani uzakhumudwa ndiwe ndi agogo ako aja panyini pamakoso wamva eti
mcp kuwina kudzakhala nkhondo wait n see
Mbambande mr kalindo mumatiimilila 🎉🎉🎉🎉
These honorable 8 DPP MPs, Imran Mtenje are wise people.
Go ahead men and women of God.
Bravo the D.C.. .. you have represented the Malawi people by warning the Germanys who dubiously want to buy our island from these unfaithful leaders of today, Chakwera
you guys dont know anything about lease... coz the same agreement that happened between Golden peacock and Malawi Government, but youre being fooled. politicians are just the same
Boooooon kalindo president ❤
Mmmmmmm sanje basi, mwagwa nayo A Bin Kalindo waboza uyu
Always with you the DC , keep fighting for Malawians , you're the
Tsono inu born kalindo zimene mukulankhulazi mupindulapo chani? Munthu pano sangakwiye ndi uthenga wamunthu wam'sala; chakwera my vote
That is true mr president bon kalindo UDF zachamba ayi please 🙏 😀 😢 👏 UDF don't do it pls 🙏 😢 😞 😫 😑
100 percent speech, all the way from Mulanje Lujeri
Mr DC thank you lero ndiye mwakamba mfundo yamphamvu,chonde inu atsgoleri a udf ugwiritseni bwino ntchito uthengawu
Atupele ndi kape aaaaaaa dpp boma ❤❤
Bon this is geniun truth,auze amvetsetse
Boooon kalindo❤❤
Born kalindo ndiwe mutu wako sugwira mesa unali iwe wemwe ndi aziazko achina Brian Banda ndi ena munkachemerela ndikuwathandizira Kuti alowe muboma nde lero chifukwa chakuti akumanani kaudindo lero mukumanena Kuti MCP ndiyankhanza Kodi nkhanzazo ayamba lero poti akumanani kaudindo ? Usawapange choncho amalawi musamawatenge ngati ndizitsiru wamva ? Dairy basi amalawi andituma amalawi Ake atiwo angakondwe ndizausiru zakozo ,,, usamasocheresa anthu wamva,, nkhani ya alliance ndi ufulu komanso choice cha chipani kusankha opanganawo alliance osati uziwapangira zochita wamva Kodi iweyo ukuona Kuti ungakhale ndinzeru kuposera aliyense zopusa basi
Thom chihana and Kamulepo kaluwa fought for democracy in malawi achina bakili joined kumapeto ndikutenga boma
Koma bakili muluzi wake ndi yemwe uja amanena kuti MCP ndi ya magazi manja uja kapena ndi wina siuja amatiuza kuti MCP ndi chipani cha kupha lero chasanduka chabwino amulakwisa mwana
Pa English ponkhapo panditenga kuti aziva anthu woipao the DC bon kalindo we love you so much our president ❤❤❤❤🎉🎉🎉
Amene wayambitsa zoitana mcp ku convention ya udf achotsedwe mchipani
Kaya apanga gwilizano otani ife nga nga nga kwa APM ndipo sitikugwedezeka pambuyo pake nyoooooooooomiiiiiiii mwana oooooooosa kwambili love u brother
yha azawayitane asatana amenewo
Asiyeni apange mgwirizano waowo ,kuti UDF itheretu tsopano
UTM my vote
Zamphamvu mr DC. Osaopa, osafooka Osatopa. NG'alulasation
Ngat zili choncho UDF woyeee MCP woyeee very very powerful
Bond kalindoo eeeshii really ur the king of Malawian and fear no one 🎉🎉 dad
Proud of you the DC Bon A.K.A Akawiniko
Dzuka MALAWI dzuka! !!!.....Likoma island will fully belong to Germany company. Likoma island will become an iconic international tourism center where a marvelous CASINO will be established. But the agreement is not clear on how Malawi will benefit from the CASINO. And also it's unknown how much this island have costed.
Here in south africa there's a place where they have their own president and currency so it will bethe same with malawi 1day Germany coming back buying our island?? Ooh no malawi ukupita kuti??
A Malawi anzanga TISALOLE kuti agulitse LIKOMA ILAND please please please its our worth ,komanso inu A UDF kulodzedwa ANjomba Atupere ungwi nambo Chichi chele .
Bwana zimene mwauza bwana atupele mwawacenjeza mbali yanu ifeso tikut asanyodzele zomwe mwawauzazo❤
zandalezi ndi ziafiti zokhazokha and a UDF ndimakapenso angaitane nyasi za mcp ndithu asaaaaaa koma a udf ganizani kawiri
M'tsogoleli wa chipani Cha udf adali a Chair osati adyela alelowa
Continue fighting good fight we are standing together with you
Kumalawi kulibeso ngati the DC amanena chilungamo koma amalawi ife tinalozedwa kwambili Kaya ku pepela Kaya
Your the best Mr Bon Kalindo mumatiimilila
Kkkkkk kodi Bon lilindo yo ndi openga mutu wake ukuyenda bwino bwino koma kodi iyeyo Mesa ngwa DPP brother's party kodi ngomenyala ufulu kapena kumphwanya ndikuwophyeza ufulu wa Malawi kodi aku wona ngati a Malawi ndi ana ake or what
Ndipo sizingatheke UDF ndi MCP kupanga Alliance.this it's my real party .. Shanil Zimbiri anaphedwa ndi Chipan cha MCP chomwechi .and Atcheya aja Ali ndinkwiyo kwambiri pa imfa ya Shanil Zimbiri Muluzi .. koma kuitanidwa Kwa akuru akuru ena a MCP ku UDF convention sizikuthanthaudza kuti we are together with MCP ..sikuti ndimadana ndi The DC ayi this guy it's my poor president
Waiwala zoti mcp inapangapo alliance ndi Mcp uli ku Malawi konkuno iwe??
@@mikesandali8425 ndichifukwa chani Atcheya anali oyambilira kupereka mafuno abwino Kwa malemu Bingu before kumalidza kuwerenga ma vote .Atcheya amazindikira sanga kuti MCP ikanawina akanazuzidwa kwambiri .and legas yawo ikanaonongeka chifukwa anaranda mphavu ku MCP nde abwezereseso mphavu zomwezo ku MCP sizikanachita ubwino ... And siku lorumbikitsa Bingu Atcheya anapasidwa udindo orandira alendo akunja chosecho panali udani waukuru pakati pa Bingu ndi Atcheya.Panali nkhondo yapasi apa
Mr DC we love you so much
Mdani wa UDF ndichipani cha DPP chinatibela mavoti titamuwinisa bingu wayiwala wausili iwe yeti kalindo
That's true let us fight for Likoma our beautful island 🏝
Good men boon kalindo
Ngati izi zilizoona UDF ikutha ndithu 😂😂😂
Munaithesa kale ndi Mesa munaibela boma udf
UDF ndi chipani chomwe amakonda makolo anga kma chandikhumudwisa eeshi panopa ine nganganga ndi dpp 🔥💪
Kaka koma anthu amaselo mutpusitsa bon kalindo dpp,mcp,udf, palibe angakhale wabwino kwa aliyese
That's true speech br
Zimene inapanga DPP ndibingu ine ngati wa UDF sindimaiwala uziuza alomwe azako bon kalindo wanva ndiwe galu kwambili
Akangotero mutu wao sugwira ife nde tili nganga nd Apm 💙💙more fire bon kalindo kulakhula chilungamo dzuwa likuswa ntengo 👏👏👏
APM my vote 💙💙💙 🌽 √
Muyimila dpp agalu inu, mukuona ngati sitikudziwa.
Uku ndikuyankhula kopusa chifukwa kalindo si wa udf nde palibe chifukwa chomalankhulira chipani cha udf and akulankhula ngati kuti palibe democracy mu mdziko muno. Munthu kapena chipani chimakhala ndi ufulu wopanga zomwe waganiza ndipo palibe chifukwa chomuletsa kupanga zomwe munthu waganiza ndipo ndiuchitsiru munthu kumamupangira maganizo pamoyo wake. Asiyeni a udf apange zomwe akufuna osati zomwe mukufuna. Funso langa nali ; kodi mose unayambira kulankhula muja unapindulapo chani??
Ingotengani makasu muzikalima chifukwa zandalezi zikuonetsa kuti simumazimvetsa maka pa ufulu wa munthu momwe umakhalira and mwalephera pamenepa Phiri
Amene akufuna old man brothers party be they in a side of opposition you have a light, UDF, afford or MCP you have a light to decide but not kuwapusisa Malawi that is nonsense. Kanundu umamenya iwe umamngula kuti?
The worst decision from atupele muluzi.
Udf usayelekeze kulowa chipani chamasatanic chonde takuuzani ife ngat mwalowa zanuzo
KOMA KODI KUMAKHALA KULOZEDWAAAAAAA KAPENA CHIYANI ? ANTHU AMENE MUKUTSUTSANA NDI KALIMDO KUMACHEMERERA MCP KUPEPETULIDWAAAAAAA CHANI MITU YANU SIYENDAYI NDIPO MULI NDI TSOKA ATUPERE USALOZEDWE KUKALOWA KUNG'ONA UDZAFA NGATI MALEMU CHILIMA
UDF kuitana Mcp ndiye kuti mwana wakumbukira kholo lake,ngati UDF kulibe lero nchifukwa cha kusayamika kwa Dpp so if I was Atupele I could have form alliance with Mcp
Sogolo la udf analiononga ndi alomwe osayamika kuzela kwa bingu wamutharika,,, kuno kum'mwela ngati kunagawikana anagawa ndi bingu basi
Never ever dpp and udf go into collisions with mcp ndipo chikangawa afune asafune akuchoka 2025 dpp,udf, utm and aford will unite
Ngati UDF ikupanga choncho ndiye yangoonetseratu kuti siyikuganizira a Malawi konse......Nanga Bakili Muluzi akuti bwanji pa nkhaniyi ngati Chair komanso president opuma?....
Bon kalindo osaopaaaaa moto kuti buuuu ❤❤❤ to Malawi
Komaso kd kalindo ungolira ndiuphawi ubwere ndizakupase thumba lasoyo ugalubwako
Kalindo akusowa polowera ndipo ufune usafune mcp ndi udf komaso pdp zikugwilizana
Kod paj tili ndi chipaniso pdp😅 muziko lino eti eeeeee
Koma UDF mmmmm mwanganiza bwanji sitikufuna mupange ngwirizano ndi chipani chakuphachi a chair bwerani mukhonze chipani chanu
Pita nayo uko nkhalamba yakoyo zomwe ya Chita udf ndi maganizo abwino ndiye democracy ukufuna kuti paralytic president Peter to rule never never. Ndipo English yako Kalindo shame on you.
Atcheya ndi JZU anali pamgwirizano mu 2009 elections osanamapo apa. Vomelani kuti MCP is very strategic & clearly outsmarting the opposition 😅😅
Yes strategic pokupha anthu you are very much true but satisfied pachilungamo ayi pokupha Ali number 1
Ndiwe chitsilu bo. Kalindo
Ngati zili Zowona UDF nde mwatha basi, anthu akutulukani ndipo Asilam ambiri akutulukani
Kalindo mumakwana populumutsa a Malawi yose bho mapemphero alipo achitetezo chanu daily ambuye azikutetezani Moyo wautali akalindo
Kkkkkkkkk koma mkulu uyu mutu wake udasokonezekadi, kuyesetsatu kudetserera ukhaula sunati. Akuti amalawi amutuma m'malo monena kuti wadzituma, Osamakhala ndichimoyo chonyansa akulu.
2009 MCM inagwilizana ndi UDF koma sanawine chisankho
Zoonazomwemukunenazo amarawi sakondadzikorawo amakondandarama siyeni lnupanganichachanucho kuwauza.osareka avakusongoro osareka popeza chisiru chimatikuribemurungu koma pitan
UDF ndie itha pamenepo ka anthu aisika mene zinthu zikuvutila pa ground akapange gwilizano ndi mcp anthu awasika ngati akunyengelela masiku ano ifeo sitikufuna mcp ndie ayesele kupita ku mcp akhawula a udf awona azipanga za fodyazawozo mmmmm
UDF apa pokha nde musokoneza zinthu...please muunikilepo
UDF inatha akangomalizisa chipani cha UDF awonaso ayisika anthu ambili amene anasalawo wallah km atupele akufuna kuthesa chipani cha UDF apange zimenezo anthu sakuwelengaso kuti ndi ndani anthu mosabisa UDF ikutha pamenepo ikangoyelekeza basi
Kkkk chair sunudziwa eti waiwara kt analankhurapo bakiri atapanga mgwirizano ndi John mtembo adaati mundale mulibe mzako wamuyaya komaso mulibe mdaniwako wamuyaya,Kodi DPP ngati yudziva mphavu chofunira mgwirizano ndichani?akalindotu mukhumudwa
Udf izipita ino ndi nthaw ya dpp utm aford akasoneza mavot adpp muzawona meme izasesele dpp, umphawi wawavuta nanga atan udf izipita aford utm mway wanu
More fire Mr Born Kalindo
Olo a udf atapíta ku mcp ko dpp singaluze anthu adyera
Atupere muluzi sadziwa chimene amafuna, and he's so weak in politics, he will never rule Malawi as long as he keeps combining he's party with other parties!!!
Timakunyadilani auzeni Mr dccc always with you
Apm my vote
Wawoneka kuti Siiwe womenyera ufulu wa anthu koma omenyera ufulu wa DPP ndi a Malawi ake a ti amene akutuma
Boooooooon Kalindo ulemu wanu komwe mliko DC wanga kwabasi mumandinenera zoona pa moyo wanga
ngatiwakutuma ndigaluzakoyo akupendrkesa ifeachilomwe tikudana ndipani zachibanja ifetivotela boraachewawa. yooomweyo mcp motokuti buuuuuuuuuuuuuuu
Olira samutseka pakamwa mose.muja akalindo munayambira muja moti pali chomwe chimasitha....apulofeti ot asing'anga ndiwe galu
Aliyese wa MCP page ino pa nyini pa manu takapangeni ma page anu mbuxi inu nyini zanu
Iwe ndi mbuzi kwambiri,nchifukwa chiyani umapanga attack anthu mmalo momayankhula nfundo zothandiza dziko? Nthawi zonse kuyankhula zopusa zokhazokha, ife tikukhulupilire bwanji? Mmbuyomu umatukwana Chilima ndi Chakwera,Pano ndiye uliyanayo nayo mtsogoleri WA dziko ? Umoyo wako ndi otani? Galu kwambiri!!
A UDF mukufuna aslam azivutikabe ku palestrin
Misozi ya Kalindo simdikuiona wina akut Kalimdo akulira 😂 chilungam chowawadi et Kalindo alibe zonyasa ndye aulura bwanji zonyasa zake km.kusadziwa mkufa mkomwe Bon Kalindo timzamkumbukira siku lina zmwe akunenazi just wait and see
Atupere chonde usatelo usayesere kutelo UDF maso athu ali paiweyo
Ndilipambuyo paAPM
What is you're problem mr kalindo ,mudayamba kale kutisokoneza ife anthu ,inuyo ndi azanu aja akuti akufuna kukapepesa ,mmmmmmmm ndinuso adyera
Osaopa osatopa osafooka mumatiimilira💪💪💪
Muuze mchiyankhulo cha kwawo ambassador ameneyo 😂😂😂😂
Aboni kalindo munanenspo kuti mnakhala Inu bwezi sindingavomele kuti kuti andithesela mulandu bwezi ndindiauza kuti bola ukathelebe kukhoti kochifukwa chosava asaulosi anachivomela sizi anafapo
Kodi udf kulozedwaa chain?
UDF Inatha imapeza mavoti 200 Malawi nyonse