Amen pastor twibu tikukutsatilani mwachidwi, Ambuye azikuwonjezelani nzeru monga anapeleka kale, chifukwa si inuyo koma mphavu ya mulungu imene I kutilankhula. Nthawi ndi ndiyomweyi, ngakhale nthawi ya Nowa anthu ambiri amanyalanyaza, Pepa m,bale wanga. Mulungu watuma Nowa wathu wa lero. Amen pastor
Amen pastor twaibu,mumatilimbikisa siku ndi nthawi mulungu azikutetezelani komaso apitilize kutetezela ifeso tose tikuva uthengawu ndi kuwugwilisila ntchito in Jesus name Amen
Zoonadi ambiri tatayilira tiyamike Mulungu potikumbutsa zo fooka zathu kudzera mwa Brother Twaibu amen.
Ambuye atithangatire tataikadi. Tikonzeni Yehovah wathu kuti tiyendenso ndiiinu muuzimu ndi muchoonadi. Amen
Mr Twaibu ine kupanda inuyo moyowanga wa udzimu sumadziwika sogolo koma panopa chifukwa cha uthenga wanu wabwino moyo wanga ukudzindikila njila yoona mulungu kudzela mwa Yesu khrist adzikusogolelani pamodzi ndi ifenso ndipo tikakumane kumwamba tikachitile umboni
Nthawi yathadi amen mtumiki wa ambuye ambuye akudalisen
Amen pastor twibu tikukutsatilani mwachidwi, Ambuye azikuwonjezelani nzeru monga anapeleka kale, chifukwa si inuyo koma mphavu ya mulungu imene I kutilankhula. Nthawi ndi ndiyomweyi, ngakhale nthawi ya Nowa anthu ambiri amanyalanyaza, Pepa m,bale wanga. Mulungu watuma Nowa wathu wa lero. Amen pastor
Amen abusa ife timakusatirani mulungu akudaliseni
Zoonadi nthawi ndiye yatha
Tiyeni tisinthe abale
Amen mtumiki
Zikomo ndasundika my God bless you Amen
I want to go to heaven
Ambuye akudalisen atwaib komanso aonjezele chitetezo painu
Amen pastor twaibu,mumatilimbikisa siku ndi nthawi mulungu azikutetezelani komaso apitilize kutetezela ifeso tose tikuva uthengawu ndi kuwugwilisila ntchito in Jesus name Amen
Amen
Amen 🙏
Zoonadi nthawi yatha ambuye akubwera posachedwa
Mutipatseko link ya wasap group la a Twaibu ❤
chat.whatsapp.com/JCJdMsSiiRn3Tk4IXjyf8n
@@livingforchrist-malawi9476 thank you so much May God bless you 💖