Utumiki wa a Twaibu - Kutambasula za pemphero losweka mtima, lomwe Mulungu sadzalipepusa

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 5 ก.พ. 2025
  • Ku 1 Samuel 1 kuli nkhani ya Hannah yemwe anali ndi chosowa. Atapemphera mwachilendo, Hannah anayankhidwa ndi Mulungu ndipo anapeza chosowa chake. Kodi mukudziwa kuti malamulo ndi madongosolo a zipembedzo zathu akhoza kukhala chotilepheretsa kuti tipemphere mosweka mtima?
    Mverani kutambasula kwa a Twaiba, womwe akhala ku chipembedzo cha satana kwa zaka 17.

ความคิดเห็น • 19

  • @stewartkazembe1174
    @stewartkazembe1174 ปีที่แล้ว

    Amen Amen kupephera mene Mzimu oyera wakuuzira osati zamalamulo ampingo

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 ปีที่แล้ว

    Munasowatu a Mr twaibu

  • @markbanda7434
    @markbanda7434 ปีที่แล้ว

    Amen Mr twaibu pitilizani kutiphuzisa ndikutidyesa mawu abwino my GOD continue to bless you and your family amen!

  • @shadreckthandaza1059
    @shadreckthandaza1059 ปีที่แล้ว

    Uthenga uwu wachoonadi ukulalikidwadi pa dziko la pansi, amen amen

  • @shakiraameen8001
    @shakiraameen8001 9 หลายเดือนก่อน

    Amen man of living God

  • @JosephNdenga-jl2lm
    @JosephNdenga-jl2lm ปีที่แล้ว

    Amen and amen

  • @anneythomondo-tp9kn
    @anneythomondo-tp9kn ปีที่แล้ว

    Amen

  • @AaronMakoni-r2w
    @AaronMakoni-r2w ปีที่แล้ว

    God bless u Mr twaibu ahmidi hamid alli....mwapulumutsa anthu ambiri muthenga wanu

  • @PetroKachingwe-jf7dh
    @PetroKachingwe-jf7dh ปีที่แล้ว +1

    Amen that's powerful message
    Ndipangeni add mma group anu A Twaibu ine Petro Kachingwe Brantley Lunzu
    Koma pano ndili kuno ku South Africa Jbrk

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 ปีที่แล้ว

    Ameni mutumik

  • @FrancisYohane-t6o
    @FrancisYohane-t6o 4 หลายเดือนก่อน

    Mulungu akupase mabvumbunso ochuluka

  • @PiliranWazili
    @PiliranWazili หลายเดือนก่อน

    Ngt pali group ndpangen add plz

  • @angelinamulewa4100
    @angelinamulewa4100 ปีที่แล้ว

    Mau achoonadi awa

  • @AaronMakoni-r2w
    @AaronMakoni-r2w ปีที่แล้ว

    Ndipangen add ngat Pali whtsap group pls

  • @eusebioarmando
    @eusebioarmando 11 หลายเดือนก่อน

    Amen