KULINJI YA LERO MWAIONERA KALE? KODI MWAMVA? KOMA INU MWATI ZIKUCHITIADI IZIZI A MEC NDI A NRB?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 41

  • @allieadam3235
    @allieadam3235 วันที่ผ่านมา +3

    PK thanks mmatiyimirira, kkkk
    Funso ndilakuti mmesa atsekula okha,

  • @maxwellmajawa6091
    @maxwellmajawa6091 วันที่ผ่านมา +2

    Zoyakhura mogulidwazi mwayamba liti ??? PK tazitengani anthu ena awawa ndi otukwanitsa atenga za Mr Kasakula,ukati munali kuti nde chani ????

  • @MikeMbewe-m8t
    @MikeMbewe-m8t 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu onse amene ali ndi zoyenera kulembetsa koma sanathe kulembetsa apasidwe mai akalembetse. Projected number of expected number is about 11,000, 000 koma anthu less than 8 million anatha kulembetsa. MEC lorani aliyetse akhale ndi mwai olembetsa 😊

  • @veronicajana5225
    @veronicajana5225 วันที่ผ่านมา +1

    Anthu ambiri anabwerera chifukwa cha chidodo taking much time and wina athawira kuntchito. Komanso mpata ku zitchito umavuta and panopa chifukwa chani akupanga limite? Akuopa chani? It is our right to register and the mec people should take professionals

  • @EVERSONBANDA-j8h
    @EVERSONBANDA-j8h วันที่ผ่านมา

    Being a citizen of this country BAYANA ,for sure that people got upset because of Systematic , so ,the MEC should not put a limit ,Hon Njawala he is right to say that it should come for registration generally

  • @OmexMainala
    @OmexMainala วันที่ผ่านมา

    Aaaaa ok amenemwantenga leloyutu ndiye panjapenipeni tikukanika kuyankhula molakwika chifukwa chainu pk

  • @DanielAlinafeImedie
    @DanielAlinafeImedie วันที่ผ่านมา

    Bayana Chunga musaoneke kuphunzira kwambiri bambo, zomwe amachita a RNB ndi MEC simumazidziwa? MCP yakudyatu

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso วันที่ผ่านมา

    Achotse ana mu system imeneyi
    Ambiri ndi ana

  • @FysonChapita
    @FysonChapita 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiyetu akanagosiya basi chifukwa siziyendabe koma akanati aliyese amene Ali ndikuthekera alembetsa basi

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 วันที่ผ่านมา

    Ine a chunga mozoyankhula zao ndimaona kuti amaimila MCP coz even iwowo akudziwa kuti anthu amabwenzedwa pazifukwa zodziwa okha a NRB ndi a MEC pena anthu amauzidwa kuti magetsi athima ma geniset awo amakhala opanda mafuta pomwe mafutao amapatsidwa,amai ena a MEC ndi aja anachita kukana kuti zaku court zanuzo ine sindikudziwa kanthu,akayamba kulemba munthu zimawatengera chinthawi kuti athane ndimunthu mmodzi zimenezo maumboni alipo pomanamizira network pamenepo mkumati nthawi ikuonongeka ndiye a chunga azikati ngakhale mayeso amakhala ndinthawi yet apa nthawi yomwe inapelekedwayo a MEC ndi a NRB amangoseweretsa nthawiyo

  • @ernestSalabada
    @ernestSalabada 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chunga muchotseni ntchito ku Times akuonkngerani Business

  • @ernestSalabada
    @ernestSalabada 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Jawala Iweyo ndikatundu

  • @Efellofredson
    @Efellofredson 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bodza asambo izi zimavuta kumwela ndikumpoto chigawo chapakati zimatheka ndiwana omwe anthu awa apanga kale zomwe amafuna mce nrb anatumidwa ndi mcp kuti apange zokomela mcp nchifukwa akumati tifune tisafune boma sitikusintha zolinga zawo nkubela mec ndi nrb si ijayo takhala tikuidziwai ayi iyi ndi ya chakwela

  • @MissoutNiceday
    @MissoutNiceday วันที่ผ่านมา

    NRP ikuzikolakola pogwilantchitobwanji?

  • @GeniusPoultry-ew4pg
    @GeniusPoultry-ew4pg วันที่ผ่านมา

    Bayana chunga apite ku mbc radio ukuonanga zinthu

  • @PatrickMaulid-qq4zx
    @PatrickMaulid-qq4zx วันที่ผ่านมา

    Ife tikapita Malo olembesela amatiuza kuti mafomu atha ndiye tikanalembesa bwanji??

  • @YasinterKapinga
    @YasinterKapinga วันที่ผ่านมา

    Chifukwa tu anthu ambili anabwelela 😊

  • @edgarchirwa8172
    @edgarchirwa8172 วันที่ผ่านมา

    Kodi mukamati 7M+,Ana ndi angati pamenepa

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 วันที่ผ่านมา

    Mxm palibe chazeru apa kodi chovuta ndi chani kuti athu alibedwe

  • @LevieMwanayaya
    @LevieMwanayaya วันที่ผ่านมา +1

    Aliense alembedwe Pali Ena anali ncipatala pano Ali kunja ndie asapasidwe mwai olembesa ndie ufulu palibetu

  • @Ernestkamvazina
    @Ernestkamvazina วันที่ผ่านมา

    Kuno ku chileka ma ID athu mpaka pano mukuziyendetsa bwanji zinthu zanu agalu inu

  • @JbIb-xh5gm
    @JbIb-xh5gm วันที่ผ่านมา

    Ngati kuli kuyambila ayambile zose asachite asasankheso ayi aliyese alembese basi akasankha ndekulakwisano chifukwa pali ena inathela nthawi Ali pazele nankha iwowo asakalembeseso

  • @YasinterKapinga
    @YasinterKapinga วันที่ผ่านมา

    Nanga kwa omwe anapita tsiku lomaliza nde anchedwa thawi inatha nawo asakalembeseso

  • @EmmanuelKapichi
    @EmmanuelKapichi วันที่ผ่านมา

    CHUNGA NDI WA MCP UYU

  • @honestchunga693
    @honestchunga693 วันที่ผ่านมา

    Anthu amangokhala samayikilako attend or apiteso anthu enasakalembetsaso

  • @JulietKapata
    @JulietKapata วันที่ผ่านมา

    Aliyese alebese asatilamule

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno วันที่ผ่านมา

    Izi zisativute apa angoyambilanso wanji kulembela tisamazungulilane apa

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani วันที่ผ่านมา

    Adzadziwa bwanji kuti amene anabwezedwa nthawi itatha ndiwomwewodi😂😂😂

    • @RejoiceKaliya-i9t
      @RejoiceKaliya-i9t วันที่ผ่านมา

      Nanenso funso langa ndi lomweli. Adzadziwa bwaanjiii kuti anabwenzedwa ndi awa?

  • @veronicajana5225
    @veronicajana5225 วันที่ผ่านมา

    Ngati mpata wafika tonse tilembetse aliyense watsala

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 วันที่ผ่านมา

    A MEC ndi amwano, mwana wa Tembo.

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwayamba kutikaikisaso

  • @NelsonMzoma
    @NelsonMzoma วันที่ผ่านมา

    Dziko lantundu wanji losapanga za serious

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g วันที่ผ่านมา

    Bayana. Ukhale ndi nzeru::aliyense ndiololedwa

  • @allieadam3235
    @allieadam3235 วันที่ผ่านมา

    Ena tinali kunja tafika pompano Nde tikufuna tirembetse nawo basi

  • @VincentKalata
    @VincentKalata วันที่ผ่านมา

    Samboyo ndi chislu akuesa ngt akuchenjera

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g วันที่ผ่านมา

    Awareness siinali yokwanila::

  • @GeniusPoultry-ew4pg
    @GeniusPoultry-ew4pg วันที่ผ่านมา

    Sambo. Uziganiza kod mesa unapita ku school unayamba wadzichongapo wekha anthu akukuuza kut sikugwira bwino ntchito iweukuti ukugwira bwino who told you....?

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    You are lying lyana , everyone one must regester it's the right to vote.

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 วันที่ผ่านมา

    Chunga is just sell out who doesn’t like his country

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 วันที่ผ่านมา +1

    Ine a chunga mozoyankhula zao ndimaona kuti amaimila MCP coz even iwowo akudziwa kuti anthu amabwenzedwa pazifukwa zodziwa okha a NRB ndi a MEC pena anthu amauzidwa kuti magetsi athima ma geniset awo amakhala opanda mafuta pomwe mafutao amapatsidwa,amai ena a MEC ndi aja anachita kukana kuti zaku court zanuzo ine sindikudziwa kanthu,akayamba kulemba munthu zimawatengera chinthawi kuti athane ndimunthu mmodzi zimenezo maumboni alipo pomanamizira network pamenepo mkumati nthawi ikuonongeka ndiye a chunga azikati ngakhale mayeso amakhala ndinthawi yet apa nthawi yomwe inapelekedwayo a MEC ndi a NRB amangoseweretsa nthawiyo