@@BersonMalunga-i4g ndipo tidzaonetsetse kuti he is the one. Tidzamvera mau , and ka sound kake kaya anakapeza potani. Mwana ameneyi ndi ' Check mate', if you don't check your move, He will strike!!!
Mafunso nkumati Kodi nthawi imeneyo amaziwa kuti mtsogolo muno zizawika kuti amajambulidwa? Zoti zizakhala pa Radio zimenezi amaziwa? Lerotu ndi izi tikamati MCP ndi chipani cha magazi ndichakupha ndizonama? Lero SI izi zikuchitika ndendende ndi mmene zawachitikila a Bishop Msusa komanso ndi ma Bishop onse omwe akufuna kuthana nawo. Bravo Bakili Muluzi TV... History is the best teacher
Ana ama 2000 ngat ife tadziwa zisisi zomwe sitinkaziwai zokhuza kamuz ndcipan cake CA MCP , indeed history is the best teacher, happy new year bakili muluzi TV I like u so much,God must bless you
History repeat itself, when old people telling us we thought the lying to us the same system of punishing people there against the views it's what happening now. All the best Bakili Muluzi TV continue teaching us am wishing you happy new year i hope this coming year you will come with more teaching and information God will be with you.
❤❤❤.....you are the best..yes history is the best teacher...and you are the chancellor.....we love you and love you... May this 2025 be the most fruit full to your life... God is in control control always stay blessed. No one God is watching and will protect you in every step you will be taking....
History is the best teacher tifunilanji umboni wina kuti mcp ndiyoyipa pano kamuzuyo Ali kuti nanga temboyo Ali kuti wamoyo aliyese adzafa ndithu ndiye osamaziwona nga ti siudzafa kuzuza a zawo zoona
Listening from mziza home city History is the best teacher. We love you bakili muluzi tv. Wishing you the very best happy new year of 2025. Plz never give up komaso mokupephani nkhani zina muzizikimbitsa tizaziwe zoonadi in future ❤
History is the best teacher MCP asayellekese nkubwelella boma lisamallry llawononga mallawi nkwambilli 2025 by 16 September asayanga mafusso onkusana shinkangawaw sinkwanje 🤛🇲🇼🇿🇦 lives in sautha Africa estan cap 🎤
Mwamva mene akuyankhulira ndi anthu okupha awa inu munthu ukayankhule mosaopa kuti ameneyo tikoza zoona ,ufiti weni weni this is a democratic country zopusazo musiyiletu a MCP dziko lino silakwanu
I said thank you Lord Jesus for life ,continue keeping us safe including Bakili Muluzi tv amatidziwisa ,kutiphunzisa mbiri ndi zochitika kuyambira kale ndi lero mbiri ya Mcp zikomo Bakili muluzi tv, Mcp yathapo basi mu dzina la yesu khristu
Kkkkkk km izii amavela anthu aja because ngat amene aja amavela sazapelek complain kena bakili muludzi tv ndi munthu opwa kwambili eeehh amazipeza bwanji izii ameneyu
History is the best teacher indeed, koma onse omwe amapanga upoo umenewu ali kut pano?? Kunkuyu, Chimwendo, Zikhale, Mkaka, Gotani Hara, Chakwera ........tsiku lanu lidzafika ndithu anzanuwa ankatumbwanso ngat inu lero ali kut?????
Anthuwa sazasintha even patavuta motani, They will shed blood in what it takes only God will save this nation for we trust him. Dear God protect us all and our beloved Bishop
Tinazuzika kwabasi kuombera manja pa gate ya Nsanjika akayamba CROP INSEPECTION ,kubisala pasi pa Bed ayouth makhadi ngati ulibe ,ngati ulibe amatenga china chilichonse achipeza pa khomo ,A kamulepo Kaluwa anali freedom fighter Nthawi imeneyo Makolo amamvera ma RADIO yawo usiku anthu atagona otherwise awamanga kapena kusowa Amaulula zisisi za Kamuzu zomwe Amalawi sakudziwa m'mene akupangira Bakili Muluzi TV we need to THANKS Honorable Kamulepo Kaluwa it wasn't easy during the Ruling of Kamuzu Banda today your voting the same PARTY many people died .
❤Ndikufunirani 2025 opambana in a Bakili muluzi TV 🎉🎉 popanda inu ife ndiayani🙏🙏🙏
The best Tv of the year Bakili Muluzi
Second TTV hot current
3rd Comrade Ntanyiwa
4th The DC ❤❤❤❤❤
Indeed, history repeats itself. MCP ikamagwa imamenyana ndi ma bishop. #Bakiri Muluzi TV forever
Chonde bwana chipan chikazasitha zaonekelen kufuna zakupasen mon wogwilana zanja. Big up God bless you bigy
live
@@BersonMalunga-i4g ndipo tidzaonetsetse kuti he is the one. Tidzamvera mau , and ka sound kake kaya anakapeza potani. Mwana ameneyi ndi ' Check mate', if you don't check your move, He will strike!!!
😂😂😂😂😂 koma ameneyu akuwoneka sakhulupilira munthu I believe kuti even nkazi wake SADZIWA
Mafunso nkumati Kodi nthawi imeneyo amaziwa kuti mtsogolo muno zizawika kuti amajambulidwa? Zoti zizakhala pa Radio zimenezi amaziwa? Lerotu ndi izi tikamati MCP ndi chipani cha magazi ndichakupha ndizonama? Lero SI izi zikuchitika ndendende ndi mmene zawachitikila a Bishop Msusa komanso ndi ma Bishop onse omwe akufuna kuthana nawo. Bravo Bakili Muluzi TV... History is the best teacher
Mcp sizalowaso boma ikangotuluka ndipo chipani chimenechi chimayenela kuth basi
Ndipo amapanga record ndindani? Bakali muluzi Tv....mumatimvetsa kukoma..history is the best teacher.
Don't worry chimenechi chitha basi😢😅😢
Eee koma Bakili iweyo, aaaa zoona umatha kufukula ase History is the best teacher indeed receive your flowers 🌸🌹
Ana ama 2000 ngat ife tadziwa zisisi zomwe sitinkaziwai zokhuza kamuz ndcipan cake CA MCP , indeed history is the best teacher, happy new year bakili muluzi TV I like u so much,God must bless you
Sifukwa chimene munalengedwera ndi kutizindikiritsa Ife osadziwa God bless and protect 🎉 you best TV BMTV history is best teacher
Kod boss iwe zithu izi umazitenga kut,,,iwe ndi one boss🔥🔥🔥🔥🔥live from mzuzu university
Inesotu Nde madabwatu nawo bigy wa😂😂😂😂😂😂😂 koma ulemu wao
Katundu owopsa zedi uyu zedi ❤❤❤
Katundu omanga ndimawaya
Ukupanga pg yanji
Zoonad amwene kod iyeyu amazisokola Pat and wazipeza bwanj
TV ndi yomweyi kusintha kulibe ,history is the best teacher indeed, Agalu awa atikwana azipita 2025 kupha basi ndiye ikhale nkhani muyaluka agalu inu
Our God should continue blessing you sir...may his wings covers you so that enemies can't see and harm you 🙏
History is the best teacher, wa bakili muluzi TV ambuye akusunge ndi moyo wautali. Happy new year, mcp imapha ngati tarmec ophera makoswe
One off the best tv Bakili muluzi ....
History is the Best teacher
May God bless Bakili Muluzi TV
Leave long
History repeat itself, when old people telling us we thought the lying to us the same system of punishing people there against the views it's what happening now. All the best Bakili Muluzi TV continue teaching us am wishing you happy new year i hope this coming year you will come with more teaching and information God will be with you.
Tv of the year pa history am proud with you Bigman .l wish you all the best in 2025
Asala ambewu ndi angati mu kagulu kameneka lero. Asatana, History is the best teacher. Happy New Year BMTV
MCP followers mwayimva history ?? Manyazi bwaa ?😂 chipani chakupha wanthu, cha history yokhetsa mwazi waanthu 🤯🤯zigawenga.
❤❤❤.....you are the best..yes history is the best teacher...and you are the chancellor.....we love you and love you...
May this 2025 be the most fruit full to your life...
God is in control control always stay blessed. No one God is watching and will protect you in every step you will be taking....
Man of the year bakili muluzi tv
History is the best teacher tifunilanji umboni wina kuti mcp ndiyoyipa pano kamuzuyo Ali kuti nanga temboyo Ali kuti wamoyo aliyese adzafa ndithu ndiye osamaziwona nga ti siudzafa kuzuza a zawo zoona
Abambo Ake as nabelo😂😂😂kuchititsa manyazi
😂😂😂😂
Listening from mziza home city
History is the best teacher. We love you bakili muluzi tv. Wishing you the very best happy new year of 2025. Plz never give up komaso mokupephani nkhani zina muzizikimbitsa tizaziwe zoonadi in future ❤
Bakili mulizi TV #1..inuyo big pa history mulibe nzanu❤❤❤❤
Big man tipatseni zambiri kuphunzira sikutha. History is part of life
Iwey ndi munthu wamkulu bro respect
History is the best teacher ❤❤❤❤ I wish you the blessed 2025 may the good Lord bless you and your group and your family 🎉🎉🎉🎉🎉
History is the Best Teacher koma mumasungira....Bravoooo
Bakili muluzi tv ndi captain long live bro bakili muluzi
Anthu oipa a mcp congress lelo ndi izi mungokonza mwa speech yanu History is a best teacher BMtv
Umbuli wa MCP amayankha zinthu za public zomwe sizingawapindulile
History is the best teacher
Ife tikanena Mcp iyi ndiyamagazi Anthu muli anasitha lero siizii!!
Zikomo kwambili bakili muluzi TV ❤❤ best teacher history
History is the best teacher MCP asayellekese nkubwelella boma lisamallry llawononga mallawi nkwambilli 2025 by 16 September asayanga mafusso onkusana shinkangawaw sinkwanje 🤛🇲🇼🇿🇦 lives in sautha Africa estan cap 🎤
Bishop wavumbulusa wa pa zala
Apa sopano ndayiziwa MCP
Sizayi voteraso
Koma inuyo mumatha kufukula zinthu zobisika...big up boss 💪💪💪💪
Imeneyo ndiyo MCP ngati simadziwa ana inu😢😢
ma Bishop ambiri adakalipo iwo eni moyo alikuti no wonder mwana wa Tembo Mirabell ndi mfiti naye
Bakili Muluzi tv we still love you you are freedom fight in this generation happy new as we are going to 2025 ❤
King Man sopano ulemu wanu wa nthawi zonse❤❤❤
Ndimakunyadilan mfumu yanga mulungu azikuthetezani nthaw zonse
History is the best teacher❤ chonde tikachosapo bomali zaonekereni tixakuziwen🎉
Much Respect to You,Bakili Muluzi Tv
Hilda at ndi chairman wa azimai😂😂😂
Mwamva mene akuyankhulira ndi anthu okupha awa inu munthu ukayankhule mosaopa kuti ameneyo tikoza zoona ,ufiti weni weni this is a democratic country zopusazo musiyiletu a MCP dziko lino silakwanu
Jon tembo anali munthu woyipa, chifukwa choti "you" basi nkhani yafika apa
History is the best teacher😂😂ATI akaonane ndi bwana lero Ali kuti aliyense adzafa basi
Bakili muluzi tv mulungu akhale nanu mmene tikukalowa 2025 🎉🎉🎉 mulungu akusamalikeni ndi family yanu history is the best teacher 🎉🎉🎉
Bravo brother, MCP zigawengadi
Our teacher of history we love you bro history is the best teacher ❤❤
You can only access this audios from MBC.big up bwana mumatha.olo pa court mutha kudzipanga defend.history is really the best teacher
Information naye imakhala ndi nkhani ina ili yonse koma kuti uyipeze its not easy not at all
Osazayelekedza zoonekerazo
Shiiio pipo hate progress. Kakha mchgomamo. All de best
History is the best teacher uwu ndiumboni waukulu kuti anachita kuphedwa chilima
History ija it's the best teacher indeed
I said thank you Lord Jesus for life ,continue keeping us safe including Bakili Muluzi tv amatidziwisa ,kutiphunzisa mbiri ndi zochitika kuyambira kale ndi lero mbiri ya Mcp zikomo Bakili muluzi tv, Mcp yathapo basi mu dzina la yesu khristu
Indeed history is the best teacher
Zoyezekanazi zidayamba kalekale eti😮😮 mcp eish i never knew ndimangomva
History is a really best teacher.
ABMtv Akakhala Kuti sanatuse audio tsiku limenelo timadwala Ngat chinachake chasowa mthup tsiku silikoma Ngat sindinavele bmtv
Kod bwana ......... bas chonena ndilibe mulungu akhale nanu happy new year
Oooo yes boss mumakwana ife amene sitimaziwa Zambili panopa tikuziwa Zambili kuchokela Kwa inu big up BK TV we are proud of you stories
History is the best teacher ever ❤
Wishing you a prosperous new year bro BM TV forever ❤👍🇲🇼🇿🇲🇿🇦
History is the best teacher indeed!
Bakili TV Viva your no 1 because of this history
History is the best Teacher 👌 ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Uyu anali Munthu Woyipa ProMax eeeeeh 🙌🙌🙌
History is the best teacher 🔥🔥🔥💪💪💪
Ine ndilibe mawu kani agulugunyinda abwantasawa akupitiliza zamakolo awo zikomo boss mr BM tv potiululila
Ife timadalira inu nde chonde osazatipusitsa kusintha nkumanena kut voteran mcp pamenepo nkhondo izavuta big up bakili muluzi tv 💪💪💪💫😅
Uyu ndiwankulu kuposa Malawi ❤❤💪💪🤝
Ndiye mukundiuza kuti mwana wake Anabel Mtalimanja angakhale wachilungamo pazisankho zikubwerazi?like father like daughter
Achikhulile inu ndakutayilani katengo good job God bless you be ndimoyo wautalii🎉🎉🎉
Mmmmm Your so blessed and talented Boss❤❤
Bakili Muluzi TV mngwabodza musamamuvereeee😂 kumtundako pali bodza apa?😂😂😂😂😂
😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂 chimwendo, chakwera, nkhumba ng'oma zikhale bwanji pamenepo palinso Bodza? Iyi game yatha iyi
Kkkkkk km izii amavela anthu aja because ngat amene aja amavela sazapelek complain kena bakili muludzi tv ndi munthu opwa kwambili eeehh amazipeza bwanji izii ameneyu
Pita oko idiot mcp ndiyakupha
Kkkkkkkkkkkkkkkkk. Bodza lanji?
Wekha sukumva Kodi?
Akuti tikonza?
Kwacha!!!!?
This is deep. People of Malawi we must digest this with all senses. Other wise may God help us. IJN.
I support Bakili Muluzi TV
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 mbambande Bakili muluzi tv Chanel.
Inuyo mwayenela kulandila ulemu big ❤❤
A ward imafunika inu bigman ❤
Ndikukufunilani kulowa chaka cha new one bwino ur the best
The best teacher in the world😂😂😂
Best historically chancellor of the year!! Ambuye akupatseni chitetezo chochuluka, Onse okupha amzawo sjs lero alikuti?
All the best Bakili Muluzi Tv 🎉
History is the best teacher indeed, koma onse omwe amapanga upoo umenewu ali kut pano?? Kunkuyu, Chimwendo, Zikhale, Mkaka, Gotani Hara, Chakwera ........tsiku lanu lidzafika ndithu anzanuwa ankatumbwanso ngat inu lero ali kut?????
Best teacher🎉
Choyamba happy new year 🎉my brother Bakili muluzi TV
This is the same thing happened last week by those so called concerned religious leaders..... Indeed history is the best teacher
Koma awa zawavuta ma unknown bishops without churches
Tikumva zinthu zot znakambidwa or makolo anthu asanabadwe big up my bro
Thank you brother you are best God bless you brother on 2025 ❤❤❤❤❤
History is the best teacher
Bakili Muluzi tv tikiyidziwa ife ndimeneyo imafukula zasasi penipeni BT big up boss man 💪🏽
History is the best teacher 🔥
Mcp chomwe mungadziwe inuso mudzafa ndithu. Palibe chamoyo chizazembe imfa
History is the best teacher but bakili muluzi tv is the best too 199 %
History is the best teacher,the best tv forever😂😂bakili Muluzi tv forever.
History repeats itself continue my brother ❤❤
Even a MCP akati aziwa zinthu amabwera ku page yanuyi bwana
Happy new year our teacher may God bless you brother indeed history is the best teacher ❤
Anthuwa sazasintha even patavuta motani,
They will shed blood in what it takes only God will save this nation for we trust him.
Dear God protect us all and our beloved Bishop
Tinazuzika kwabasi kuombera manja pa gate ya Nsanjika akayamba CROP INSEPECTION ,kubisala pasi pa Bed ayouth makhadi ngati ulibe ,ngati ulibe amatenga china chilichonse achipeza pa khomo ,A kamulepo Kaluwa anali freedom fighter Nthawi imeneyo Makolo amamvera ma RADIO yawo usiku anthu atagona otherwise awamanga kapena kusowa Amaulula zisisi za Kamuzu zomwe Amalawi sakudziwa m'mene akupangira Bakili Muluzi TV we need to THANKS Honorable Kamulepo Kaluwa it wasn't easy during the Ruling of Kamuzu Banda today your voting the same PARTY many people died .
You're excellence bakili muluzi😊😊😊😊😊😊