Amene amadana ndi Bakili TV ndi mfiti wakupha wa MCP koma ine ndi akubanja kwanga onse we love this TV ever mpaka mpaka tili nanu nanu timakukondani ndipo mupitilize kutipatsira nkhani zokomazi❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Eeeee big,,, history is the best teacher indeed,,,ndidali mbuli ine,,, I regret the day I casted my vote for this guy,,, fisi ndi fisi ,,, I do request you sir next mutiuze zomwe zidali mu letter imeneyi
Komansotu anamutumizira track onyamula chi container ndi kumuza archbishop Chiona kuti takutumizilani mphatso atabisamo msilikali atanyamula mfuti ndiye Arc bishop Chiona atayilandila container anangoyi pakila patapita masiku ana tsekula anapeza msilikali uja atafa mfuti yake ili pa mbali ntchito za tembo ndi mcp sitimayiwa ndipo sitizayiwala History is the best teacher 👏👏👏
Koma big iweyo lero ndiye watulutsadi mbiri ya MCP eeee .....Naa apa pokha chikangawa wamutha basi.Komaso lero ndakhulupiliradi kut History ls a Best Teacher.....Koma Iweyo Ndi Katundu Ase ine m'manja ndaomba🙏🔥🔥
Ndimakonda Bakili Muluzi TV, Limpopo FM, The DC Bon Kalindo timamva nkhani zoonadi zenizeni ndipo ngati maso a Malawi tatsekuka tatsekuka ndi ma amenewa.... History is the best teacher
History is the best teacher, you really love your country Bakili Muluzi TV continue teaching us. This crocodile government what there knows is to kill and the happy when people there struggling like there it is now.
History is the best teacher ❤❤😮😮 inuyo a BMTV I wish you long live ndithu MCP 1992 Audio's kufika lero 2024 eshhh its not a joke respect.Anthuwa ndiakupha bas ndipo sadzasinthaso ayi.
1999 born son izizi ndimangova mukamati kunali commotion yoopsa kwambiri in 1992 mmmm Kuti khaaaa bakili muluzi iweye eee 25yrs down in the line now for the first time ndavakova speech iyi mmmmmmm receive flowers

Bakili TV is number one TV of Malawi never hiding anything 🎉🎉🎉🎉🎉
Km nde iweo ndare sudziwat aaaa kkkkk hahaha kape iwe
Iweso chitsilu@@ChrispineShabalala-u8z
Iwe nzako ndi ntanyiwa basi
I silute you Bakali muluz vt.
This is my first time to listening this audios
Umachedwa kutiko adaah
@@FaroukSaliemNdipo kaya amachedwa pati kaya asephana ndizambir
Lelo ndine oyamba kumvera odiyoyi history is a best teacher number one
Ukunama iwe ine
Nde oyamba
@Pangolinimwhahaha kod pangolin 😢
Ayi nosenu mukunama oyamba ndne
@FelixAndafu 🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌
Hahahaaa kulimbirana u top fan kumeneko?
2024 award bakili muluzi tv best ever in malawi
Bakili muluzi is a best
Exactly he deserve this tv is the best of the best
Me too 🎉🎉🎉🎉
Ase bakili muluzi tv iweyo Umakwana wallah ine ndizanabadwe apapa ndakulupilila kt history is best teacher ❤❤❤❤❤❤
Koma apa ndiye wa mcp mwamutakasa matumbo ndi Thu Bakilimuluzi TV ndi one🎉🎉❤
Koma iyi mwayisinja big eeeeish❤❤. Wa MCP akomokatu.
Guys let's take this guy seriously eti,, zomwe amanena zimakhala zoona kwambiri, let's support this guy and pray for him wherever he may be
This guy is a genius eish
I Salute this Brother from BAKILI MULUZI TV❤❤
Koma anthu akupha inu
Zoona big
Seriously❤
History is the best teacher, abwana ulemu wanu ndagwada pamapazi anu big, God bres & protect u❤❤❤🎉
Zoonadi may God BLESS this man behind Bakili Muluzi Tv
Koma mumasunga zithu..... history is a best teacher indeed
Bakiri muluzi TV ❤❤❤🎉🎉 i love u (Tv ndiyomweyi sitikusintha)
Ndakutayira kamtengo mnyamata wa Bakili Muluzi tv mpaka kufukula zimenezi😢😢😢😢😢😢 long live Bakili Muluzi tv❤❤❤❤❤❤❤❤
The best journalist in Malawi ever since.....
I think this guy is not a human, he's an angel... History is the best teacher.... Amalawi history sitimaisata tilidi mu umbuli wazawoneni..
Eeeee big,,, history is the best teacher indeed,,,ndidali mbuli ine,,, I regret the day I casted my vote for this guy,,, fisi ndi fisi ,,, I do request you sir next mutiuze zomwe zidali mu letter imeneyi
Koma uyu amasaka mbiri heavy eeee ❤❤
MCP ndiyakupha kuyambila kale History is the best teacher big up Bmtv
Komansotu anamutumizira track onyamula chi container ndi kumuza archbishop Chiona kuti takutumizilani mphatso atabisamo msilikali atanyamula mfuti ndiye Arc bishop Chiona atayilandila container anangoyi pakila patapita masiku ana tsekula anapeza msilikali uja atafa mfuti yake ili pa mbali ntchito za tembo ndi mcp sitimayiwa ndipo sitizayiwala History is the best teacher 👏👏👏
Mwina kuteka ena mumakana kuti history best teacher bakili muluzi TV imanena chilungamo
Ati amakonza,Kaya nduna ikangosewera timakonza eeeh😢😢😢anthu akupha,oyipa awa.
Best tv yatulukira masana❤
🙌🙌🙌🙌🙌 eti idzizi si za Chauta😮
History is the best teacher 🙌🙌🙌
Continue my Brother until our country healed You are in the hands of God am watching from South African And God bless You
Mmmm apapa waponyera kwa kuya ayise😂😂😂Kuswa kuswa 🔥🔥🔥👑👑👑
The best teacher is history❤
tikuva nawo zinthu zoti olo enafe sitinavepo mmmm keep up bakili muludzi tv I love this TV timamva nawo zambiri zomwe sitikuziziwa
umboni upose pamenepa, history is the best teacher 🎉🎉
Jezebelo pamtumbopako galuiwe ndipo uzafa imfa yowawa panyelopako
Koma big iweyo lero ndiye watulutsadi mbiri ya MCP eeee .....Naa apa pokha chikangawa wamutha basi.Komaso lero ndakhulupiliradi kut History ls a Best Teacher.....Koma Iweyo Ndi Katundu Ase ine m'manja ndaomba🙏🔥🔥
Mkulu uyu amankhala kwa Mulungu ❤🎉 Ndipo Mulungu wamubweresa with a great mission yoti tichoke mumdima.
Akamuna odziwa kwafwanyulura history mamtheradi awa ndi akatundu enieni Bakili TV💪💪👍
Komatu lelo mwang'alura bro😂😂😂😂😂 number one
Kumalawi kunonso sindikumuona munthu ofukula mbir ngat bakili muluzi tv chilungamo ndthu tizinvere tokha watching from Mozambique 🇲🇿❤❤❤❤
Exactly 👌👌👌👌
Iyi Tv NDI One two kulibe
Ndpo inenso chonena ndilibe
Ku Area 30 amadana nayo BAKILI MULUZI TV Koma Amayionera be 😂😂😂😂
@@MandalaChaona 😂😂😂😂
History is the best teacher mcp ndi Kangova koma apa ndaziwonela 🤔🤔🤔🤔🤔
History is the best teacher 💕 koma chilima uja anatiponya kuchiphedi srs😢
History is the best teacher bakili muluzi tv ndi katundu best tv ever
Bakili tv mwangoyenera kulandira dziko la Malawi ngati award yanu basi,inu mwina mbiri ya bambo anga mulinayoso 😂😂😂
😳😂😂😂😂😂💔
Best tv🎉🎉 history ndiyofunukadi
Mbili ndi phuzilo labwino= history is best teacher ❤ izi ndizowona ulemu wanu brother
Chipani Cha MCP chithetsedwe please 🙏🙏
Bakili TV the number one 🎉🎉❤❤ history is the best teacher
Best TV in Malawi, we love you Bakil Muluzi TVi❤❤
Eeee koma tamva nawo zomwe timangova ndi anthu kuti kunali mavuto koma eeee bakili muluzi tv respect
Malawi ndiwanu boss ulemu 🎉🎉🎉🎉 more fire
History is the best teacher thanks for the audio keep it up
History is the best teacher
Zikomo bakili muluzi 📺 ❤❤❤
Timanena mobweleza bwereza history is the best teacher
HISTORY IS THE BEST TEACHER 🔥🔥🔥🔥 BAKILI MULUZI TV UDZAWINA AWARD TIME WILL COME MARK MY WORDS❤❤❤
Watching from Johannesburg in south Africa but from machinga we support you brother am very very happy u exposed these criminals mcp
Bakili muluzi TH-cam channel, you're my shining star !!
We love you bakili TV history is best teacher
More fire pambali panupo big boss inuyo ndikhani zinaaaaaa
Best historian for ever you have to live longer
Ndimakonda Bakili Muluzi TV, Limpopo FM, The DC Bon Kalindo timamva nkhani zoonadi zenizeni ndipo ngati maso a Malawi tatsekuka tatsekuka ndi ma amenewa.... History is the best teacher
History is the best teacher. History so educative i had to watch it twice
Munabwela kudzakhala big boss.thanks
The best tv ever indeed stay blessed & protected our History teacher
😮😮😮😢😢😮😢😢😢😢😢😅😢
History is the best teacher
History is the best teacher 😢😢😢😢😢😢
Best wishes Bakili Muluzi, Mulungu akhale ndinu
Our best tv ever in malawi
Bakilimuluzi tv ndinu machine ❤❤❤❤❤
Ndakusokosela kulinga utava izi Mr bakili muluzi TV wakambatu musowaso umboni wanji apapo this Chanel must stay 4ever
Ndani sakudziwa nkhanza zomwe mcp imapanga. History is a best teacher
History is my best teacher. Bakili muluzi Tv is the best
❤❤❤❤❤ I love this TV not zodiac times only bakili muluzi tv is the best TV in malawi
History is the best teacher, you really love your country Bakili Muluzi TV continue teaching us. This crocodile government what there knows is to kill and the happy when people there struggling like there it is now.
Iwe wa Bakili Muluzi TV ase iweo ndi one ase, history is the best teacher straight,, Chakwera is going
This is deep searching. What an archive you have
Best bakili muluzi tv ❤❤❤
History is the Best Teacher
Best TV ever 🎉mumati menyela ufulu ndi kutiuza zoona ,pano malawi waola😢
History is the best teacher I love Bakili muluzi tv.
Best TV in Africa 😊
Best TV ever, history is the best teacher
Eeeeh kma these guys ankaona ngati kamuzu ndi mulungu eti asaaah 😢😂😂😂😂😂
Kunali anthu opusa Kwambiri panthawi imeneyo.Kumamutchula Kamuzu kuti ndi mpulumutsi ndipo zonse ku Malawi ndi zake za Kamuzu basi
History is the best teacher ❤❤😮😮 inuyo a BMTV I wish you long live ndithu MCP 1992 Audio's kufika lero 2024 eshhh its not a joke respect.Anthuwa ndiakupha bas ndipo sadzasinthaso ayi.
1999 born son izizi ndimangova mukamati kunali commotion yoopsa kwambiri in 1992 mmmm Kuti khaaaa bakili muluzi iweye eee 25yrs down in the line now for the first time ndavakova speech iyi mmmmmmm receive flowers
History is best teacher mpaka ma audios ama 1992😢😮 BMTv number one
Mwaswera bwanji sir,the best tv ❤❤❤❤
Bakili Muluzi TV, you are very excellent and eloquent in history. Keep it up!!
History is the best teacher ulemu wanu timangova Kt kale Kunal nkhaza km ndzvera ndekha mmmmm
History is the best teacher King wathu
Boss kuxabwela masana pati❤❤❤❤❤❤ history is the best teacher BM tv
Mumatha Bigman,History is the best teacher
History is a best teacher mkango ndi mkango or utanyowa mvula siungakhale Mbudzi Mcp ndichipani cha kupha ndipo siyingasinthe
Indeed you are the best teacher
Kmaa awa atipweteka 🙌🙌
History is the best teacher
Wow!! This should win the best audio of the year. MCP kills people.
Allah alipo comrade atimenyera khondo basi
history is the best teacher 😢😢😢😅
MCP chipani cha zikwanje
❤❤❤ no weapon formed against you shall prosper...keep relaxing God is watching and shall protect you wherever you at.....
We love you Mr .....
WOW..!! Makolo anthu anavutikadi ndi MCP..!! 😮mpaka pamenepa bale..? 😢 Ndamva chisoni..!!
Kma big inuyo simasewela....even Chikangawa samwa nanu Madzi. Great Job
Bakili muluzi tv timakukondani ndi ntima onse .tiyeninawoni agaluwa
History is best teacher indeed
Bakili muluzi tv is one of best t.v. in Malawi
Long live Bakili muluzi tv receive your flour💓🎄
Kufukula nkhani eeeeish❤❤
Best content creator of all time❤
Ukunva bwanji wa mcp iwe komwe uliko.Muhooo muhooo weluuu muhoneee walala walala .. History it's a best teacher..
Wathawa yekha wekha sukuona kuti or achina Jessy alimziii panopa boma ndilomweli tisitha president basi
Adhaa mhoneeeee onaa radiiooooo werrruuuu😂😂
Ayi ndiribe mawu history is best teacher
Kma mayi wachigwilizano eehh😂😅...Fiti yeniyeni
🎉🎉🎉History is best teacher
Kamajekete😂
Nkhumba😂 mhuuu 😅
😂😂😂😂😂😂
History is the best teacher keep it up brother Bakili Muluzi TV 🔥🔥