NKHANI YA BUSHIR + YA PETER MUNTALIKA/ NKHANI ZIWIRI ZIKULU ZIKULU

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 14 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 420

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 7 หลายเดือนก่อน +21

    We need him back kaya mulankhula bwanji koma just know kuti we are going to vote for him,amene akuti anyamatawo apanga chani pa unyamata waowo? Peter my vote

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 7 หลายเดือนก่อน +12

    We really need our president peter muthalika❤

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 7 หลายเดือนก่อน +15

    The man is so loved and needed by Malawians, his old age is a sign of wisdom. Those that claim to be young are doing nothing to the common Malawians.

  • @ErustusPhiri
    @ErustusPhiri 7 หลายเดือนก่อน +10

    Leadership is not the old age, but the reposibility.

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 หลายเดือนก่อน +16

    Peter Munthalika he's really educated guy who can improve our country as hr did before, president sikuti azilimayi nkhani ndi nzeru zamunthu basi. APM my vote ❤❤❤❤❤❤

    • @ThomasMaulidi
      @ThomasMaulidi 7 หลายเดือนก่อน +2

      APM ayimenso basi anyamata zithuzi zawamvuta basi. Kulamula boma amadikilana pamene mitsonkho akutolera tsiku ndi tsiku

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 7 หลายเดือนก่อน +2

      @@ThomasMaulidi Ndipo brother Thom, anyamatawo zikuwakanika kaaaah uwone katundu wakwelera ndipo anakwelera APM atangochoka kumeneko 2020, mmmmmm thumba la cement linali pa 6 pin nthawi ya APM. Chakwera kungolowa kukaika pa 29 pin. Thumba la fertilizer APM linali 17 pin mwamavendor ndipo Chakwera kungotenga 110 pin. Ndie chomakakamira Kuti Nyamata Nyamata Ndi chain????? Muone mmene Chakwera yo panopa Malawi wamuonongera mmmm

    • @ShabanIssa-il6nc
      @ShabanIssa-il6nc 6 หลายเดือนก่อน

      Alamule bas Apeter

  • @joelkabambe
    @joelkabambe 7 หลายเดือนก่อน +5

    Zoti okalamba sangalamule dziko nzabodza. Maiko ena akuchitabwino pa ulamulilo wa anthu okalamba kuposanso muthalika. Anthu akulankhula chonchiwa ndiongotumidwa ndi MCP cholinga anthu agwe mphwayi pa za Peter muthalika.

    • @Doreen-r3w
      @Doreen-r3w 6 หลายเดือนก่อน

      Inuyo mukulankhura chabe kod anyamawao apanga chan akagwere uko chakwera ndi chilima ife tifuna adad amuthalika

    • @BisalomuChimphako
      @BisalomuChimphako 2 หลายเดือนก่อน

      Inuso bodza limenero bweretsani chitsanzo cha maiko omwe akulamulidwa ndi nkhalamba

    • @ShakirahCassim
      @ShakirahCassim 2 หลายเดือนก่อน

      Palibeso apa piter muthalika yemweyo

  • @KenedyJolamu-rs9xx
    @KenedyJolamu-rs9xx 7 หลายเดือนก่อน +4

    Koditu omwe akuyakhula zimenezowo sikuti azika vota ndi iwowo ayi Ovota ndi ife nde APM my vote💙💙💙🔥🔥🔥

  • @OdreckNdemanje
    @OdreckNdemanje 7 หลายเดือนก่อน +11

    Peter Mutharika has a vision,,not that omuzungulira akumukakamiza,,but the masses want him.

  • @AntonSimony
    @AntonSimony 2 หลายเดือนก่อน +1

    amen mukuti peter sazawina vote yanu nd banja ranu muzapange zotheka koma ife adad oyee

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 หลายเดือนก่อน +9

    Chikuni chachikulu kusunga moto❤❤❤❤❤❤

  • @XasankaalibeeyNuur
    @XasankaalibeeyNuur 7 หลายเดือนก่อน +7

    Akuyima apm akufuna kt asayime ndicholinga aziba panyo panu

  • @misheckchinjala.g
    @misheckchinjala.g 7 หลายเดือนก่อน +3

    Ameneyo akuyimabe or atanena bwanji

  • @ShorishKenneth
    @ShorishKenneth 7 หลายเดือนก่อน +4

    l am still ❤❤❤❤ Ada zakukarambazo ukuziwa ndiwo bs Ine chakwera ndamuda ndikanamutukwana popeza mwaresa pachakwera pake 🎉🎉🎉😅😅😅

    • @FRANKBEULA
      @FRANKBEULA 7 หลายเดือนก่อน

      ❤athu oyakhulilapo pandale akulakhula Fundo zomveka ❤kma kunena zoona ,zithu pano zakwera kwambili ,end revolution it's too high from 7 percentage to 44 end boma lawo labweleka loan it's 9 tillion kwa 3years ,,,,ma loan mu dziko ndiyamene amapangisa kut ziko lizikweza revolution end of that katundu amakwera mtengo ,,,,mamvuto amakhala athu akumudzi ...... So ifeo sitikufuna Muthu wamkulu kapena mwana aiiii tikufuna Muthu ositha zithu basi ,.

  • @LuciusMowa
    @LuciusMowa 7 หลายเดือนก่อน +1

    panopa sitikufuna achintamatanso ayi alutibera ndalama zathu zamisonkho ife tikubvutika kwambiri ngati mudziko muno mulibe ndalama zambili akuteng ndalama kumakagawa kumisonkhano mmalo moti akanapita kukapereka ku makampani kuti mitengo ya zinthu itsike lero akuswerwtsa anthu akubvutika chonchi peter muthalika wooyeeeeee 2925 enawa alephela kuyendetsa dziko

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza หลายเดือนก่อน

    Wokalambayo ndamene amatudyetsa bwino mufune musafune God will fight for us

  • @Hisense-dq5wq
    @Hisense-dq5wq 3 หลายเดือนก่อน +1

    Ayimeso adadi ❤❤ Allah bless you pitha 🎉🎉

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 2 หลายเดือนก่อน

    We need him back as soon as possible, we really love him so much ♥♥

  • @Allieukacha
    @Allieukacha 7 หลายเดือนก่อน +2

    Ife tikufuna Peter Mutharika ayimeso.bas

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 หลายเดือนก่อน

    💙💙💙APM adzasitha zinthu. Afiti a MCPigs mukufuna mupitirire kupha anthu.

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g หลายเดือนก่อน

    Anyamata kumba beta dadi ❤

  • @GodsonLindan-hn4kp
    @GodsonLindan-hn4kp 7 หลายเดือนก่อน +4

    Kod ukaswiri wanuo anakupasani ndani? Anthu opusa inu eti. APM is my vote thanks.

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 7 หลายเดือนก่อน +2

    We still love ❤️ him

  • @DolothyMakumba
    @DolothyMakumba 7 หลายเดือนก่อน +1

    Palibe zimenezo kod Mesa anali mboma momwemo amalephela bwanji akagwele 😢uko

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 7 หลายเดือนก่อน +2

    Ife tikufuna utsogoleri wabwino osat president wachinyamata koma mbuli dziko likungoonongeka lopanda president

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We need Big boys.
    APM my vote✅
    In 2020 rate it was 45%❤
    From 2021 to 2024 rate 145%😢
    imagine???? 😮

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 หลายเดือนก่อน +2

    DPP pachiongolero wina afune asafune❤❤❤❤❤

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 7 หลายเดือนก่อน

    As amalawian Peter Muthalika he has lights to be a president again if he tied on the way he will give the one he trust that his not going to disappoint Malawians we need peter back

  • @PreciousBanda-el1tb
    @PreciousBanda-el1tb 2 หลายเดือนก่อน

    Straight Professor a Kula...

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba 7 หลายเดือนก่อน +5

    Akuluakulu ake ati zopusa agalu inu mufuna muzibaeti

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es 2 หลายเดือนก่อน

    We need our own responsible president petert arthur muthalika

  • @GiftSalijeni
    @GiftSalijeni 7 หลายเดือนก่อน

    APM bas....akuluakulu andaleo bwanji apite ku mcp ndi ukuluukulu wawoi azikaba limoz....

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef 7 หลายเดือนก่อน +5

    Mantha awo

  • @PraiseJere-t4u
    @PraiseJere-t4u หลายเดือนก่อน

    Ayime adad imani

  • @SHARFBASHIR-t7s
    @SHARFBASHIR-t7s 7 หลายเดือนก่อน +2

    Amusiye Peter mutalika ayimile amalawi akasankha sogoli yemwe akufuna yene ndi sa voter Peter mutalika

  • @AhmadIsmael-l5q
    @AhmadIsmael-l5q 7 หลายเดือนก่อน +4

    weather u like or not apm is coming into power

  • @Owen88887
    @Owen88887 7 หลายเดือนก่อน +2

    APM my vote apoayi bola osavota

  • @MagangaLeman
    @MagangaLeman 7 หลายเดือนก่อน +1

    Nkhani ndiyoti malamulo akuwalola kuyimila ??
    Osati ndi okalamba

  • @McdonaldChimwala-w9z
    @McdonaldChimwala-w9z 7 หลายเดือนก่อน +1

    Ameneyo wayankhula bwino kwambiri,anthu azavote okha.

  • @DeversonRodgers
    @DeversonRodgers 6 หลายเดือนก่อน

    I love peter 2 much is the one who save malawi

  • @SofieRafik
    @SofieRafik หลายเดือนก่อน

    We need him no matter his age but his love

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 7 หลายเดือนก่อน +2

    Mufune musafune Apm akuyimaso ndipo azawina osat mbuzi zomwe zilipo panoz zikapitirize kuvala nyau

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 7 หลายเดือนก่อน

    Ngati wakalamba bwanji anyamatawa zikuwabvuta?

  • @PreciousLesani-c2x
    @PreciousLesani-c2x 2 หลายเดือนก่อน

    Akuyenera kuzaima osat omuzugulira ayi

  • @malawigeneralguide1646
    @malawigeneralguide1646 7 หลายเดือนก่อน

    Agogo wo akapume ....kodi kulibe anthu ena ku dpp?

  • @NifuDagas
    @NifuDagas 2 หลายเดือนก่อน

    Ameneyo waboza wamutumayo akunama ine ndimuvotela

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 2 หลายเดือนก่อน

    We love him Amp ❤

  • @alainkawema5459
    @alainkawema5459 7 หลายเดือนก่อน

    Peter Munthalika vote ndiyako basi❤90 %

  • @GloryRudraksh
    @GloryRudraksh 4 หลายเดือนก่อน

    Akaswiri olankhulira za ndale enawa ndi a mcp eti?

  • @TrysonChimenya4-fm8nt
    @TrysonChimenya4-fm8nt 7 หลายเดือนก่อน

    Policy for presidency period in Malawi is 2 terms which is 10 years, it doesn't denie the aged to stand, lets not confuse With Pension Age, these are different things to compare. Let him stand and See what the majority will choose.

  • @GraciousKhonje-k8f
    @GraciousKhonje-k8f 2 หลายเดือนก่อน

    Peter muthalika will win no matter what

  • @ChrisLessie
    @ChrisLessie 6 หลายเดือนก่อน

    Abwerereso Peter ❤

  • @AnorldJohn
    @AnorldJohn 7 หลายเดือนก่อน

    We love you Mr president

  • @MESEEDMRMEMO
    @MESEEDMRMEMO 7 หลายเดือนก่อน +1

    Sinzolakwika Peter Munthalika aimenso.

  • @PaulFrank-tj2mc
    @PaulFrank-tj2mc หลายเดือนก่อน

    Dpp oyeee

  • @thokoJames-gp8mk
    @thokoJames-gp8mk 7 หลายเดือนก่อน

    3:35 Achaima inu ndinu agulu la nankumwa inu zainu tikuziwa kale, anthu ngti inu ndiamene mukumasokoneza chifukwa chazolankhula zanthu zaziii zongofuna kuwasokoneza amalawi asiyeni apange zomwe iwo akufuna ngt anthu azawakonde ndie kuti azawavotera

  • @MariamChipoka
    @MariamChipoka 2 หลายเดือนก่อน

    He is a rigth person and a presdent to malawians

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op 7 หลายเดือนก่อน

    My vote dpp❤

  • @MathewsMANDUTU-lh6oo
    @MathewsMANDUTU-lh6oo 7 หลายเดือนก่อน +2

    If God says yes who can say no,,, we want change, we need APM

  • @samsonhavenoyayshonga2609
    @samsonhavenoyayshonga2609 2 หลายเดือนก่อน

    Tikufuna Peter Mutalika abwelere mboma

  • @SahilKagwa
    @SahilKagwa 7 หลายเดือนก่อน

    Akumuopa Peter Muntharika yo kkkkkkkk ndiufulu wake kuyimanso

  • @ThokohKalonga-je9rx
    @ThokohKalonga-je9rx 5 หลายเดือนก่อน

    Komatu muyambitsa nkhondo inu, iweyo amene ukunena zoti sangayendese zinthu bwino chifukwa chakuti wakalamba machende ako 2025 boma ndipo ndidzabwera kuzavota

  • @Veronahkapito
    @Veronahkapito 6 หลายเดือนก่อน

    Apm my vote chakwera wandililisa sugar mpakana 3600😢😢😢 chimanga 50 pin ayi malaulo ndithu dpp imatisamala potchipisa xithu osati kutivesa pain

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 หลายเดือนก่อน

    Achinyamatawo, Chakwera ndi MCP apanga zonyansa zambiri.

  • @KassimSteven-j1z
    @KassimSteven-j1z หลายเดือนก่อน

    Ndipo ndiye timuvotera

  • @FrezaMatekenya
    @FrezaMatekenya 3 หลายเดือนก่อน

    My vote adad

  • @EmmanuelNgamuti
    @EmmanuelNgamuti 2 หลายเดือนก่อน

    How old is current Nigeria president, American president and Donald Trump?

  • @YousufMpunga
    @YousufMpunga 2 หลายเดือนก่อน

    We need him here nomuter wat ppl can say

  • @RuthMsangwa
    @RuthMsangwa 7 หลายเดือนก่อน +1

    Ngt amunthalika akula ndye kutiso palibe cifukwa chowakakamiza acikulile anthu mmamidzimu kukavota nthawi ya zisankho

  • @MatthewsJanuary-r1y
    @MatthewsJanuary-r1y 2 หลายเดือนก่อน

    Zimenezo ndizopanda nzeru. Ngati Peter sangasinthe, ndekuti ndi uti amene achepetse mavutowa?
    Awa si anthu oona zoona ayi.

  • @KenedyJolamu-rs9xx
    @KenedyJolamu-rs9xx 7 หลายเดือนก่อน +1

    Osamatokosa dala anthu mwava wakula wakula nde kuti chani za chamba basi Peter akuyimaso komaso awinaso💪💪💪💪💪💪💙💙💙💙💙🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @MartinMaunda-li7mj
    @MartinMaunda-li7mj 7 หลายเดือนก่อน

    APM my VOTE

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 หลายเดือนก่อน +1

    APM my vote ❤❤❤❤❤❤

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl 7 หลายเดือนก่อน

    APM my vote

  • @IanAllstal
    @IanAllstal 2 หลายเดือนก่อน

    Pieter Atha kuwinaso Anthu akumu3ra heavy mukanena zakukula osadanda pazakhala Achinyamata othandizira A pita Ali phe pa mpando wa ndarema 2025 DPP Boma 💪💪💪

  • @LembeniMtenje
    @LembeniMtenje 7 หลายเดือนก่อน +1

    Mulekeni munthu ndi ufulu wake kudzaima . Ngati anthu sakumufuna idzaweruze ndi vote. Inu dzavotereni munthu wakukhosi kwanu. Ife amene tikumva kuwawa ndi BOMA la tonse, tizavotera peter muntharika.

  • @PetrosChimenya
    @PetrosChimenya 7 หลายเดือนก่อน

    Ayamba kale Dad ipatseni moto ❤❤❤❤❤❤

  • @HaniethOsmanPop-thii
    @HaniethOsmanPop-thii 6 หลายเดือนก่อน

    Akuluwa sangamangidwe even atalakwa

  • @AubreyWilson-j8w
    @AubreyWilson-j8w 3 หลายเดือนก่อน

    My vote

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 7 หลายเดือนก่อน

    Ernest inuyo palibe chomwe ukuyakhula apa Garu wachabe chabe, ngati ukudya ndalama zabomazo usamanene za age limit apa

  • @AlexSaidon-pq5pu
    @AlexSaidon-pq5pu 6 หลายเดือนก่อน

    Akumuwopa muthalika awina

  • @LuciusMowa
    @LuciusMowa 7 หลายเดือนก่อน

    Apm ndigwero lopulumutaa amalawi pa mabvuto akukumananawo mdziko muno anthufentizimuyamika peter muthalika zinthu zinali zochipa kwambiri kusiyana ndi pano amalawi tonse tikutha kusiyanitsa tokha kumanena chilungamo ndibwino mulungu akutha kunonso ndi chifukwa anthu akufuna peter muthalika kuti a were so mboma Apm my vote 2025 wooyeeeeee

  • @MagdaraneChidamula
    @MagdaraneChidamula 7 หลายเดือนก่อน +1

    Kukalamba kwa chani anyamatawo akuchitapo chani mumangoganiza mutalankhula eti osamatero aliyense Ali ndiufulu musiyeni ndiufulu wake Mesa anyamata amati azasintha zinthu pano zasintha anthutu sakudana ndi chakwera koma ulamuliro wao anthu tikuzunzika or ulamuliro wa amutarika fertilizer anafikapo 100000 iwowatu ankati ndi anzeru lerobwa abale ukakhala pa kariyalaa umati driver satha kuyendetsa koma yendetsatu goo

  • @austinhowa5116
    @austinhowa5116 7 หลายเดือนก่อน

    Mutharika ndiye yankho,inuyo ndi acongres.

  • @ChikondaManda
    @ChikondaManda 2 หลายเดือนก่อน

    Pali funso pa nkhaniyi adzakoza bwanji pakuti mavuto anabwela ndi iwowa mmmm zikufunikadi kuganiza kwambiri

  • @FestusPhiri-v4s
    @FestusPhiri-v4s หลายเดือนก่อน

    Adada omweo peter tikufuna chitukuko osati kumaphana ngat a mgalu

  • @chikokaSagonja
    @chikokaSagonja 6 หลายเดือนก่อน

    Aimilebe Apm palibe chowalephelesa kamba kakukula kwawo Apm my vote

  • @MacwilliamMilanzi
    @MacwilliamMilanzi 2 หลายเดือนก่อน

    Amusie alephere ekha president samaendetsa dziko ekha

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g หลายเดือนก่อน

    Ukunama chakwera amene aononga dziko

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi หลายเดือนก่อน

    Vote muthalika

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 7 หลายเดือนก่อน

    Kukaramba sivuto zikufunika ndi zeru zoyendesera dziko tikuwafunabe adadi mwina fertilize wungazasike mtengo chomwe tikufuna ndi nsima basi wosati tizigonera batata tatopa mkazi wumamuziwa wubwino wake wukakhara Kuti wamuthamangisa watenga mkazi wina ndiye akasiyana zochita pamene wumalingalira kuti ndikadaziwa sindikanapanga zimenezi

  • @phirimacdonald8638
    @phirimacdonald8638 7 หลายเดือนก่อน +1

    Palibe zokalambazo muziziwa ndiinu, ndi anthu akumufuna akumuzi osati inu , mwamva

  • @isaaczidana2914
    @isaaczidana2914 7 หลายเดือนก่อน +1

    Amusiye APM adzaime, Palibe chifukwa chomukhomelela nayeso Ali ndi ufulu oyimaso

  • @mustafailanga2585
    @mustafailanga2585 7 หลายเดือนก่อน +1

    Akalamba ndichani zausilu akalamba amusiye zaisilu apm oooooooyeeeee chamba

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 7 หลายเดือนก่อน +1

    Akalamba ndambuyawo Kodi mufuna anene kuti okalamba sazaponya nawo voti

  • @BestMaloni
    @BestMaloni 7 หลายเดือนก่อน

    Za ziii Angadzasithe chaniso Amuthalika zinawakanikakare

  • @AlfredSternChapweteka
    @AlfredSternChapweteka 7 หลายเดือนก่อน

    A George chaima alephera kulankhula, chifukwa mavuto omwe alipo siomwe akunenawo ai. And akuyankhula monga otumidwa ndi anthu ena. APM ndi mtsogoleri yemwe angapangitse zinthu zitsinthe

  • @DanJJJr
    @DanJJJr 2 หลายเดือนก่อน

    Undule ndi wa MCP

  • @JamesAnusa-vd6hh
    @JamesAnusa-vd6hh 3 หลายเดือนก่อน

    I love him so much

  • @MoosahPonda
    @MoosahPonda 2 หลายเดือนก่อน

    ❤iyimeso

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 7 หลายเดือนก่อน

    Apm my vote ..MCP anyamata oganiza BHO akagwere uko mbanva zokha zokha DPP boma