A DAVID MBEWE KU BLANTYRE __12 October 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 55

  • @OwenchangnyaMkandawire
    @OwenchangnyaMkandawire 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    The guy talking after him messes the whole interest of listening to mbewe.asachite Ngati Ali mtchalichi

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 วันที่ผ่านมา +2

    David Mbewe akuyenera u president osati ngati Chakwela wakupha vice wake coz of udindo

  • @ImmanuelndagomaKondowe-n1v
    @ImmanuelndagomaKondowe-n1v 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Inunso mukufuna kuzapeza experience pa dziko la malawi ngati Chakwera😂😂😂

  • @JoãoChirwa-n3l
    @JoãoChirwa-n3l วันที่ผ่านมา +1

    Uyu ali mbalume waenela kukhala president guys❤❤

  • @phillkaunda5623
    @phillkaunda5623 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Who new chakwera would be like now? My fellow malawians, if u come to politics in the name of God, u will never make it. Vote as u wish time will tell, no truth in politics what they want is money

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    My hope ineyo guys Mr mbewe God bless you Sir palibeso wina

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande วันที่ผ่านมา +1

    My vote on you Dr.

  • @FidesChandama
    @FidesChandama วันที่ผ่านมา +2

    Tatopa ndi mabusa chakwela adabwelaso ngati mgelo koma lero ndi chilombo cha mitu 9 ndiye ngati muli abusa pitani ku church

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z วันที่ผ่านมา

      Exactly chilungamo chenicheni azibusawa tisawakhulupilire amangofuna kuba azipitad ku church

  • @DavidKanyemba-n2s
    @DavidKanyemba-n2s 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ambewe omwewo kuti wawawawawaaaaa

  • @ChristopherMakupe
    @ChristopherMakupe 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ameneo akuma comentayo asiye anthu tomzvera speaker

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We don't need this government again mcp is going now chikangawa walephera kuyendedza dziko la Malawi nonsense 🙄 government 🙄 😒

  • @Moses51
    @Moses51 วันที่ผ่านมา

    We need standing together tisalekelele

  • @HendersonKanyada
    @HendersonKanyada 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂uyu size yake ndi fredo pa njawala sagafike

  • @AKMASEKO
    @AKMASEKO 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mfundotu apa palibe olo zitatani sangawine ndipo sadziwina

  • @madalitsomakawa9708
    @madalitsomakawa9708 วันที่ผ่านมา

    I like achimwene akuyankha pa mic po

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi unali nsonkhano wa home cell yanji

  • @andymasingajunior
    @andymasingajunior 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma Ndale zimachepetsa Kaganizidwe! All 18 and Malawians adzilembetsa opanda ID, masanje credible electro-process

  • @ShaibuMbwana-wv9nj
    @ShaibuMbwana-wv9nj 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amatiyo yes pansana pake koma Mbeweyo ali bho

  • @talandilabenedicto
    @talandilabenedicto 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe ukumayika dzimawu dzako dzokometserawe kakhale komaliza akaka kupanga zimenezi, ulendo wina udzawaleke ambewewo adzayankhule okha popanda wina osokosera.

    • @McdonaldSairo
      @McdonaldSairo 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndpo ndiye akusokoneza bwanj

    • @talandilabenedicto
      @talandilabenedicto 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@McdonaldSairo mwene, akundinyansatu kobasi uyuyu kkkk

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅 inuyo boss ndi one Mr mbewe

  • @pilirani3536
    @pilirani3536 วันที่ผ่านมา

    Mmm lnemani zomwe mudzapenge osati kuweluza azanu

  • @ibrahimchalimba5985
    @ibrahimchalimba5985 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi muli ku church kapena ku nsokhano??😂😂😂😂 A mbewe muuzeni commenter wanuyo asiye kut zizikoma than akupangazo😂 akasiyamo mwina muvoteledwa ndithu

  • @chiletsokazembe-ri4ic
    @chiletsokazembe-ri4ic วันที่ผ่านมา +1

    mesa inu ambewe ndinu aneneri bwanji osatiuza kut mulungu wakuyankhulani nkhani za ngozi ya ndege

  • @ShakiraJackson-x8w
    @ShakiraJackson-x8w วันที่ผ่านมา

    Malawi manvuto sa dzatha basi kuyambira mcp,dpp,utm,or udf sikuonapo apa amene angapulumutse mmawawiambewenso ndiye ayi

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe วันที่ผ่านมา +1

    abewa nanuso 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komaso anthu omwe ali mayiko akunja apezeleni yoti nawoso atha kuvota or alikunja komweko ife tikamava ndi momwe dziko likundela zimatiwawa kwambili timafuna boma ili likudzuza kwambili katundu wadhula kwambili ka ndalama komwe timatuzila abale athu sizikutheka kamba kodula zinthu mu dziko lathu

  • @RobertSamuel-mr1fw
    @RobertSamuel-mr1fw 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chipanichi tachikonda kma iwe ukumatsatizira mawu ambewe usiye kundale ndikuchurch usiyanitse usapangeso

  • @MaryNgola
    @MaryNgola วันที่ผ่านมา

    Iyaaaa ukuyesa kumpingo kwako et,mpakana okometsera? Zankutu

  • @ChanceZambika
    @ChanceZambika 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkkk kmaa iwee

  • @DoniasKamwana-l7r
    @DoniasKamwana-l7r วันที่ผ่านมา

    Powerful

  • @AlexanderBilliat
    @AlexanderBilliat 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuyankhula mophuza kkkkkk

  • @RuthUnderson
    @RuthUnderson 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uyu akulankhula mosatana ndi ambeweyu akundisokoneza kuti mdimvele bwino bwino

    • @happiemwasomola703
      @happiemwasomola703 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Alowetsa church akulu ameneo koma zopanda plan zomwe wanenazo

  • @Nthambi-zg4nu
    @Nthambi-zg4nu วันที่ผ่านมา

    Anthu osiya za mulungu kuyamba ndale pali nzeru ?

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z วันที่ผ่านมา

      Palibe nzeru akulu akufuna kuba basi

  • @ChimwemweRajab
    @ChimwemweRajab วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk makwana bwana😅

  • @christopherchikankhen
    @christopherchikankhen วันที่ผ่านมา

    Zaziiii

  • @AustinSaidi
    @AustinSaidi วันที่ผ่านมา

    Akuyesa ali pa guwa.

  • @lindadzaoneni
    @lindadzaoneni วันที่ผ่านมา

    Aaaaa inu mukuikira mang'ombe mwayesa muli mu church? Tamusiyeni President ayankhule opanda mang'ombe anuwo.😅

    • @MCAnthonyNdau
      @MCAnthonyNdau วันที่ผ่านมา

      Koma inu etini

    • @AustinSaidi
      @AustinSaidi วันที่ผ่านมา

      Akuti zimzimveka mwauzimu kkkkk

  • @MCAnthonyNdau
    @MCAnthonyNdau วันที่ผ่านมา

    Kumsonkhonso mpaka omasulila ngati kuchurch

    • @AustinSaidi
      @AustinSaidi วันที่ผ่านมา

      Wayesa ali pa guwa kkkkkk

  • @DamianoGabriel-sh2mf
    @DamianoGabriel-sh2mf วันที่ผ่านมา

    Koma inu mulimba mtima mungawine 50+ 1 koma ndale pena mmm

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z วันที่ผ่านมา

      Kkkkkkkkkk

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 วันที่ผ่านมา

    Za ziiiiii

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma uyu wabwera

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t วันที่ผ่านมา

    Zoonadi Mr Mbewe timasuleni ife Amalawi musingazamotozi tikuvutika Malawi 🇲🇼 waonongeka

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh วันที่ผ่านมา

    Ndisaikepo comment kma 😅😅😅