MGWILIZANO WA DPP UTM UDF KOMASO AFORD WANUNKHIRA KU KONVESHONI YA DPP

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 133

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 2 หลายเดือนก่อน +21

    🙏plz apm gwilanani manja atupele plz ombolani dzikoli mai p kaliati chotseni chekwera achihana plz atambo chonde amalawi azikhalira kuthawi moyenda coz uyu chakwera

  • @JustinWBanda
    @JustinWBanda 2 หลายเดือนก่อน +12

    Ndipo ngati zili Chocho mulungu adalise kwambili🙏🙏🙏🙏🙏

  • @MaryNgwira-s5z
    @MaryNgwira-s5z 2 หลายเดือนก่อน +7

    Chilima bwezi ali moyo achinkhla kuti ali ku Dpp Peter ali ndi umunthu

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 2 หลายเดือนก่อน +7

    We want national unity of political parties. Thanks a lot

  • @abeckbanda846
    @abeckbanda846 2 หลายเดือนก่อน +7

    ❤❤❤❤❤❤ tiyeni tiyendeleni limodzi UTM UDF AFORD and DPP Tiyeni tyendele limodzi

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน +10

    Ndipo mulungu atikomele m,tima abale tikungopepha kuti mulungu atichotsele zikhanilazi tatopa ndi chikangawa party

    • @GospelSoldiers-sr7np
      @GospelSoldiers-sr7np 2 หลายเดือนก่อน +1

      Mulungu wathu ndiwamoyo amamvatu kulira kwa Amalawi

    • @lastonmasoatenganji-bs5gf
      @lastonmasoatenganji-bs5gf 2 หลายเดือนก่อน +1

      Amen 🙏

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 2 หลายเดือนก่อน

      @@GospelSoldiers-sr7np kulilakwiratu dzina la Mulungu bwana kundaletu kulibe uzimu chonde ganiza mwaulemu pamaso pambuye

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mukunya chakwera bomaaa ndiyekuti 50+1 Palibe chakwera saona satutumuka akuumbuzani sizoyesa

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 2 หลายเดือนก่อน +2

    Game Changer I salute you Brother

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 หลายเดือนก่อน +2

    Exactly this is president of malawi well respected man Dr Peter muthalika true man muthu osapha muthu olemekeza omoyo wamuthu

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli 2 หลายเดือนก่อน +4

    More 🔥🔥🔥💯 gwirizano

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 2 หลายเดือนก่อน +6

    Gwirizano umenewo ulibwino kobas talila kokwanila iyaaaa

  • @AgnessMita
    @AgnessMita 2 หลายเดือนก่อน +1

    My vote

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน +7

    Ndipo uku ndiye kubwera Dpp apa yanyamuka waboma uyu

  • @OmexMainala
    @OmexMainala 2 หลายเดือนก่อน +1

    More fire more fire ❤❤❤❤❤❤❤

  • @damianokachingwe3531
    @damianokachingwe3531 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zachamba basi mmesa ndi dpp ikungofuna kugwiritsa zipan zinazi by the end big problem will come

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 2 หลายเดือนก่อน

      Bola MCP itachokabe Bas

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 2 หลายเดือนก่อน

      @@EmmanuelNtago ukunamatu iweyo pitala walephera ngakhale kupanga hold convention kulephera kudzayankhula pomaliza chifukwa chokalamba ndie angayendetse dziko ameneyo

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 2 หลายเดือนก่อน

    Ndakunyadirani.🎉❤🎉❤

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma iwe game change ndiwe mbuzi yamunthu zaziii palibe chimene tikumvapo apo peter sitikumufuna bora anali munthu wina mukufuna tizayambeso kukhala pakhomo 6oclock chifukwa chwopa zigawenga zanuzo inuso ndinu munapha chilima mukunamizira mcp muganiza kuti sitikuziwa kuti panayenda ndale agalu inu

    • @ChristopherKawilam
      @ChristopherKawilam 2 หลายเดือนก่อน

      Mmmmmm inuso ndinu abodzaso bwanji nde ngat ndi DPP bwanji kubwela ma report a kugwa Kwa ndege ( sometimes you need to close your mouth and open your eyes )

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 2 หลายเดือนก่อน +2

    My vote❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ DPP

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t 2 หลายเดือนก่อน +4

    Inde MCP yizipita kwawo even ,ppls party ,asale Okhla amcp ,atiphera chilima azipita azikavina gule

  • @ChejaliChirwa
    @ChejaliChirwa 2 หลายเดือนก่อน +2

    💙 My vote

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 หลายเดือนก่อน +1

    Palibe chomwe mungawine anthu asankho inu ziko pano likuyenda bwino ,kusinthasintha ma president sikutithandiza chifukwa peter ndiwokalamba apanga chani

  • @PeterKaiya
    @PeterKaiya 2 หลายเดือนก่อน

    Apm my vote

  • @DavieKalonga-y5j
    @DavieKalonga-y5j 2 หลายเดือนก่อน +1

    My vote Dpo

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 หลายเดือนก่อน

    Game changer ing'alure ❤

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 2 หลายเดือนก่อน +1

    Dpp wooooooooooo

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 หลายเดือนก่อน +6

    UDF DPP UTM AFORD kungotheka mcp izathera pomwepo ndithu 😂😂😂

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 หลายเดือนก่อน +3

    Kokolilikoyo adzipita nthawi yake idapita ndi mtsamunda mzake uja samatha chichewa kamuzu ..inu sinthawi ya makhadi ayi chikangawa next year azikayimba ng.oma kudambwe zikhare /chimwendo adzikavina

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 หลายเดือนก่อน +1

    My vote Dppppppppppppppppppppppppppppp

  • @MackstarAbinala
    @MackstarAbinala 2 หลายเดือนก่อน

    Yes

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 2 หลายเดือนก่อน

    💪💪💪💪💯 kwayaka moto🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera nambala wani,kulalika nambala wani,umbava nambala wani,chigololo nambala wani I, Chikangawa forest Chakwera woyeeeee wakupha wakupha aa

  • @DerickZiba
    @DerickZiba 2 หลายเดือนก่อน

    Compliments Malawi

  • @ArthurTerrison-xp7ir
    @ArthurTerrison-xp7ir 2 หลายเดือนก่อน

    Dppppppppp woyeeeeeeeeeee

  • @StainDandize
    @StainDandize 2 หลายเดือนก่อน +1

    ❤❤

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 2 หลายเดือนก่อน +1

    DPP woyeeeee, Peter mutharika woyeeeee

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 2 หลายเดือนก่อน +2

    Gemucheja udziweichi utm sikupanga naozagwilizano umeneo chilima adatiphanyila phanje tikupita kuchisankho tokha zimenezo udziuza audf omweo

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 2 หลายเดือนก่อน +1

      Kma simungawine

    • @AishaChibwana-b8o
      @AishaChibwana-b8o 2 หลายเดือนก่อน +1

      Aaa akudziwa ndi Mulungu zowinazo koma ife gogoyu ayi sitikupanga nawo

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@AishaChibwana-b8oineso ndikudana ndi gogoyo coz sangalole kut pule akhale wa utm amakakamila pampando ife tikufuna president wa utm basi

  • @ChikuMega
    @ChikuMega 2 หลายเดือนก่อน +1

    Guys gwilanani manja bas tigwese athu akuphawa ambuye azikudalisan

  • @BakaliYassin
    @BakaliYassin 2 หลายเดือนก่อน

    ❤ exactly kulakhura kwabwino respect

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 2 หลายเดือนก่อน

    More fire morefire😊

  • @Hamzamabvuto
    @Hamzamabvuto 2 หลายเดือนก่อน

    This is so amazing

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 2 หลายเดือนก่อน +1

    Massive alliance ever

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 2 หลายเดือนก่อน

    🙏🙏🙏🙏🍊🍊

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu amakonda munthu wodzichepetsa, Mulungu lowereraniponi ndithu musalore satana apambane, tichitireni chifundo anthu talapa tinasankha molephera ti khululukireni Mulungu tithandizeni kutisankhira Atsogoleri amene adzawombole dziko lathu la malawi

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 2 หลายเดือนก่อน

    Congratulations Mr game changer

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 หลายเดือนก่อน

    UTM and AFFORD musamadzaliretu mtsogolo muno ayi kumatulutsa tizizungu twanu takuti GENTLEMANS AGREEMENT. Chifukwatu a Lomwe onsewa akuti tiombere dziko kuti akunena zoona ayi AKUTHAUZA KUTI BWERANI MUTIOMBOLE KU OPPOSITION KUNO KULIBE MIGODI NGATI MMENE ANAYANKHULIRIRA CHAPONDA CHIFUKWA AKUTI MIGODI ILI MBOMA.

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 2 หลายเดือนก่อน

    ADAD 2025

  • @ChikondiSabe
    @ChikondiSabe 2 หลายเดือนก่อน +1

    Enanu museguka mimba ndinthu kkk chikangawo achoke basi

  • @SavicoJastin-vj7pt
    @SavicoJastin-vj7pt 2 หลายเดือนก่อน

    Tikunyadirani ifeeeeee

  • @SheiraChilaya
    @SheiraChilaya 2 หลายเดือนก่อน

    Atuluseni mcp apiteso kuholiday

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 หลายเดือนก่อน

    A UDF ndiye anatha kale kale alibe kolowera.

  • @AubreyWilson-j8w
    @AubreyWilson-j8w 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo mukagwirizane zoti report la ndege lituke osainva

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 หลายเดือนก่อน

    Gwirizanani guys muchose chipani chakupha .udf,aford ,utm ndi dpp chonde gwirizanani.Apm wakula kale adzakusiyiran .chachikulu mwachosa chipani chamagazi kuti malawi awomboledwe

  • @TrinityMaloko
    @TrinityMaloko 2 หลายเดือนก่อน

    Tazikonda ife zimenez alemekezeke mbuye shiver

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 2 หลายเดือนก่อน +2

    ADAD OMWEWOOOOO!!! KUMENEKO NDIYE KUBERAAÀA!!! I INENSO NDIKAKHALA NAWO KONKOOOOOO!!!!

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ineso ndili wosangalala kwambili zo tupere thawi yake maso kusongolo ndi adadi mulungu akudalisene moyo wako nose inshall allah tiyangidwa ziteka komaso mcp ekschoka boma xs bas mapa kare wosaziwonaso

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 หลายเดือนก่อน

    A Malawi takhalani serious peter mene wakalambila paja akhalenso nsogoleli ,munthu wafika stage yoziyipsira yekha angakhale nsogoleri

  • @DonnieKamenya
    @DonnieKamenya 2 หลายเดือนก่อน

    MCP 2025,Bomaaaaaaa!
    Mulungu adalitse Malawi.

  • @KaliyapaSeeter
    @KaliyapaSeeter 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ok tanva❤

  • @GotepoBanda
    @GotepoBanda 2 หลายเดือนก่อน

    Umatimilila aise pitiliza kutiuza ase more fire peter

  • @christopherchikankhen
    @christopherchikankhen 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ubwino Wake chisankho nchamuntina mwaekha

  • @michaelmvula134
    @michaelmvula134 2 หลายเดือนก่อน

    Zipani ziphatikizana potengera kuchuluka kwa mavoti omwe wotsogola adzapeze. Kwapafupi kuphatikizanso zoluza zonse pamoza kapena otsogola ndi ena oluza. 17th September, 2025 will devide Winners from losers.

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 หลายเดือนก่อน

    Alliance ndiyimeneyo tiyen tipange koma peter asakhaletu president nayeso ngwatsakho peter mmmmm bola utm

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwela adulidwa 2025😂😂😂😂galu wa pusident 😂😂😂

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza 2 หลายเดือนก่อน

    Zomwe timayembekeza ndi zomwezo tiyeni amalawi tikavote mwaunyinji tikachose nyasi izi zamagazi

  • @SuzgoDhlamini
    @SuzgoDhlamini 2 หลายเดือนก่อน

    More fire🎉

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 2 หลายเดือนก่อน

    Ndipo Akapanga zachibwana game chang'r mwamalize akutinyasa kwabasi a mcp tikukhala mosamasuka ife muziko mwathu

  • @NtchindiChirwa-l8o
    @NtchindiChirwa-l8o 2 หลายเดือนก่อน

    Mwachita bwino kuphatikizana tikumenyeren limodzi

  • @BoscoKalua
    @BoscoKalua 2 หลายเดือนก่อน +1

    Tikuwonga kukhala pamoza vipani vyose vya kususka boma ivyo mukorerana mu unenesko ise nase TIKORERERANA NAVYO kwa THUNTHU----mu UMODZI MULI MPHAMVU

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza 2 หลายเดือนก่อน

    Tithokoze atsogoleri onse amane mwachita mngwirizano umenewo tiyeni tichose achakwera ife timagwira ntchito ndi manja athu osat kudalira ngongore

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t 2 หลายเดือนก่อน +2

    Ndipo takondwa ,atiwombole mu Ng,anjo ya moto, MCP olo yipange Makani yipta kwawo ndithu

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 2 หลายเดือนก่อน

      Kutereko sudalime ndi khobwe yenwe kumati dpp ikuombole ukuona ngt adzakupatsa ndalama

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 หลายเดือนก่อน

    Nde atasogolele gululi ndindani poti peter zintchito zake tinaziona kale mwina muyikepo atupere ndi amene asogole

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 หลายเดือนก่อน

    Ali ndimoyo oziwa mavuto amalawi mulungu azimudalitsa Dr Peter muthalika

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 2 หลายเดือนก่อน +1

    My vooooooote

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 หลายเดือนก่อน

    Zikomo big man ulemu

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli 2 หลายเดือนก่อน +1

    Pangani ngwirizano plz😭😭😭 plz

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 หลายเดือนก่อน

    Mgwirizano uwu ndiomwe ungachonse chipani chamagazi chakupha cha mcp.

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 หลายเดือนก่อน

    Thwerenyenye ❤

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 2 หลายเดือนก่อน

    Tiomboleni pa moto uwu wa MCP chifukwa tikupsa ndithu

  • @AnnieBanda-rb2dk
    @AnnieBanda-rb2dk 2 หลายเดือนก่อน +1

    Please tiyeni titelo abale chikangawa chakwera watitopesa abale

  • @PraiseMasinga
    @PraiseMasinga 2 หลายเดือนก่อน

    Zilibwino kwambiri tatopa tinakhuta nsima ndi kale tinamwa tea ndi kale

  • @RemaniNkhoma
    @RemaniNkhoma 2 หลายเดือนก่อน +1

    chipani cha chakwera chaka cha 2025 apitaso kumbwe kukavinidwa

  • @luciarashid1961
    @luciarashid1961 2 หลายเดือนก่อน

    ❤🔥🔥🔥🔥

  • @thulambale2836
    @thulambale2836 2 หลายเดือนก่อน

    Zitsiru angale a afford ngati angapange mugwilizano ndi a galu awa a DPP

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko 2 หลายเดือนก่อน +1

    Apita mwaganiza bwino pangani uchamuna sinthani dziko

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 2 หลายเดือนก่อน

      Koma apitawo pulizi alliance yi asakhaletu president 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @sarahmphande6108
    @sarahmphande6108 2 หลายเดือนก่อน

    If it like this atleast malawi will be restored from those nfwit

  • @dounderamanda530
    @dounderamanda530 2 หลายเดือนก่อน

    💥💥💥💥

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 2 หลายเดือนก่อน

    Koma zinazi zaziiii ndiye mukuganiza kutsina mutsogoleri ndiko kusintha ziko palibe chimene mukulankhura ndipo kungoti azipani zinawo ndiwo nzeru alibe nanga konivechoni yanu ndiye enawa akapangaku chani zaziii amalawi ake ati naweso iwe tatiye uko ukuti chakupha nayesa iweyo ndiwe wadura anthu ziwaro malubino mwatha azimayi kuchosa mabele anthu kwapopa magazi zaziiii kuphako siyani ndipo dpp ndiyo yinawomba theki muluzi kuti chipani cha udf chithe kumanga bakili muluzi ndiye mutiwuza chani njoka ndinjoka singasinthe mawanga wanachosedwa peter palibe chimene anali kuchita pamene inuyo ndinu mulindimagazi ngamalubino mumalawi muno zaziiii

    • @ChristopherKawilam
      @ChristopherKawilam 2 หลายเดือนก่อน

      So if you said That kusintha president that can not change anything so why DPP munayi chosa m'boma???

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 หลายเดือนก่อน

    Exactly white man

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 หลายเดือนก่อน

    Tikuyamika kwambiri fundo yimeneyi, MCP yichoke basi a Malawi sitikuifuna.

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 2 หลายเดือนก่อน

    Nkhululu

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 2 หลายเดือนก่อน

    Ngat zili chomwechi zilibwino mcp isuthepo eish tapanga zithu amalawi

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 2 หลายเดือนก่อน

    MCP Isegulatu m'mimba apa. 😂😂

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 หลายเดือนก่อน

    A utm plz musalole kut pule akhale adadie muononga chipani akulawo awo ngat zilizimenezo pule achokere ku utm basi muzingowalowetsa azanu pampando zoona inu a utm ayi

  • @FlorenceNkhata-f5l
    @FlorenceNkhata-f5l 2 หลายเดือนก่อน

    Tikufuna mgwirizano ndi zipani zimezo zingati Khalre bwino kwambiri

  • @osmanwanja3733
    @osmanwanja3733 2 หลายเดือนก่อน

    Mcp iwezeka chaka chamawa amvanyekwe

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 หลายเดือนก่อน

    Amenewo akulalatayo wadya ndalama ameneyo moti polalata kwakeko ndalama zikulowa pamenepo,,a Malawi chenjelani

  • @Sofi-p1v
    @Sofi-p1v 2 หลายเดือนก่อน

    Zathapo basi

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 หลายเดือนก่อน

    Chonde pangani zomwezo zamugwirizano tatopa ndi MCP palibe chomwe yikupanga zinangobwera kuzangowononga

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 หลายเดือนก่อน

    Valema wanthu na chikangawa ngeyingafumapo waka mwahuno

  • @MustafaMtuma-un4jc
    @MustafaMtuma-un4jc 2 หลายเดือนก่อน

    Mumantha bro timakudyadilani