Zomwe ukukambazo JB ndizoona zenizeni ndipo boma likanati liziganiza ngati chonchi bwenzi zinthu zikuyensa bwino anthu ena chomwebamafuna ndi chakudya cha siku ndi siku big up JB
......akuluwa zaonekeratu kuti kwa iwowa kusowa kwa fuel nkoyamba mu Malawi. Have you forgotten kuti even nthawi ya Bingu fuel anazasowapo country wide? Ana okulira mu social media awa!!!
Zomwe ukukambazo JB ndizoona zenizeni ndipo boma likanati liziganiza ngati chonchi bwenzi zinthu zikuyensa bwino anthu ena chomwebamafuna ndi chakudya cha siku ndi siku big up JB
Facts comrade
JB ndi munthu wokonda ziko lache ngakhale ali ku America amakonda a malawi amayankhulira mavuto alikunowa.
Chakwera ndi Anyamata ake anali busy kugawa njinga za kabaza anapanga plan yokut ndalama zogulira fuel azikhalire pamodzi ndi azikhale ng'goma
An iron sharpens an Iron. Salute JB
JB ndimafuna titayankhulana mwapaderadera...ndingapange bwanj kut nditero
Wisdom in those words
Consumption of social media information requires a critical mind as there is much that qualifies for the trashcan. There is an example in this clip.
......akuluwa zaonekeratu kuti kwa iwowa kusowa kwa fuel nkoyamba mu Malawi. Have you forgotten kuti even nthawi ya Bingu fuel anazasowapo country wide? Ana okulira mu social media awa!!!
Zikumvekatu koma
Izi ndi zoona ku malawi anthu akuvutika kwambiri fuel kulibe ndiposo kulinjala feteleza audulitsa zinthu zonse zadula
Umakwana JB
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
Kwanuko kuilbe koma ife tikugula panopa
JB tell them chikangawa samava
Chitsiru ichi osamaola tudzwi togaluto ku mene umakhalako.
Tell them JB
Zooona zokhazokha 💔💔💔
Mumakwana inuyo JB
Kambisisa amve
Koma jb
Chilungamo choka choka
c
Mboli yako
JB sanakambemo zakhondo or zofuna kupha muthu usilu et
Mumvesele bwino bwino mumva wanena kuti akufuna atafinya winawake
Simukulakwisa Braz Chakwela Mapwala ake