Koma funso ndilakuti iyeyo samamuyhandiza skc ku ma mavuto monga ku court komanso atamva kuti chilima wasowa mpaka kumveka kuti wamwalila bwanji iyeyo sizinamukhuze, and chiyambileni mwiniwake chilimayo sitinamuone akupanga misonkhano ndikuona makaka a MCP ndi UTM ali limodzi
Ma interview onse a usi ndisaname sandisangalatsa chifukwa samayankha mafuso omwe akusidwa amangothawathawa zomwe zimakayikitsa anthu kut adziwapo kanthu
Kumakhala ndi chilungamo
Koma funso ndilakuti iyeyo samamuyhandiza skc ku ma mavuto monga ku court komanso atamva kuti chilima wasowa mpaka kumveka kuti wamwalila bwanji iyeyo sizinamukhuze, and chiyambileni mwiniwake chilimayo sitinamuone akupanga misonkhano ndikuona makaka a MCP ndi UTM ali limodzi
Tsatana uyou manganya oipa
Manganya mutu wake sumagwira,munthuyu ndiwa ma comedy