ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Pastor ndiwe musilikali wamulungu ngati David may God give you more power
Keep it up brother chiyambi chazeru ndikuwopa mulungu,,komaso muchenjele bro satana ndi onyenga
You overcome the world pastor glory be to God.
Powerful Jesus ❤
Ambuye akule popeza Ali moyo
Izizi sizamapempelo zachamba basi azimayi okhaokha koma kutengeka azimayi akadakhapa nonse
😂😂😂😂😂 inu mpaka kutema iyaaa mukupanga busness
Kumapemphelo mumapita ndazikazathu okha okha mamuna iwe wekha.. Muzafa
Amen satana ndiolephera muchilichonse
😂😂😂😂Ndeazimai okhaokha?
😂😂😂😂😂😂 ankayesa muli ma sauzande mu chakhumi mpaka kulolela kufuna kuluza moyo
Amen munthu wamulungu
Ukalandira vumbulutso Mulungu amakhala kuti akuchenjeza, apa abusawa samayeneranso kupita kuphiriko coz anauzidwa kuti akachitidwa chipongwe
Koma mulungu Nd wadongosolo
Munyanya azibusa kod mapephelo anji opita azimai onkha onkha ndi atsikana 😅😅😅 mandidabwitsa bwanji panakakhala anyamata alipo sibwez zitachitika ataa
Amen and Amen
Aaa atengeso tithe apapokha sindilora😂
Amen
awa sabusa aaaaa
Zachamba bas
Ndiye kuti azibambo kunalibe kkkk chopitira ku phili ndi chani mulungu amakhala ku phili za u here basi
Ndiye pokhala prophet mukundiwuza kuti kufikira lero Mulungu sanakumvumbulutsireni kuti masiku ano si masiku otorera chachikhumi?
Kkkkk afusen
😂😂😂😂😂 mphamvu ya mulungu kumuuza munthu kuti ateme nzake?
Davite anapha goliati mesa mphavu yake inali ya mulungu yomweyo
Mboro 😂
😂aaaaaaah sizautumikinso izizi shut up .ngati zilichoncho aliyense akhalatu prophet thupi lathuli naturally limatha kututumuka ngati pali chilichonse chotutumusa.
😂😂😂😂😂😂😅
😂zauhule
Pachakhumi chokha m,busa sangalole kutengedwa,nanga chikatengedwa akadya chani,
Kkkkkk koma abale
Mmmmm
Kkk koma chakhumichi akadakhala Kuti sanatenge athuwa sakadakhapana ndithu Masiku otsiliza kudzadzuka azitumiki onyenga osatengeka
X
😂 azimai a eniwakewo stupid