MAI MUMBA WHY? ~ LERO KHOTI LAMALIZA KUWELUZA MLANDU WA MAI MUMBA UJA ~ NDIPO KHOTI LAGAMULA IZI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 30 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 138

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    I love the way u have connected with Jaki show ..

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Tikudikila mlandu wa minister Kunkuyus' assistant wopha witka.

  • @YusufAjida-t8r
    @YusufAjida-t8r 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Mlandu umenewo waveka kwa bas nanga chikangawa akhakala zaka zingati kundende

  • @khadjahmustafa365
    @khadjahmustafa365 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ali ndi zaka. Zingat mmaiyu anthuni

  • @LivielMabvuto
    @LivielMabvuto ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmm izizi Nde kukwanitsa kugamula Koma za ndale ndekulephera

  • @GraceMwene
    @GraceMwene 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Kutheka sanaphe ndi iwo koma zinangolakwika kuti sanasate dongosolo la bwkno

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Azimai tengeranipo phunziro munakukamo. Mulipo gulu koma kusagwidwaaa😅

  • @PatriciaChikusa
    @PatriciaChikusa ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmm mayi ameneyu ndi satana oyenda ndimapazi

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Mai woipa uyu mmmmm

  • @charleskazembe5728
    @charleskazembe5728 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbuzi yamzimayi

  • @MacJohn-e3i
    @MacJohn-e3i 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ayi akadye nyemba dora imeneyo sadyanso

  • @ELLENKANJERE
    @ELLENKANJERE 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmm uyoyo afwele koko

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Judge wa nzeru azimai adyera

  • @WilfredMatebule
    @WilfredMatebule ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mungoyankhula moyowakundende simukuuziwa

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God is the right judge ,he will judge us fairly.

  • @KentWilliam-r2v
    @KentWilliam-r2v 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zosayenda R. I. P Mrs mumba ndinu oyipa kwambiri 😢😢😊😊

  • @kondwanidonald4711
    @kondwanidonald4711 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkk, thanks for the judgement....this is a really example to everyone.... GBV

  • @manasemaposa
    @manasemaposa 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Lord of mercy give her mercy let her found your salvation.

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    amuchita bwino, nkazi oyipa kwabasi aneneyi😢 enanso anzeru ngati zimenezi atengelepo phunziro😮

  • @LivielMabvuto
    @LivielMabvuto ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Apa mpakamwa ndalama zimutulusa paja sizimanamatu kumalawiko aaa

  • @WellsLikambale
    @WellsLikambale 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Achitabwino alipo azimayi ambiri opanga zimene ena aphuzirepo

  • @WysonAdamu
    @WysonAdamu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    awachita bwino sitikifuna majesibelo dziko

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Maiwa anadyesa Amina awo poison ndipo maiwa ndifiti

  • @jaffahbattirey3423
    @jaffahbattirey3423 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mumakwana

  • @KelvinNyirenda-v1y
    @KelvinNyirenda-v1y 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Yeyeye zooonanadi Atengelepo phuzilo akazi

  • @AdamMakala
    @AdamMakala 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkk mamabaja alelo

  • @victorkatekesa5049
    @victorkatekesa5049 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmmmm koma azimayi mumudziwe Yesu

  • @LovenessMagombo-t3c
    @LovenessMagombo-t3c 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chuma mpaka kuchotsa moyo wa amzanu? It's so bad

  • @MontfortMuhime-t6w
    @MontfortMuhime-t6w 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akatuluka ndalama zimupulumutsa

  • @IshmaelNgeyani
    @IshmaelNgeyani 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Azimayi ambiri amatero akaona mamuna wawo alindindalama amafuna adyeokha kuiwala kut maphunziro ake ndalama zimacokera kwamakolo RIp mai

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komano amaiwa azaombela okha pamwendo,munthu mamuna wako wamwalira chonyamukila siku lomwelo mkumapita ku town ndichani??amayenekela akhale ma week or mwezi kumene

  • @MaggieMkandawire-ki5mu
    @MaggieMkandawire-ki5mu 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Yes ndiolakwa

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mai uyu ndi hule akanamutchaja life in prison 53 years ndiyochepa kwambiri

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iiiii akhale komweko azikacheza nda anzawo akawapeza komweko, Mai wakupha 😮😮😮 ukalambila komweko uyisova

  • @RalphNoniwa
    @RalphNoniwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ena atengerepo phunzilo. Mzimayi oyopa.

  • @ChifuPoal
    @ChifuPoal 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Maiwa eee simunthu

  • @SaidiBaneti
    @SaidiBaneti 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iiiiiii koma akadzi 😢😢😢

  • @HamidavioletYassin
    @HamidavioletYassin 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    53 years kundende kulibe ma shop ndilamayo mukadyela kutiko

  • @esthermalixani2244
    @esthermalixani2244 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amuchita bwino coz ndimai oipa asatulukeso akafere komweko

  • @Chimsbojan
    @Chimsbojan 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kodi channel ichi ndi china mmapanga za Blenac?

  • @Otisi-t3y
    @Otisi-t3y 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Umbon waperekera ndanii Kono sizinachitikepo dzaka dzimenedzo

  • @SamsonKankhomba
    @SamsonKankhomba 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma apanga bwino kuti azimayi ena atengerepo phunziro

  • @DavieChamasowa-p1g
    @DavieChamasowa-p1g 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Uyu anapha munthu m'modzi, nanga Chikangawa anapha anthu 9. Amugamula zingati?

    • @UssenNjirinah
      @UssenNjirinah 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkkkk koma yaaaa

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Iwe chisilu bwanji.... Inali ngozi imene ija... Are they the first to die on a plane crush😮

  • @SophieLupiya
    @SophieLupiya ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmm

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani yamai mumba yikufanana ndiyachilima ndichifukwa chani presdent analetsa anthu kufufuza ndege itasowa.kwa usikuonse .komanso ndege yinafika kumzuzu koma anaibweza.chakwera nayenso akuyenera kukakhala kundende zaka 100 chifukwa anafa ndi anthi 9

  • @VincentNyabanga-dw9uj
    @VincentNyabanga-dw9uj 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azimayi amabelekedwa hvy Men always die silent, life in prison,

  • @ChristopherSekantole
    @ChristopherSekantole 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mai oipa kwambiri

  • @CharityMkandawire-t8u
    @CharityMkandawire-t8u 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nde kupita kundende ndalamaso osazidya chaphindu ndi chani Mai opusa

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndalama ndi satana..mai oyipa

  • @ThialingsonChiphwanya
    @ThialingsonChiphwanya 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ause mu mtender basi .
    winaso ndi uyu wangit zori ngat sakumva chinsecho akukonzekera kupanga zomwezo

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Sizikusiyana ndi kufa kwa anthu 9 mundege 50 50 zikufanana a boma nawonso akukhudzidwa nawo pa kunyalanyaza kusaka ndege ndi mabodza ochuluka kuuza dziko.

  • @lucksonmoonga4426
    @lucksonmoonga4426 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Afufuzidwa mokwanila.anatengapo mbali pa ifa ya amuna awo.

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    R.I.P mayi oipa iwe!!!!

  • @Edward-t2z
    @Edward-t2z 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akaseweze basi

  • @patrickscott9086
    @patrickscott9086 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azimay kufuna kusala nd chuma 😢😢😢😢😢😢😢😢 mwawophysa

    • @LeonardBlair-mq6be
      @LeonardBlair-mq6be 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      yap azimayi Ofuna kusala ndi chuma ngati zomwe amapanga azimai apa jon

  • @VicentMalopa
    @VicentMalopa 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    My Fellow Classmate 😢

  • @madalokantchewa7703
    @madalokantchewa7703 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Abambo enaake mbali zakuno anakhala kundende ogwiririra mwana wakwaneba atamupasa lift kukubwera mvula chosecho anali akuchoka kuchibwezi.atuluka ku ndende after kuti msikanayo sakubereka kubanja zinthu sizikuyenda atapita kumapemphero namuuza kuti aakaatuluse abambowo akapepese kubanja lonse .but abambowo anakula due for retirement kutuluka mbiri inaipa sanamugwirilire koma mwana amkaopa makolo ake. Nde zina zimakhala zobvuta
    Koma maiwa ngati adapanga izozo nde mnzamanyazi ena atengerepo.phunziro

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Eeeeh zovuta

  • @HarryMsyamboza
    @HarryMsyamboza 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mumafotokozeela bwino kwambili pa nkhani zonwe mmalankhula zimanveka bwino kwambili

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ma judge ake achinyengowa aaaaa alandira ndalama atulutsa

  • @StellaChimesya
    @StellaChimesya 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ena atengerepo phunziro azimai akumipanda plz tengani phunziro apa

  • @DavieNgauma
    @DavieNgauma 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😢😢

  • @LawrenceNguluwe
    @LawrenceNguluwe 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Walandila malipilo

  • @WisdomThupa
    @WisdomThupa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    So sad

  • @ChifuniroChintengo
    @ChifuniroChintengo 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amayi achipongwe awa,eti kumasekelera

  • @BrandinaMphuka
    @BrandinaMphuka 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mayi oyipa kwambiri chumacho akadyera kundendeko

  • @OjesYahaya-g4w
    @OjesYahaya-g4w 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akabwelako posachedwa zaka zamasiku ano ndizafonkongo

  • @TamalaMwamlima-gk5im
    @TamalaMwamlima-gk5im 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amai mukafera kundende shame on you mama chuma chako ukagwira ntchito ndiwe

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    KHANIYI MKAIMVESERA BWINO IKUNGOFANANA NDIYACHILIMA , NGAT MAYIWA ATAMANGIDWE , CHAKWERASO AMANGIDWE, CHIFUKWA NAYESO ADAUDZIDWA CHAMA 10 KOLOKO KUTI NDEGE YASOWA KOMA ANTHU ADAYAMBA KUMAKASAKA 4 KOLOKO , ZONGOONESA KUTI CHAKWERA ADAPHA CHILIMA ,CHAKWERA AKHALE KUNDENDE ZAKA 63

  • @AliceJere-k9v
    @AliceJere-k9v 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Much as the court has passed its judgement...God will have to remain the overall judge in anyone's case. It might be true or false,,, Amayiwo n God are only true witnesses...Koma mwina ife sisaaweruze. Pajanso ku ndende kumapezeka Ena oti sanalakwe but they pleaded guilty before the court of law...

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Alipo ambiri azimayi akhalidwe lotere koma kusagwidwa.

  • @HabiboZimba
    @HabiboZimba 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mayi oipa uyuu

  • @FuloJakobo
    @FuloJakobo 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Hahaha ifende sitidzakuwnan

  • @FatimahJemes
    @FatimahJemes 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Heeee zovuta kwambiri

  • @billymkamanga6879
    @billymkamanga6879 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mulungu amuchitire chifundo! Not good

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zaka 53 life in prison imeneyo nanga musingu ali nawowo mmmm ndi life in prison,

  • @WevsoniGoliyat
    @WevsoniGoliyat 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Samakonda amuna awo

  • @MadalitsoSamuel
    @MadalitsoSamuel 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chigamulo chosangalasa ena atengerepo phunziro makhoti athu akugwira ntchito

  • @ModesterWilliam-g7z
    @ModesterWilliam-g7z 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Boma lake lomeneli

  • @DoncliffFrankKambwani-k4k
    @DoncliffFrankKambwani-k4k 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani ikumveka bwino adamupha ndi iyeyo mkaziyo.

  • @GraceJumbe-h6t
    @GraceJumbe-h6t 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Rest in peace dear brother akayankha awa

  • @MuhaShaibu-x5x
    @MuhaShaibu-x5x 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Eeee zaka 53 mmmm koma ndy eee

  • @SamisonLevison-z5p
    @SamisonLevison-z5p 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amuna samapha akazi awo Azimai bwanji?Banja sichibale musaphe mwana wa eni.Mukulakwa

  • @PeterWillard-o3d
    @PeterWillard-o3d 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akadyere ndalama komweko kkkkkkkk

  • @Esa-u3t
    @Esa-u3t 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    R.I.P Mai

  • @RollandChibambo
    @RollandChibambo 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    So painful and shameful

  • @SamwaJohn
    @SamwaJohn 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mai wachabe akafere koko

  • @RobertMalanda
    @RobertMalanda 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azimai okonda ndalama amatero

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwina anawapatsa poison Mai oyipa akuonekaso ngati oyembekezela

  • @thokozanindalama
    @thokozanindalama 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    mu mtima salowana zowona kukongola koma mtima woyipa

  • @JamboNdaona
    @JamboNdaona 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmmmm zosayendatu

  • @GelardMvula
    @GelardMvula 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    analakwitsa kwambili mayiwo

  • @JosephMuliya
    @JosephMuliya 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zilibwino

  • @DaauudHajj
    @DaauudHajj 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    chibwana

  • @PeterNgalauka
    @PeterNgalauka 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amenewo akayike prison yazibambo😅😅😅

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Cholinga chake chikhale chani? kkkkk

    • @PeterNgalauka
      @PeterNgalauka 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @bs-malawi akagwire ntchito yakalabvura gaga kkkkkk

  • @LimbaniKakhuta
    @LimbaniKakhuta 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God see even in darkness let her test pain

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Machimo

  • @YusufAliki
    @YusufAliki 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Rest in peace

  • @adammuhammad6898
    @adammuhammad6898 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zakazo zachepa ndi mayi oyipa uyu

  • @DorothySaidi
    @DorothySaidi 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kulakwa mwana wamzawo,mtima wanji azmai,ndalama basi

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkaz oyipisisa uyu amuchita bwno galu ameneyu