Inetu ndinamuona kale Khalidwe lake lomwe anaonesa asali resendent, ndinaziona kale ndiyedi akapitilira ndi Khalidwe lakeri Bola akhale nsongoleri wa achewa okha basi afune asafune asatitopese ayi ifeyo, ndikulephera kwakeko azidya misonkho ya achewa okha basi chifukwa akupanga zamanyi busa ameneyu
What ur saying it's true, dzino lino laola ndthu mmmm zomvesa chison malawitu ali pamoto, km mulungu akuona let them continue what the are doing misonz yanthu ambiri ikufika kumwamba mmmmm usogoleri wakanika wa achakwera oooooo
Iwe bon kalindo ndiwe amene unkalimbikisa nawo ma demo ochosa jane ansa kuti anathandizila kubela zisankho za 2019 lero usokoselapo chani apa ine nde ndatopa nawe asiye a opposition apange za maganizo awo.
Tinkangokuyang'anani mukuti ai bola atilamulire opemphelawa.....hmmm ife nkumati ngati munthu ali opemphera za genuine angakalowe chipani cha MCP? MCP ? Kulibe chi khristu ku MCP.... dambwe lokha lokha😢🤮
Iwe umati kulemera kumasintha munthu kumene ndinu nomwe munawayika agaluwa ndiye tikufuna inu nomwe muchitepo kanthu tikufunatu muyende malitseche ngati mmene munayendera nthawi ija kuti muwachonse anthu anuwi akutizuza ife a Born Kalindo chitaponi kanthu ndithu 👏
Ndipo live
Ndipo Bon asasambire mmanja opposition side iyeyo ndiyemwe analowetsa MCP m'boma nyapake
Kalindo,mtambo chilima ma judge, Judge Kenyatta George Phiri livingstonia synod ndi amene muchose Chakwera ndi MCP.
To my side l don't blame anyone l blame chilima he is the brought us to this situation poti munthu ukakhala pabwino poyipa pamakuyitana
Yeah chilima was bad guy for sure
Koma Chakwera ndi busad kapena ayi zikwanjezi abusa zoona 😭😭😭 Ambuye tipulumuseni atipha I fe ndinjala ndiumphawi komatso zikwanje
Zoonad Army nayo yapanga zoputsa kulephera kugwira ntchito yake dzulo yokhazikitsa Bata pothamangitsa a MCP❤❤❤
Ndipo athu awaa mulungu awaka thee ndithu athu oipa ntima mgati manyi akamwazi akundi nyasa sana me mm😊
Chilima anatiputira nkhondo 😢😢
Biyeni munatilakwira
Inetu ndinamuona kale Khalidwe lake lomwe anaonesa asali resendent, ndinaziona kale ndiyedi akapitilira ndi Khalidwe lakeri Bola akhale nsongoleri wa achewa okha basi afune asafune asatitopese ayi ifeyo, ndikulephera kwakeko azidya misonkho ya achewa okha basi chifukwa akupanga zamanyi busa ameneyu
Mau mau Bon kalindo
Muma yesesa the Dcc ❤❤❤😊
Ine ndimaganiza kuti tikamapita kumademo nafe tizitenga zikwanje
Olakwa ndine kubadwira ku Malawi 🇲🇼
Kkkkkkkk
😂😂😂😂😂 ayo ineee
MwalirAtu bwana Winiko
Lero amzanu akukubwezerani zanu zija
Ambuye tipulumuseni Ife Ana Anu😢😢😢😢😢😢
Tangoganizani kuti mmaiko ena akamamvera zomwe zuchitikazi,...akumati chani... Malawi on fire 🔥🔥🔥
Sakudabwatu,,mmesa anavotera nkhondo ya Israel ndiye akadabwe nzikwanje zija?????
Mkulu wa mec ifa ikumusata mukhulupilile mau anga
Waona bwanji ase
live
Iwe ndi one❤
Thanks my dc
Amenewo mawu tiona ngati alamulile
Kip on resting in peace Biyeni 😭😭
Ine sindingakalembetse kalembera zikundinyasa kwambiri
What ur saying it's true, dzino lino laola ndthu mmmm zomvesa chison malawitu ali pamoto, km mulungu akuona let them continue what the are doing misonz yanthu ambiri ikufika kumwamba mmmmm usogoleri wakanika wa achakwera oooooo
MALAWI NDI DZIKO LOMVETSA CHISONI
DZIKO LOONEKA NGATI LILIBE MTSOGOLERI
DZIKO LOONEKA NGATI LILIBE APOLISI
DZIKO LOONEKA NGATI LILIBE A AMY
KUMATHAMANGITSA ANTHU NDI ZIKWANJE APOLISI ALI POMPO
KOMA NDIYE NDI UTSOGOLERI ODABWITSATU
The DC'S mwana woooopsa kwambiri
Ndipo atiphatu agalu amenewa khadzuladi iwe bon tikumvatu kuwawa dziko lathu lomwe 😭😭
Vuto si Chakwela ayi opposition ndi yongona inuyo sumungakwanise kutenga zikwanje zipani zonse mpaka kuchita matha ndi anthu ochepa ngati amenewo
Kmatu zoona zake vwana❤❤❤
Kma wagona lero THE DC yu???? Mmmh kma yah Zinthu zaipaa
Ambuye wina Ali yense wa m cp amene ananyamula chikwanje m'manja mwake mumukanthe
Ine pa nkhan zonsez AMENE ndimamuda NDI chilima.
Chifukwa cha nsanje ndi kusakhutitsidwa Kwa chilima ndikomwe kwabala zonsez
Ndiye anthu mukamamuchemererabe chilima ndimaona ngat njokayo mukumenya Ku mchira
Ndi chifukwa azitsogoleri opumao angokhala chete
Paja mumkati dziko ndilachinyamata.
Hamimu Jali Machinga
Stupid Government
Iwe bon ndi mzako mtambo ndinu amane munatiika mu silempani ya mafuta owilawa nde tichotseni chonde
Tichoseni pa moto mulungu tawonani ana anu tikulira
Ndizoona pang'no pang'no iyi ndikhondo
Good kuyangula monfeka bwino bwino chifukwa chilungamo ndichopoteka namachende ameneyu akufuna kuphesa amalawi mboli yake chakwela galu
Tinyamulanso zikwanje mwaiwara ma cadet.
Bvutonso ndiiweyo kalindo ndiye u must fight for it coz yr the one u put chakwela president
Pepho lathu a Bon Kalindo inu ndi timu yanu yomwe inkapanga mademo nthawi ya Peter Munthalika kuti achokepa mpando panganisoni chimodzimodzi kuti chikangawayi achoke. Chifukwa anthufe tikuzuzika ndithu boss.
Mcp 🙌🏿🙌🏿
Kma kalindo ndiwamwano chikangawa kuthamanga kuposa chinyawu pa ma demo mmmmm
Kkkkkk
Ukhale ndi moyo wautali the dc
Don't blame d late Chilima,also him didn't expect or predict his death,koma antuwa dyela
Koma ndipo inu? Ankanenanso yekha kuti ndinkakanatu ine mgwirizano umenewu ndiye kumampanga blame nkulakwa
Zikwanje zinayamba ndi dpp
Kumalawi kulibe democracy 😮
Km ine mtima ukundipweteka azipani zotsutsa akusiza akugona mopweteketsa mitima yawanthu
Iwe bon kalindo ndiwe amene unkalimbikisa nawo ma demo ochosa jane ansa kuti anathandizila kubela zisankho za 2019 lero usokoselapo chani apa ine nde ndatopa nawe asiye a opposition apange za maganizo awo.
Tiswana bas takozeka ifeeee
tiyakhuriren
Zoyankhula zakwana kwao masamba Kwa2 masamba zikwanje Pali ponse army yake itiyo a2 oti akuchta kulemba wanyumba mwake angatani
Zoonatu waiwala chakwerayi
2020 kuma demo atavala ma glass oyang’anila mitengo mu chipiku shame 😂😂😂
Mchewa ndichomcho amafasa ukamamuthandiza koma zake zikyenda, amakhala ngati sakukuziwa
Ndipo simukunama. Ine ndine mchewa koma nduuvomeleza. Anthu amakusowetsa tulo kukubipa kupempha ndalama. Ukangowatumizila angoti ziiii....olo zikomo olo until olufuna zina....
Koma omwe munalowesa mcp munatilakwira pano ufulu watha taonani 😢😢
Gyz cibadwileni canga izizi sidadziwonepo, Kodi nthwi yomwe cikangawa amkagwila ntcito ku cipiku anayamba wawonapo izizi zikucitika mmalawi muno? Inenso nkhondoyo nde ndikuyionadi
A Bon Kalindo mwanyoza ma Bishop dzulo poti sakuchita propaganda
Blame to born kalindo,chilima,ndi mtembo
Ndipo nkhondoyo tingawine ndife anyamata osusa chifukwa tilipo ochuluka zedi
😭😭😭🤣🤣🤣ndipo Bon Zina ukaziona eeeshii ☹️
Ngati kuli anthu opepera pa dziko la pansi ndi achinyamata
Mmmmmm tigawane zigawo bas
Ndipo zowona zakeee
Mademo ku south konko osat Lilongwe ukuopa chikwanje DPP inali ndi mfuti 2011
Yiyambe basi tili ready chifukwa inu a oposition ndinu mukupangisa izi
Chikangawa party chipani chama khuluku
Chitanipo kathu the dc basi
Ayi ndithu musati nthawi ya dpp ma cadet amakhapa anthu, ndiye bwenzi mukuyamikira kuti mu nthawi ya APM mademo anu munkangoyenda mwa ufulu mopanda kuopysezedwa ngati pano. Nomwenu kusakhazikika kwanuku kwatipweteketsa ife a Malawi osauka tikuvutika kwambiri chifukwa cha inu nomwe. Munkachita mademo mutakhuta, fuel ali pabwino, mutakazinga ndi mafuta otchipa, fetereza otchipa zambiri. Ine sindingakukhululukireni nonse mwatipweteketsa iyaa.
Mmakwana big
Ayi siyeyo chakwera ,,,chakwera wangokhala nzina lokha basi koma chimene chija ndi chiwanda , ndiye kumati kuli tikusintha boma chaka cha mawa osangonena kuti basi tikuopa akongeles atenge dzikori likhale lawo chifukwa inu onse otsusa boma ndinu zitsiru musamakhale ngati ochenjera pamaso pa anthu kumaonelera zauchisiru zikuchitika ngati izi zoona inu munthu modzi yekha chakwera kmuopa komadi inu azisogoleri omwe munalamulira malawi kumangoyang'ana basi paka asilikali komwe muliko kumati apa malawi ali bwino bwino koma malawi yeah ndifedi anthu omvesa chisoni iwe amene ukuti kalindo sipaja ukati ndiwe owooopsa kwambiri uli ndi ndodo tulusanitu
Army ndipusa kwambiri yangoti chete
Mukhoza kuti thandiza mutati dziko tigawane ife kumupoto timachita bwino kale timalima President chihana atha kuti lamula
Ubwino wake wazikwanjeyo a kubvutika ndi njala to see tili pamabvuto tinyela limobzi😅😅😅😅
Please nonse ma opposition mukamabwera this mademo nose mutenge zikwanje asatitole a MCP
Mbeu yoipayi munaizala ndiinu lero, mukuyembekezera kuti achite zavwino,, munayenda Malawi yonse kupangira campaign asatanawa, bola muzingoyang'ana palibe chabwino munganene, , asiireni anthu ena athana nazo okha, inuyo dekhani basi
Big zoona
A MDF akuteteza mapiri ndizomwe anaphunzisidwa,tiwamvesese zinazi si mbali yao.Asilikali oteteza dziko ndi anthu tilibe.
Akanakhalapo chilima akanamuchosa yekha mzakeyi ndipo ndikukhulupilira akanapepesa ku mtundu wa amalawi anatilakwira zedi mcp ndi yamagazi
Zonsezi ndi chilima😭😭😭😭
Anasiila mkhondo
Wadya bomwebu amenewa mwava kuno ndi kuntchisi north
Akutivutitsa lero ndi chilima ndiamene anatiika mulamuliro wakuphau
Onse anatenga zikwanje nd mbuz zokhazokha pamoz nd asogoleli awo
Zonsezi ndi chilima amene anapeleka mavuto oterewa mmmm ana athu ali pamoto koopsa
Zoonadi chilima anatilakwila
Joyce banda anamulimbikisa Chilima.....ndi Azibusa osiyana siyana😢😢😢😢😢😢 Amvuye tipulumuseni Ife...Ana anu
Ambuye
Kma sizingapindulile chakwera o m,busa wanji okondankhondo
akupanga sokomela oka achakwela
Mhuh....😭
Koma chilima wasiya nkhondo kunjakuno
Komatu padzana paja munali nonse muli ku mademo kumathamanga ñgati gule wamkuluyo inutu ndi achina chilima munayika pamavuto ndiye muchotsane kaya muphana nonse munali limodzi
Zizawavotera ndi zikwanjezo
Iwe ulibe naweso watolela ife timaziwa zonse kuti umalandila
Busa wake wa pansi pa nyanja
Dziko lathu likufunika mtsogoleri ngati Ibrahim Traore wa dziko la Burkina Fasso basi.
Zinazi mmmh zatilaka.
Pakufunika mtsogoleri wokonda dziko lake pamodzi ndi anthu ake amdzikoli osati a mtundu wake okha ayi.
Ndikukhulupilira kuti tsiku lidzafika loteloro.
Munthu yemwe adzatenge dzikoli anthu tonse nkudzati anali kuti nthawi yonseyi?
Nthawi imeneyi , idzafika ndithu.
Chokaaaa iweee mbuli ya munthu!!!!!
Kd inuyo umakhala ufitii chani?momwe dziko likuyendelamu simukuona kupepela chonch bwanj inu ndiolankhulisa molakwika kwambiri imxeew
Kodi iwo aopposition osango nena kuti saanga nawo chisankho bwanji
Koma a pac alipo
Afiti opemphera alikodi
😭😭😭😭😭
Mcp machimo
Zafika pomvesa chisoni eee
Palibepo chamuyaya..
Mmmmmmm ndimangomva kuti mcp ndiyakupha eeeeeeeee ulamuriro wachakwera watiwonesa zinthu mulungu timenyereni nkhondoyi
Tinkangokuyang'anani mukuti ai bola atilamulire opemphelawa.....hmmm ife nkumati ngati munthu ali opemphera za genuine angakalowe chipani cha MCP? MCP ? Kulibe chi khristu ku MCP.... dambwe lokha lokha😢🤮
Iwe nde walakhula munthu wanji...wa mau Amulungu....kukayamba ...ndare eeeeish😂😂😂😂😂