One thing Im proud of this chipani is that simunakatenge ngongole ur contributing it in other way round mukalowaso m'boma muzikaganiza choncho osamangokatitengera zingongole
Koma kusapezeke wa ma regret -tu uku chipani ichi ine ndimakaika ngati chizalamulire ziko la malawi, why mwini wachipanichi anaonese chidwi kwa osauka pamene anayamba kuona mavuto ochuluka kuposa ulamuliro wa Dpp. Kwa ine malemu amene aja ndinali mmozi oti mwina titha kuonako ndati koo , kusintha koma atangokhala pang'ono ndinaona kuti zonse ankanena zija amanama , chifukwa chani ndikunena izi kuti malemu anatinamiza . Anakakhaladi kuti zikoli akufuna asinthe miyoyo ya osowa amaenela kupanga chothekela kuliuza ziko kuti 1 pepani tinakunamizani za feteleza kuti muzagula mosika pa chifukwa izi, ndimavuto ena amene anabwela otiphinja pansi pa tonse alliance. Boma chiloweleni m'bomamu anangoti chete ngati sizikumukhuza, chimene amayankhula ndi mmiyambi, kwa ifeyo ngati amalawi timapindula chani ? Ine ndinamutuluka Kuma early early zausilu ndimadana nazo. Ine sindili mgulu loyamikila munthu akamwalira panene amapanga zofoila ali moyo never so I don't think enawa angakonze zinthu ngati mmene ndinkaganizila chilima asanalowe mu tonse alliance koma nae anangokhumudwisa amalawi ena ngati ine so kwa ine nkumangoyang'ana basi but not support them as utm. What can do is kulemekeza zochitachita zao koma za sogolo labwino kuzikoli ndinachosela kale kale, anthu andalewa ai zikomo kagulu kochepa koma koipisisa. And zikoli ndilochepa than maiko ena koma anthu ovutika timafinyika chifukwa cha andale ngati amenewa kuipa ntima basi mmalo moonjola zikoli ku moyo opemphapemphawu wativuta kwa zaka zochulukawu
One thing Im proud of this chipani is that simunakatenge ngongole ur contributing it in other way round mukalowaso m'boma muzikaganiza choncho osamangokatitengera zingongole
Wow ndazikonda zinali bwino kwambiri anthu ogwirizana
Awesome
Kabambe my vote 🗳
UTM Congratulations ❤❤❤❤❤
Dinner yaphanvu kwambiri🔥🔥🔥
It was a very beautiful event
Anthu ali ndalama amwene ovutika ndi tomwefe kkkkkkkk
Kukana ma donation ndalama zochepa amatero?
Nkazi kabambe watchenatu
A kaliati ndalama alibe eti
Nkhumati ndarama kulibe kumalawi
Ndalama anthu azitenga kuti. zipani dzosauka ndi dzimene dzimaba dzikalowa mmboma😢😢😢 amalawa awa ndi mavuta enaso
Kuteroko kusauka kwanu mumapasanso anthu ena
Atanakakhala osauka bwenzi akupeleka ndalama zonsezo?
Mmm nice anthu ndinu ovuta kod mumafuna zikaneike mumangoganiza zoipa zokhazokha basi mmafuna akakugwarireni kti muwapatse katapira😜😜😜😜😜
Kkkkkkk ndipo@@fraiserkapito-yb2ob
Vuto la ku Malawi ndi kuba ndi kupempha
Zosangalasa, uwu nde timati umodzi, zipitilile pakana mutsogolo
Very interesting anthu awa alindima NDARAMA njawara amapanga chani kupezeka ndi NDARAMA chichi
Ndi business man
Njawara ndimunthu wandlama amangooneka kunyozeka ,kuyambira 2010 ameneyo zake zinayamba ku muyendera nthawi imeneyo
Very Interesting😂
Zamphavu izi osati za chikangawa
Amene akukuwawo maka azimayi akugwesa mavuto azibambo😅
Manganya wasonkha zingati?
In other Njawalayo ndidolo kwambiri
Awa akubecgawa akazamabweza akawina msazadabwe akuzatoleka zomwe anabecha😂
Alipo angapange debate ndi Kabambe the burning Spear 🔥
Yes.
God. Noone can withstand God.
Where is Kaliat phokoso lose lijaaaa????
UTM more fire
Kodi engeeneer kambalaya is the husband to kaliati?
No.
He has a beautiful wife and 3 genius kids. His wife is right there sitting beside him.
Kaliati Ali ndi mamuna wake.
Anthu ali nzochitatu salengeza inu mukhalira yomweyo yomanena anzanu kuti ndosauka
People they got money but they never said it's nough 😅😅
And kuumila anthu awa 😂😂😂
UTM woyeee
Bola apapa musakhale mukutenga ngongore kuti mukazalowa m'boma muzizaba nkumabwexa
Koma anthu muli ndalama eeh
Zinali bwino kwabasi kumwamba kulemekezeke
Makobilitu
Koma guys 😢😢😢😢 dziko ndilokondera
Anthu muli ndi zoseweretsa ndalama eti Pic mpaka ma million aaaaaa ineyo ndichitenga pa social media ndichipanga download iya😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂koma ndaseka bro
Chipan chafuko🎉
Akanayamba from 10,000 kumakweza mpaka K1m
Athu azatibela walayi
Adzabwezeletsa tisaelekedze kuwavotela awa adzatipha kuposa nkhalamo inai 😂😂😂
Koma kusapezeke wa ma regret -tu uku chipani ichi ine ndimakaika ngati chizalamulire ziko la malawi, why mwini wachipanichi anaonese chidwi kwa osauka pamene anayamba kuona mavuto ochuluka kuposa ulamuliro wa Dpp. Kwa ine malemu amene aja ndinali mmozi oti mwina titha kuonako ndati koo , kusintha koma atangokhala pang'ono ndinaona kuti zonse ankanena zija amanama , chifukwa chani ndikunena izi kuti malemu anatinamiza . Anakakhaladi kuti zikoli akufuna asinthe miyoyo ya osowa amaenela kupanga chothekela kuliuza ziko kuti 1 pepani tinakunamizani za feteleza kuti muzagula mosika pa chifukwa izi, ndimavuto ena amene anabwela otiphinja pansi pa tonse alliance. Boma chiloweleni m'bomamu anangoti chete ngati sizikumukhuza, chimene amayankhula ndi mmiyambi, kwa ifeyo ngati amalawi timapindula chani ? Ine ndinamutuluka Kuma early early zausilu ndimadana nazo. Ine sindili mgulu loyamikila munthu akamwalira panene amapanga zofoila ali moyo never so I don't think enawa angakonze zinthu ngati mmene ndinkaganizila chilima asanalowe mu tonse alliance koma nae anangokhumudwisa amalawi ena ngati ine so kwa ine nkumangoyang'ana basi but not support them as utm. What can do is kulemekeza zochitachita zao koma za sogolo labwino kuzikoli ndinachosela kale kale, anthu andalewa ai zikomo kagulu kochepa koma koipisisa. And zikoli ndilochepa than maiko ena koma anthu ovutika timafinyika chifukwa cha andale ngati amenewa kuipa ntima basi mmalo moonjola zikoli ku moyo opemphapemphawu wativuta kwa zaka zochulukawu
Khala ndi mcp yakoyo ukuuza ana
Guys is this editing guys 😂😂😂😂😂 nkhan yake ndye it😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂