MIMA IKHILE MASO VISUALIZER DIR MJOZIE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 30 มิ.ย. 2024
  • #afrobeats #newmusic #mimaikhile #afroculture
    Mima ikhile_Maso visualizer
    Shot By DirM-Joe
    Audio :Produced by Ikhile
    Mix N Masterd by Djbrown at loyal hustle the factory.
    Subscribe to my youtube channel for more creative content from ‪@Marfixmima‬
    LYRICS
    Kunja kuno akazi alipodi amuna alipo
    Amitundu yonse
    Ena achikondi ena izi anazisiya kale mmh
    Kuli ozimva aliponso oduka mitu
    Ena asukulu ena othawila pa window
    Ena aili busy kusaka ndalama
    Ena ali busy kupanga ndalama
    Kumadera kumaderaku
    Kumafunsa uzapezeka wasusa zizakuvuta
    Sizifunka phuma kwachuluka zoluma mmh
    Iwe udekhe udekhe udekhe eeh
    Iwe udekhe ukafuna kusaka
    Iwe wokondedwa iwe udekhe
    Maso ankhono (uzawaona mm mm uzawaona aa)
    Maso a nkhono (uzawaona mm mm uzawaona aa)
    Akangoyenda mothimbwidzika
    Mtima upeze nkhuku yoweta
    Sagula pa nsika uzalikitika
    Nde amuna akumabwera
    Amagalimoto akapalansa
    Onsewa tuwa nde aja
    Anabwera dzana ali ndi nkazi muzidziwa???
    Inu pachangu pachangu pachangu
    Sizigwila ndi chikondi pachangu
    Inu mwachangu mwachangu mwachangu
    Mukabwerako kubanja mwachangu
    (MUKABWERAKO AAH)

ความคิดเห็น • 26