Bad energy people kkkkkkk chomwe mmutu mwanu chimadutsa ndi manyozo basi kutanthauza kut mukulephera kuthana ndi mavuto anu. Simudziwa nyimbo inu mwayamba kumvera liti sound inu. Iyi ndi mikhatheya. Authenticity at its best no pseudo this is Prof Matumbi ndi mizu. Raspekt to the I general.
Learn from late Lucius Banda. He was able to move with time and adjust accordingly
This is nice. Reminding us of good old days ❤
Salute Nyakwawa...
😂😂😂 the art of being a good visitor is to know when leave
Love it
So clean, Legend
Tonse chilungamo tikuchidziwa kuti kwavuta ndikuvomereza.
Dj faka Vinyo watha by Mlaka Maliro. Iyi tayedzeka kaye
Your good at story telling through muzik
Iweyo uli bwino vuto ndichipan chomwe unalowa iyaa
Generation 😊
Pano tikumvera another style of music 😊
The legend is back
😅💥💥📌🔥
The flow is nice, simple and straight
Pananangongala, tilitonse watha😂😂😂
Nyakwawa🔥🔥🔥
Your welcome Anne matumbi ❤❤❤❤❤
Anatha maniwa ingosiyan bro😊😊😊
Nyakwawa is back good tune by limbani from American
Very nice 👍
Mr sono bambo a anyooo 🎉🎉🎉🎉🎉❤😂😂
Inuyo matha😂🔥🔥koma simakhala nazo serious
Watha matumbi avomereze azingodya ndalama za chakwera basi
Manyaka eni eni alipo angamvensele nyimbo ngati izi awa kuyimba simbali yawo
big up ma men ......
😂😂😂😂😂 Zopusa basi, I operation bwezani ndechan😂
Uziyankhula bho, umvesese uthengawo
Nothing you know munakulira kumudzi or munabadwa 2010
Legend receive your flowers 🌹
Pano anthu sangavele sete zakozi galu iwe sutha kuimba umkadalira Vic Marley pamtumbo pako
Simutha ndipo simunathepo
Nyakwa
Nyakwawa mwawakumbutsa anthuwa kale lawo
Awa nde manyi komaso zovunda
Anatha awa ananyaya kunyoza Anzawo nthawi imenewo instead of focusing on the future of their Career. Lero nzawo akudyerera ku Ireland
😂😂😂😂 wishing you merry Christmas nyakwawa
Tikumangitsani mukutithera bundle
😂😂😂😂 aaaa ma flow anjiso awa
very very good❤❤❤❤
Iwe udatha ngati boxer wa chikangawa
Oyimba ndi oyimba basi
Matumbi umathaa
Very great a tumbi
Yes true story
Kodi Ras Dema ndi m'bale wako?
Very very nice 👍
Nice song 🎉🎉 kmatu adawa usilikali ungakhale
🤣🤣🤣🤣🤣 kod ukukaikila zot ND slkal ameneyoo
Official announcement: Matumbi watha lelo pa 28 December 2024.
Nthano chan
Mwapala
Ine kulibe that time
Bola muzingoimba zolira zija mmh
Palibe chomwe wapanga apa
🔥🔥
History kapena Nyimbo?😅😅😅😅😅😅😅
Ndakatulo kapena nyimbo
Ndakatulo ndi nyimbo ,en nyimbo ndi ndakatulo
@@Amunandife3212koma mzosakoma satha kuimba
@Musa1828-l5d 😂😂😂😂😂
Umakwana tumbi
Big man himself
My favorite
No message on these song,mwatha amatumbi
Phalala😢😢😢😢😢
Nyakwawa
Tisanabadwe kkkkkkkkkk😅
Keep burning gee but try new styles
🤣🤣🤣🤣🤣. Umakwana nyakwawa koma kwinako tizanenabe 🤪🤪🤪
Umakwana
😂😂😂 2mbi
Siyan inu aaaa nde ndichan ichi😢
Matumba
Galu
Nthano😂😂
Ragga mofin madala 😂😂😂
He is good
But the keeper reacted quickly 😂😂
Thanks
Pano musapota MCP yomweyo inu ndachitsiru eti.
Mbolo pa chipumi!!
2mbi
Cheers 😂
Zinavuta basi luso linatha
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nyimbo zanji izi 😂😂😂 izi singafike 20 vuwuzi😅😅
Check the views now😂
Mmmm
MATUMBI AKA MAN THUMBI mwanyamula K2C kkkkkkk? chala mu tri
Bad energy people kkkkkkk chomwe mmutu mwanu chimadutsa ndi manyozo basi kutanthauza kut mukulephera kuthana ndi mavuto anu. Simudziwa nyimbo inu mwayamba kumvera liti sound inu. Iyi ndi mikhatheya. Authenticity at its best no pseudo this is Prof Matumbi ndi mizu. Raspekt to the I general.
Thambus up to nyakwawa ❤❤❤
😂😂😂😂
Muuzeni gibo peason akuphunziseni kuimba
anthu mukumverabe rubbish izizi
Matumbi oyimba wanthawi yathu koma we don't like your political games
This song can be here for hundreds years can't reach hundreds thousands viewers
😂😂😂
Ndiye poti yamenya kale 15K upanga bwanji pamenepo?
Rastaman,,embrace the new styles or hang up the boots... Palibetu chilipo apa aaaaah ...not making sense 😂😂😂
😂😂😂😂
Ngati sakukusangalatsani inuyo mungopanga zani
Father wati ma new style mukunenato ndi Matum bi aise
If u should've known u won't have commented. Only that you'll come back regrettably asking for forgiveness.
no skill
Don man himself
Umakwana