Nyamata wina wa luso , wapanga njinga ya moto ya olumala wina Ku nthini

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 41

  • @ShadreckKaleso
    @ShadreckKaleso 6 หลายเดือนก่อน +2

    Luso lapanwamba kwambiri💪 Mulungu adalitse koposa🙏

  • @HenryGulani-fq5js
    @HenryGulani-fq5js 5 หลายเดือนก่อน +1

    Ndikuyamikila padzimene mukupanga mukutitsegula matso pakuti Ku tolatola tsikwabhp pitilidzani chonde 🙏🙏🙏🙏

  • @BlessingJohnas-hu7lj
    @BlessingJohnas-hu7lj 6 หลายเดือนก่อน +3

    Mulungu amudalise Mechanical ameneyu ndipo Amupatse nzerunso zochuluka kuti apitilise kuthandiza enanso 🙏🙏

  • @AndradeAndre-ss7pr
    @AndradeAndre-ss7pr 6 หลายเดือนก่อน +1

    Deus deu tudo aos homens para dar certo, força meu irmão,colega mecânico! Vamos apoiar as boas iniciativas

  • @santosmodesto3480
    @santosmodesto3480 3 หลายเดือนก่อน +1

    Grande Homem.

  • @Maklanalfredo
    @Maklanalfredo 6 หลายเดือนก่อน +1

    Welcome back anyamata koma mukusowa this days

  • @GiboTakondwa
    @GiboTakondwa 6 หลายเดือนก่อน +1

    I am Malawian watching from Cape town aboma afufika pompano mbaleyo athandizidwa mekanikiki ameneyo Koma abomawo asapezelepo njila yoti alemelelepo paja ena ndiosusuka aboma ena

  • @JoãoChirwa-n3l
    @JoãoChirwa-n3l 6 หลายเดือนก่อน +3

    Mulungu adalise ❤ south

  • @RabeccaGama-f7m
    @RabeccaGama-f7m 6 หลายเดือนก่อน +1

    Brilliant 🔥🔥🔥🔥

  • @yamikanifischer
    @yamikanifischer 6 หลายเดือนก่อน +1

    Keep it up bravo africa

  • @marynkhata9707
    @marynkhata9707 6 หลายเดือนก่อน +1

    Zikomo mulungu wachifundo mumapanga zodabwitsa mwapanga zodabwitsa kwa mechanic ameneyu 🙏

  • @JoaoNarcisio-ig1gs
    @JoaoNarcisio-ig1gs 6 หลายเดือนก่อน +3

    Grande talentoso

  • @eunicemsuku-il2fd
    @eunicemsuku-il2fd 6 หลายเดือนก่อน +3

    Luso lanu Mulungu akudalitseni bro

  • @alicehananiya
    @alicehananiya 6 หลายเดือนก่อน +1

    Ameneyo ndie mulungu wakummwamba amapeleka luso posaona maoneke amunthu

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 6 หลายเดือนก่อน +1

    BOM talento, continuar com o jovem mestre

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 6 หลายเดือนก่อน +2

    Iiii talented man

  • @Franciscojequemosandikonda
    @Franciscojequemosandikonda 6 หลายเดือนก่อน +1

    Zili booo pamenepa agova ndi a CK.❤

  • @Lameckbwanali-l3v
    @Lameckbwanali-l3v 6 หลายเดือนก่อน +2

    Ulemelelo upite kwa mulungu

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 6 หลายเดือนก่อน +1

    Kusowa anyamata inu koma eeee mumativesa kuvesa ❤❤❤

  • @EmmanuelSambani
    @EmmanuelSambani 6 หลายเดือนก่อน +2

    Powerful message

  • @thokozanikaligwenjere5503
    @thokozanikaligwenjere5503 4 หลายเดือนก่อน +1

    Nkhani yabwino koma nyimbo ikumveka pansipansipo ikukwera kwambiri volume izikhala yotsika

  • @MalikiAlex-wn8jc
    @MalikiAlex-wn8jc 6 หลายเดือนก่อน +2

    Aboma apange plan basi ❤

  • @balancosemanalckgovate8464
    @balancosemanalckgovate8464  6 หลายเดือนก่อน +1

    Thanks

  • @HurryBeston
    @HurryBeston 6 หลายเดือนก่อน +1

    Luso lopambana ndithu, osaziyang'anira pansi chilichose ndi chotheka bola kuyikirapo mtima

  • @cictechnologies1091
    @cictechnologies1091 6 หลายเดือนก่อน +2

    Tiyamike mulungu pokupatsani zeruzoterre

  • @MalizinaKalilizo
    @MalizinaKalilizo 6 หลายเดือนก่อน +1

    Ambuye ALEMEKEZEKE KUMWAMBA

  • @LawrenceBenson-ib2le
    @LawrenceBenson-ib2le 6 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo amudalitse osat pang'ono.

  • @thokozanikaligwenjere5503
    @thokozanikaligwenjere5503 4 หลายเดือนก่อน +1

    Cholinga cha program ndi choti timve nkhani yodabwitsa osati nyimboyo

  • @HarodKaliati
    @HarodKaliati 6 หลายเดือนก่อน +1

    Ine harod kaliati ndikuonela B's kuno ku qatar

  • @Godflybanda123Godfreybandamaxw
    @Godflybanda123Godfreybandamaxw 6 หลายเดือนก่อน +1

    Zabwino zonse mulungu gwachifunfo

  • @davlinchokazinga1993
    @davlinchokazinga1993 6 หลายเดือนก่อน +1

    ❤❤❤❤❤❤

  • @LawrenceBenson-ib2le
    @LawrenceBenson-ib2le 6 หลายเดือนก่อน +1

    Baramço semanal ❤❤❤❤

  • @ramseycrown483
    @ramseycrown483 6 หลายเดือนก่อน +2

    Anayimba nyimbo imeneyi ndani nanga mutu wake ndi chiyani?

    • @balancosemanalckgovate8464
      @balancosemanalckgovate8464  6 หลายเดือนก่อน

      Tayikamo nyimbo zambiri, nyimbo yake ndi ikumaveka pakaditsa ma minitsi angati?

  • @CHIMWEMWETAMBALA-p4q
    @CHIMWEMWETAMBALA-p4q หลายเดือนก่อน

    Mulungu wa zatheka bwanji

  • @DomingosJosé-t2m
    @DomingosJosé-t2m 3 หลายเดือนก่อน

    Zilibwino

  • @zamadulasimango6972
    @zamadulasimango6972 6 หลายเดือนก่อน +1

    Ulemu wake mechanic. Njinga ili ndi reverse gear sizophweka.